😂😂😂😂! Koma ai zikomo chakwelayu wabwelesa mavuto akuluka coz siutendele uwu apa tikuti ndi comedy koma zikuchitika live live ishiiii fans ikuvutika ndithu .
Che Mandota osamangojoina anzanu muzifunsa kaye. Anzanu adajoina kumaliza maliro a eni nkumati sister wanga wapita anthu nkuwaitanira pa mbali nkuwauza kuti amwalirawa ndi amuna. Then adangosintha chuni 😂😂