Oyenda ndi lupanga nayenso adzamphedwa ndi lupanga..ndipo sizodabwitsa kumphedwa kwa munthu ameneyu..ntchito zake zampangila umboni..panopa alinso ku gehena..
Ulemu wanu bwana its a sad story dziko lonse la pansi lingoyang'anira kuphatikipo maiko onse a chislamu osapangapo kanthu pamene maiko achikhrsitu onse akuthandiza Ayuda inna li llah wa inna ilaih rajooon
Ndimene structure ya government yawo ilili sizidabwitsa mayiko ambili ena amapanganso choncho mwachitsanzo iran kuli prezident komano supreme ruler ayatollah ndi amene ali pa mwamba pa zonse
@@alfredbanda1693 Ndakumvetsani boss; olo ku England kuja heard kuti Prince Charles has no power to interfere ndi za politics komano zamipingo or ma charity activities and sangalamule dziko kuti lilowelele nkhondo only Prime Minister ndi amene amapanga ziganizo. It's crazy.
@@user-frasernamaona14 paja don't forget kuti prince or queen amakhala nkulu wakhonda like mene alili chakwera but yes mphamvu zimapatsidwa kwa pm koma prince akhoza kupanga declare but not implementing it. Only pm can both declare and implementing it
Example wapeleka kale kuti,,,Zimbabwe ibwele kumalawi ndikumalanda Malo a Malawi,,,kodi mungakhale Chite poti inu Achristu mulibe mwano?Nanga patapezeka gulu losakondwa ndizimenezo ku Malawi,,,,,Kodi gululo likhoza kukhala la zigawengaso?kapena poti ndigulu la Chisilam?
Israel inagwilitsa ntchito drone ya militaly nkuitumiza ku Beirut Lebanon mkatikati mwa dzikoli ndipo Israel intelligence Monsad inkamuwerenga ma movement Ake...mpaka anamupenza drone inalowa pa window nkuphulika nkupha onse mchipindamo..ndipo Israel inati onse Adani Ake ndi oyenda akufa..kumbukilani Israel Ili ndi most intelligence in the world
We really appreciate he really gave us the good information but he must stop talking side as a good journalist. Kufunika asiye kumanena kuti "HAMAS ndi zigawenga" it's not good ndi anthu amene akumenyera ufuru mu dziko lawo inunso mukudziwa
Example wapeleka kale kuti Zimbabwe ibwele ku Malawi kumazalanda malo A malawi,,,kodi Malawi ingakhale chite?nanga patapezeka kagulu kosakondawa ndizimenezo,,,gululoso likhoza kukhala la zigawengaso?kapena ayi poti awa ndi Asilam amwano?you need think before you talk,,,that's why tikuti enanu simukudziwa chifukwa chomwe Israel ndi parastine ikumenyana,,,chomwe mukudziwa ndichoti Hamas inakaphulitsa mu Israel pa 7 October koma simukudziwa kuti chifukwa chiyani,,,,