Bro @ Vincent the minimum resolution i a can get is 360 p koma ma screen akuluakulu sizikumaoneka bwino kwenikweni is there an opportunity kuti tingapeze atleast 720p or 1080 even 4k so much the better.. thank u
Ulemuwanu,ankasa. Pempho...ma player mukuthamanga kwambiri, balance your speed please. Mibawa pelekani nthawi yabwino yokonzekeretsa a lendo, provide equal vedio quality to all. Don't forget you're targeting hard to reach areas,beyond eye site.