And all of you guys are so special, real talent iyi guys! Iyiyo iyi ndi talent mbambande, you are touching many young souls. Bravo, lots of love to you all.
ati uyu ndani, SELINA she is Tadala ameneyo analinso chibwenzi cha BIMA kkkkkkkkkkkk henewe komano its behind the seen Sukuzwa iweyo Selina , mulibho guyz
Nkhan ya min bus yo ikumandipasa chidwi kwambir😂😂😂 My wife is a Doctor ndkuvuta kwa zinthu pa malawi ineyo chete ndimayendesa min bus yathu . This is real life pa ground the youth are living in denial.😂😂
Khaniyi kut ipitilile kukoma, Selina ndi hannareen akuyenera agwilizane chochita kut amukhawulise bhima alinukhe dziko avutike then azabwereranenso ndi Selina ngat banja ndipo mapephero aja azalowe pakat pawo kut bhima azakhale okhulupilika pa Selina. Then mulongo wa Selina azakwatilane ndi hannareen kut chilamu cha selina ndi hanna chizakhale chikupitilila. Inu mukuwona bwanji gys