😂😂😂😂😂😂😂 Bhima nditambwali mumatha guys mwatipatsa ka film komaliza chaka chino kanali bho heavy hana Mbambande selina befiya mlonda wadyela ankolo abima a Dc makwana guys nose mwatenga mbali mu ma film ose achakachino ya zama love❤😂❤😂😊😊😊😊
Koma musalekere pomwepatu, kungoti mwina tidziwe ngati muli ndi account special for such series, mwina mkumaponya limodzi limodzi kanganyase, just thanks giving and pushing such works ahead. Put some details please.
Mmmmm koma guys it must have been tiresome, but you made our days. It's a masterpiece. Can't wait to see you guys in anything you are planning to do, bravo guys!!😊
You've had a very good run guys, and I've been glued to this RU-vid channel not to miss an episode. But, are you really impressed with the ending? Ndikuona ngati mukaipangenso bwinobwino
Eeeeh koma ma series amenewa taphunzira zinthu, tadzudzulidwa, tadziwa, takondwadi kwabasi, aaaayyaa ambuye akudalitseni a Selina, Obethia, Obima, Odankeni, and everyone of you.
A MC ati mindipatse ndalama zanga 😂😂😂 this was really nice guys thou mwatisiya mmalere koma woow it has been a nice episode since day one ❤ Selina umakwana
Komaso, bwanji tisamanene finale, mwina we could leave some room for continuation subject to whatever factor. Ndiye ofunika kuyesa kumapeza mawu ena oti yatha but...anything can happen....may continue or not. Kaya tiphunzitseni zimatani pa point imeneyiyo.
Eish .... Iliyonse mumahita ma guy.... Mwandisangalatsa from the beginning ... Where did u get this courage Selina😂... Bhima umatha.. Koma berthia iweyo mkatundu eishh