Character ya Selina in the play ndi yoopsa and such women amawameneyera nkhondo ndi Mulungu. Amakhala pheeee sikuti amakhala kuti apusa koma kumakhala ija Amati khala chete nkondo ndimenya ndine. The repercussions which follows are always dangerous. Azibambo let's not take advantage of such innocent women one day is one day God will fights for them.