Oimba kungoyamba ndale anthu amaku tulula bas apapa amukonde dan lu ndi a DPP bas azipani enawa sangamukonde Dan Lu tsogolo loimba waliononga ekha ndiwe oimba wabwino nyimbo za ndizokoma km mawanga a DPP wobasi ndamene awononga zinthu sorry bro
Kuimba ngati kuli Mbali yake sangasiye Koma ngati isali Mbali yake Asiya komaso politics ndiyoipa amapha luso la oyimba chifukwa kuyimba umafunika uzosangalatsa anthu onse ndiye ukapita Ku politics zimavuta Kuti zitero chifukwa Mbali yomwe iwe Uli pankhani ya politics ndikomwe anthu amakusapota kwinako ayi so oyimba Aku Malawi musamalowe kwambili kumeneku luso limantha chinsazo ndi mkasa komaso tikapita kuzambia organise family nthawi ya edigar Lungu anatheratu chifukwa anali Mbali inayi panopa sindikunkhulupilia ngati anthu ambiliachipani cholamula angavere nyimbo Za Dan Lu