Тёмный

Zimene Akunena A Bon Kalindo Kuti Tisamapeleke Misonkho Ndi Za Sataniki - Charles Ben Longwe 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 29 тыс.
Просмотров 6 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox, Ben Longwe says that Bon Kalindo’s remarks about not paying rental income taxes are satanic and go against biblical principles. He also criticizes the Democratic Progressive Party on various issues in this pro-government audio.
Pa Nyasa VoiceBox, Ben Longwe wati zomwe Bon Kalindo ananena zakusapereka msonkho wa renti ndi za satana ndipo zimasemphana ndi mfundo za m’Baibulo. Iye akudzudzulanso chipani cha Democratic Progressive Party pa nkhani zosiyanasiyana mu audio yomwe imalimbikitsa bomayi.
#malawi

Опубликовано:

 

20 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 192   
@BertharrySecurity
@BertharrySecurity 2 месяца назад
Kape ndiweyo Ben longwe mbuzi yamnthu
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад
Ben Longwe ndikupemphe chinthu chimodzi, ukamayankhula zopusa zakozi usamatchulepo Mulungu. Usamaone ngat maganizo ako ndi maganizo a Mulungu...
@OmanSichone
@OmanSichone 2 месяца назад
Yes, atsachure za mulungu
@AffickChaona
@AffickChaona 2 месяца назад
The DC Bon kalindo mwana opsa kwambiri ❤❤❤
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад
Ben longwe kulakhula mobveka bwino macadet onse ziiiiii!!!! More fire beni
@HappinessKapombeza-ut9mo
@HappinessKapombeza-ut9mo 2 месяца назад
Makadeti ake ati GALU iwe?
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 2 месяца назад
Zaonekelatu kuti iwe ndi iwe chitsilu chachikulu kwambiri. Bingu sianadzipatse yekha dzina anapatsidwa dzina ndi anthu chifukwa Cha dzabwino zomwe iye anachitila Malawi. Ndi iwe munthu opanda nzelu Siya kutchula dzina la Mulungu pokamba zombwambwana apa
@roseshema7010
@roseshema7010 2 месяца назад
Ndpo inu angolankulaso ngat akufa mawa bwanji 😅😅😂😂😂
@thulambale2836
@thulambale2836 2 месяца назад
God bless you Ben longwe. Galu Za DPP ndi bon kalindo ndi azizake
@CourageSydney
@CourageSydney 2 месяца назад
Aaaaaa ineyo sindipeleke misonkho zizithera ❤kwanukoko achewa
@jumahanaph2613
@jumahanaph2613 2 месяца назад
Machende ako ben longwe
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m 2 месяца назад
Choka satana iwe bola DPP inangomumanga Bakili Muluzi lero lino tikumuona, nanga anganga akowo atiphela SKC 😭😭😭😭😭😭 sitizamuonanso for ever ana asatana inu, kumusiya nkazi ndi ana pa umasiye mulungu akuoneni, ndiwe opanda nzeru Ben longwe
@paulgodfrey3361
@paulgodfrey3361 2 месяца назад
Anthu anga akuonongeka chifukwa chakusaziwa! Okufa saziwika a Ben Longwe even inuo you can die kungomaliza vn yanuyo ..
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 2 месяца назад
Ben longwe ndikatundu kwabasi😂,,,,, more fire Mr Ben
@DalisoulThom
@DalisoulThom 2 месяца назад
Ukamalankhula uzivala kondom ukudandaula zakumangidwa kwa bakili ndi chifukwa Chan munapha chilima poti ndiamene anakulowesani m'boma
@ibrahimbamusi109
@ibrahimbamusi109 2 месяца назад
Kape wamkulu ndi Ben longwe odya mwana wake
@martinmoyo4211
@martinmoyo4211 2 месяца назад
Good Ben Longwe
@MosesTangwe
@MosesTangwe 2 месяца назад
Chitsilu mwa zitsilu zinazake ndye chimenechi,anthu anasya kumvera ma audio ake opepelawaa
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo 2 месяца назад
Mbuzi iwe Ben Longwe..... Tapita ukayankhe mulandu ogwirira mwana wako south Africa
@FosterChilumba
@FosterChilumba 2 месяца назад
Chikangawa Ben Longwe ukumvesa chizoni Koma ndalama ndi SATAnadi eeeti
@HypeGallery-ur9xd
@HypeGallery-ur9xd 2 месяца назад
Ben ndilibe mawu nanu ambili koma ndingoti mantchende anu a ambiance ndi chakwela yemwe ukutiona utsilu galu iwe😢
@maclouddickson
@maclouddickson 2 месяца назад
Mbudzi ya munthu Ben Longwe
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 месяца назад
Telera nyani abwana🔥🔥🔥
@MustaphaChimangeni
@MustaphaChimangeni 2 месяца назад
Ben lonyo ine sindinkadziwa Kuti ndimphawi ndamuona dzulo face to face 😂😂😂shame I believe an still promise this would ben lonyo adzafa osauka ndani angakupedze iwe olopogona ulibe shame we know Kuti wapatsidwa chilango choti uzinyoza opposition especially DPP pofuna kufuta milandu yako poti ulibe kolowera panyini pa malemu mayi ako galu iwe
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 2 месяца назад
Nkhumba zija adaba Ben longwe ku farm kuthawira ku Malawi bwana akuvuta kuno
@PatrickChirwa-cv5cd
@PatrickChirwa-cv5cd 2 месяца назад
Ben Longwe for once ukunena zoona. Mombera University ilikuti. Anja Dan Lu bwezani ma salary auphunzitsi.
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад
Ndi zitsiru izi zongofuna podyera a
@freemanconwell7286
@freemanconwell7286 2 месяца назад
Ben Longwe amandinyansa kwambiri masiku ano and sindifunanso kumamhmva pa ma platform ngati yanuyi
@kanjibamumba4963
@kanjibamumba4963 2 месяца назад
Ben longwe ndi mbuzi basi here in Lusaka Zambia
@LexzoMagwax
@LexzoMagwax 2 месяца назад
Umuuze Ben Longweyo ALIBE NZERU ndipo azapanga regret kwambiri
@ChrisSambani
@ChrisSambani 2 месяца назад
Panyapako Ben longwe....za ifa ya kuchikangawa bwanji
@mijerimasiye7310
@mijerimasiye7310 2 месяца назад
Iweyo longwe ndi Bon kalindo kape ndindani mesa kape ndi iweyo Longwe,Longwe yankhula ngat ndiwe mmalawi osayankhula phrase
@giftnyirongo-ey3qy
@giftnyirongo-ey3qy 2 месяца назад
Pepani bwana mademo Alipo
@paulmgombebanda-mr19sate
@paulmgombebanda-mr19sate 2 месяца назад
Inetu ndinkakutenga wanzeru ndipo Mulungu oweruza olungamayo akuweruze iweo ndikupanda nzeru kwakonko. Let Bingu rest in peace, iwe osangodya ndalamazo bwanj osati uziputira mkwiyo waoweruza Olungamayo..
@MichaelJannah-hn9qv
@MichaelJannah-hn9qv 2 месяца назад
Ben longwe ndi galu uyu
@FisherAction
@FisherAction 2 месяца назад
4 years yonseyi anali kuti ayamba izi chifukwa apha Chirima wopanda nzeru iwe mbuzi yamunthu
@roseshema7010
@roseshema7010 2 месяца назад
Ndpo inu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 2 месяца назад
And ndasiyira panjira kunvera
@ChristopherMunlo
@ChristopherMunlo 2 месяца назад
🎉zopanda nzeru
@EmilyBanjachikwatula
@EmilyBanjachikwatula 2 месяца назад
Machende ako ben chitsiru cha munthu udzingodya ndalama za magazizo mmmmmmmgalu wa chabe chabe holy ghost fireeee
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад
Ben musafooke bonikalindo ndi chisilu uyu iwe ukunena zazelu
@UseniMailosi
@UseniMailosi 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂
@HamissMaidaz-x4h
@HamissMaidaz-x4h 2 месяца назад
Chitsilu ndiweyo galu iwe patumbo pako ndi beni longwe wakoyo panyapako
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
Chisiru ndi amako ndi abambo ako anakubala patumbo pako
@Andrew-nz9sh
@Andrew-nz9sh 2 месяца назад
I use to listen to ben longwe but now I don't think he has heart of human being
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
He have lion heart
@ThomasMaxwell-ks7yi
@ThomasMaxwell-ks7yi 2 месяца назад
Zoona auze telela nyani❤❤
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 месяца назад
Kuba konseku mmabomawa Bakili Muluzi is a pioneer patriotic Robber of our all president of Malawi Robbers
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 2 месяца назад
Abwana ben longwe mudapereka nsonkho pogwilila mwana wanuyo, tikufuna report ya ndenge palibe kuyamikila chakwela wanuyo before report iwe ben ngati wathawa kuno chifukwa chogwilila mwana wako usachuluke nzeru chikanapanda izo bwedzi udakali kuno
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d 2 месяца назад
Ben longwe vuto siyiwe ukuyakhula vuto ndi amako anakubala iwe mwana wokunyamadzi iwe mwana wokula mapilikano wadyela iwe wopanda fundo iwe wopusa iwe popeza ndalama zaphweka ku mcp tiyeuwa dyele, mulungu akulange ,akutembele iwe mwana wokoza pa mphatsa iwe
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 2 месяца назад
Iwe misala imeneyo Ben longwe
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 месяца назад
KOMA BAKILI MULUZI NDI YEMWE ANAYAMBITSA KUBA KUBA LONSEKU MPAKA LERO.PIONEER WA MAPULESIDNT ONSEWA AKUBAWA NDI A BAKILI MULUZI.SO WAKUBA NDI WAKUBABE.
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 месяца назад
Ben Longwe Ma ARV akumulamula Mopusa, Chozelezeka Ichi
@EDSONKAMVAZAANA
@EDSONKAMVAZAANA 2 месяца назад
Kodi mulungu wake UTI amene mukumugwiritsa ntchito aben longwe, mulungu yemweyo akuwonetsani inuyo ngati muli achirungamo ndi boma lanu.
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 2 месяца назад
Iwe usatiphunzitse kutukwana wamva Ndiwe galu kwabasi Chitsiru cha munthu
@GiftFrancesco
@GiftFrancesco 2 месяца назад
Mbuz iy Ben longwe
@AmiduKachingwe
@AmiduKachingwe 2 месяца назад
Patumbo PA Ben longwe galu iwe
@chrisneySwanepoel-yu5vd
@chrisneySwanepoel-yu5vd 2 месяца назад
Ben longwe ndiofoila iwe Batry kalindo uja ndi dolo osat kape ngat iwe
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 месяца назад
Beni Longwe ndalama za magazi ukudyazo usavuka nazo ndi dzikotu ili uziona
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 месяца назад
Tikupita kumademo madzila ako iwe wamatha iwe. Tiyamba kutenga ku mcp usadandaule galu iwe😊
@Aisha-db6ds
@Aisha-db6ds 2 месяца назад
Uyuso ndiye uti
@HappinessKapombeza-ut9mo
@HappinessKapombeza-ut9mo 2 месяца назад
Kayatu abale inu?
@HappinessKapombeza-ut9mo
@HappinessKapombeza-ut9mo 2 месяца назад
KKK.....KAYATU,MBUZI IYI YACHOKA KUTI KAYA?
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
Achisiru awa
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 2 месяца назад
Aise ukuyankhula zaifa yazanu bwanji iweyo ukuzitenga ngat wamuyaya machende ako unamupha chilima ndichakwerayo unapanga plani usiye kuyangulako uzikapanga uhule ndi kazi wako wanva Mai yolamu ndi fit machende ako Ben
@GodfreyRchizombwe
@GodfreyRchizombwe 2 месяца назад
Nawenso uzikamba zanzelu ngati wankulu mesa kufa ndi nthawi,akupasa zingati kodi iwe
@HarryKandani
@HarryKandani 2 месяца назад
Panga zako Ben Longwe
@ClementbWatches
@ClementbWatches 2 месяца назад
MMM uyu Baibulo lake lit agwilisa ntchitolo. Iwe Ben kape wa munthu sudamve kut musamaonjezele Po nkhomesa nsokho. Mbudzi ya Garu . Onyenga Mwana ozibelekela wekha.
@PreciousChlima
@PreciousChlima 2 месяца назад
Ben longwe alibe ma nyumba kuno ndipo ndikape 😂😂😂 ndalama zikuphani inuyo,, angakunyengereren ndindani
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
Mwina ndi misala yomwe.we ikumuyamba ben longwe pita kuchipatala akakuyedze isanapitilire pansana pako ndi cakwera wasatanic yo
@BlueTicksound-ow4fq
@BlueTicksound-ow4fq 2 месяца назад
Mau abwino maganizo opusa anati kaisala ipite kwa kaisala yes mfuso kodi misokho amangopereka ndi zopusa zomwe? Ndiyetu munuwake wa dziko lino ndila mulungu tisalipire. Nyumba wamanga wekha cement odura yomwe timalipira pugurayo wachepa?
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 месяца назад
Galu iwe Ben Longwe
@LottiAffati
@LottiAffati 2 месяца назад
mbuzi yamunthu iyi inu Ben longwe nde nkachaninso
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад
Iya tizipereka misokho yachani koma chakwera ukufuna uzitidyerandarazathu sataniki iwe chakwera ni beni longwe
@StephanoMaganizo
@StephanoMaganizo 2 месяца назад
Iweyotu unalandila ndalama mtaoneka ukulankhula zopusa chikangawa iwe
@ApsChap
@ApsChap 2 месяца назад
Kape Ben longwe
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад
Chitsiru wa chabe-chabe iwe Ben Longwe
@OmanSichone
@OmanSichone 2 месяца назад
What about Chinkangawa iwe?
@fosterkatemba1269
@fosterkatemba1269 2 месяца назад
Mbuzi yamunthu Ben Longwe khala chete
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 месяца назад
Ben longwe machende ako, alipo amene anganyengelere iweyo unathawa kuno ku south Africa chifukwa cha uchisiru wako umphawi wako ndalamazo uzingodya
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 2 месяца назад
Ben longwe machemde abambo ache😢
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 месяца назад
Kodi benlongwe umazitenga iweyo ngati ndani GALU iwee anakupasa zambiri eti koma Kupha anthu bas
@IbulaKeneth
@IbulaKeneth 2 месяца назад
Wadyesedwa chibazi
@SprianoJeke
@SprianoJeke 2 месяца назад
Ali ndi Mbali awa anthu akudya ma banz Ife tikupita pa msewu zopusa zakozo ukoo
@JamesDaud-jz7uq
@JamesDaud-jz7uq 2 месяца назад
Kape uyu,,,, zomwe akuyankhula ndi za ziii zikuoneka kuti chibanzi chikugwira ntchito
@AdamzChirwa
@AdamzChirwa 2 месяца назад
Wumanena zona ben longwe zikomo kwambili pitiliza Dpp njakuba yinaba bomala UDF
@PreciousChlima
@PreciousChlima 2 месяца назад
Pajatu a longwe munanena kuti mukukwera ya boma ife sitikukupanga sapoti
@BMDMasulani
@BMDMasulani 2 месяца назад
Ben ndimbuzi umafuna Malawi ...adzivera iweyo aliyense umati ndioyipa wabwino ndiweyo? Ukulimbana ndi maliro uchitsilu Bingu wa munthalika anali munthu wabwino osati agalu anzakowo
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 месяца назад
Misala basi Ben longwe
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 2 месяца назад
ABen Longwe mnafuntha...mungosiya
@OmanSichone
@OmanSichone 2 месяца назад
Yaah, because of money.
@LisaKamanga-l3z
@LisaKamanga-l3z 2 месяца назад
Ngati mai ake a Ben longwe ali moyo muuzeni kuti nyini yaamake
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 месяца назад
Mega farm ake atiwo manyi ako iwe kodi von kalindo amayakhula live nkumamuona akumangidwa nkumamuona kodi pamenepa dolo ndi ndani galu iwe unayakhula uli kunja machende iwe
@EDSONKAMVAZAANA
@EDSONKAMVAZAANA 2 месяца назад
Ndikuwona ngati munthuyu alindi vuto la mu bongo akumwa mankhwala osadyera chifukwa born sakuti Anthu asalipire misonkho ka anthu, alipira misonkho komaso akufuna adzigulasoa stiker. Anthu adziripira misonkho kangati? Chitsiru mburi
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 2 месяца назад
Ogwilirira team
@grantnailuwa
@grantnailuwa 2 месяца назад
Azikatolela kwawo ameneyo zopusa basi
@JohnsonMaulana
@JohnsonMaulana 2 месяца назад
Ben longwe 😢
@ScrarNation
@ScrarNation 2 месяца назад
Kodi kape uyu zoti anatha samaziwa
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 месяца назад
Kutukwana ayi apa baben longwe naoso ndi uflu wawi wolankhula
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft 2 месяца назад
Ngati Pali chisilu pa dziko lonse lapansi nde ndi chi Ben longwe nzelu chilibe ,ndi chisilu chokha chomwe chingamalimbane ndi okufa may the Saul of late Bingu continue resting well,pa thako pako Beni longwe. Alongwewo anakango bunyura than to have a useless boy like you,ukukamba zopepesa chifukwa ukuziwa Kuti uzapepesaso Kwa Malawi Kuti ndinka sapota chakwera ndinkalakwisa pepani Malawi Za misonkho zakozo ndi ka chakwera kakoko simukuziwa agalu inu
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 2 месяца назад
Pamsundu pako
@MussahJenala
@MussahJenala 2 месяца назад
Mwe wana angangawen mwasaalile paliphwisilyaolwo
@princenyumwa2550
@princenyumwa2550 2 месяца назад
Machende onyala abambo ako galu iwe
@lacksonsiyadi943
@lacksonsiyadi943 2 месяца назад
Malawi muno zoonadi satana anaenda chokwawa😂😂😂😂
@LeonardChinomba
@LeonardChinomba 2 месяца назад
Panyelo pamako iwe Ben longwe
@AkibuMdala-sr1dy
@AkibuMdala-sr1dy 2 месяца назад
Ben longwe nose akwanu machende ako pamosi ndi chakwerayo
@jeuzywandasigner4908
@jeuzywandasigner4908 2 месяца назад
and ben longwe by now he should be in prison for 23 years 🤣🤣🤣🤣 wa mfana ndipo asakaike agalu awawa akaluza chaka chikubwelachitu azathawa ndi n'tudzu akuyankhulazi
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 2 месяца назад
WaSatanic ndiwe ndi Chakwera wako
@amosphakira7936
@amosphakira7936 2 месяца назад
Iweee ndikape kwambiri mulungu akukanthe ndithu . Ukuchula mulungu paxinthu cosayenera ambudxi yamunthu
@roseshema7010
@roseshema7010 2 месяца назад
Komaso mu ndale osamatchulamo mulungu plz
@MarkGonda-qr4vm
@MarkGonda-qr4vm 2 месяца назад
Inu mwathana ndi sks amene anakuthamdizani kutenga mwampitisa kuti sks
@smikemw7
@smikemw7 2 месяца назад
blind mind, you think like a fool U think like all malawians ogona eti we wake up now my bro
Далее
A DPP Kwawo Ndikufuna Kudzaba Mu Boma - Ben Longwe
35:40
Ine Ndi Activist Wa Boma - Charles Ben Longwe
23:33
Просмотров 3,5 тыс.
Charles Ben Longwe - Malamulo A Democracy
27:18
Просмотров 1,6 тыс.
Bon Kalindo Mzeru Alibe - Isaiah Sunganimoyo
10:06
Просмотров 7 тыс.
CRUISE 5 WITH BYSON KAULA - DEATH ROW SURVIVOR
50:51
Просмотров 99 тыс.