Ndiye muzidya school yomweyo 30 years Ku school zaka zodyelela 10 kumaganiza mwa fast Ada a wawa amaxiwa life chiganizo pompopompo azungutu amaphuzila komanso akupangazina sonoifekuno akut Ku college mpaka 30 years kubwelelamo kusowanso nchito ndiye mwapanga Chan look shap ikufunika a papa kuchangamuka
Ukunama iwe ku church masiku ano ndekuri ndaramaka achina bushiri sukwawona iwe kt aremerera mumpingo iwe kumarawi ndiziko rosanva kurimbikira kwacha yake yomweyo ikugwa deiry kuremera kwapampanje nde kt waka khwimira kayetu apobi uzingo zunza thupi rako ndi hard working mpaka ukarambatu auzeni anthu chirungo akuru
Business yopanda yesu palibe yosatheka musaname yokhayo ya kwa Bushiri itheka paja ndi miracle money 😂😂😂Mwana wa joka iwe lero ukuti tisiye za mulungu mmmmmm