He's real UTM....sakulimbana ndikuzinamiza kumagula nsalu za DPP or za UTM nkumaveka zigoba...iyeyu ndi mfundo zake zokweza Malawi 🇲🇼 typically SKC thinking....akuchita kuonetsa kuti SKC amamukonda ngakhale anali ku Blue camp! Kusiyana ndi enawa ochita kudzidzimuka kunamizila, kuzinamiza, komaso kuwanamuza abwana 😂😂😂😮😮
A😂😂😂 ongofuna kugwiritsidwa ntchito ndi chikangawa awa ndale zaku Malawi zomvetsa chisonitu zolankhula ndijungoti mpulumutsi uja wafika Soasidwe mpata 7 out of 100% Kufuna kusokonedza mitu a Malawi basi