Тёмный

ZOMWE VICE PRESIDENT MICHAEL USI WAYAKHULA KWA MA VENDOR A PAZIBOLIBOLI LERO MU NZINDA WA BLANTYRE 

Makosana
Подписаться 87 тыс.
Просмотров 29 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

6 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 114   
@KayMohamed-g7d
@KayMohamed-g7d Месяц назад
Kodi maesa pafupi ndi immigration bwanji wosapita kumeneko akulimbana ndi malo woti kulibe mvuto ambiri
@SophieMbengo
@SophieMbengo Месяц назад
Tidyatuu Koma MCP ikuchoka basiii,kudya ndiulere
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Месяц назад
Amalawi ndalama zo akunena manganya mugulisa moyo ziko ana anu pamutengo osika. Komaso muwuzeni kuti timaowoza zisiro zaboza kuti ziziwike uchisiro wake. Palibe andale amene amatuma anthu kuti aziwowoza. Palipose pamene mungapite nkhani ndingongole ndikuti amalawi akusangala ndingongole. Amalawi please ganizani mozama atsogoleri ndi fundu less ya ngongole. Munthu wazeru sayika ndalama pasogolo koma amapereka zofunikira kwa anthu osati ndalama. Ndalama simulandila nose kuma school ithandiza nose chipatala chithandiza nose misewu chakudya osati ngongole ndikupupuluma kumeneko
@victorkachepa3515
@victorkachepa3515 Месяц назад
U Vice winawu. Hopeless. Becoming NEEF officer zoona?
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Ndipo ndizoonadi ambuye atithandize
@Nga-y1k
@Nga-y1k Месяц назад
Gwilani ntchito basi
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Kodi osamuthibula bwanji kape ameneyu
@HarryKandani
@HarryKandani Месяц назад
Tapitani ku immigration bambo a sikono
@SymonZemben-gd3ne
@SymonZemben-gd3ne Месяц назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤸🐐
@Anti_social_938
@Anti_social_938 Месяц назад
Very well said Mr Vice President Sir.. Mumakwanira
@andreabanda7838
@andreabanda7838 Месяц назад
Malawians let’s be careful.
@LidyaGoodson-fb4tt
@LidyaGoodson-fb4tt Месяц назад
Amen
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Apanga bwanj tsogolo mmayesa munkat mupereka ntchito 1 million nde mumati adzitani
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu Месяц назад
Muziyenderanso kumuzi muone umphawi not ntown mokhamo.
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 Месяц назад
Zachibwana
@user-kt2yc6dp7q
@user-kt2yc6dp7q Месяц назад
Please bwana kudya ndi ulimi tindalamato pitisani Ku fertilizer tigule fetereza mochipa osati k 100,000 thumba limozi
@gkay-striker
@gkay-striker Месяц назад
Nde zikwana anthu angat ndalamazo amalawi osapusa
@enockkanyerere784
@enockkanyerere784 Месяц назад
Be careful Malawi
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Месяц назад
Chinjerani akufuna kukupusitsani Ambuye!
@gearardphiri6904
@gearardphiri6904 Месяц назад
Nice said Mr v president
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Месяц назад
Azingoyendera osati kuwauza kuti avotere mcp. Mcp ichoke basi
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 Месяц назад
Bambo athu aShaker,Mr Odilo &Gift kazembe ndskuonani😄
@BusumanNzengeza
@BusumanNzengeza Месяц назад
Ntchito 1 million zija zili kuti chisankho chisanafike other wise dpp my vote
@mayachikadewa7551
@mayachikadewa7551 Месяц назад
Mmmmmmm ndale
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t Месяц назад
Tapitani kuchipatala mukawawone anthu odwala amene akusowa mankhwala osati kukawona ogwila nthito ayi
@BrightonKennedy-jd6fl
@BrightonKennedy-jd6fl Месяц назад
Iwe usi ndi chipani chako cha MCP ndiweso ukumatuma achinyama kumawowoza mumizinda ndi miseu,powapasa ndalama. Ndiye ukuti chiyani
@LottiAffati
@LottiAffati Месяц назад
koma the DC uja nkatundudi sizija amanena zija izi, kampeni yavutadi pamalawi end kubomaku kuli dola zoseweretsadi eti
@lukepangani1373
@lukepangani1373 Месяц назад
Dr utsi he is busy collecting data good job
@PreciousHenderson-qc1hq
@PreciousHenderson-qc1hq Месяц назад
Tidya ndalamazo koma your fired
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
Atsanakhadzikike usi watsegula kare file kuva udindo kukoma akuti
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Месяц назад
Afunseni kuti nchifukwa chiyani izi zabwera nthawi yino kuti muonese kulephera kwa chilima ; voti ndi mumtima
@RobertNyaude
@RobertNyaude Месяц назад
Kachibowo malunga ndakuona braz kkkk
@musasiyama9423
@musasiyama9423 Месяц назад
Vice president wopenga uyu, alibe mfundo
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m Месяц назад
Abazanbili akufna atpake Ife azatnamizle pa m'mawa Kut tinadyanawo
@user-jb5hr4rz2s
@user-jb5hr4rz2s Месяц назад
Pano nde akuti ndalama zopanda chikore mesa iyeyo akupanga kampeni ,si booza ana anthu azavutika kugula zinthu ,tikapanda kusamala
@Brihippo
@Brihippo Месяц назад
Akuti fuso not ndemanga bwanji Kodi
@YamikanKhofia
@YamikanKhofia Месяц назад
Mwajijirikatu
@emilynthite6545
@emilynthite6545 Месяц назад
Kumbali yanu mukukwanisa koma mukafikenso kumapasipoti kulinso mavuto
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi Месяц назад
Ndalamatso ndizatu amalawi osakana landirani koma osapanga mistake kukafotera mcp please anthu awa akutipanga chikole .awononga kwacha alibe mphanvu pano
@praisechikuni8200
@praisechikuni8200 Месяц назад
Chaka cha mawa wina alira
@giftblack7690
@giftblack7690 Месяц назад
Mupusa kwa Nthawi yochepa yomweyi ndithu kkkkkkk tabalandilani muzawavoteleso kuti muzililabe ndi mavuto omwe akufuna akuyiwalitseniwa timiyezi tochepa tomweti kuti muzalile kwa zaka zinaso 5 😂😂😂😂😂😂 ine pheee kuno kupanga ndalama zanga
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Месяц назад
Just listen to him he said July and August 😂😂😂 which July?
@YamikaniMwale-bo7cv
@YamikaniMwale-bo7cv Месяц назад
This type of leadership is nonsense,,,where were you in the previous years,,,mwatifuna pano??? I can't forget and forgive you guys,,,manganya stop blind folding malawians plz,,supervision yomwe mukupangayi is full of fault finding not rectification,,
@OliverChimsewu
@OliverChimsewu Месяц назад
Ausi akuwoneka ngati ndiotha zinthu,zaziii basi,mwaziwachilima uli pamutu pako ndichikangawa nzakoyo .truth shall prevail.our anger will not vanish unto our memories.
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 Месяц назад
Never vanish suspect akupezekabe
@Nga-y1k
@Nga-y1k Месяц назад
Malawi ndi ndale zake, ine Phee kukumverani kkkkkkk
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Месяц назад
Manganya mukumva kukoma mutamupha chilima kufana udindo chosecho anakuyikani kale pabwino kumuphasa km zikoli muliphe ndi dr chikangawa
@MirriamKambale
@MirriamKambale Месяц назад
Bambo a sikono ndi Tikuferanji tsopano
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
Atsanakhadzikike usi watsegula kare file kuva udindo kukoma akuti nde antinte ndevu akuti aoneke ngati Chilima🙄🤔
@user-ti9yk4eg2l
@user-ti9yk4eg2l Месяц назад
😂
@RabanChiumia
@RabanChiumia Месяц назад
Awa assavutike mwiniwake amakwanitsa chilima awa alibe molaro
@user-lg6ym4hz3w
@user-lg6ym4hz3w Месяц назад
Waaaaa nza boma kwene kkkkkkk ndikanakhala ku Malawi ndikanazitenga kuzidyaidya ine cheteeee
@YohaneColumbus
@YohaneColumbus Месяц назад
Microphone ndiodula kwambiri Kodi?
@MADALITSOJoseph
@MADALITSOJoseph Месяц назад
Sakunama anyamata kungozuka basi ku mow
@user-ln5hw7dn9g
@user-ln5hw7dn9g Месяц назад
Asanduka adad
@lawrencemakina2882
@lawrencemakina2882 Месяц назад
Good advise VP
@user-rv8gi4ro6r
@user-rv8gi4ro6r Месяц назад
Nkhani ndi yakuti kodi ndalamazi siotse omwe angalandile ..sizingatheke kuti musitse zinthu kuti wina aliyetse aziyetse kumbali yake not ngongole ..ngongole salandila yonse
@StevenMughogho-m1f
@StevenMughogho-m1f Месяц назад
Mantha akewo😂
@realsu7816
@realsu7816 Месяц назад
Ine mundipatse number ya vp'wo ndili nawo zowalankhula
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 29 дней назад
😂😂😂😂😂koma bambo a.SIKONO
@ClydeNyasulu-tk6fj
@ClydeNyasulu-tk6fj Месяц назад
😂😂😂koma
@aaronmagombo9805
@aaronmagombo9805 Месяц назад
Ndalama zabooka kuboma kobasi
@ChikumbutsoTsalangu
@ChikumbutsoTsalangu Месяц назад
1 million ndi drama nanuso akulu
@AndrewUnbreakable
@AndrewUnbreakable Месяц назад
Ngati akupanga comedy
@cyrusmichael6906
@cyrusmichael6906 Месяц назад
Wayamba bwino
@Brihippo
@Brihippo Месяц назад
Koma ndalama izo mutipasadi
@user-ox4dh3ey6b
@user-ox4dh3ey6b Месяц назад
Michael Usi Ali ndi matama
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 Месяц назад
Nanunso pali za matamanso pamenepa?
@emmanuelpiffano259
@emmanuelpiffano259 Месяц назад
Campaign yayandikira 😂😂😂😂
@user-vn6di8hc1v
@user-vn6di8hc1v Месяц назад
Za ziii sm old song
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS Месяц назад
Amalaw tachangamukani achilima amkatani Kodi pano anatisiya mmanja mkhosi mabodxa okhaokha anthu Andale ndi agalu tsekurani maso amalaw musangopusitsidwa
@AbudulLatfu
@AbudulLatfu Месяц назад
Kape wachabechabe iwe
@hopembendela
@hopembendela Месяц назад
Uyu anamutuma uyu akusokonezani
@TroubleKatsala-jp2li
@TroubleKatsala-jp2li Месяц назад
Sizikumukhalayi
@MercyMbisa
@MercyMbisa Месяц назад
Eee kuchita kusaka anthu kuti awapase ngongole zavuta kumpanda
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma Месяц назад
Anyamata landirani ndalama zo zaphweka koma chonde tisazavoteleso MCP
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Месяц назад
Iweyo asakupatse udya mwano wako omweo
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma Месяц назад
@@MarvellousTech-kz6no ndidya Koma vote yanga yokha asayembekezele
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Месяц назад
Chikangawa iwe pelekani Kaye kuno nanga mwayambila paja osapeleka ndalama
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Месяц назад
Hypocrisy
@musasiyama9423
@musasiyama9423 Месяц назад
Wasowa zokamba uyu
@RabanChiumia
@RabanChiumia Месяц назад
Mfiti izi
@EdwardSamuel-xj8qq
@EdwardSamuel-xj8qq Месяц назад
Wachamba manganyayo
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk Месяц назад
😂,,😂😂😂😂😂km usi wabwera ndi ululutu
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 Месяц назад
Iwe ukanakhala president ndiye zikanakhala bwino heavy.........koma vice mmmmmmm
@victormaluwa6710
@victormaluwa6710 Месяц назад
2024
@Steven-q4u
@Steven-q4u Месяц назад
Mmm Koma tiona zinthu mu 2024 kutseia pakamwa anthu kkkkkk
@JefreyMtambo
@JefreyMtambo Месяц назад
Apresdent kkkk
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du Месяц назад
Apanga bwanji sogolo alibe dzochita machende ankhuku
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow Месяц назад
Ifeyo tidya zimenezo co ndi zathu basi
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v Месяц назад
Moti chakwera atati afe Lero basi mtsogoleri akhala USI 😂😂😂😂😂😂 manyaka enieni
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 Месяц назад
Ma plan a mulungu aposa amuthu
@PraiseKadzitche
@PraiseKadzitche Месяц назад
Mulungu amakweza zowoneka zonyozekazo. Read the story of Joseph in the Bible.
@user-ji4xn6me8d
@user-ji4xn6me8d Месяц назад
Uyu nchitsiru sure
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Месяц назад
Ukhalira yomweyo yotukwanayo
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Месяц назад
Tapitani ku immigration, passport yannga mpaka pano
@victorkachepa3515
@victorkachepa3515 Месяц назад
Mavuto kwabasi, Kkkkkkkk Kkkkkkkk!
@Steven-q4u
@Steven-q4u Месяц назад
Via chikangawa ayedzeka Nadi ndale ndi usiku
@user-ve2ts3yr2n
@user-ve2ts3yr2n Месяц назад
Bwelani ku mzuzu bwana usi
@GoodsonJulio-n8f
@GoodsonJulio-n8f Месяц назад
Ndalama zimenezi mmalo moyika kumakampani kuti katundu asike mitengo koma kumangolimbana ndizazii
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Месяц назад
Akuti atsitsa chaka chamawa
@CorneliousKaliat
@CorneliousKaliat Месяц назад
Mthawi yanu yatha inu.mutifune lero
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Guys mukakamileni ameneyu mudya naye matsiku ano mpata ukapezeka chita nawonu nawoso akumba ndalama za boma mukuziwa kale zandale zilibe ntchito
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
Iwe kamanganya ndiwe kachisiri bwanji upite ku imigireshoni uko uone nimumene anthu akuririra ukurimbana nianthu omwe akugurisa ziboribori uziwanamiza anthu inu segurani maso osazawapasa voti ayi
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug Месяц назад
Tengani ma 10milion😅
@mathewsmbaluko8522
@mathewsmbaluko8522 Месяц назад
Ife tizakuyamikani ngati nzipatala mutakhala medicine osati zimenezo
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug Месяц назад
Nde nu nkhatabay mupita liti
@Martha-m6e
@Martha-m6e Месяц назад
😂😂😂😂😂komatu.
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Месяц назад
Chikangawa
@MwabiMughogho-kc8lb
@MwabiMughogho-kc8lb Месяц назад
Eee kwatani
@MercyMithie
@MercyMithie Месяц назад
Zosamukhala
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Месяц назад
Inetso ndikapita ku Malawi ndikukasapota mcp ndikadyele ndalama zaulele mvote ili mtima chifukwa kwasala sewelo ku Malawi
@jamiajafali6619
@jamiajafali6619 Месяц назад
Abambo asikono chibwana icho
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Месяц назад
Kupunsa agalu inu
Далее
Cristiano Ronaldo Surpassed Me! #shorts
00:17
Просмотров 15 млн
Я ж идеальный?😂
00:32
Просмотров 72 тыс.
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Просмотров 7 тыс.
Cristiano Ronaldo Surpassed Me! #shorts
00:17
Просмотров 15 млн