Тёмный

ZOMWE WAPANGA ZIKHALE NG’OMA NDI AMAYI AWA LERO PA NSONKHANO WA MCP LIVE LIVE ANTHU AKUONA 

Makosana
Подписаться 95 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 139   
@isaaczuze
@isaaczuze 4 часа назад
My vote is for Apm osati chipani cha zisilu zili apazi ....mukugawa ndalama ndiyetu mupeleke ndalama kwa munthu aliyense mmalawi muno ......chipani copanda maso mphenya....chipani choyendesedwa ndi mbava komanso zigawenga
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo 4 часа назад
Chipani chosakoma ichi ife ndi ana adadi moto ku buuuuuuu🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau Час назад
Muzilemba kwa adadi any komweko man
@amosmuluwane4182
@amosmuluwane4182 4 часа назад
Azikhale ndalama zimenezo muzazilira tawonani kukatoto ground mmenekulili anzanu sakugawa ndalama koma anthu kusowa poima Malo atha uku.
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 4 часа назад
Camera ikungoonetsa mbali imodzi bwanji mbali inayo kulibe anthu kkk
@Alexkalonga-t9s
@Alexkalonga-t9s 4 часа назад
Idyani ndalamazo koma Apm ndiye votiyo
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 4 часа назад
Ndiye kupusa anthu anyake akulandila ndala ena alipomwepo akukagona ndi njala boma lopusa kwambili ili kumapeleka ndalama pa msonkhano zimenezo ndizosaloledwa pa malamulo a democracy akulu awa ndi mbuli zedi
@EmmaOsman-w3p
@EmmaOsman-w3p Час назад
Ndpo kulibe anthutusotu muone anzanu ukoooo dpp.woooyee🎉🎉
@WisdomMwale-j9h
@WisdomMwale-j9h 13 минут назад
Uku...Anthu achokako ndi Ndlama Zambili Man....eeeh Amayo ine Misonkho yathu!!
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 4 часа назад
Mukunama ana mwachepa, avotele njalayo?
@WisdomMwale-j9h
@WisdomMwale-j9h 15 минут назад
Inu Akutha... misonkho yathu awa!! Kumango gawa Ndlama .....eeeh Amayo!!
@XxTang
@XxTang 2 часа назад
Palibe changers chomwe nduchionapo apa zaziii zeni zeni APM my vote❤❤❤
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 4 часа назад
Zikhale wachinda Mai gotani Hala pochoka Ku ekwendeni😢😢
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau Час назад
Ndiwe chitsilu kwambili iweyo Suma chinda pamtumbo pako
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 45 минут назад
Kkkkkkk😂😂😂😂😂 Malawi
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 4 часа назад
Mkasi sagula ndindalama iwe kappe
@EmmaOsman-w3p
@EmmaOsman-w3p Час назад
Soo osapeka nyimbo zanu bwanj njenje zanzanu mmma azikhale 😅😅
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 4 часа назад
Angakumbvotereni ndani anthu opanda chisoni ngat inu sindinawonepo anthu akudya chitedze inu muli busy kugawa ndalama shame mupenga chaka chake ndi chino
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 часа назад
Ndipo anthu oipa, anthu akudya chitedze Iwo Ali busy kugawa ndalama, ndi gulu logulira anthu mowa banja lawo likufa ndi njala.
@AndyGama-m2u
@AndyGama-m2u 3 часа назад
All the best Athu ambiri mumavutika coz mumakakamila mbali yoluza ndiye zanuzimenezo at the end of the day mumangokhala wokhumudwa komanso akhwiyo pa zaziiiiii
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 4 часа назад
PAKUPHA WANTHU MUPHENGE CHAKWELA
@AuphieBannet
@AuphieBannet 4 часа назад
Zamanyaaaazii
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 3 часа назад
Mukuyimba nyimbo za Peter
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 часа назад
Koma boma ilii guyz kumangogawa ndalama bas, APM my vote
@BlessingsLuclus
@BlessingsLuclus 54 минуты назад
Kwacha kwacha lelo mayako zikhale ngoma njekete ayabeloyo ife ana adadi
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 4 часа назад
KUKULA KONSEKO NO MANYAZI ZACHIBWANA BASI
@IbrahimMatola-h4i
@IbrahimMatola-h4i 4 часа назад
Kukuoneka ngati kumalirotu kukumvetsa chison
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala Час назад
Kod anthunu muli pa chinamwali bwanji azikhale ndinu master saimon onenelela 😅
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 36 минут назад
Anthu opusa osaona ndimmene ziko likuyendela kutengeka ndi tchele wa lelo
@frankgondwe8584
@frankgondwe8584 2 часа назад
Giving a dancing lady 200pin...anthu akuona pamsonkhanoo... This is too much... Eeeish..😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 4 часа назад
Zaziiiii adyereni ndalamazo mwalephera manyazi mulibe anthu okupha inu
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Час назад
Mukamaliza kugawa ndalamazo muwauzeko anthu za ndege ija
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 55 минут назад
Adadiwo ndeye also ndiyekut kulibeso odzavotela nanga adadiwoaaaaaaa siziona
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 4 часа назад
Mdala ndiwechindele chomene mahala wulije.
@kenmasta
@kenmasta 4 часа назад
Idyani ndalama zokubazo,munyera next year...APM akunokolani
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 3 часа назад
Political principles must be revised or soon Malawians will be divided
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 9 минут назад
True
@HazlathAdmack
@HazlathAdmack 4 часа назад
Zikhale ng'omayo mawu ngati akulila ky mutu😂😂😂😂
@peterlowole7841
@peterlowole7841 Час назад
Remember that your days are numbered, don't forget that money is our own money, you gonna pay back,
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh 54 минуты назад
Brave dpp ❤🎉❤🎉 apm my vote
@RajabShahida
@RajabShahida Час назад
Adikilenso utm ku njamba freedom park pa 28 September
@langfordmhinji
@langfordmhinji Час назад
Nde muwagaile onsetu ndalamazo pamsonkhanopo
@GeraldGomati
@GeraldGomati 3 часа назад
Amalawi ndife amvesa chisoni, kululutira mzawo akupasidwa ndalama iwo akapita kunyumba akagona ndi njara
@ClementkapelulaNkhoma
@ClementkapelulaNkhoma 4 часа назад
MPhavu ya mowa
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 41 минуту назад
Kamajekete wangozazana ndi sisi ulibe mfundo mose wayambila chakwera moto!! Nenani fundo zogwila mtima
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 4 часа назад
Wasangala nadi thanks
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Час назад
Koma mcp guys 😂😂😂😂 anthu ngat achita kuwafukula mufumbi zosabeba
@UrdPahuwa-vf8ce
@UrdPahuwa-vf8ce Час назад
Anthu amabvala chobvala china mkati,kusonyedza kuti idzo zongolandira,akamapita uko abvula ma t-shirt amenewo
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 50 минут назад
Kodi ngat anyamata naga kuikaso agogo aaaaaa ai bola kukhala Malawi sadziwa chimene akufuna sachidziwa
@khoviwaedward
@khoviwaedward 10 минут назад
Nsonkhano opanda mfundo ngati uwu za ziii zeni zeni.
@ellensambo6323
@ellensambo6323 3 часа назад
Viryeni waka mbwenu wavotera uyo wakumanya 😮😮
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 10 минут назад
Nyimbo zaku dpp kubela nyimbo kkk
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 4 часа назад
Ndalama zokubazo machende ako iwe kamajekete 😅😅😅😅😅😅
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau Час назад
Iwenso ako pamtumbo
@ChristopherJohn-z5z
@ChristopherJohn-z5z 2 часа назад
Ukumana buz za anthu mufuna muzimangabe anthu
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 часа назад
Zikhale alibe mfundo zoyankhula zake zopanda mutu
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Час назад
Camera man akuonesa mbali yomwe kuli anthu😂😂😂😂 ....pamene katoto kuli fupmbi lawanthu uko
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 3 часа назад
Aledzera zikhale mmmm ambuye tengeni
@babranzima8120
@babranzima8120 4 часа назад
Chalezera ichi chibekete cheneko
@JefreyMtambo
@JefreyMtambo 2 часа назад
Akukingani anzanu pa katoto ground
@AustinMhone-r3s
@AustinMhone-r3s 2 часа назад
I support only federal system of government people are suffering in Malawi the poorest country in the world I don't support individuals.
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Час назад
Ndalama zimenezo muzazilira amalawi akuvutika agalu inu pekani nyimbo zanu musagwilitse zathu za dpp ai dpp boma ilo
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane 4 часа назад
Bola adad koma izi ndye ayi kukamwa mbeeeeee ND ndalama anzanu akudya chiteze koma chikangawa ine ayi sindizakuchonga orooooooo
@JessiemwaleMwale
@JessiemwaleMwale 3 часа назад
Mwanya nayo see mzuzu APM bomaaaaa
@UmaliDaili-nd6uu
@UmaliDaili-nd6uu 4 часа назад
Zaziii zopanda tchitho azanu koma mwaona azanu kuseliku sakuperekha ndalama adyereni vote ili mutima
@isaaczuze
@isaaczuze 3 часа назад
Uchisilu kugawa ndalama mwachsawawa ... Misonkho ya wanthu
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 6 минут назад
Camera simayenda bwa?😂😂😂😂😂kuwopa kuyaluka kuti kulibe anthu
@traceydelport977
@traceydelport977 4 часа назад
Malo moyankhula zachitukoko
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 4 часа назад
Ankolo Zikhale akamwapo ndi choncho
@mussayassin3868
@mussayassin3868 4 часа назад
Zaziii iwe galu kwabasi anthu akupha unu
@ChibakuliKaisi-cm3hn
@ChibakuliKaisi-cm3hn 4 часа назад
Suwukhumakha bholo yanu yozadulayo😂😂
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 4 часа назад
Ukuwanamizatu anthuwo iwe zikhale
@DanielZunguza
@DanielZunguza 3 часа назад
Kodi analedzela zikhaleyu bwanji???
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 4 часа назад
Palibe chomwe chikuveka manyi eni eni tamuwoneni zanu peter inu mulibe manyazi kodi
@AishaYassini
@AishaYassini 3 часа назад
Kamajekete. 😅😅😅😅 akafikilira kudwala2 amaneyi guyz
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 3 часа назад
Mahule zigawenga mbava achure chikagawa
@Kelvinbanda-c3x
@Kelvinbanda-c3x 2 часа назад
Aline nyimbo akhululukileni
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 2 часа назад
Ili ndiye boza inu pakatoto momwe panalili athu mmmmm pitani pa times live mukaonele
@GeraldGomati
@GeraldGomati 3 часа назад
Kamajekete wayiwara pompano anapasa ma delegates ma millions koma sanakamuvotele
@milliambandah1939
@milliambandah1939 4 часа назад
Ndalama zakuba mulibe nfundo koma kugawa ndalama Nzeru palibe
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 3 часа назад
Wanthu wakwithu uyo wana boza kukupusikani chaaaaa kuvotelaso chakwela yy wanthu wakwithu please chalo iro sono chanangika onani njala muchalo umo
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 4 часа назад
Kod a MCP mkubela nyimbo bwanji😂😂😂
@Janaphiri
@Janaphiri 3 часа назад
Omvotera amp ndi mtesi mweeee
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 часа назад
Utesi zikhale kkkk Tikumtemwa yayi
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 10 минут назад
Anthu okupha awa zitsiru kkk
@DanielZunguza
@DanielZunguza 3 часа назад
Ndalamazo landilani ndi misokho yanu imeneyo,,anachita kukubelani kuti adzapangile compain.
@RhaudanRhaviwa-i8b
@RhaudanRhaviwa-i8b 38 минут назад
Koma iwe Pepe Kale nthawi Yako yatha😂😂
@LenoMvula
@LenoMvula 2 часа назад
Chitesi icho
@CosmasMaluwah-mh4ji
@CosmasMaluwah-mh4ji Час назад
He's drunk Kamajekete 😅😅
@UseniMailosi
@UseniMailosi 4 часа назад
Ma 2 thousand misonkhoyatu yapweka
@HopeMalika-b9k
@HopeMalika-b9k 2 часа назад
Usawanamize anthu kamajekete iwe
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 2 часа назад
Ndalama izo musungeko mawa muzazikumbuka kujere
@AyandaPhungula-bg9ql
@AyandaPhungula-bg9ql 3 часа назад
DPP boma basi
@WisdomMwale-j9h
@WisdomMwale-j9h 17 минут назад
Eeeeeh Amayo Misonkho!! Yathuu!!
@GeorgeMphaya
@GeorgeMphaya 3 часа назад
Utm boma
@Atheeeefire
@Atheeeefire 2 часа назад
Ma guy awa azayenda cha mpeni
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 2 часа назад
Pajatu.akt wadya gotani
@HedgensChisale-n4b
@HedgensChisale-n4b 4 часа назад
Machende ako zikhale pomozi ndi chakwela wakoyo
@JosephLemani-qq1is
@JosephLemani-qq1is 4 часа назад
Zosabhebatu bola kwa dadi kuli mfundo ndi anthu ambili
@MjombaMoosa
@MjombaMoosa 4 часа назад
Mau ngati chule. Walila kale iwe that's why ukulepela kuyamkhula
@JefreyMtambo
@JefreyMtambo 2 часа назад
Lyani ndalama boma nilo lili lu MZ
@Janaphiri
@Janaphiri 3 часа назад
Mcp boma dpp opositiona mpaka2030
@jahiemmusa8796
@jahiemmusa8796 4 часа назад
kkkkkkk koma sikale ng'oma ndimbusi yamunthu
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 3 часа назад
Malo mowapatsa zochita akuwapatsa ka 2 hand kachani za usavege
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 11 минут назад
Masanje enieni kkk
@BrotherPaul-ln2ld
@BrotherPaul-ln2ld 2 часа назад
Malawi Chiteze Party (MCP)
@AyamiMustafa
@AyamiMustafa 3 часа назад
Agalu inu muvotelana nokha zauchikape malawi ayi sakufuna
@MeriaMasinga
@MeriaMasinga 4 часа назад
Kodi kamwamo mulichani?
Далее
HA-HA-HA 👊  #countryball
00:15
Просмотров 1,1 млн
연준 (YEONJUN) ‘GGUM’ Official MV
02:44
Просмотров 9 млн
Donald Trump speaks at town hall in Flint
1:00:21
Просмотров 61 тыс.