Тёмный
No video :(

ZOMWE ZILI KU ZOMBA NDIZOMWE ZAYANKHULIDWA LERO PA19 July 2024 

HOT 265
Подписаться 77 тыс.
Просмотров 23 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

4 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 187   
@GraceSilumbu
@GraceSilumbu Месяц назад
Work up malawi please time is gone don't sleep with this things without no sense
@WhiteThamanga
@WhiteThamanga Месяц назад
Meyer osafuna kubitsa mau Stadium idayamba 2017 muwulamuliro wa adad
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Zithu sizilibwino 😂😂😂🔥🔥🔥 machende akuyabwa chakwera
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 Месяц назад
Chakwera okupha mboleyake
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz Месяц назад
i dont know what is happening in this country 😊
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Komatu Mr Chikangawa akudziwa kuti ngini silibhoooo😂😂😂
@ChawingaMwaseteza
@ChawingaMwaseteza Месяц назад
Zomba si ya anthu ofoila,amadana ndizopusa
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq Месяц назад
Ufune usafune uchoka basi a Malawi si mbuzi ayi
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v Месяц назад
Ndiyemwati kuli chinamtindi cha Anthu😂😂😂😂
@isaacthawani5442
@isaacthawani5442 Месяц назад
😅😅😅 koma Mr Usi udindo wamukulira
@EviChio
@EviChio Месяц назад
Ovotela iwe ndiye wamisala ndithu
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie Месяц назад
Zakuvutanipo apa basi bye-bye 2025😂😂😂kkkk
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 Месяц назад
Community ground not stadium
@user-ei6ji9qj8u
@user-ei6ji9qj8u Месяц назад
😂😂😂😂 Inu mukuti kilibe athu awowo ndi zidole
@user-xc3jz1qg8p
@user-xc3jz1qg8p Месяц назад
Zidole kkkkkkk
@Mahmoodwargison-op2gm
@Mahmoodwargison-op2gm Месяц назад
Martse💔 as musician anazazisa sivo chilima💔 as VP anazazisa bingu iwee sogoleri ukanika kuzazisa ka zomba ground😏😏😏😂
@MustapherLino
@MustapherLino Месяц назад
😂😂😂😂 koma chakwera alibe manyazi
@MarthaPhiri-q8m
@MarthaPhiri-q8m Месяц назад
Ine kuva chisoni kwambiri 😢muthu osakondedwa ngat wazola bubu😂
@PreciousHenderson-qc1hq
@PreciousHenderson-qc1hq Месяц назад
Mr chikangawa uziona siunati this is just a beginning awa ndi matelazi spa nde watha bas kkkkkkkkk
@frankdonovanntambira
@frankdonovanntambira Месяц назад
Mongokumbutsana inayamba nthawi ya Adad ZIKOMO Sizachikangawayu ayi
@user-qd7sz1pf1i
@user-qd7sz1pf1i Месяц назад
Vinyo wathapo basi😂😂
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Месяц назад
Uku nde kulibeko vote yanu mungoona m,mene zili
@giftsalijeni6962
@giftsalijeni6962 Месяц назад
Chikangawa
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 Месяц назад
Manyadzi bwaaa
@imraanJafal
@imraanJafal Месяц назад
Kkkk inu maboza basi kod ndalama zikubedwazi tiziti simunamve
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga Месяц назад
Khalfani chete inu.Chakwera wabwera kuzakhala.musivaa
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga Месяц назад
Musova
@raymondthewethe4627
@raymondthewethe4627 Месяц назад
Koma shirt iyi nde ndiyolimba 😂😂😂
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Месяц назад
😂
@MatiasChimsakasa
@MatiasChimsakasa Месяц назад
Kom a amakamera chipongwe bwanji mukuzumula kopanda anthu kkkkk ife tili pambuyo pa pule nga nga nga 😂😂😂😂
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Месяц назад
Manyazi ayambako kulibe anthu kkkkk
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Месяц назад
Kkkk
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx Месяц назад
Chala chamwinidi sakandira kuchipsepse ndaonera apa, anthu kulibe, angobwera omwe atengedwa pangolo basi😂😂😂😂😂
@Steven-q4u
@Steven-q4u Месяц назад
Mm kwavuta zizindikiro zoti good bye mr chikangawa
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 Месяц назад
Chimwendo ali pa chintchito 😅😅
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t Месяц назад
Anthu akuzomba Kodi onse anafa ndinjala nanga anthu alikuti kulibe anthu uku manyazi bwanji
@PatriciaTikhiwa
@PatriciaTikhiwa Месяц назад
Koma guez dziko ili ai ndithu amayor zoona mwanenazo apaa mwalakhula moipora bwaa
@PatriciaTikhiwa
@PatriciaTikhiwa Месяц назад
Aaaa nanga kuzomba kuli zitukuko? Aaaa ndrama howooo zauphawi chi!mwendo Kodi ndi bausa wa person
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 Месяц назад
Kulibe anthu 😂😂😂😂
@FrancisMwafulirwa
@FrancisMwafulirwa Месяц назад
😂😂😂😂
@VictorMillanzie
@VictorMillanzie Месяц назад
😂😂😂😂 kuribe anthu 😂😂😂
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 Месяц назад
Pamenepo pali president? Ndiye koma Chakwera as,manyazi bwanji? Waona Wanthu ayamba kuku thawa, ukakhala wosakonda amzako nawonso sakukonda,koma chimwendo Banda Ndi Chakwera si ndiwo akupherani Wanthu aja ku Chikangawa kuja? zitsiru zaku Dambwe, M'malo moti mugule Chimanga mugawire M'malawi Aliyense, Muku konza ground la mpira,Wachipiku, Ndi wazi suzo akumana majokala okha okha basi heeeee koma ziriko ooo
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Месяц назад
Kulibe anthu kkkkk
@frankdonovanntambira
@frankdonovanntambira Месяц назад
Mongokumbutsana inayamba 2017 nthawi ya Adad ZIKOMO
@NebotPatrick
@NebotPatrick Месяц назад
My vote 😂😂otukwana katukwanani apule ali mweee😂
@user-un8yq1gg2i
@user-un8yq1gg2i Месяц назад
Koma MCP kungotulukanso m'boma ulendo Uno, padzatenganso dzaka dzambiri kuti idzalamulenso & sindikudziwa kuti adzagwiritsa ntchito mfundo zake ziti kuti akope amalawi
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Месяц назад
Mpira wachan Malo mwanjala kusitsa mtengo wazinthu busy zampira stadium ya Peter muthalika iyi kkkkkkkk
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx Месяц назад
Anayambisa stadium ndindani kodi.?peter muntharika osati zamanyi zanuzi mapazi anu
@agnesmadeya-di8oi
@agnesmadeya-di8oi Месяц назад
Ng'ona Style
@chisomotaika4479
@chisomotaika4479 Месяц назад
It’s very many pple bwanji😁
@samsonpadiwa9185
@samsonpadiwa9185 Месяц назад
Stadium yoyamba 2017 a Mayer atero tapangani zanu from scratch bwana
@FelixMadeya
@FelixMadeya Месяц назад
Kkkkkk tikamanena kt MCP sinapange chitukuko nokha mwamva Chimwendo akuti chitukuko ichi ndicha Chakwera nthawi yomweo Councilor sanachedwe avekere ntchito iyi anayamba 2017 kkkkkk
@AbdullahMsosa
@AbdullahMsosa Месяц назад
Bolaninsoni msonkhano wa e MP umakhala ndi anthu ambili
@JesseKanjanga
@JesseKanjanga Месяц назад
Mizimu yaanthu9 ikukantheni,DZIPHE INU ndi VP wakoyo
@user-jt1hs9lc8x
@user-jt1hs9lc8x Месяц назад
Nkazi wina uja wachibwezi uja amusiya
@user-xe1so5xj2w
@user-xe1so5xj2w Месяц назад
Azimayi ndioononga basi
@user-rg6hn7mt6w
@user-rg6hn7mt6w Месяц назад
Chikangawa .uja anatiliza 😢
@phillgatoma4857
@phillgatoma4857 Месяц назад
Koma dzamanyadzi kwambiri kuchita kusowa poyambalatu😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@HalimaShafie-o7g
@HalimaShafie-o7g Месяц назад
Agalu ngati awa kwaombela mmanja no sense chakwera anthu akumwalila ndinjala muli busy kupanga za mipira
@user-xc3jz1qg8p
@user-xc3jz1qg8p Месяц назад
Crocodile party 😂😂😂😂😂
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Месяц назад
Useless president Dzukulu wake wa satana Mr Chikangawa
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Месяц назад
Ka Dr Manganya kango nyung'unyuza maso uku ndi uko ngati nka boardguard
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Manganya, Chakwera, monica komaso anthu onse a MCP pamtumbo panu anthu onukha kuthako pagulu inu
@user-lb5gt4uv3s
@user-lb5gt4uv3s Месяц назад
Koma adzimayiwa ndizitsiru
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 Месяц назад
Konzani economy, mpila sitionera tilindinjala
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Zomba yose ija anthu akabwera otelewa kkkkkk MCP zavuta basi kkkk
@KennedyMitochi-nz8fp
@KennedyMitochi-nz8fp Месяц назад
Anthuwa achita kubwelanao si anthu akuzomba aai
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Pali ana wokha wokha apa and anthu Ake ndi 250 onse anali pa msokhano
@GeraldGunde
@GeraldGunde Месяц назад
Moni wosope!!
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Месяц назад
Anthu ochepa choncho bwanji? Kapena udali msonkhano ongozizimutsa
@Maliet-nh6kf
@Maliet-nh6kf Месяц назад
Rest in peace Thomas che nkhumba chibade by malo mowapasa mgayiwo muwapasa mpira akatani nawo
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Chakwela palibe chako 2025 example ukuwona wekha no vote for you
@PeterBeaton-r4t
@PeterBeaton-r4t Месяц назад
Koma a president malayawo ndye amawakondatu
@robsonmoyo8572
@robsonmoyo8572 Месяц назад
Cholakwika choti munapha chilima cholinga munjoye
@BraveMphande-ln2ho
@BraveMphande-ln2ho Месяц назад
Drama yonkha yonkha pa Malawi kuwona a vice president ndi drama payonkha
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim Месяц назад
Iwe meyor iwe samala iyitu home ground yathu
@wakisawinga2744
@wakisawinga2744 Месяц назад
Koma nde kulibe anthu ambilitu,😢
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Месяц назад
Mukat kuli athu ochuluka apa? Kkk mukuzinyenga nokhat
@FelixPhiri-w1z
@FelixPhiri-w1z Месяц назад
Km ndye zachibwanatu anthu ake amenewa
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs Месяц назад
Chimwendo Banda ndi manganya wamkulu ndani
@mkhokholasamuzonda5094
@mkhokholasamuzonda5094 Месяц назад
KOMA MCP INATHADI , MUONE UTM ITAPANGITSA CANDLE LIGHT PAMENEPA MMNENE PANGAZAZIRE,
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Месяц назад
Eti amwene
@MerySaid-uw3cm
@MerySaid-uw3cm Месяц назад
Wakumpha
@user-lh4nx4hw7x
@user-lh4nx4hw7x Месяц назад
Musayiwale kuti anthu awa salengeza za komwe akupota amangodzidzimutsa mutha kuwona kuti palibe zokhala pa mpando
@juliussamson6212
@juliussamson6212 Месяц назад
AMANGANYA MUFERAPO CHITUKUKO CHAMIPILA ANTHU AKUFA NDOWUPHSWI MACHENDE ANU AWUSI NDIWE CHAKWERA
@mikesandali8425
@mikesandali8425 Месяц назад
Chakwera boma
@robsonmoyo8572
@robsonmoyo8572 Месяц назад
.busa wotani sure muzafa imfa yomwe apita nayo azanu lk 6:38
@user-wu4tl2yn9e
@user-wu4tl2yn9e Месяц назад
Manganya akungooneka ngati kamwanatu
@ClaraMkandawire-d2k
@ClaraMkandawire-d2k Месяц назад
Biyeni 😭😭😭
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Месяц назад
Zakaria zinayi zonsezi munali kuti lero chifukwa mwapha abale athu 9 aja ndiye mwayamba zokopi zokopi kupita kuti tikudikira mwachidwi zomwe zimachitika kuchikangawa
@user-nf1re1vf8i
@user-nf1re1vf8i Месяц назад
Koma guys a president ndi a VP kupitaku ground lot sanamalize😂
@GeoLikwanya-cb9gn
@GeoLikwanya-cb9gn Месяц назад
Ai kma sizili bwino moopa mlengi
@Patrick-m6r
@Patrick-m6r Месяц назад
Ntchito adaipezadi kkkkk
@innocentkhumbanyiwa4780
@innocentkhumbanyiwa4780 Месяц назад
Yankho yanga ili pa ballot paper
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z Месяц назад
Koma achimwendo muli ndi chitchito 😂😂😂😂
@happyjuniormlowoka
@happyjuniormlowoka Месяц назад
President plus vp anthu obwera kukhala amenewo mzifutse 😢😢
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Месяц назад
Kwangokhala ngati mwambo wachiliza Dala.. Chanu palibe. 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Месяц назад
😅😅😅😅😅😂😂😂
@JohnAsendi
@JohnAsendi Месяц назад
🤣🤣🤣🤣🤣Apulezideti. Nduna. Ndi vp kukhala nga ntsongano wakasala zamwanyazi
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Месяц назад
Koma mbc iwe mutolankhani pola moto pali anthu apo ngati kuchita kuti kwabwela nkhwimbi la anthu kulibe anthu uko
@HalimaShafie-o7g
@HalimaShafie-o7g Месяц назад
Chikangawa yomweyo mwaiwala kuti wapa chilima
@YahayaKondwan-mo8hu
@YahayaKondwan-mo8hu Месяц назад
Olo manyazi mulibe kuli namtindi w a athu pamenepo
@HerculanoFranciscoZavuata-q9b
@HerculanoFranciscoZavuata-q9b Месяц назад
Achakuela atsike paudindo
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga Месяц назад
Mavuto anu nchiani kodi.
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda Месяц назад
Agaluwa nthaw yonsey analikut kuyenderako. Anthu kulibeko manyaz bwaaaa....mphuno ngat mabuno
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q Месяц назад
Bye bye mcp ndipo muziona 2025
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 Месяц назад
Mphavu ya fafandede azimayiwo
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq Месяц назад
This is no sense Malawians will neva forget your foolish goverment
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow Месяц назад
mwati kuli Chigulu eti? kkkk😊
@giftbanda7690
@giftbanda7690 Месяц назад
Nde mwati gulu eeti kkkkk
Далее
BON KALINDO KUNG'ALULA MWA NYOO!! 5 September 2024
43:54
😱ЖИВОЙ Чехол на Айфон🤪
00:38
Просмотров 246 тыс.
Timings hated him #standoff #timing #meme
00:14
Просмотров 430 тыс.
NRF Awards Sun City
2:19:01
Просмотров 14 тыс.
THE DC BON KALINDO KUNG'ALULA 5 September 2024
17:11
A MOSES KUNKUYU KU PROGRAM YA KULINJI
39:13
Просмотров 16 тыс.
Opening Ceremony of Lanka Premier League 2024 #LPL5
34:47
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 249 тыс.
😱ЖИВОЙ Чехол на Айфон🤪
00:38
Просмотров 246 тыс.