Тёмный
DZIWE TV
DZIWE TV
DZIWE TV
Подписаться
Ngati Muli ndi Maganizo kapena mukufuna kuwadziwitsa anthu zomwe mumapanga tilembeleni pa dziwetv@yahoo.com


Dziwetv ndi Channel Yomwe makamaka ikuyang'ana kwambiri nkhani Zandale Mdziko lino. Kuwadziwitsa anthu zomwe Mtsogoleri wadziko lino walankhula ndi azitsogoleri ena azipani zina. Dziwe simalimbikitsa Ulamuliro wankhanza ndipo timapanga Support ulamuliro Osamala Malamulo.

Anthu omwe alibe information zomwe zikuchitika mdziko mwawo ndi anthu omwe ali otayika.
ZOMWE ZAGWA LERO MZIKO MUNO |
18:03
2 часа назад
KWACHEMA  KU CONVENTION YA UDF UKU |
15:14
4 часа назад
BON KALINDO LERO PA 1 OCTOBER 2024 |
18:35
7 часов назад
UKU NDE KWACHEMATU |
22:43
7 часов назад
KUNG'ALURA KU HOT CURRENT  UKU |
57:18
9 часов назад
DRAMA YACHITIKA KU UDF NDI IYI LERO |
21:33
12 часов назад
BON KALINDO LERO PA 28 SEPTEMBER 2024 |
17:06
14 часов назад
ZOMWE ZILI KWA AMERICA 27 September 2024
22:17
14 часов назад
ZOMWE WADANDAULA DAN LU NDI IZI |
37:08
16 часов назад
KUGWEDEGWEDE KWACHEMELATU |
24:25
16 часов назад
Комментарии
@amontchuwa6876
@amontchuwa6876 2 часа назад
Ayao okha okha owina 😢😢😢😢😢
@EsetaGerate
@EsetaGerate 2 часа назад
❤❤
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 2 часа назад
Thawi kachitsiru wayamba liti za 1 minute 😢😢
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 2 часа назад
Chitsilu cha bambo uyu
@JosephyTembwe
@JosephyTembwe 3 часа назад
Fuso lot zithu zikuyenda bwino ndimawona ngt zimafunika kt timifuse Dan lu muwona bwaj?
@Josephchilabade
@Josephchilabade 3 часа назад
Wakudya zake alibe mulandu ndiye chipani chalke
@rashidadan2533
@rashidadan2533 3 часа назад
UNGA chakwela wabweletsa fertilizer mixing with dothi , that's a good achievement as Malawians
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 часа назад
Munthu ukamafa amasekeka makutu Olo atakuuza motani sungave
@Josephchilabade
@Josephchilabade 3 часа назад
Wasowa kopita
@AdamSteven-ne9hg
@AdamSteven-ne9hg 4 часа назад
UDF ndichipani cha mphavuu . Koma zimangovuta
@kondwanivyalema9449
@kondwanivyalema9449 4 часа назад
Ndikamene kanapha chilima ndikameneka kamunthu kofupi ngati mchimba womaliza pa mtumbo pake😮😮😮😮
@AnyuxyJulias
@AnyuxyJulias 4 часа назад
Yakhan funso musathawe thawe
@HiltonZaone
@HiltonZaone 4 часа назад
Four year palibe chenicheni ayi
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 5 часов назад
Awawa osawavotera awa akutiperekado MMANJA MWA mikango chifukwa cha ndalama komaso mipando.achair adziwe kut akumudokonezera mwana waoyi sazalamulira dziko la Malawi.
@LovemoreSambuke
@LovemoreSambuke 5 часов назад
Mbuzi ya munthu
@GRACEKUMWEMBE-rv2se
@GRACEKUMWEMBE-rv2se 5 часов назад
Mpaka mawu kusasa ndi za ziiii.kulimbana ndi boma mpka liti
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 5 часов назад
Aisha mambo point of correction palibe chimene MCP chabwino achita kungoononga economy kokhaku ndikuduludwa mutu kwa dziko ndipo Palibe chabwino chimachitiks so don't make us stupid we know that Mcp has failed there is nothing you can say that mcp did this as a good thing never
@austinvincent773
@austinvincent773 5 часов назад
Mau amphanvu
@AYATUMARTIAL-q3c
@AYATUMARTIAL-q3c 6 часов назад
Zikuwawawa a DPP ndicani?? Dan luu nkhani yake ili pakamwa ndi adpp ,coona cake adpp Ali ndi pakamwa pobooka.
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 7 часов назад
Chisiru iwe Chikangawa chomwe wapanga kupha chilima kuononga ndikugwesa kwacha.thats is the last trip yomwe wapitira ku UNGAko uwona 2025
@SifatiMoses
@SifatiMoses 12 часов назад
Nonsense anthu akukudikilani kuno za munthu munapha uja, musawayiwalitse anthu ndi izi. Ndiliti lomwe munayima panokha ngati dziko.
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 14 часов назад
Atibamize apa
@MussaSamuel-vm5ry
@MussaSamuel-vm5ry 14 часов назад
Kukuyu mbolo yake
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 14 часов назад
Pelekani commission of inquiry tidziwe zoona zen zeni
@LuskaMoses
@LuskaMoses 14 часов назад
Garu ameneyu aka apepha ufiti kuti tamaliza bwanji anthu atsala kumalawi 😢
@HalimaShafie-q9k
@HalimaShafie-q9k 14 часов назад
Iwe mumakonda anthu kumupha chilima bas ndichitukuko chimene mwapanga mulungu akulangen
@HalimaShafie-q9k
@HalimaShafie-q9k 14 часов назад
Mukufunika mdulidwe chikangawa iwe
@HalimaShafie-q9k
@HalimaShafie-q9k 14 часов назад
Mboloyanu chakwera galu
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 14 часов назад
Namondwe ochita kukonza. Cholinga utinthe ife alomwe ,,mulungu akuone
@KinziWindasoni-h4b
@KinziWindasoni-h4b 14 часов назад
Kkkkkkkkkkk Koma chikangawa yayalukatu
@BilalAliyah-k1f
@BilalAliyah-k1f 15 часов назад
Mfiti iwe unapha chilima galu
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 15 часов назад
machende ake chakwera mbuzi ya munthu chigawenga chongokhalira kupempha basi
@DicksonLutere
@DicksonLutere 15 часов назад
Mwana wanzako akachita bwino kumayamikila UDF ndi MCP atha kuyenda limodzi
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw 17 часов назад
Koma Catherine maulidi wandisangalatsa kwambiri mmene wapangira coverage ya ma convention azipani big up madam
@brieembroidery3134
@brieembroidery3134 18 часов назад
TIMES TV
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo 18 часов назад
Tangoonani akulephera kuyankha slogan,zilikotu ziliko,!
@EsetaGerate
@EsetaGerate 18 часов назад
Kumkuyu machende ako lweyo ndamene unatsogolera kupha chilima
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 18 часов назад
Manganya munthu sakhala wa Ambuye awiri, ngat ndi Utm khalani a utm, ngatinso ndi MCP khalani a MCP. Taonani mwakanika kuyankha funso.
@AliceGeorge-il6ig
@AliceGeorge-il6ig 18 часов назад
Boma lolephela,,chisankho akanangoti chikhale mawa,,tiagulule Mano afiti a mcp
@RobertGalatiya
@RobertGalatiya 18 часов назад
Kodi kunkuyu ndekuti tiziti sukugwilizana nozo zomwe apepha mai chilima zo?
@GreyMwanyimbo
@GreyMwanyimbo 19 часов назад
Welcome to the mighty MCP
@RonaldodalitigerSpencerDaliRic
@RonaldodalitigerSpencerDaliRic 19 часов назад
mukatero pamenepa mwa joiner zakutumbo zanuzo....muzanyaaa ndithu..kaye zimaso
@MasegoModukanele-xg2hj
@MasegoModukanele-xg2hj 20 часов назад
Mofaya udf
@Lydia-t4b
@Lydia-t4b 22 часа назад
Apatu ndiye mwaonesadi kuti ndinu independent Times proud of you Times TV
@DouglasDazuKamwendo
@DouglasDazuKamwendo 22 часа назад
DPP payokha ndiyokwanira sikufunikaso kupanga campaign.
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 22 часа назад
Kumeneko ndikuyankha mopepera, ubwino wake nonse amene mukutchulidwanu you know the truth Mulungu adzakuyalutsani ngati mukuzitenga madolo.
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 22 часа назад
Ndiye kuti zawo ndizimodzi zokuphazi
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 22 часа назад
Akunkuyu olo azengereze chotani komabe kafukufuku adzakhalapobe basi akatswiriwo ndiye Commission of inquiry ikukambidwayo ndipo olo mufune musagune zichitika mpaka mupezedwa nonse
@AnyuxyJulias
@AnyuxyJulias 22 часа назад
Zosadetsa nkhawa iziii komwe kwalowela udf imaluza and marck mt wards iyiyi taonelana
@AnyuxyJulias
@AnyuxyJulias 22 часа назад
Esh