Тёмный
MALAWI TODAY
MALAWI TODAY
MALAWI TODAY
Подписаться
This Channel aims to inform, educate, Entertain and help Malawians.
CHISALE ACHOKE 2020 // ZIngaiwalike
2:08
Месяц назад
Brian With Msonda // Zingaiwalike
8:37
Месяц назад
MALAWI VS BURUNDI HIGHLIGHTS (Goals)
4:13
Месяц назад
UTM IGULIDWA POSACHEDWA//  Bon Kalindo
17:16
Месяц назад
KUFA NDI NJALA UTAPHODA // DENIS MAHATA
29:56
Месяц назад
BRIAN BANDA NDI PETER MUTHALIKA// TIMES
1:02:25
Месяц назад
Ati Gule uyu Salivina Bwino Mmbwalo.
7:28
2 месяца назад
A Kaliati Ayankhulatu
57:45
2 месяца назад
Комментарии
@MinaMazenge
@MinaMazenge День назад
Men of god
@MinaMazenge
@MinaMazenge День назад
Oh my God
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 2 дня назад
People mukamvesera ndi khutu lawuzimu zinthuzi zikumveka zoona ndthu koma twaibu mbari imodzi ya SATANIC sanatuluke ayi ndipo mpake amakwanitsa kumatsata ma protocols awo. And twaibu sanamasulidwe zeni zeni ayi chifukwa munthu otulula SATANIC sangamakhale pama programs awo mkumawonabe zonisika za SATANIC. mpamene muone kut mwendo umodz wa Twaibu ukanali kumidima ndipo take care naye uyu. HOSEA 4 VS 17
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 3 дня назад
Machimo kkkkkk
@HarleyLemani
@HarleyLemani 4 дня назад
My Lord, I am crying for my country, please bring it back...
@joanngrey8385
@joanngrey8385 5 дней назад
Bodza
@MartinBeza-w7t
@MartinBeza-w7t 5 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Tikusowani
@FalesichiutsiFalesi
@FalesichiutsiFalesi 6 дней назад
Talking to God is a serious business and not such a trush
@FalesichiutsiFalesi
@FalesichiutsiFalesi 6 дней назад
God can not listen such a prayer
@wisdomwizzie9944Jahblessevery1
@wisdomwizzie9944Jahblessevery1 6 дней назад
Kuona mimbaa mmene zakhutila within 4years iyiyi mmmm,, apapa tinaluza genius ngat dziko and will never find someone better than him
@vincentkachisi2932
@vincentkachisi2932 7 дней назад
HOW CAN I GET MANY OF HIS VIDEOS
@MalawiToday
@MalawiToday 7 дней назад
Try visiting his page on Facebook and send him a message
@Mobilot2android
@Mobilot2android 7 дней назад
Yah we need Mr Dausis presents mmmm mdala ameneyi ngobebesa however he failed us by lefting Dpp to Ng'ona party
@LETUSCHIPHUPHU
@LETUSCHIPHUPHU 7 дней назад
Ur legacy will still be alive ❤biyen
@gibsonnyasulu9432
@gibsonnyasulu9432 10 дней назад
Koma abale inu aaaa 😭😭😭😭😭😭😭💔💔💔💔 Oh God
@AnnetMndelemani
@AnnetMndelemani 10 дней назад
Akupatsa zingati????. Apa tizingopemphera kut chilungamo chiyende ngati madzi??¿,Inu munatani kuyitulutsa before pa 10 june.???
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago 10 дней назад
Koma kwachemeratu
@Lawrencenkhoma-b2s
@Lawrencenkhoma-b2s 10 дней назад
Lucias banda Ndy kuti samadwala kkkkkk
@issahmaloto9141
@issahmaloto9141 10 дней назад
😂😂😂 papa
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 11 дней назад
Inkuludingi inuyo.
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 12 дней назад
This interview needed social distance 2m each other 😂😂😂😂
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 12 дней назад
Mafutso amwana kkkkk Dausi 🔥
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 12 дней назад
Brian ndi Dausi interview yanu imabeba 😂😂😂😂😂😂😂
@JohnAsifathom
@JohnAsifathom 12 дней назад
Ziko lanthuli kupita pasogolo zizavuta mulungu adatipasa munthu uyu kt apitise zikoli koma timadana naye kaganizidwe kwanthu amalawi ndikopusa kwambili timasekelela zopusa pasogolo pake ndikumalila
@blessingsbandaa
@blessingsbandaa 13 дней назад
Nxaaaa
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 14 дней назад
Awatu ndi comedy not interview
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 14 дней назад
I would believe only if this video was released b4 the dismiss of SKC ngati mmene adapangira warn wa Bakili Muluzi TV uja kuti mdziko muno mwalowa asilikali aku Israel omwe apangidwa hire ndi MCP.
@leonardkayere9421
@leonardkayere9421 12 дней назад
Wanva koma date yomwe amayankhulira nkhaniyi?
@PatrickKamphimba
@PatrickKamphimba 15 дней назад
You changed my mindset, u r someone so special
@juliussamson6212
@juliussamson6212 15 дней назад
CHAKWERA KUSELIKU KWAZOSEZI KWABISALA IFA YANU NDITHA KUWONA TSOGOLO LANU PAZOMWE MWANKHALA MUKUCHITA KUCHITILA AMALAWIAN NKHAZA NDIPO MAPETO AYIZO MUDZAFA MOSANLHALA BWINO MWINA CHILIMA NUNAMUPHA BWINO KOMA INU ACHAKWERA MUKATENGERA MASEWERA MBALAME NDIZO ZIDZADYE INU CHIFUKWA ANTHU MASIKU ANO SAGANIZA NGATI 1964 AI TAKE CARE NDITHA KUWONA MWACHULUTSA KUMANGA ANTHU MWAYILA KUTI KULI NDIMOKALASE SUCHONCHO ANTHU ATOPA NANU CHOTI MUZIDZIWA MUKUKHALA CHIFUKWA CHAWANTHU OKHAWO ANAKUZUNGULILANIWO OSATI ZIKA ZA MALAWI ZIKUFUNANI AI ILO NDIBODZA LALIKULU INE NDI WAPALI LILONGWE KOMA INE NDANKHUDWA NDIZINTCHITO ZANU CHIFUKWA MUDZIKO MUNO TONSE NDIFE AMALAWIAN KODI NDINU MTUNDU WANJI WAMUNTHU CHIFUKWA INE NGATI MCHEWA NDIMENE NDIMADZIWAWILA MCHEWA ZIKUSEPHANA NDIZIMENE MACHITA INU MWINA MAKOLO ANU ANALI ODZIKONDA KUTHA MUNANGOTI MWAPHA MR CHILIMA ALIYESE OYIPA KWA IWE SUPEZE MTENDERE KUFIKILA IWESO UPITE KUMENE KULI MZIMU WA CHILIMA NKHOPE IKUSITHA IFA YA CHILIMA IKUWONONGA NKHOPE YA CHAKWERA MUZIMUWONETSA AKAVULA TITEDI WA SATANIKIYO
@InnocentBanda-f4d
@InnocentBanda-f4d 16 дней назад
Look for him again 😂😂😂
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 17 дней назад
A twaibu wa akunena zoona .ine ndaonapo anthu ku lunzu kwathu akuti anali bwino bwino .koma amanita kwa asing'anga kuti alemere Kenyansa ndipo.amapatsidwa ma kondition.olo zochita .olo zizimba .kuti azidhita koma akadzalephera adzafa..ndipò ambiri olephera kukwanitsa zozimbazo amàfa ena amapenga misala ena amasauka koopsya @ zina za ziźmbazo .ndi izi @ Asamagone ndi akazi awo @ Azigona ndi amai ao @ pomwe panyanye akakanda padzapunduka @ Azigona ndi ana aò @ Adzipha anthu kwao pachaka chilichonse.@Adziphe umuna wao..mpaka zaka 5 alatero mchaka cĥa 5 adzamwalira zangozi olo za dzidzi dzi.etc
@SellahBanda-cg9kh
@SellahBanda-cg9kh 18 дней назад
Akatundu
@MarkElia-i7q
@MarkElia-i7q 18 дней назад
Koma awa sazamenyana😂😂😂
@dysonchikunje1992
@dysonchikunje1992 18 дней назад
This guy is so genius,
@SolomonKafere
@SolomonKafere 18 дней назад
Brian Banda ndinu ,otsutsa mpaka kale
@SmilingFarmhouse-tf5ct
@SmilingFarmhouse-tf5ct 19 дней назад
Kkkkkkkkkkk axanga ama highschool please tamamasulilani English pleax
@MCLoudZeka
@MCLoudZeka 19 дней назад
Brian ndi Dausi eeeeee
@RobsaiSaidi
@RobsaiSaidi 19 дней назад
To be honest DPP was a mature government..this MCP came when economy was better, imagine a bag of maize was raised from 5000 to 12000 Malawi kwacha. Now its over 30,000 kwacha 😂 then presidential movement, very worse. Dausi was correct to say APM was moving not anyhow 😂
@RobsaiSaidi
@RobsaiSaidi 19 дней назад
Izeki ndi jakobo😂😂....awa azipanga panga
@WakuMalawi
@WakuMalawi 20 дней назад
Nicholas Dausi sounds like an extreme manipulator. Very weak mind.
@georgekesten3975
@georgekesten3975 20 дней назад
We need this guy again to interview him
@Littlefair7
@Littlefair7 21 день назад
Iwe unapitako? Koma ubulutu umenewu bwanji?
@ZachariaKapiyeEnock
@ZachariaKapiyeEnock 21 день назад
Nthawi imeneyo 1,000 dollar ili pa 7 50,000 pano ili pa 2.6 mita
@Felixbanda-q6p
@Felixbanda-q6p 21 день назад
shupit malawian prothert satanic
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 22 дня назад
Alikut kodi
@salimopromise
@salimopromise 22 дня назад
I like this combination 😂😂😂
@PetroAwazi
@PetroAwazi 22 дня назад
Mukanachula onse, why enawo mwasiya nkuchula okhawo anamwalira?.
@HildaMbizi
@HildaMbizi 22 дня назад
Wakakuwopani na fundo zinu chifukwa chake walikukukomani ku Chikangawa
@rozertmbale9545
@rozertmbale9545 22 дня назад
Koma Dausi zizunguzi muzitenga kuti?
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 22 дня назад
Anasakaniza ma colour ndi saulos ndi chakwera why munamupha chilima yekha
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 22 дня назад
Mcp propaganda zaboza izi