Тёмный

Brian With Msonda // Zingaiwalike 

MALAWI TODAY
Подписаться 10 тыс.
Просмотров 28 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 83   
@isaacimmantambala5294
@isaacimmantambala5294 Месяц назад
Brian knows how to handle anthu amwano, bwana ndinu professional indeed,, thumps up
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc Месяц назад
Brian Banda wausiru uyu ndamene anathandzira kugwesa boma 2020
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Месяц назад
Vuto la Kumalawi ndilimeneri, inu m'ntola nkhani amakhala ndi mbali? Iye amangofunsa kutengera ndi mmene akuwonera, taganizani nthawi imene ija ndi pano, chilipo chomwe mukuchiwona kusintha ndi Brian Banda PA mafunsidwe kapena kalankhulidwe???
@WisebornKapito-i5x
@WisebornKapito-i5x Месяц назад
Honestly speaking Msonda had an upper hand. Brisn apapa anapala . Next timehe needs to prepare, His questions were very personal.
@ChawasoMlotha-ys6bf
@ChawasoMlotha-ys6bf Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 Brian ndi machine
@JoannaNAMA
@JoannaNAMA Месяц назад
Nthawi imeneyo ma dollar akupezeka m ma bank mbwe mbwe, koma lero mmmm 😂😂😂
@kingtiles-g6q
@kingtiles-g6q Месяц назад
kom brain anthu azakumenyani amwene kkkkkk koma mumakwana kumalawiko kwambiri
@RossanaMitha-tl9in
@RossanaMitha-tl9in Месяц назад
😂😂😂 koma Burayani amandiwaza bwanji.kkkkkk
@HassanMussah-i9j
@HassanMussah-i9j Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 eishee vuto ndi wangayu kufusa fusa
@AliajoeAliajoe-vv1wo
@AliajoeAliajoe-vv1wo Месяц назад
Akugwila m'boma koma angosala mutu okha😂
@mrkachama
@mrkachama 23 дня назад
Mafuso opusa awa
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Месяц назад
izi zakale zonda akudwala kwambili nthawi imene analandila nthandizo lakuchipatala kuchokela ku dpp
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 Месяц назад
Kodi mr Nsonda bwanji mwano😅😅😅😅
@SymonZemben-gd3ne
@SymonZemben-gd3ne Месяц назад
Interview yakalekale iyi bwana bwanji Kodi🤣🤣🤣🤣🤣🤸🐐
@TriciaFaluku
@TriciaFaluku Месяц назад
Kkkkk kma brian anakoza 😂
@MoosaSame
@MoosaSame Месяц назад
Kkkkkkk msonda ndiwakuba uyu mtayenu Brian Kkkkkkk
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Месяц назад
Guys nsonda is not about ma ARV, its just it's behaviour asanayambe kumwa anali chonchi kale, respect him don't criticise him
@BennieKanama-yr3sh
@BennieKanama-yr3sh 20 дней назад
😅😅😅😅Msonda amazemba mafunso
@MustafaAbdullah-pb5zv
@MustafaAbdullah-pb5zv Месяц назад
Kkkkk Amsonda,mwamtsamwitsatu Brian
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 Месяц назад
Eeee Koma mukuti mzondayi mutu Mwake sapeza bwino sure. mtolakhani amafusa fuso lina lililonse chifukwa amava zimene anthu amayakhula ndiye akasale kudya nkhani yake iti kkkkk koma
@StevenAmosiBanda
@StevenAmosiBanda Месяц назад
Kkkkkkkkkkkkkk koma
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Месяц назад
Kodi awa dyela loyambila kale 😂😂😂😂😂
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Месяц назад
AAA nanga zija lelo siizizotu kuti sonda ndiofoyila
@Stretor
@Stretor Месяц назад
Koma nde zinaliko2 kkkkkkkkkkkkkkkk
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Месяц назад
Palibe chipani chomwe ndikuona kuti chidzakhoza chilichomse Sindikuonapo wabwino Chifukwa omse omwe ajutikota lelowa Ndiomwewomso ankatokoza kuchotsa zipani zamumbuyomu Leloso anthu omwewo akuchotsaso chipani chomwe amkawauza anthu kuti votelani awa Padziko lapamsi Wangali yambone😮
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Месяц назад
Zowona komano apa zafika Pena pochita kuwona ndi mwana yemwe 😢😢😢
@MussahJenala
@MussahJenala Месяц назад
Brayani iweyo mbambande ❤❤❤
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Месяц назад
Ken Nsonda ali ndi Manyi pakhosi
@AdinieMakumba
@AdinieMakumba Месяц назад
Brayan unakumana ndi Mvula zakale
@SAMARTEDWART-b1j
@SAMARTEDWART-b1j Месяц назад
Kkkkkkkbkoma brayani banda ndi wani mmmmm
@wilbroadm
@wilbroadm Месяц назад
😅😂😂kkkkkk
@S-rr1eu
@S-rr1eu Месяц назад
Msonda,,, kuphwanyika mutu ngat mulomo wagalu
@hawardmkandawire673
@hawardmkandawire673 Месяц назад
😂😂😂
@yassinn5634
@yassinn5634 Месяц назад
Nthawi imeyo Brian Banda akunyoza DPP akusapota MCP pano ata muchotsa ku State house anatembenuka akusapotanso DPP yomwe ankainyozayo. Dziko lapansi ndilozunguliradi. A Msondawatu apa ntchimo lawo linali lakuti alowa DPP basi.
@watsonmhango8794
@watsonmhango8794 Месяц назад
Nsonda ndi wamwano😂😂😂😂😂😂
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Месяц назад
2014 kuna chema😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂kkkkkkkk
@zamanmwachumu554
@zamanmwachumu554 Месяц назад
Brian no apapa simunathe boss
@esaumvula1133
@esaumvula1133 Месяц назад
Kkkkkkm zilibwino ❤😅😅😅
@RestarUmi
@RestarUmi Месяц назад
Wachita bwino kumukhaulisa amenei kkkkkkk
@JasonMailos
@JasonMailos Месяц назад
Msonda pamtumbo poko kazikomwani mA ARV-wo basi
@FLEACHERMsonthi
@FLEACHERMsonthi Месяц назад
Hahaha 😂sadya kwanu kkkkkk
@DysonKamama-yh7hq
@DysonKamama-yh7hq Месяц назад
Ati koma za tikitizija😂😂😂
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад
Mavuto ndamodzi DPP inaliso mavuto pp inaliso mavuto kkkkk osanamizanaso mavutosadzatha dzikolabas
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Msonda ndi wamisala uyu ma ARV amukwana
@hawardmkandawire673
@hawardmkandawire673 Месяц назад
😂😂😂
@OrisChitseko
@OrisChitseko Месяц назад
Koma chidzukulu cha A nanjayiko
@Okalekale
@Okalekale Месяц назад
Ndiye nkumati DPP ilowensi?,never sitinayiwale,ogona yekha
@Mgabehganesh
@Mgabehganesh Месяц назад
😂🤣🤣
@JoeMussa-d8u
@JoeMussa-d8u Месяц назад
😂😂😂😂😂
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 Месяц назад
Brian ndi satana uyo tamusiye
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma Месяц назад
Unya mabi nsonda satana ndiwee
@HanafiBadat-i8s
@HanafiBadat-i8s Месяц назад
Zakale kale izi
@JoeMussa-d8u
@JoeMussa-d8u Месяц назад
😂😂😂😂
@AskMeDalitso
@AskMeDalitso Месяц назад
A Nsantha ma ARV sanawayanjetu
@AroushMussah
@AroushMussah Месяц назад
Koma kumeneko 😂😂😂😂😂
@SostinMatchado-z2o
@SostinMatchado-z2o Месяц назад
Koma abale eeeeeh kulankhula kwabwanji kumeneku
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago Месяц назад
😂😂😂😂Koma kunachema
@NyangwaKoma
@NyangwaKoma Месяц назад
Koma asonda ndonyasa
@AddjaihAddisMsukwa
@AddjaihAddisMsukwa Месяц назад
Ziliko kumeko
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад
Eya zakale koma kumavutaso khani zandalama sleep ai
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi Месяц назад
😀😀😀😀km yaaaah
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Месяц назад
Anthu omwa ma ARV amakhala amakani
@FRIDAYBANDA-m8i
@FRIDAYBANDA-m8i Месяц назад
Amsonda you are very brave more than a jounalist
@TrumanMadan
@TrumanMadan Месяц назад
Kkkkkkkkkk
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t Месяц назад
😂😂😂😂yatha changu
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt Месяц назад
A msonda iiih sizinthu
@MaryBanda-n3h
@MaryBanda-n3h Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 Za 2024
@JamesDismael-z4y
@JamesDismael-z4y Месяц назад
A Nsonda mumakwana koma vuto tinakuluzani koma ndimakukondanibe basi
@DixonChimanya
@DixonChimanya Месяц назад
Nsonda boli yako
@felixmavuso8120
@felixmavuso8120 Месяц назад
This interview was not so constructive . So personal. Brian tried.
@RajabShahida
@RajabShahida Месяц назад
Kkkkk brian ndi 1 msonda ndi chitsiru
@ShajaCaleby-w8b
@ShajaCaleby-w8b Месяц назад
Brian osamatelo pepan chepetsan moto
@ThomasGondwe-g4x
@ThomasGondwe-g4x Месяц назад
Kunachematu
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo Месяц назад
Kkkkkk
@MillioussBrighton
@MillioussBrighton Месяц назад
Kkkkkkkk
@kaybillionaire7732
@kaybillionaire7732 Месяц назад
kkkkkkkkkkkkkkkk
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Dpp nthawi yawo imeneyo
@MilikaKilion-tn1bn
@MilikaKilion-tn1bn Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@LilyMbewe
@LilyMbewe Месяц назад
😂😂😂😂
@hawardmkandawire673
@hawardmkandawire673 Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@mussatambuli6077
@mussatambuli6077 Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад
😂😂😂😂😂
Далее
Nancy vs Che Nkope - Apatseni moyo wautali
11:05
Просмотров 3,7 тыс.
Brian Banda Interviews Ken Msonda
8:37
Просмотров 48 тыс.