Тёмный
Hanifa Mw
Hanifa Mw
Hanifa Mw
Подписаться
Hi - its Hanifa mw !

This channel explores my discoveries and perspectives on various topics through entertaining documentary like story -style videos!

Follow me for behind the scenes, teasers, and everything in between:
📸Insta -Hanifamw
facebook - @Hanifamw

Business/Sponsor Inquiries //hanifamw.suggestions@gmail.com
zionetsero Za Polisi Ku Blantyre
3:45
2 месяца назад
Mabvuto Kokhwima
10:36
2 месяца назад
MCP Kumangochi Yayaka Moto
10:08
2 месяца назад
EXCLUSIVE: Interview With Zacc Kawalala
48:59
2 месяца назад
Milandu Yakuba Ya Saulos Chilima Yatha
11:13
3 месяца назад
Nawo Osatira Chipani Cha  UTM Akulira
11:22
3 месяца назад
Nawo Achinyamata A MCP Akulira
14:00
3 месяца назад
Zinthu Zikungokwera Monga Mwa Dzina Lawo
12:38
3 месяца назад
Akuti MCP iwinaso 2025 Zifukwa Zake Nazi
10:51
3 месяца назад
Fredokiss-Andale Akunamiza Achinyamata
11:18
3 месяца назад
Комментарии
@CharityKantunda
@CharityKantunda 5 часов назад
Ufiti ulipodi
@ChikondiBJosaya-pr1zu
@ChikondiBJosaya-pr1zu 6 часов назад
Mmmmm izi ndizidabwisandi
@user-sm8gx4vf1v
@user-sm8gx4vf1v 10 часов назад
Inuso za bodza nde ayi mudzipemphela
@AllanMtambalika
@AllanMtambalika День назад
Aaaaaa zimenezo zikuchuluka hvy
@user-vl8uw8mc3u
@user-vl8uw8mc3u День назад
Dpp ndi Apm woyeee
@alomuddin8801
@alomuddin8801 2 дня назад
Pepani amalawi tiyeni tikavote km Kuvota mam zeru chonde x 2 tivote a Malawi, Mcp ichoke m boma chilichonse chadula
@JaziraHaward
@JaziraHaward 2 дня назад
Gumulila
@daviechannel8603
@daviechannel8603 3 дня назад
Mmmmmm
@ChimzyEntertainment
@ChimzyEntertainment 3 дня назад
Pangolin wenwen 😢😢😢
@NeoSoko-mo2gw
@NeoSoko-mo2gw 3 дня назад
Mayi kd anakupasani zingati moti paka inu muzichimwa chotele
@HumphreysBanda-e7g
@HumphreysBanda-e7g 3 дня назад
Amatero anthu ndi Obama zimachitika Koma anthu akewo sakhalitsa ndipo imakhala plan ya asi Ganga amatenga ma information kwa anthu a pakhomo kenaka kumabwera gulu Lina mkumati ayi siwanu ndi wathu imakhala ma plan awo
@HendersonDziwa
@HendersonDziwa 4 дня назад
❤chkondi sakakamiza khanza gwelo lake nd imfa
@ChippiepalsMikwamba
@ChippiepalsMikwamba 4 дня назад
Kungotithera bundle basi.. Nyimbo ili kuti?
@RajabKhombe-l4l
@RajabKhombe-l4l 5 дней назад
Ambuye enkha akuziwa
@MerryWayson
@MerryWayson 6 дней назад
Yothoyo mwanambwaaaaa
@SilviaKamphonje
@SilviaKamphonje 6 дней назад
God is good
@IssahAluba
@IssahAluba 6 дней назад
Wakufa samadzuka mayiwa Ali okwima aaaaa
@EsmaelsebastiaoSebastiao
@EsmaelsebastiaoSebastiao 6 дней назад
Pornografia african
@MarhaKamowa
@MarhaKamowa 7 дней назад
ndiko lamalawi linachuluka kaduka kwambuli kaduka akuchedwetsani amalawi mulungu amadalitsa kwaolimbikila bwana skeffa ulemu wanu chanu sikanga chanu ndichanu bas
@CharlesMatope-xg6ln
@CharlesMatope-xg6ln 9 дней назад
Yes that's true komano gobo anaipitisa kuchamba chamasiku ano
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 11 дней назад
Bushiri si polofiti
@user-fy5lw8vk9k
@user-fy5lw8vk9k 11 дней назад
Kodi mukutichani Apapa...Ngati mwasowa zoposita pa line
@DavieKaumphawi
@DavieKaumphawi 11 дней назад
Wonderful story 😮
@VeronicaChimoyo
@VeronicaChimoyo 11 дней назад
Mmmmmmmmmm bodza mmesa mwanena kuti munthu simukumuziwa aaaaaaa
@user-bp4hp6qv1r
@user-bp4hp6qv1r 12 дней назад
Anthu oipa inu
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc 13 дней назад
Mwachita bwino galu uyu chakwera
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 14 дней назад
Chakwera ndi shit asatipusise tiphanapo
@GreciphiriGaute
@GreciphiriGaute 14 дней назад
EEE ayi uyuso atiopsa
@leahkasiwa5033
@leahkasiwa5033 15 дней назад
Muuzeni kuti ndine abwere azanditenge
@KingstoneMnelemba
@KingstoneMnelemba 16 дней назад
Prophet wanji opanda dzina?
@PemphelaniTcheza
@PemphelaniTcheza 16 дней назад
Bushiri sanathawe koma adabwelera kwawo😅😅
@BenardNawasha-sc7he
@BenardNawasha-sc7he 16 дней назад
ru-vid.com/video/%D0%B2%D0%B8%D0%B4%D0%B5%D0%BE-HvVup_rcu8M.htmlsi=z4Lg5daEg4tmPwcb
@CharlesMkweche-n2s
@CharlesMkweche-n2s 17 дней назад
@OswinDzama
@OswinDzama 18 дней назад
Zodabwitsa😮😮😢😢😊
@user-dg7sl1eu1n
@user-dg7sl1eu1n 18 дней назад
😂😂😂😂😂
@PaulNtonya
@PaulNtonya 19 дней назад
Mukunama kuti zikolino ndilosauka ndinunokhanokha anthu osakonda dziko lathu lino inukuwina rero mufunaso muremere kaye inundiabare anu apaparibewabwino
@levisomba9017
@levisomba9017 20 дней назад
Osangowelenga bwino bwaaa
@user-by6ky8qm8v
@user-by6ky8qm8v 20 дней назад
Kaye ma Diples😂
@FrankYohane
@FrankYohane 20 дней назад
Ndondocha za prophet zimenezo! Anthu anamuza Yesu samalani afuna kukupusitsani,ndiye zili masiku ano
@FrankYohane
@FrankYohane 20 дней назад
Samalani abale nonse mu dzina la yesu awa tikuti ma profit ndi asing'anga akutiphera abale athu ngati ndondocha kenaka ndikuwanweza ali olumala ife tiziti profit koma uyi. Tili masiku otsiliza osaiwala zimezo abale chonde abale samalani nawo amenewa
@MercySatumba
@MercySatumba 20 дней назад
Tionetseni wokufayo
@JoyceTembo-ii1ot
@JoyceTembo-ii1ot 20 дней назад
Kazi ndiwaboza mamuna wake sangafanane ndizake zochitika muthu aliyese alindisungo
@WilessiKacherenga
@WilessiKacherenga 21 день назад
Mmmmm zovuta bwanji
@ElinaBanda-gh7ye
@ElinaBanda-gh7ye 21 день назад
Nanga zadress lomwe anavala akumwalira anaziwa bwanji😅
@VanessaSimpokolwe
@VanessaSimpokolwe 21 день назад
Amene wamva mumimba ndi amene amasegula......ngati akufuna Baja lithe is it a problem....go ahead miracle ...banja sichiphinjo
@emmakamwendo1370
@emmakamwendo1370 21 день назад
Awesome
@bdbigdream9015
@bdbigdream9015 22 дня назад
Amalawi akaona nkhungu lofiira eish
@SanudiMcDonald
@SanudiMcDonald 22 дня назад
DPP singawine payokha popanda chipani china chothandizira 🤞
@GiftMbewe-z4u
@GiftMbewe-z4u 22 дня назад
God is going to judge one by one.
@FelidaKazembe-u1l
@FelidaKazembe-u1l 22 дня назад
Zovetsa Chisoni