Тёмный
No video :(

Zinthu Zikungokwera Monga Mwa Dzina Lawo 

Hanifa Mw
Подписаться 72 тыс.
Просмотров 7 тыс.
50% 1

Zinthu Zikungokwera Monga Mwa Dzina Lawo

Опубликовано:

 

26 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 34   
@ContentCorgi-kx3tb
@ContentCorgi-kx3tb 3 месяца назад
Chakwela amandibhowa kwambili muthu ameneyu Anabala ndan galu ameneyu
@mamulemathekga
@mamulemathekga 3 месяца назад
Chakwera ndiyeza nyanya kwambili sindusiku dura kwambili kunenaso ona achakwera alepela kotelatu oloyve mtili kujon tikuva kuwawa kwambili 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@getrudekaphesi1917
@getrudekaphesi1917 3 месяца назад
Zosayenda eeeeiish
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 3 месяца назад
Malawi wathu watha zedi
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Tikanakhala ogwilizana amalawife tikanasakha chipani chimodz chomwe chizawine,vuto tikuvutika koma aliyense akukavotera yemwe akumufuna zosatila zake timavote to tinyemedwanyemedwa koma aaaa
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 месяца назад
Chakwela mbava
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 месяца назад
Akut ine ndi chakwera kut tipikisane ndingawine ndine😂😂😂😂😂😂iiiii kma chakwera Ai ndithu
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 3 месяца назад
Km kunena zoona anthu akuvutika kwambiri zomvesa chisoni kwambiri
@user-ub1vt2kq4s
@user-ub1vt2kq4s 3 месяца назад
Chakwera must go,chifukwa akuba kwambiri wasaukitsa dziko la Malawi kwambiri
@Pangolinimw
@Pangolinimw 3 месяца назад
chakwera mapwala ake alipwisi
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 3 месяца назад
Chakwera must go no matter what next year
@dontreybanda278
@dontreybanda278 3 месяца назад
Chakwera achoke basi
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 3 месяца назад
Dpp woyeeeee boma
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 3 месяца назад
Komasotu dzinadzi ndidzofuna munya muwona
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 3 месяца назад
Mapwala ako
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 месяца назад
chatsika koma APM only hope for malawians chakwera out and must go 2025
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 3 месяца назад
A Malawi tikuvutika chifukwa azitsogoleri ndi akuba.
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 3 месяца назад
WE NEED REFERENDUM IN MALAWI PLEASE
@UseniMailosi
@UseniMailosi 3 месяца назад
Chakwera ndiorepera
@GeorgeLungu-bt6hf
@GeorgeLungu-bt6hf 3 месяца назад
Achoke Palowe ena
@DavidCazembe
@DavidCazembe 3 месяца назад
Kkk 😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 3 месяца назад
Chakwera he's the worst president ever in Malawi history.
@JesterChakalamba
@JesterChakalamba 3 месяца назад
Anthu Inu palibe olamulira yemwe azapanga zifuna zanu palibe only Jehovah basi izi or mutalankhula bwanji or mutasintha bwanji muzalira mpaka kale mpaka ufumu wake ubwele basi mwana obadwa Kwa mkazi sangakoze zinthu kulibe
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 3 месяца назад
NO PAIN NO GAIN GO BACK 2 SCHOOL BOY
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 3 месяца назад
Nanunso simukutha kuwona Zoti Zinthu zidadokonekera? Nthawi ya ulamulilo winauja anthu amapanga blame? president like Mesa kutathaudza Nthawi imeneija zidali bwino than now. Ndi president waumbuliyo
@JesterChakalamba
@JesterChakalamba 3 месяца назад
@@ThokohKalonga-je9rx whether you like or not trust me zinthu sisizasinthapo mpaka kale may be your young you don't know where we were ndipo tikupita kuti just do your part kuti udye munthu sangathe mavuto Ako gwilantchito
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Kod akuyakhulira kut awawa
@JesterChakalamba
@JesterChakalamba 3 месяца назад
Ndinabadwa mama 70 from 1994 up to now palibe Chaka katundu atsikapo momwe zinthu zinayambila kubwela nthawi ya Bakili sizinasinthepo tamawawuzani zolimbikitsa azigwila ntchito molimbikila osati kudalira munthu n0
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 3 месяца назад
Mwan bu make buu go back 2 school sml boy
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z 3 месяца назад
Machende anu
@JesterChakalamba
@JesterChakalamba 3 месяца назад
@@user-tk6wf2eg4z gwila ntchito mphangwa izi sizikupindulira
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Awaso akuyakhula zamkutu apa,
@YusufuKaifa-fr4wt
@YusufuKaifa-fr4wt 3 месяца назад
Nziko la malawi akusangalala anthu Ali ku boma basi koma ntosefe tili kunja kwa anthu a boma .. tikusphya moto ndithu 😭😭😭😭😭😭🥶🥶🥶
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 3 месяца назад
Komatu wanthu wenawa NKU tembereredwa, ngati akuvutika Wanthu abwino bwino kuli bwanji wopunduka koma sibwino choncho popeza munamu sankha nokha muzaona chochita ife tatchona kunja kuno kumeneko tina choka Kale Kale
Далее
O'ZBEK VA TOJIKLAR ROSSIYADA TERAKT UYUSHTIRISHDI!
08:41
WILL IT BURST?
00:31
Просмотров 20 млн
Dokotala Wa Misala || School Days
14:47
Просмотров 237 тыс.
CHIBANGILI CHIKUPANGA ZODABWITSA KU BLANTYRE PART 1
13:53
ANTHU ATHA MANTHA AKUIMBA ZACHILIMA PALI APOLISI
14:14
O'ZBEK VA TOJIKLAR ROSSIYADA TERAKT UYUSHTIRISHDI!
08:41