Mr president,,,,you're responsible to bring the solutions,,,,not asking us the way forward,,,,just command what suppose to be done,,,,adzikupisani mr ussi,,,fundo
Amalawi munansanga wolakwika mbambadi course wochakwela wolibe mfundo nthawi zonse amakalila mawu amodzi please next time we need be very careful pangani yonsanga upule chifukwa ntchito iyi sintchito yamasewela ayi yy😢😢😢😢😢😢😢😢
Mr president how many advisor do you have? Is it a speech to tell malawians? That is speechless, am not against with you but as president mumayenera kukhala ndi fundo zogwilika, zopasa chiyembekezo koma mmmmmmm tidabesa amalawi koma Mulungu atichitira chifundo
Mmmmm koma pa chakwela nde tidabetsa basi kuchitakusowa ndi mfundozomwe iiiiii amalawi basi tilibe chiyembekezo? Chakwela ndi panja pa munthu😢😢😢😢😢💔💔💔💔💔
Andale inu muziyamika chifukwa kuno ndi ku malawi, koma kunakakhala kuti ndi ziko la mkhongo ine ndinakakhala mmgulu lopanga upo okuphani for sure inu nonse ndi mbeu yoipa kwambili.
Chilungamo, kuvotela (Ras Chikomeni Chirwa) munthu wapadela, amene ali ndi mfundo zothandiza dziko la Malawi, Dpp, Utm,Mcp Udf, no more we need new leadership.
Kkkkkk inu kodi ndindani mukamakhala mumati ndini ndani Eliya wabwera Abushiri alipano mukawauze Ambuyanu kuti Eliya wabwera mukamalira Achilima ali apo Achakwera ali apo dziwani kuti aEliya wabwera amanena ndani Bushiri kapena ndani mManganya sazatheka
A usi koma muli ndi ku mudzi inu,? Ngat mulinako mmapita koma? Mwayankhula ngat mukukhala kunja kwa dziko linotu, kuyankhula kot akuchemeleleni mabwana anuwo zomwe zili zaziiiiiiii ndizotipsetsa ife mitima
Kunyoza mtsogoleri wa dziko ndi tsoka.Anthu a kumwera kwa Malawi savomera kuti utsogoleri achakwera ndithu ndi . mtsogoleri wathu lero,mpaka pomwe Mulungu afune.
Muzizipemphelela nokha ndani amene angamataye nthawi yake ya padela ndikumapanga za inuo ngakhale iweo usi fodya bas uzipemphelele wekha wamva iwe za ugalu basi
This country we have start war 😢 guyz amene mwakozekha bweran ku Dm tayamba group yomwe tingayambitse force acting komaso u'll get salaries b4 kulowa nchire
Usi ndi team yako yonse ya tonse alliance simukuziwa chomwe mukunena, munataya pangano posachita zomwe munalonjeza God will punish you. Iwe Usi uzikanyadira kuthandizidwa zoona pomwe inu mungoba ndalama xa misonkho??? Shame on you tonse alliance.
Chakwera always speaking zosagwira mtima ndizosemphana 😢 mwaiwowa mulibesi utsogoleri wamdziko apite ku ubusa kwaoko. I will not say tye truth to you mr president simutha kuyendetsa dziko 😂😂😂😂