Тёмный

AKUFUNA KUPANGA ALLIANCE NDI MCP ALI OLANDILIDWA | 

DZIWE TV
Подписаться 31 тыс.
Просмотров 2,9 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

10 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 34   
@Lingstone-r3z
@Lingstone-r3z 25 дней назад
No more to join with MCP never
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 25 дней назад
Agalu inu a MCP ,kuti kumene mukuyika moyo wa munthu wakumudzi patsolo,anthu akupha inu,palibe amene atapange nanu alliance ulendo uno, ndiponso chilungamo ndichoti popanda kubela simungawine zisankho,mukadzangowina tidzazwiilathu kuti mwabela
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 25 дней назад
Zisankho za Normal Simungawine a MCP, Mukamuzutse kaye Chilima ndi ena 8
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 24 дня назад
Kwambili akadzuse chilima chifukwa adamupha chilima pofuna udindo ndiy asake owajoina munyaaaa
@PaxKinley
@PaxKinley 25 дней назад
MCP MUKHAULA MUNYA MULIRA KUGWA KUJA NDI KUMENEKU PALIBE ANGALORE ZA UCHITSIRU UMENEWO.... KUBA, KUPHA
@Marymahendra
@Marymahendra 25 дней назад
Sorry nobody else wants to join MCP party in the future until Jesus Christ comes back xx
@JustinMdala-c1t
@JustinMdala-c1t 25 дней назад
Kodi chipani chimenechi anthu Ake onse NDI osagwira Mitu bwino bwino pamwamba phaka kumutsi palibe amakamva zogwira mtima kumangoyankhula Ngati Ali maliseche
@user-cv3zw9ic6d
@user-cv3zw9ic6d 25 дней назад
Ndipo azipami musalore kugwiliza a ndi Malawi Chikangawa Party mukufuna zipani zilalowa mgwilizano muzawaphenso ngati Chilima agallu inu
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z 25 дней назад
Mwapha chilima pofuna kuti chakwela wanuyo alamulitso
@user-hl1jt6eo3d
@user-hl1jt6eo3d 25 дней назад
Kk wachedwa utalawilila sister
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 25 дней назад
Muisova amene akufuna kukafera ku chikangawa apite 😅😅😅
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 25 дней назад
palibe chipani chomwe chingapange alayance chifukwa mcp ndi chipani chokupha tawonera pa chilima mayi inu pantumbo panu ndithu munya muwona
@ManganiStanley
@ManganiStanley 25 дней назад
agalu ngti inu Pali wina angalore kt ajoine anthu oipa ngti inu
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 25 дней назад
Mcp iwalani zoti anthu akhonz ku join inuyo anthu ambiri akukuopani chifukwa ndinu okupha okupha oononga simusamala zaanthu
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 25 дней назад
Eeeeeeee mpaka alliance ndi mcp???? Koma kukhala kufunanji
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z 25 дней назад
Muiwale kuti mupanga gwirizano ndi ena Mwapha chilima
@isaaczuze
@isaaczuze 25 дней назад
Anthu okupha amene angachite nawo ubale ndani ....muona ndi ziko ili
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 25 дней назад
Ntolankhani okongola km masamu anatulukira pawindo
@JorgeSacuate
@JorgeSacuate 25 дней назад
Mayi oputsa iwe. Mufuna mupeze ngalawa yowolokera?? Muzawaphe kawiri mukazavoteredwa. Iwe ndi chakwera wakoyo cha.......................chanu
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 25 дней назад
Allience ya ukapoloyo tiyeni nayoni ukoo
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c 25 дней назад
Wasowa n,tengo ogwila azionaa
@user-wl7xn3or6d
@user-wl7xn3or6d 25 дней назад
Eeee mwaphela chilima muja anga pite ndani eee ndinu oopsyaaa kwambilili
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 25 дней назад
Chipan cha magazi manja and khope yonse ya chakwela i kumaoneka magaz okha okh a achilima ndi athu ena 8
@Martha-m6e
@Martha-m6e 25 дней назад
😂😂😂😂mwaganiza bwanji MCP
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 25 дней назад
Alimi afodya tanjoya boma lomweri basi mukatibera enanu
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 25 дней назад
mcp bomaaa kuti buuuuuu 2030 woooo
@user-hl1jt6eo3d
@user-hl1jt6eo3d 25 дней назад
@@mabvutochimkondenji910 iwe where where your mind.your not normal
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 25 дней назад
Ngozi ndi ngozi ku brazil adamwatila anthu 62 pa ndegenso
@MzadziWanga
@MzadziWanga 25 дней назад
Kma sanavulidweko zovala ngakhale president wakonko sanaime kufufuza ngozi itachitika
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 25 дней назад
Mwanya mwadya chilima yemwe uja ndiolose ndikakutafune asaaa ndani akufunaso ku chikangawa
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 25 дней назад
Ndipo mukadakhala kuti mukufuna kulamuliranso next erections mukadasutsana kaya zopha chilima zija koma mudady mfulumila ndiye zikuvutani ndithu😊😢
@Ghama-k4i
@Ghama-k4i 25 дней назад
Apiteso ndan angalore ndenge
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 25 дней назад
Inu palibe angakuyandikileni ufiti wanu uli pamtunda
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 25 дней назад
Munya.inu.amcp.muona
Далее
AGRICULTURE POLICY CONFERENCE 2024-MALAWI
3:46:29
Sameer Suleman anapangidwa attack ndi MP wina wa MCP.
11:31
A NAMIWA AYANKHULA MOSAOPA🤔🤔🙌
34:56
Просмотров 22 тыс.