Тёмный

ANANDIKWATIRA NDILI NDI ANA ATATU KALE...true love 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 58 тыс.
Просмотров 26 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

1 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 46   
@mirriamwilliam-nq9wg
@mirriamwilliam-nq9wg 4 месяца назад
Zikuchit kukoma ngat zisathe mmmmm ndazikonda kobas,,, inenso chisomo chindigwere Amen
@bandacharles82may
@bandacharles82may 4 месяца назад
Very interesting story. I hope this story will inspire alot of people. Provided that its belt on the basis of true love.
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 4 месяца назад
Zabodza Anthu opephera amanama kwambiri mmalo moti anene zoona amanama ponamizira dzina la Mulungu
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 4 месяца назад
Osamathamangila kuweruza sionse abodza ena ndiophera km Ali asatanic amenewo ndye abodza osamatenga opephera ose ndabodza ena akupemphera Ali thumwi zasatana ena akupemphera Ali ake Eni Eni aMulungu samalani poyakhula
@jennyx6914
@jennyx6914 4 месяца назад
she cant keep the secret of dreams to her husband akuti zamaloto akumvera pompa boza boza leni leni ili onse amafunana kale
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 месяца назад
Nde anthu a Satanic ndi achilungamo?? Nanunso mumayankhula mopepela bwanji. Adakulodzani mukamugwadire
@violetpotani
@violetpotani 2 месяца назад
​@jennyx6914😅😅😅😅
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 4 месяца назад
Komatu nyimbo zinazi ndiutumiki eish, am not here to judge but sometimes we have to ask yourself about your position .mkazi wabusa kukonda nyimbo za anthu ovula kuchita kuyitsata
@HortencioSamuelOfessi-e5c
@HortencioSamuelOfessi-e5c Месяц назад
Koma zodabwitsa bwanji zimenezi zosangalatsa kwambiri mwanipatsa chitsanzo chabwino niyerekeze NDI ABRÃO NDI SARA ZIKOMO 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 4 месяца назад
Komaso ukapedza nkazi okulilapo ummm amakakamilatu kkkk abusa kupanga ukwati nkazi woti ndiobelekapo kare
@CatherineMtchona
@CatherineMtchona 4 месяца назад
Ndazikonda ambiri tikuvula chifukwa cha ana mmmmmm ambuye tsegulani makomo
@jennyx6914
@jennyx6914 4 месяца назад
12 years nkukhala uli pa banja? after might prayers anakhailita yekha yekha ndi family ya abusa zoona? anali ndi mission mzimayiyu ulape ulape plz mzimayi iwe chonde
@jennyx6914
@jennyx6914 4 месяца назад
inenso ndikuona boza mu story iyi bcz sanali maneba how come osungitsa key. adutse wapafupi kwambiri? again munthu omukonda ngati akuthetsa chibwenzi akanafunsa why? whats wrong? ndiwachimaso maso pastor ameneyo
@violetpotani
@violetpotani 2 месяца назад
😅😅😅😅
@EnifaJosafati
@EnifaJosafati 4 месяца назад
Zili bwino kwambili God is good
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 месяца назад
Kupeleka madzi kwa bambo chogwada ai zikomo
@violetpotani
@violetpotani 2 месяца назад
Apa tivene kaye zinazo pambuyo😅😅😅
@GracePhirie
@GracePhirie 3 месяца назад
Nde bambowa anali virgin ok😂
@chisomodouglas2084
@chisomodouglas2084 4 месяца назад
Mayiwa nyimbo asankhayo ndimmene akutanthauzilira sindikuwonapo vuto enanu mumathamangila kuweruza ena chonsecho nyimbo mukuti zachikunjazi mu 4n mwanu zilimo ndipo mumavera kma akavera wina walakwitsa
@richardbanda3677
@richardbanda3677 3 месяца назад
Great couple; friendly, kind and full of advice. Timakunyadirani anthu inu!
@nifaKutaumbe
@nifaKutaumbe 3 месяца назад
Taziwa zimene zinali behind the journey of this wonderful couple
@EthelOsman
@EthelOsman 4 месяца назад
Mmmm mulungu alipodi anthu tikugwila zibalo poti ana tilele tonse ambuye Zikomo
@Catherinembowe
@Catherinembowe 4 месяца назад
Atumwi munasonyeza kukhwima mmaganizo ndinu chitsanzo chabwino
@GeorgePatels-go7wj
@GeorgePatels-go7wj 4 месяца назад
Ndiye mai busa kusankha nyimbo yachikunja why?? Mmmm ayi zikomo utumiki
@GeorgePatels-go7wj
@GeorgePatels-go7wj 4 месяца назад
Ndiye mwamuna wa mai busa oyamba kumwalilira kutulo mmmm ??? Akuti mzimu wa amuna awo ngati akumva , akufa sadziwa kanthu bii
@vatineseduwin
@vatineseduwin 4 месяца назад
banja ili landisangalasa kwambili mulungu segulani makomo
@PetroKachingwe-jf7dh
@PetroKachingwe-jf7dh 4 месяца назад
That's interesting story God bless our families
@BerthaChisoni
@BerthaChisoni 4 месяца назад
Ndinaphunzila nawo abusa akazi ku primary school
@JuuuKomba
@JuuuKomba 4 месяца назад
Waana awili atha kundi hala zisomo zilipo kuno 😂
@NaomiGondwe-og5hg
@NaomiGondwe-og5hg 3 месяца назад
God bless your marriage ❤
@ishmaelbofa1159
@ishmaelbofa1159 4 месяца назад
Koma abusa inuyo musangalala ndimoyo owawawu
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 месяца назад
Ai musamatero kuchepetsa nthawi
@BilaliMatemba
@BilaliMatemba 3 месяца назад
True love indeed 💕💕💕
@PiliraMlaviwa
@PiliraMlaviwa 3 месяца назад
So interesting.
@frankchiwawa4795
@frankchiwawa4795 3 месяца назад
Hoooo
@NaomiGondwe-og5hg
@NaomiGondwe-og5hg 3 месяца назад
Interesting ❤
@MgGondwe
@MgGondwe 4 месяца назад
Amen
@Omwale
@Omwale 4 месяца назад
timaina ta mBaiBulo😀
@oburybindula-nf7ek
@oburybindula-nf7ek 4 месяца назад
Aaaa Linda ulipo mmmm missing
@RabeccaGama-f7m
@RabeccaGama-f7m 4 месяца назад
Zosagalasa
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 4 месяца назад
Ambuye chimodzi modzi
@highcallingglobalministries
@highcallingglobalministries 4 месяца назад
komatu anthu inu,,,
@JosephChikoko-to3ji
@JosephChikoko-to3ji 4 месяца назад
Do as the spirit leads
@Richardmkandawire-vm6id
@Richardmkandawire-vm6id 4 месяца назад
Good lesson guys
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 4 месяца назад
Eeeeh! Nkhani yopatsa chidwi❤❤
@Desmond-q7r
@Desmond-q7r 4 месяца назад
Mabodza kkkkkk mazitumiki who ever mapemphero zokolo mbeta ndiye zolingazawo aaaa
Далее
DAXSHAT!!! Avaz Oxun sahnada yeg'lab yubordi
10:46
Просмотров 515 тыс.
Goshen City,Mangochi
1:15
Просмотров 86 тыс.
BRENDA KOSAMU, LOST & FEARED DEAD
19:12
Просмотров 43 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY  SERIES 21/12/2022
27:04
Просмотров 162 тыс.
DAXSHAT!!! Avaz Oxun sahnada yeg'lab yubordi
10:46
Просмотров 515 тыс.