Тёмный

COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - 30/09/2024 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 57 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

30 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 57   
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 6 часов назад
I respect your mtanyiwwa and everyone else has been in Malawi arraund shitpha two nsanje
@cmsanyama200
@cmsanyama200 6 часов назад
Welcome back honourable Mtanyiwa.
@OssmanAbubaker-w3x
@OssmanAbubaker-w3x 6 часов назад
Ulemu wanu bwana Ntanyiwa mumatiimilira ife tatopa ndi MCP anthu okupha
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 часов назад
My broh ur welcum MCP ikufuna anthu adziwapembeza wauze kuti ife ai timaopa Mulungu yemwe analenga kumwamba ndi dziko lino basi uthenga umenewo ukafike kwa asatanawo
@RoseThindwa
@RoseThindwa 5 часов назад
Eish Malawians tinasakha molakwika boma ili more tricks Tiyeni tigwirane manja pamseu commission of inquiry ikuchedwa
@Halima-i4x
@Halima-i4x 5 часов назад
Ausen aziwe 😅😅😅😅 aona chaka chamawa kkkkkkkkkk
@violetpotani
@violetpotani 5 часов назад
Yofunikatu yeniyeni osani manyaka and anthu wo okhudzidwawo plus boma asakhale nde zithekadi
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 6 часов назад
May God protect you comrade
@ErnestAllex
@ErnestAllex Час назад
Ife ndalama tidya kma vote tikuiziwa kopita nayo 😂😂
@EryvinMhango-zl3oh
@EryvinMhango-zl3oh 6 часов назад
Wlcm bck Mr mtanyiwa
@MariaNyamwera
@MariaNyamwera 5 часов назад
Or achonge mavotiwo koma mcp ikuchoka afune asafune out
@PetroMatias
@PetroMatias 6 часов назад
Koma abale musamasowe
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson Час назад
Kutha uku MCP there's no way the ruling party busy buying musician to perform in your not rally it shows they don't have confidence the will loose weather they like it or not DPP is going to kick them out.
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 5 часов назад
Mpakana achina Makhazi kuzaimba ku nsonkhano?? Mhh Chikangawa Party Misalatu iyi. Ndiye azabwelensotu azavote.
@prettytambala5687
@prettytambala5687 4 часа назад
Osati avota kale, paja zawo zikuchitikiratu😅
@EllenGomani-i4f
@EllenGomani-i4f 6 часов назад
Mumakwana big🎉🎉
@NaldodasilvaSilva-s1l
@NaldodasilvaSilva-s1l 6 часов назад
Following you my brother
@ziwani3682
@ziwani3682 6 часов назад
Anthu amcp akumazitenga ngt timilungu ting'ono ting'ono amalawi pakufunika tigwirane manja pokana usilu omwe akupanga anthu amcp
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 часов назад
Mwayankhul zoona izi akuzitenga ngt dziko amaendesa ndi iwoo
@GiftWilliam-t1z
@GiftWilliam-t1z 6 часов назад
We are together here in Lusaka
@prettytambala5687
@prettytambala5687 4 часа назад
Akalowedi mcp a UDF wo hiyaaaaa
@YusufJimmy-v1o
@YusufJimmy-v1o 5 часов назад
Ayimba nyimbowo ndi akuti???
@ChisomoNthembanji
@ChisomoNthembanji 6 часов назад
AMtanywa inuo ndi one mumakwana
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 5 часов назад
Ntanyiwa, pls ukabwera kuno asamanene mayendedwe ako kapena komwe uli,ukamangidwa ife tizaziwa zinsinsi zaboma kwa ndani?
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 4 часа назад
Ulemu wanu biggy Ntanyiwa 💪 mulungu apitilize kukutetedzelani ndithu...
@Dineojere
@Dineojere 5 часов назад
🙏🙏 sanga ber murugu aku won
@JonaSato-j8e
@JonaSato-j8e 5 часов назад
Ulemu wanu bwana❤
@JosephMwadzama-f4u
@JosephMwadzama-f4u 2 часа назад
Welcome Mr ntanyiwa matimilira inuyo biggy ❤️❤️❤️
@MaryChimowa-f8u
@MaryChimowa-f8u 4 часа назад
Welcome brother ntanyiwa Mulungu alinanu 🎉🎉❤
@MagretMvula
@MagretMvula 3 часа назад
Mulungu anmve zo dandaula za malawi ndi moyo was nthaniwa wathu ameni
@BrownMatonyola-xi3lb
@BrownMatonyola-xi3lb 5 часов назад
Tizikuikizani mapephero nthanyiwa Malawi ali pamavuto
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 4 часа назад
Comrade ntanyiwa kaswiri kwambili ❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
@FredKanyerere
@FredKanyerere Час назад
May God be with you comrade.
@AlidihGanie
@AlidihGanie 2 часа назад
Nyimbo yikuchitakunyekabwino 😢😢😢😢😢
@FredKanyerere
@FredKanyerere Час назад
Comrade Ambuye akudaliteni.
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek Час назад
Ma vote alepheleke inu Tapangani zotheka
@BlessingsGama-j3r
@BlessingsGama-j3r Час назад
Mulungu akutetezeni nonse ma comrade
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Час назад
Ndipo kasungu ndiyozindikila kwambili
@BlessingsGama-j3r
@BlessingsGama-j3r Час назад
Truck imeneyo tizaing,amba
@DiannaJanga-y4k
@DiannaJanga-y4k Час назад
Welcm Mr tanyiwa more 🔥🔥
@StevenShawa-o1b
@StevenShawa-o1b Час назад
Keep it up comrade ntanyiwa
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 5 часов назад
Welcome Mr Ntanyiwa
@RajabuWhite-l3s
@RajabuWhite-l3s 5 часов назад
Mulungu akhelenanu kuli konse mungayende
@pidongaluh-pb9og
@pidongaluh-pb9og 47 минут назад
Comrade ulemu wako ndthu
@ZainabHajj-q9d
@ZainabHajj-q9d Час назад
Big up ntanyiwa 🎉🎉
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 26 минут назад
Ndichochodi Mr Tanyiwa
@JustinaMwah
@JustinaMwah 47 минут назад
Mumakwana Mr mntanyiwa
@S-rr1eu
@S-rr1eu 3 часа назад
2025 akupita mmakola mwawo
@EthelShombe
@EthelShombe 20 минут назад
indeed
@Felixbanda-q6p
@Felixbanda-q6p 6 часов назад
Welcome back ntanyiwa
@ChristopherChakanza-y4t
@ChristopherChakanza-y4t 3 часа назад
More fireeeeee
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 4 часа назад
Comred welcome
@WilfredGunya1
@WilfredGunya1 5 часов назад
Ndipo tiri pa mbuyo pano
@ShiehllaMachilika
@ShiehllaMachilika 2 часа назад
Mumatiimirira bwana
@AlidihGanie
@AlidihGanie 2 часа назад
Ndipo mbambande
@McmariaMafura
@McmariaMafura 9 минут назад
Umakwana
@ChanceZambika
@ChanceZambika 3 часа назад
Umakwanaa
Далее
БЕЛКА ЗВОНИТ ДРУГУ#cat
00:20
Просмотров 705 тыс.
Police cordon off Lusikisiki massacre crime scene
30:25
MCP INAZIYAMBA YOKHA ZANKHONDOZI
3:18
Просмотров 2,9 тыс.
Chita Mwanzeru
6:02
Просмотров 563
AMALAWI ANZANGA KOMA MWAIMVA IYI?
6:01
Просмотров 7 тыс.
Dzimwe Hondo
11:45
Просмотров 214 тыс.