Jetu amatha kungoti kumalawi umbuli umatipweka sitimaziwa kupangana support km kunyoza. I love you Grandma jetu i'm watching you from south Africa capetown
Mayi wapeza chochita, let's congratulate her , mumafuna kt azikupemphani . Muziwalambila omwewo omwe amakupatsani ndalamawo kt muziwachemerela. At that age but she managed to come up with a song , that's great achievement. This is very sad to hear that people who have many followers discouraging someone coz of the age.What a roll model .Mwakhumudwitsa dziko
Respect what the old woman is doing guys , paka sindingapite ku show kwa jetu Malawi tusungira anthu opondera love each other , pake zinthu zimativuta kuti zizitiyendera
Kuli ambiri kuimba saata koma antu amawakondera moraro basi, ena angomukondera chisoni ndikufuna kumunyoza Joy Nathu, but the fact will remain the same and can not change the song, saatha
Kuli ambiri kuimba saata koma antu amawakondera moraro basi, ena angomukondera chisoni ndikufuna kumunyoza Joy Nathu, but the fact will remain the same and can not change the song, saatha
Jesus akuyimba bwino moti apitilize luso lake kuti ngati pali Ena okalamba Aliso ndi luso Lina abwele poyela I love ❤ Jetu anthu awo ndi afiti kwawo usawavele
Pass my humbly respect to her Manager for doing good example potiwonetsa ndikutiphuzitsa kuti Agogo ndim'dalitso komanso tinayenera tiwasamale ndikuwathokona pantchito yobeleka makolo athu
aMalawi timakondwa tikamawona anthu achikulire akutonzedwa kuti ndi mfiti that's Y now tikunyasibwa ndi Jetu but to my side am very grateful to see Jetu being happy,healthy and enjoying lifestyle if U could listen to her when she was saying ine pamoyo Wanga sindiname ndadyapo KFC or Ku Nando's Pano ndikutokoza kubeleka ndikwabwino ,I hope munavapo
Amalawi tinazolowera kuona agogo mtown mu akupemphetsa ndie jetu pa level yake akuitha let's support her , tikumudikira pa 26 apa kuno ku island kuti azaipatse moto
Iiiiiiiii! Amatha jetu ndi gogo wathu ameneyu wa chi malawi, enawo alibe ntima wa chikondi that's why samankonda to me si-kuti ndimazikonda kwenkwen koma zimangondipasa moti ndithakhala kuti kuthekela kwa chuma ndili nako nditha kungonthandiza bsi , posatengela kuti ndimazikonda olo ai why ndi olimbikila kusiyana ndi kumangokhala anapeza zochita jetu bsi let's support her kunyoza si sikungathandize kwa gogoz ngati imenei
JETU samatha kuimba ziribe kanthu Bola iye akupanga ndalama and mbiri yake pa Malawi pano iri paliponse, zikumgowapweteka azitsiruwa chifukwa iwowo sakutchuka and they just wanna be famous ponyoza JETU,Iwe ndi ndani? iye ndi JETU, Yomweyo Galu iwe
hate chabe musiyeni munthu apange zomwe akufuna, after all anthu tikumamvera nyimbo zina just because of the rythme not the actual message so jetu musamupange demotivate, saturday tiliso ku show ya jetu