Тёмный
Sam Malvitha
Sam Malvitha
Sam Malvitha
Подписаться
More than just entertainment
Nthenda Yomwe Anadwala Lucius Banda
6:25
14 дней назад
Upcoming Artist Xander B
8:26
21 день назад
Ndani Angatenge Malo A Chilima Ku UTM?
6:07
21 день назад
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Месяц назад
Mbiri Ya Saulos Klaus Chilima
6:41
Месяц назад
Mulungu Wamulankhula Jetu
2:35
Месяц назад
name any 5 African countries you know
4:32
Месяц назад
Oimba Omwe Sanvera Nyimbo Zao
6:34
2 месяца назад
Gibo walila tritah atathesa chibwezi....
7:04
3 месяца назад
Mbiri Ya Skefa Chimoto
9:33
3 месяца назад
zomwe zachitisa kut Tamia amangidwe
3:17
4 месяца назад
Zinthu Zomwe Mungapange Pa WhatsApp
13:37
4 месяца назад
Mr Ibu, zovuta zomwe anakumana nao ...
5:51
4 месяца назад
Nyimbo zolimbikitsa anthu kugwira ntchito
4:18
4 месяца назад
Mbiri komanso chiyambi cha Cutey B
5:18
4 месяца назад
Mkangano wa Lucius Banda ndi Bingu
13:20
4 месяца назад
Soka samasimba .... mikuluwiko part 2
4:00
4 месяца назад
CHIYAMBI NDI KUBOOLEZA KWA PHUNGU JOSEPH NKASA
5:28
5 месяцев назад
Комментарии
@MfasaTrumpet
@MfasaTrumpet 10 часов назад
Tima artist tu timakonda kulandana akaz
@MfasaTrumpet
@MfasaTrumpet 10 часов назад
Akanakamenya
@JonathanHenry-e9e
@JonathanHenry-e9e 21 час назад
Mumakwana inuyo
@FathimaMa2
@FathimaMa2 22 часа назад
I love my brother jb I like the way you give me energy I wish I can be like you my brother I really like it
@InnocentMaganga-gd6kn
@InnocentMaganga-gd6kn 23 часа назад
Motengela nd mbiri za achimwene aja tingot anamuswadi makofi
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp День назад
Sasi 😂😂😂
@SolomonNgulube-g3m
@SolomonNgulube-g3m День назад
😢Aaaaaa pop akukamba zoona
@PATRICKKANJANGA-zw3vc
@PATRICKKANJANGA-zw3vc День назад
Apa phyzo sanamenye nfanayu I think mwanayu akuyankhura izi chifukwa anamuthoka ma wise
@user-yn6tc7dk9p
@user-yn6tc7dk9p День назад
PHYZIX IS MAN OF HUMANITY
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 День назад
Physics ndiolakwa mnyelo ndiwake?
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 День назад
Akanamuheda akanafatu😂😂
@KikaImran
@KikaImran День назад
Sukutchula maina ndie chomatizuzir kumvera nchiyani?
@taylorbanda5154
@taylorbanda5154 День назад
Amen 🙏 abusa
@ishmaelmkuluma2013
@ishmaelmkuluma2013 День назад
Nde onseo ndizitsilu
@DreysOfficial-dy1ho
@DreysOfficial-dy1ho 2 дня назад
@cleopatranyirenda7958
@cleopatranyirenda7958 2 дня назад
I wish this song was full
@EsauGwede-ky8ve
@EsauGwede-ky8ve 2 дня назад
Apa Mwafotokoz Moveka Bwin
@user-qe2lz7mx7u
@user-qe2lz7mx7u 2 дня назад
Phyzix salakwitsa mafana kudelera
@user-qe2lz7mx7u
@user-qe2lz7mx7u 2 дня назад
Phyzix salakwitsa mafana kudelera
@DidoozSanny
@DidoozSanny 2 дня назад
Kd phyzx ndi Dan lu angawine ndan 😂
@HandyChipets
@HandyChipets 2 дня назад
Not 1997 but after the UDF convention in 1994 at NRC Bingu made his UP.
@ManuelThepo
@ManuelThepo 2 дня назад
Kumenyako very mistake ngat anatero
@BosscoReston
@BosscoReston 3 дня назад
JB nd doro palibeso
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 3 дня назад
Kodi ndekuti phyzix ndekuti amatha kumenya kwambiri kumalawi kuno? Chifukwa akaka sikoyamba kunva nkhani ndeu
@user-ph3cm3zs2i
@user-ph3cm3zs2i 3 дня назад
Kaya?
@DavidBatumeyo
@DavidBatumeyo 3 дня назад
Pop young ndi dolo
@mphatsosadiki4983
@mphatsosadiki4983 3 дня назад
Vuto lokhala opanda management ndilimenelo umangopanga zinthu muchimbulimbuli,had it been kuti mafanayi akupangidwabe manage ndi Akometsi bwezi alibe well disciplined,..yekha waziwa kuti mkaziyo wapita ndi Artist nzake chomupangila approach ndichani? Phuma ngat ka mkodzo akuswani kutchuka musakutengere pamgong'o.
@livisonchinsamba5655
@livisonchinsamba5655 4 дня назад
Anali SOJA wa amphawi
@IbrahimAnussah
@IbrahimAnussah 4 дня назад
pop ndamene walakwitsa coz zomwe wayakhula phyziks ndimalangizo abwino amene akusonyeza kut pop anapanga chinachake coz phyziks ofcoz mbili yake inaipakale kut amamenya oimba
@AnnieBanda-rb2dk
@AnnieBanda-rb2dk 4 дня назад
Pop young atha akuyankhula zoona, cz abale asikana mahule ngati amenewo angakane mwamuna, nde bozatu limenero, abale mwamuna ngati wamukana Singapange phokoso loti mupakana anthu kubwera kuzafusa ayi izi ndizabosa asikana amasiku ano amenewo ili nde ndiboza loone keratu.koma zomwe akunena pop izo ndikugwirizana nazo kuti sikanayo ndamene anabwera yekha kuzapereka moni asikanafetu timaterodi mwachidule musikanayo ndamene amafusira pop nde paja asikanafe sitimaloredwa kufusira mwamuna ndeno timangobwera ndimoni basi chilunga mwamunayo atifusire
@LucyObviousMzia
@LucyObviousMzia 4 дня назад
Sindinatengepo mfundo apa😅😅😅
@SmartVictor-kz7dh
@SmartVictor-kz7dh 4 дня назад
Pop amafunika kopondedwa
@Dean-De-Matrex1
@Dean-De-Matrex1 4 дня назад
Akukamba chilungamo ndi Phyzx
@SmartVictor-kz7dh
@SmartVictor-kz7dh 4 дня назад
Akanamumenya km ah amadelera
@IssahAluba
@IssahAluba 4 дня назад
😂😂😂😂
@MorganMwanza-gy2qm
@MorganMwanza-gy2qm 4 дня назад
Umakwana iweyo
@BenardZulu-zy2zw
@BenardZulu-zy2zw 4 дня назад
❤ nice video
@JustinRoga-iy3gn
@JustinRoga-iy3gn 4 дня назад
Iwe palibe voice apa
@user-if1cd9ld2w
@user-if1cd9ld2w 4 дня назад
Akanamuponda amadelera popizo
@VeronicaSekobi-is6dk
@VeronicaSekobi-is6dk 4 дня назад
🎉❤ nice video
@AustinMizwa
@AustinMizwa 4 дня назад
Samatha kuimba😢
@Judah-zb6sl
@Judah-zb6sl 4 дня назад
Bg🎉🎉🎉🎉🎉
@JacobVictor-z7r
@JacobVictor-z7r 4 дня назад
Kodi munthu adziwe Tchito yanji kuti abwele ku American Bwana JB
@InnocentKavalo
@InnocentKavalo 4 дня назад
Continue to give us that video it's nice
@MariamChipoka
@MariamChipoka 5 дней назад
Eish bless you
@Ghama-k4i
@Ghama-k4i 5 дней назад
Koma ngat uziopa kutchula zomwe ukuziwa bola usamapange
@BosscoReston
@BosscoReston 5 дней назад
JB km mwayakhura
@BosscoReston
@BosscoReston 5 дней назад
JB ameneyo
@IssahAluba
@IssahAluba 5 дней назад
khani yabwino kwambili
@EvasiLucas
@EvasiLucas 5 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂