Тёмный

Behind the scenes Mdyangu Comedy.. 

Malawi Lovers 🇲🇼
Подписаться 24 тыс.
Просмотров 13 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

31 янв 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 30   
@billyngoma-fb2po
@billyngoma-fb2po 9 месяцев назад
Ok ok magalasi mwagula ang'ono a munthu wamkulu mdyangu akufunika a clear akulu 😂😂
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes 11 месяцев назад
Mr Kabambe mwalongotsola momveka ndipo tamva zoona agaluwa dziko likwakabika apange zotula pasi amaliza kutionongela kadziko kathuka ambilife tatopa newe chakwela mukutionongela Malawi analitu bwino uyu kumavomeleza mukukaniza basi
@user-cu7lk1ul3e
@user-cu7lk1ul3e 11 месяцев назад
😅😅nyamata osokoneza
@jamesnbandakalonga595
@jamesnbandakalonga595 Год назад
I like this comedy for sure🤩,and i don't miss it i always wash it all the way from South Africa.Keep it up people
@promisemakawa1556
@promisemakawa1556 Год назад
Timakunyadirani kwambiri, mdyangu crew ilibho kwambiri, pitilizan kutisangalatsa, more love from me Makawa
@user-nm1dc7tb6t
@user-nm1dc7tb6t 4 месяца назад
Mutibwereke diresi adzavaleko akazi anga
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 9 месяцев назад
You make us happy guys.
@user-nm1dc7tb6t
@user-nm1dc7tb6t 4 месяца назад
Ine sk phiri malingunde afurola
@user-cu7lk1ul3e
@user-cu7lk1ul3e 11 месяцев назад
😂😂😂mwashera
@user-cu7lk1ul3e
@user-cu7lk1ul3e 11 месяцев назад
tikuwoneni ❤
@user-xg5mb9ql2i
@user-xg5mb9ql2i 8 месяцев назад
Mayi shokoshoko ndiye Ali busy Ku phodatu makwana guys
@sodausuman6384
@sodausuman6384 Год назад
MDYANGU NUMBER 1
@adamlano
@adamlano Год назад
pitilizani matimvetsa kukoma or matithera bundle kkkk matiimila fanzi yakwathu ulemu wanu nonse
@davidkunje3575
@davidkunje3575 Год назад
One love to mi people dem ♥️
@leahkatenga
@leahkatenga Год назад
I wish to join this clue in future ndithu kkkkk
@yamikanimeke5706
@yamikanimeke5706 Год назад
Ndamva kuitana ndizabwera mayi
@user-ni2ce3ys3x
@user-ni2ce3ys3x 11 месяцев назад
Mumakwana
@edythnamponya7701
@edythnamponya7701 Год назад
🔥🔥🔥🔥
@makulunijames6158
@makulunijames6158 Год назад
Sansoka umakwana iweyo.
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
Zosangalatsa ndithu
@alinafesawasawa3905
@alinafesawasawa3905 Год назад
I love ❤️ you my people
@sharonjalamu8657
@sharonjalamu8657 Год назад
Kma imakhala topc yochepa plz muziesetsa kuitalikitsako
@marthastima3864
@marthastima3864 Год назад
🤣🤣
@allanmakwiti5145
@allanmakwiti5145 Год назад
KodiaChiphwanya alikuti?
@chitimbethegreat8560
@chitimbethegreat8560 Год назад
Amene amaiwala kuikayotu ndiye amatilakwira program yokoma ngati iyi isamasowe izibwerabwera sasoka analandidwa mkazi ndi a dyangu kufoira😊😊
@richardmbweza759
@richardmbweza759 Год назад
This comedy is nice and super, ndimagona mochedwa daily kuonera Dyangu pa RU-vid, thank you Frora Suya.
@ellennchambalinja484
@ellennchambalinja484 Год назад
Koma ntchito imakhalako iiii abale
@edsonjohnbakaimani
@edsonjohnbakaimani Год назад
Your comedy is truly very fascinating , keep it up.
@mwayichimchere9806
@mwayichimchere9806 Год назад
Mwayamba kuveka
@mwayichimchere9806
@mwayichimchere9806 Год назад
Km muli nyatwa
Далее
Team Chipwanya
43:51
Просмотров 9 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY SERIES...16/11/2022
29:08
Просмотров 33 тыс.
BEHIND THE SCENES..MDYANGU
40:56
Просмотров 10 тыс.
CREW PARTY YA AMDYANGUU🥳
43:05
Просмотров 10 тыс.
MDYANGU PA TIMES TV 15 OCTOBER 2021
28:26
Просмотров 31 тыс.
Chipwanya amuchotsa ntchito..
32:41
Просмотров 22 тыс.
BEHIND THE SCENES MDYANGU COMEDY
28:51
Просмотров 11 тыс.
EMBOOZI MUKATI MAAMA RADIO, WEASLE AZAWI EDITION
1:06:57