We love you Brother from BAKILI TV, LIMPOPO FM with Comrade NTANYIWA. Osatopa, Osaoopa kuwayimirira a Malawi osauka . Kumawayika pambalambanda anthu oyipawa
Big ndmadikila information imeneyo ndizoona anthu akuzipha tsiku ndi tsiku amalawi akutuluka dziko muno ku ma border atadzadza basi kusiya ma banja awo