Тёмный

PA KWAGWANJI SPECIAL MADZULO ANO KWACHEMA NDIPO NKHANI NDI YA MCP AKUTI MCP YACHITA WITHDRAW APPEAL 

Makosana
Подписаться 111 тыс.
Просмотров 75 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 135   
@jomochirwa
@jomochirwa 2 месяца назад
Congradulation brian muluzi ndi amene adali mtsogoleri wa straight basi.muluzi ankanenelatu kuti iwe ichi ayi.iremember mike chilewe akalimbana ndi mr mtafu u mp ku mulanje koma muluzi adayisova yekha polankhula ndi mr chilewe kuti apatse mpata mrs mtafu.koma chakwela ndi muthalika nooo are the same too much sleeping.
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 2 месяца назад
Anampha SKC kuti akhale muntendele panonde zimu wa SKC ukulamulatu simunati inu a MCP muphana well done wayana chunga ndi aznu wose❤❤❤
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 2 месяца назад
Cafe Maulidi ntchito am aiziwa keep it up!!
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 2 месяца назад
Wayana mchunga keep it up, ❤
@JoshuaNgosi-c8u
@JoshuaNgosi-c8u 2 месяца назад
😂😂😂 magazi a munthu ndioopya, iwo mcp amati akubisala koma mulungu akuwaika pa air now.
@PeterMajamanda
@PeterMajamanda 2 месяца назад
Timadziwa kuti wina akakhala pabwino ambiri amafuna kugwetsa,boma ndilomweli sure🔥🔥🔥🔥
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 2 месяца назад
Allah must punish this useless government anthu akupha
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂 izoizo malemu chilima woyeeee
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 месяца назад
Kalindo ananenatu kuti 2024 tiona zinthu 😅😅
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 месяца назад
Ndiye zitsiru zina zizibwera pa Kanema wa MBC, akuti program yoti a Malawi timvetsetse. Timvetsetse ndi aChamanu?
@humphreysidie4747
@humphreysidie4747 2 месяца назад
So many glitches in this video, poor job, but good conversation wth very strong points
@MangaDamiano
@MangaDamiano 2 месяца назад
Just in shot the president must step down finish
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie 2 месяца назад
Misonkho yathu ili ndi midzimu yolusa kkkk zikuwaonekela okhaokha agalu akuba kkkk
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 2 месяца назад
Mizimu yakwiya😢😢😢😢
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi 2 месяца назад
Wayana chunga, you are very intelligence, mwalakhula bwino kwambili mau anzeru Big up mr
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 месяца назад
Let them continue doing wat they are doing that’s wat is leading Malawians loosing hope in them mcp ndiyakhaza ndipo ipitilizebe kusanvanako zithandizira kuti achoke agalu amenewa.
@GreenBadani
@GreenBadani 2 месяца назад
🔥🔥🔥☔
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 2 месяца назад
Kodi usogoreri wa zikolino akulamula ndi achakwera or achimwendo?
@MontfortMuhime-t6w
@MontfortMuhime-t6w 2 месяца назад
Nice
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад
Koma ngat akumenyana iwo okhaokha chonchi, ndie Chilima akanakhala ndi mtendere kumeneko. Komatu Bon uja ananena bwinobwino za kuipa kwa anthu amenewa a ndale za usikuwa.
@JuliusNyirenda-ec1eo
@JuliusNyirenda-ec1eo 2 месяца назад
times head office now is in lilongwe bravo my comrades mumadalitsa
@MercyChimaliro-fi6mv
@MercyChimaliro-fi6mv 2 месяца назад
Ndiye kulimbirana chochi ku Mcp mungalephere kupha Chilima. Ndiye zikugwira kuti munapha Chilima.
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 месяца назад
Inu magazi a anthu anafa aja M C P yiwonazowonawona muvatu mawa wina apenga kapena awasatira anthu anamwarira aja
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
Anthu amene amatukutsa chipani m boma ndamenewa ndipo Mcp kwanu kwatha munyera muona anthu oipa kwambri 💔💔💔💔
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 месяца назад
Kikikiki 😅😅
@MadaKanene
@MadaKanene 2 месяца назад
Jona pakuku akuzimbaisa President must step down not up 😮
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 месяца назад
Ndizoona ,,akulephera kuyanganila Chipani,,dzulo akaliyendetsa,,koma zoophya ndithu
@kennethmakweya3561
@kennethmakweya3561 2 месяца назад
😮
@LoydKamtedza
@LoydKamtedza 2 месяца назад
MCP ndi manyi okhaokha nsete masimba a chakwera mr chikangawa it's killer
@JoshTech-h4r
@JoshTech-h4r 2 месяца назад
😂😂 mwapsa mtimatu
@JamesMaduka-wk8xi
@JamesMaduka-wk8xi 2 месяца назад
Anthuamenewa a mcp sakufuna kutumikilawanthu koma akufunakupanga business vuto democracy saidziwa mwachidule palibeutsogoleli ngatisakulolelana anthuachipanichimodzi nanga kwawanthu achipanichina azawatengangatianthu zikuonetsakuti anthuwa zabwino sakuziziwa akutipatsamantha amalawi nyumbaimozi kudana nangakwaena azititengamotani koma mulungu alowelelepo
@PaulChaleka-lb4vx
@PaulChaleka-lb4vx 2 месяца назад
Makina anu akuvuta
@HumphreyWillima
@HumphreyWillima 2 месяца назад
Nthumwi zonse ku MCP conversation 2024,chonde onetsetsani kuti anthu amene apangitsa mpungwepungwe uwu asapatsidwe mpando. It could be that God just wanted to expose their wicked side or how incompetent they are as leaders.
@LacksonPhiri-z2t
@LacksonPhiri-z2t 2 месяца назад
keep it up guys
@Chifundokapondodza-f6d
@Chifundokapondodza-f6d 2 месяца назад
Kkkkkk kamudzuyo adachita zambiri kunyumba kwakotu
@FaheemChipojola
@FaheemChipojola 2 месяца назад
Mizimu yakwiya 😂😅😢
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx 2 месяца назад
Ntendere ukutsowa chifukwa cha midzimu ya anthu anafaa kuchikagawa ajatu ndiye ntendere autsowa ndithu
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 2 месяца назад
Congress kkkkk
@BillySaukani
@BillySaukani 2 месяца назад
Mabvuto onsewa ndi ku khala chete kwa a presdent pamene chilungamo akuchidziwa
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 месяца назад
Yabalalika MCP......ija😂😂😂
@JohnBanda-k5y
@JohnBanda-k5y 2 месяца назад
M'mdima ungakule chotani kucha ndithu remember what skc said.
@andrewchiyembekezadimba7173
@andrewchiyembekezadimba7173 2 месяца назад
Zikuonetsa ngati kuti utsogoleriwu uli pa kaliyala. Nkhala kale ndizomwe zikuliza belu. Anthu awa alibe ulemu pa utsogoleri wao.
@HarrietMtenje
@HarrietMtenje 2 месяца назад
Mizimu ya achina Chilima sanati kuchitika zinthu kumcp amaona ngati mulungu jamus
@DauglasBowa
@DauglasBowa 2 месяца назад
Mwazi wa chilima uli ku mcp Rest in peace SKC
@MarikoDama-t1n
@MarikoDama-t1n 2 месяца назад
Pang'ono ndipang'ono a jona akufanana nd I a vice president😅
@MaxwellSakwata-wb8ep
@MaxwellSakwata-wb8ep 2 месяца назад
Koma Brian Amadabwa zabodza bwanji 😂😂😂!
@ThokozaniKaluluma-rj6rp
@ThokozaniKaluluma-rj6rp 2 месяца назад
Kkkk ndiponso
@MichaelMhango-e8h
@MichaelMhango-e8h 2 месяца назад
MCP sichipani choti chingasimthe dziko la malawi for the better of Malawians, but I know for sure the New Party is coming Eff trust you me
@henrychawinga4639
@henrychawinga4639 2 месяца назад
Inakunganatu pannel
@DeeHMugonya
@DeeHMugonya 2 месяца назад
Ndiye wabwerako ndiwosokoneza anakhala ndi m'bale akamakamba nkhani!! HOT CURRENT inali bwino kwambiri masiku amenewa mulibe akuluwo
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 2 месяца назад
5 years tikumalidza now....politics every day...dziko kumagosawukabe....
@Sarahmuskambo
@Sarahmuskambo 2 месяца назад
Ndipo ndikuyakhula zowona kuti zikubwera zambiri kuposa zimene zikuwoneka panopadi 1samueli 16:10 mulungutu samawona kunenepa kwamuthu kapena kutalika kwamuthu
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад
inu mukamaphana zanuizo kunyanja kuribe magazi oti mukamwe mungopanabasi zanuizo muyambekupha kazi uyo
@williamswira2693
@williamswira2693 2 месяца назад
Achakwera munalowa kolakwika, ngati mukufuna u president lowani kwina not MCP
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 2 месяца назад
Yakwiya nd nd midzimu
@AnockyDavidd
@AnockyDavidd 2 месяца назад
MCP must go they think themselves not Malawians look they're busy fighting each other for the sits which it really shows us kuti m'bomamo ndi dimba lawo
@marthaseda1236
@marthaseda1236 2 месяца назад
Ana anjoka aja kuno😂
@DANIELSIMWABA-ic6wg
@DANIELSIMWABA-ic6wg 2 месяца назад
Tiyenazoni
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Ndevu zamwayi akuphatikiza ndi chakwera yemwe mwachisisi kuswakuswa.
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 2 месяца назад
Convention ya akadzidzi, koma, muphana
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 2 месяца назад
This president is sleeping on duty even the issues of Chikangawa is giving us question ❓ now
@Martha-m6e
@Martha-m6e 2 месяца назад
Mizimu ya anthu 9 simaseweratu chifukwa sakudziwa chomwe akuchira.
@catherinesilverio-d5w
@catherinesilverio-d5w 2 месяца назад
Chikangawa party iyaluke basi.ma candle aja mmawaphwekesatu paja.
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim 2 месяца назад
In mcp there is no presdent coz off zitsitsi zawo chakwera he can nt do anything pomudzudzula zikhale kunkuyu chimwendo onse ndi ma presdent and the have power than chakwera.
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 месяца назад
The bleeding party woyeeeee wakupha MCP,muona aphana the Evil people of MCP Party woyeeeee, Chakwera wakupha Chilima yooo Mr Chikangawa aaa yomweyo Galu iweee
@RuthNyirenda-n4s
@RuthNyirenda-n4s 2 месяца назад
😂😂😂😂 poppy ndiuti kkkkkkk
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Vuto lachakwera Ali ndi ndale dzoombanisa anthu Mitu Mr chikangawa
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад
MCP ilibe usogoleri apa onse ndi ana osadziwa chimene akufuna ndipo mwazi wamunthu osalakwa umazuzadi ndi zoona
@BesterMpalasa
@BesterMpalasa 2 месяца назад
Chomwe mungadziwa mchakuti ku mcp kulibe utsogoleri zonse zimene akuchita achakwera amangochita kuutlzidwa sopano apa sangalankhule kanthu chifkwa anthu amene akutsutsawo ndi amene amakhala pafupi ndi chakwera
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 2 месяца назад
Mu nthawi ya boma la DPP a president a president ankalekelera ma boys and girls kumapanga ziganizo zolakwika za boma mapeto ake anapezeka nazo kunja kwa boma... Likewise, mu boma ili sizikusiyana ndi boma lijalo cos kuli anthu ena ovuta zedi musakaike mupezeka nazo kunja kwa boma next year for sure...
@AllanSamu-tr1nt
@AllanSamu-tr1nt 2 месяца назад
🤝
@ComfortMangochi-g3b
@ComfortMangochi-g3b 2 месяца назад
Iyi ndye times yonse yakumana
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 месяца назад
Izi zingosonyeza Kuti mu chipani cha MCP, mulibe anthu oganiza bhooo.
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 месяца назад
Nyama zikulu zikulu zimenezo nda zake atatu akuononga zonse I nkhalidwe lawo liwatsata mawa akuba kuwawa amenewo mawa alifatu amadziva anthu 7 menemu a iona kwa anthu amene anawauza ayouth
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 2 месяца назад
In Chikangawa party there is no leadership 😮😮😮😮
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Dzamagazi NDI chocho sidziyenda dyela linaphesa chilima
@ZaccheousPetrol
@ZaccheousPetrol 2 месяца назад
Anyamata mukuyigwila...osamva sadzamva ngati satenga mawu anu
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 2 месяца назад
Chikangawa
@PatrickMtusi
@PatrickMtusi 2 месяца назад
Komatu kutsogolera ndi mphatso tikumbutsanepo apa
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 месяца назад
Akudziwa zomwe a Kuchita a chakwera a galu wonse wo ndi awo akudziwa so oipa pa galu awowo a kupangira dala
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 2 месяца назад
Mcp siidasinthe , siingasinthe ndipo siidzasintha . Chipani chotere ndichosakhulupiridwa kuti chingayendetse boma/dziko mokomera anthu ambiri mmdziko .
@Sarahmuskambo
@Sarahmuskambo 2 месяца назад
Koma kuli zambiri zimene zikubwera kuposa zimenezo Duteronom 29:29
@NiccoGama
@NiccoGama 2 месяца назад
Kkkkkk amenyane bas atikwana ife anthu okumba mulungu amaona
@jimmieseleman9064
@jimmieseleman9064 2 месяца назад
Miziimu yakwiya
@JamesDaud-jz7uq
@JamesDaud-jz7uq 2 месяца назад
Chakwera leadership quality alibe akulephera kutsogolera dziko ndi kuchipani komwe,,,,shame
@ChitanMangon-c4j
@ChitanMangon-c4j 2 месяца назад
No Democratic mcp
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 2 месяца назад
Chipani cha MCP chili ndi eniake enanu mukungozivuta
@diamonddyson
@diamonddyson 2 месяца назад
Kwamvutatu kkkkkk
@RuthMkangala
@RuthMkangala 2 месяца назад
Mtendere kulibe uku
@ZaccheousPetrol
@ZaccheousPetrol 2 месяца назад
akana khala atsongolele bwedzi akuletsa kuti ase izi ayi.....
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 месяца назад
Nyikwi Party.😂
@ChikondiRMoses-y5s
@ChikondiRMoses-y5s 2 месяца назад
Anthu awa Ali ndi magazi mmanja aphana
@WinessMatcthuwana
@WinessMatcthuwana 2 месяца назад
Akazizi awa
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 2 месяца назад
Komatu Brian kkkkkkk
@GiftMlinde
@GiftMlinde 2 месяца назад
Kamela mann todayyy waithatuu these pple todayy akuonekaa bwino kwambliii
@Musa2Musa-z5e
@Musa2Musa-z5e 2 месяца назад
Mmakina anu akuvutatu
@YusufuKamkuwira-b3x
@YusufuKamkuwira-b3x 2 месяца назад
Akazizi adapha chilima mcp agalu ameneo
@GresanKamwendo
@GresanKamwendo 2 месяца назад
Kodi ku jamaku zumakhala bwanji?
@AllanSamu-tr1nt
@AllanSamu-tr1nt 2 месяца назад
Madolo inu mumatha ulemu wanu
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba 2 месяца назад
Ilidi ndi boma, anthu mpaka kulimbirana mpando, MCP BOMA!!!!!!!!
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
Ukunama bomA lokupha losDziwa comwe likupanga lokuba loononga losaukitsa anthu okhala mdziko prezdent. Opanda umunthu
@AdamMpalira
@AdamMpalira 2 месяца назад
Kozani makina anu anyamata inu nkhanii njaikulu iyi
@PrinceLuckKondowe
@PrinceLuckKondowe 2 месяца назад
Mu Mcp mulibe usogoleri
@swintonchirwa1897
@swintonchirwa1897 2 месяца назад
Crocodile party
Далее
I tricked MrBeast into giving me his channel
00:58
Handsoms😍💕
00:15
Просмотров 6 млн
Oduu 'OBN Cyber Media' Onkololeessa 13/2017
21:23