Тёмный

BON KALINDO 12 OCTOBER 2024 KUNG’ALURA PA SATURDAY 

Malawi Trends TV
Подписаться 47 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 76   
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 часа назад
Yes ur real agood speaker to themalawians we like u Mr Dc
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 4 часа назад
Powerful speech THE DC'S mwana woooopsa kwambiri
@vytwistthelion98
@vytwistthelion98 7 часов назад
Akulephera kuvomereza kuti akulamulira ankhalisa ku opposition
@utekagelard
@utekagelard 2 часа назад
presdent anapanga bwino kuzionesa kt alibwino,,, mbir yawo sinali bwino,,,,, tasimikiza kt alibwino achakwer
@lyiemax
@lyiemax 5 часов назад
That's the Dddddd Cccccc!!!! Our own president ❤❤❤❤
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 2 часа назад
Bwana Boni kalindo wulemu wanu
@voicedumathindwa
@voicedumathindwa 5 часов назад
Koma tatopa naye mr p he is making nyas everywhere
@RodgerChaula-r5z
@RodgerChaula-r5z 7 часов назад
Powerful speach The D C
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 6 часов назад
The DCCCCCCCC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri indeed
@Maxcarcare-g1d
@Maxcarcare-g1d 6 часов назад
The DC🤙
@SaidiBaneti
@SaidiBaneti 3 часа назад
the Dc ❤❤❤❤❤
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 3 часа назад
Tisayambepotu kusikana apa please chifukwa ndkuwona lilime losiyana nd lazulu
@Dentera215Music
@Dentera215Music 5 часов назад
Indeed wachabechabe
@mkajikosya-uq5hs
@mkajikosya-uq5hs 3 часа назад
Akanapanda kupanga zimene zija bwezi mukumunenabe
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 6 часов назад
Ku uzira kuwiri kuwiri a Bon Kalindo .
@IbrahimJames-n7k
@IbrahimJames-n7k Час назад
Bon amanena pomwe pasali bwino saimira mbali munthuyu kumavuta n kumumvetsa basi Utsiru of the year unachita ochakwera uja,iye uja amayenera kuikamasi patsogolo osati kumapangaso za ndale pomwe ali patsogolo zandale akanasiira ku opposition
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 5 часов назад
The DC ❤❤❤
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 8 часов назад
The Dc Bon Kalindo ❤ number one
@GanhoGolli
@GanhoGolli 6 часов назад
Km Chakwerayo sakuona kt akumpeperesa
@CharlesBande-yr1yb
@CharlesBande-yr1yb 8 часов назад
A bon kalindo,apatu nkhani siodwalayo,koma anakabisa chija chandege chijatu,ulipo mboni.
@bornface4786
@bornface4786 4 часа назад
Ukakhala pa top ukakhala topic
@allahslave7177
@allahslave7177 6 часов назад
Koditu mcp ija imapanga ndale zau savage ndinso za chikuwawe ngati zopanga ana, president ndi president yo zoona zija zachitika dzuro zija does it make sense even kwa anuwakewo ??? Ali ndi ndale zamangawa ndinso za uchikale just to proof ena ake wrong basi!!! Kulibe maturity uku olo pang'ono pena mpaka kumasilira andale amayiko ena okwima mu nzeru !!!
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 часа назад
Akuzunza anthu ameneyo
@ThozaChilinjasanena
@ThozaChilinjasanena 2 часа назад
bwana dc,zayambikatu mmabank zomatipasa ma k 20 kwacha pamene ku mashop ma 20 kwa akukana.takakamizika lero ku tsandard bank kukanengo.ndalandila k3000 yama 20 kwacha,apano zikuyambika zakuzimbabwe.tivutika ndithu.
@mkajikosya-uq5hs
@mkajikosya-uq5hs 3 часа назад
Inunso mwasowa choyankhula kodi president kupanga ma push up ndikulakwa mesa ndi choice yake mumafuna km muzimunena
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 6 часов назад
Mmesa iweyo ndiye umasekera kuti chakwera wa mwalira Iwe opusa kwambiri Ukufuna kutitenga ngati zitsiru Opusa iwe
@CalvinThomson-ys5zf
@CalvinThomson-ys5zf 5 часов назад
Ndi fake account ija uyu alibe page pa Facebook and wakhala akunena thawi yayitali
@yassinn5634
@yassinn5634 3 часа назад
Koma nkuluyudi ndiopepera eti ndimayesa ndi yemweyu ndi alomwe anzake a pa social media kupusatu yekha kuzitsutsa alomwe anzake opusaonso kumamuyamikira mmalo momufunsa kuti nanga zija mumanena zija kuti wagwa zija bwanji. Koma poti zitsiru zokha zokha siziweruzana ndi chifukwa zitsiru zambiri pamenepa zingomuyamikira. Iweweme umanena zomwezo. Shame on you.
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 3 часа назад
Wina aliyese amene amumunyoza boni kalindo ndi otembeleledwa
@yassinn5634
@yassinn5634 3 часа назад
Ndichitsiru chakudya masanzi ake chachita manyazi pazimene amafalitsa
@yassinn5634
@yassinn5634 3 часа назад
​@@TrizaGeorge-q8w Izi ndiye zitsiru zopanda bongo tikunenezo
@MalidadJaffalie
@MalidadJaffalie 7 часов назад
Mr BON KALINDO nsiyeni osamuwuzirazochita azichedwa ndi MA push up omwewo inu munamuwonapo kuti president akuwuzidwa zochita ndi anthu ake akuwona ngat akulamulila mpingo wakwetu uyu
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 7 часов назад
Ayi ndithu ma bodza anu aonekerera basi. Dont defend the indefencible. You were the one making it ngati kuti ena sabwala...u said it Bon
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 5 часов назад
Dc ine ku nyalila chakwela ndizasangalala chifukwa chazochita zake,
@ElifalaThole
@ElifalaThole 3 часа назад
Inu takambani zot anthu anve osat mbwelerazo
@OmarMkwandala
@OmarMkwandala 7 часов назад
Komanso nanu a bon kalindo apa mukungofuna kuzipanga clean mesa dzulo mumati uncle anu che mapwesera adwala kwambiri mukumunena chakwera yemweyu and munalankhula kuti anthu mu nsika wa lunzu anakondwera kwambiri and munatitsikimizira kuti wadwaladi ndiye lero mukuti chani? Aaaah penatu anthu asiya kukupangani follow muzikhala ngati wa Bakili Muluzi tv sanayankhulepo kanthu koma inuyo ndi Ntanyiwa anthu ayamba kukutulukani ngati Skeffa sure
@MalidadJaffalie
@MalidadJaffalie 7 часов назад
Amalume ake lelo awawulula 😂
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 3 часа назад
Manyanzi bwanji ndimabodza ako aja
@mkajikosya-uq5hs
@mkajikosya-uq5hs 3 часа назад
Tiuzeni za Che mapwesera kuti akupezako bwnj
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 6 часов назад
The DC ❤❤
@MwaadzaRose
@MwaadzaRose 5 часов назад
Mmmm ngat chilungamo
@NoahPhiri-f7m
@NoahPhiri-f7m 3 часа назад
Nkhani ndiya black box adanamizira kudwala kuzimbayitsa anthu adakabisa black box
@MarryMacrown
@MarryMacrown 7 часов назад
Zamsnyazi aboniwa
@gracekusamale7468
@gracekusamale7468 7 часов назад
Ataaa kalindo watani mesa ndi Che Maphwesela akupasa chi bazi
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 4 часа назад
Amalawi Nonse PaNnyo Panu
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 8 часов назад
Tiye nazo DC 🔥🔥😅 Ng'alura mosaopa
@AllanChabwela
@AllanChabwela 7 часов назад
Zaoneka kuti utsogoleri uwu ndiwo seweretsa zinthu ngakhale ineyo atakhala bambo anga ndiwauza kuti akupanga zopepela
@HopeLuwangakaunda
@HopeLuwangakaunda 7 часов назад
The DC 🔥
@limbanimtitima9170
@limbanimtitima9170 8 часов назад
Awuzeni chilungamo boss DC makape a mcp
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 2 часа назад
Zachakwera zilipati kodi
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 7 часов назад
Nanu aborn kalindo dzuro mmati mkunena chilungamo metsa mmatselela kkkkkkk mwayedzeka dzuro
@ChimwemweRobertJangiya
@ChimwemweRobertJangiya 7 часов назад
Team dc
@FidesChandama
@FidesChandama 8 часов назад
Ndichifukwa adagwetsa makanja uja kusonyeza kuti akudwala
@IjilanMwalija
@IjilanMwalija 7 часов назад
100% true
@MalidadJaffalie
@MalidadJaffalie 7 часов назад
Wadwala ndipo anadwazika km ngakhale apange MA push up wanva e ululu wamadwale😂
@Dickson-d5i
@Dickson-d5i 7 часов назад
Iyeyo ndi mwana kuti samakana.
@ho222nussa
@ho222nussa 8 часов назад
born kalindo bwanji kodi kodi zulo lija sitimasekera limodzi apa watiwukila kuti talakwitsa kumuseka
@AliceGeorge-il6ig
@AliceGeorge-il6ig 6 часов назад
Awuzen zoona adziwe
@lawrencemnyango5118
@lawrencemnyango5118 8 часов назад
Chilungamo chenicheni
@HassanSaid-q8q
@HassanSaid-q8q 6 часов назад
The DC muli pati chakwela sionfunila za bwino chifukwa alibe chifundo ku mtundu wa amalawi kapena walandila kkkkkk ndale ndi manyi badi
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 7 часов назад
Chakwera amanamizira kudwala
@FalyceKatungwe
@FalyceKatungwe 5 часов назад
Mwayamba kulumphamotu eti ??? zomwe mwayankhula dzulo zija mwaiwala????okay chabwino opusa ndife timakusatirani
@PreciousChisale
@PreciousChisale 5 часов назад
ABorn kalindo zomwe munenazo ndi zoona ,chifukwa zimenezija amayenera akachite kumbalinso koma chomachitira pa public ndikusonyedza kt amadwaladi ndy amafuna awachite proof the malawians kt mumanama lero siuyu
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 3 часа назад
Alibe tchito kaya wadwala.kaya sanadwale ndi muthu opanda tchito kwa ifeyo aphawi ife
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 7 часов назад
Palibe ya pa 10 bwanji a iwe kkkk
@YusufAjiruh-c5q
@YusufAjiruh-c5q 7 часов назад
Apatu zikuonetsa kut nanu bon mwadya dorrah izizi zoyankhula inu lero
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 8 часов назад
Aboni kalindo ndi anzawo ndi zisilu zokha zokha zamaboza zisilu
@AllanChabwela
@AllanChabwela 7 часов назад
Zisiru zikuyenera kukhala zonamizila kudwalazo ngati mwana zaziiii
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 7 часов назад
President ndi munthu amadwala monga munthu wina aliyese. Tiyeni a Malawi tisinthe maganizidwe.
@MathiasEgama
@MathiasEgama 8 часов назад
Zinthu zabodza timaziyankha pamene timaganizira
@MagretJailos
@MagretJailos 7 часов назад
Bon Kalindo it shows that u are now interested in talking anything baseless because u present the same issue in mockery way in name of your uncle at the estate sarcastically .What do you want to tell us wadziwa liti kuti aliyense amadwala?
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 8 часов назад
Vuto ndinuyo ,mudzifufuza kaye nkhani musanaibweletse pagulu, Anthutu adzasiya kukukhulupililani, Mudziyankhula zoona, Timakutsatilani ndi anthu ambili Sanalakwitse chakwela,chipsnda kutelo bwezi mukutibe wafa,dzitiuzani zoona Akalinfo
@KabikaBuba
@KabikaBuba 8 часов назад
Nayeso anazifuna kutelo
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 7 часов назад
If he didn't do that bwezi lero mutatokota mutajama yakebe...lero mwasowa yo jama. Ndipo anthu aona boza lanu. And ma push ups anali atatu pamenepaja?
Далее
Свинья неудачник ( Liar's Bar )
24:01
Просмотров 378 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Apatseni moyo wautali
11:05
NKHANGA ZAONA PA LIMPOPO FM WITH COMRADE MTANYIWA
19:12
Kalata ya Bwande   Friday 11 October 2024
8:32
Просмотров 3 тыс.
02 January 2016
28:06
Просмотров 129 тыс.
Свинья неудачник ( Liar's Bar )
24:01
Просмотров 378 тыс.