Тёмный

BON KALINDO 13/09/2024 NDIKUNGOFUNA NDITAKAYENDA KU LOWER SHIRE 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 55 тыс.
Просмотров 17 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 57   
@MosesMottah
@MosesMottah 5 дней назад
Madala madala mumakwana go ahead
@WitnessPhiri-y5d
@WitnessPhiri-y5d 5 дней назад
Wabaya pamenepo wina akomoka😂😂
@FlorenceMasangalale
@FlorenceMasangalale 5 дней назад
Koma Mr Dc mumatimilira anthuwa akutionjezadi idea tili pamavuto panu
@lungsTug
@lungsTug 4 дня назад
Anthu akwiyadi osati masewera........
@ElliottBelon
@ElliottBelon 4 дня назад
Aziona Sanati misa za akatolika zija simasewera
@user-dm2uj6lx6b
@user-dm2uj6lx6b 3 дня назад
Akuti ife tili pheee nanga Inu bwana pangakoni action 🎉🎉🎉🎉
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 4 дня назад
Munthu akagendedwa tisamaseke. Musayiwale kuti Chakwera ananepo "Malawi anakonza" mthawi yomwe Peter anagendedwa.
@Aaron-w9x
@Aaron-w9x 3 дня назад
Chakwera ndi bushiri asamusidwe ngat mmene Anachitira bushiri ku South Africa
@FidesChandama
@FidesChandama 4 дня назад
Madala madala yendani ife tikudalira inuyo Mr DC akundinyasa chikangawa uyu
@FreddieNkhoma
@FreddieNkhoma 5 дней назад
Zayambkaaaaa
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 4 дня назад
Lucius Banda anayimba kuti galu wako wapakhomo amakuluma kukuchotsa katumba😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 4 дня назад
The DC
@EllenDmulinde-m5n
@EllenDmulinde-m5n 4 дня назад
Tangoyambapo sitinati
@FrancisMposa-ik4mh
@FrancisMposa-ik4mh 4 дня назад
DC katundu mbambande
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 4 дня назад
Achita bwino kwambili so pamenepo kuyamba
@kingsleyMadzi
@kingsleyMadzi 4 дня назад
😂Hahaha. Zakwathu izi
@BintonDzuwa
@BintonDzuwa 4 дня назад
Mukufuna kumuphanso
@AyamiMustafa
@AyamiMustafa 4 дня назад
Ndipo iye asayelekeze kuthi akubwela kuno kubwela kuno azabwelela tembo zipolopolo kuno zonzaza kale
@VincentwhiteKapeta-q4e
@VincentwhiteKapeta-q4e 5 дней назад
Pangolin
@lonnexjeke6840
@lonnexjeke6840 4 дня назад
Waziona ku Chikwawa
@Iponga
@Iponga 4 дня назад
Chikangawa sitikumufuna
@cholegidebo7095
@cholegidebo7095 4 дня назад
kkkkkkkkkk😂😂😂😂
@MisheckAselo
@MisheckAselo 4 дня назад
Mizimu ya anthu 9 ija yakwiya, koma ndiye muzunzika simunati pajanso mwaphanso mwana ndi convoy 😢
@jaffasaidi1158
@jaffasaidi1158 4 дня назад
😂😂😂😂😂😂 Your best before 🎉🎉🎉❤❤❤
@MosesMahowe-vn2tl
@MosesMahowe-vn2tl 4 дня назад
Inu ndi winiko wanyo😂😂😂
@frankkaipa8925
@frankkaipa8925 4 дня назад
Galo ameneyo chakwela angogwesa kwacha ngati ndi yamake
@user-cf8ng2br3p
@user-cf8ng2br3p 4 дня назад
Koma Bon 😅😅😅😅😅 miyala kuno kuchikwawa yosayamba
@AngolanChinga
@AngolanChinga 4 дня назад
😂😂😂😂😂😂 iweyo ndi dolo bon kalindo imayimila malawi
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 4 дня назад
😂😂😂😂chikangawa kutawa😂😂😂😂😂
@AyamiMustafa
@AyamiMustafa 4 дня назад
Kwina kulikotse basi Miyala ameneyo
@JohnDon-f1l
@JohnDon-f1l 4 дня назад
Ndipo amuchita bwno kwambiri galu ameneyi
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 4 дня назад
Mavote sayesela
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 4 дня назад
Ndipo zandikomeraa kwambiri ndipotu aziona zikubweraa.Tatopa naye kanyimbiyu.Kukhalira kuyendayenda kuwononga misokho yathu.
@DoreenLivata
@DoreenLivata 5 дней назад
Aziona amcp abwele kuno ku limbe dzikoli laipa aiyamba kma saimaliza
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 5 дней назад
Boma ndi lomweli palibe kusitha opposition ya magogo
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 4 дня назад
@@SaidiMbawa-st6bj Chakwera anabadwa before 1964, amadaya imvi zake, anaake onse ndi a pa banja ndi zizukulu mbwembwe. In a MCPoop mukuganiza kuti Chakwerayo ndi mnyamata wa zizukulu wa imvi. Maonedwe anga ndi akuti kusapota MCPoop kumachepetsa nzeru because poop replaces your brain. Monica Chakwera wamakhwinya a ukalamba komanso oti olo atachindidwa bwanji sangatenge mimba komanso monica anasiya period kalekale inu mwayesa mtsikana. Manyi adzadza mmitu yanuyi ndithu inu a MCPoop.
@OwenZimba-b4s
@OwenZimba-b4s 4 дня назад
Chikangawa zamuvutatu😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂 dc patsogolo❤
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 5 дней назад
Kkkkkkkk mr dc ameneyo
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v 4 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p 4 дня назад
Km kunachema
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 5 дней назад
😂😂 no secret under the sun
@williamlino5253
@williamlino5253 4 дня назад
Winiko umakwana
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 4 дня назад
Zisankho zoyesela sinazione
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 4 дня назад
machende ako
@JasperKaleni-dx6nn
@JasperKaleni-dx6nn 4 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂The Dc
@MathiasEgama
@MathiasEgama 5 дней назад
Koma Ine ndikumudadwa kalindo, Zinthu zoipa zikachitikila ku opposition umadandaula,Munya Chaka chino
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 4 дня назад
Udabwe akudana ndi satanic yanuyo
@MathiasEgama
@MathiasEgama 4 дня назад
@@GladysndilimbiraBonongwe-g6c Kkkkkkk Just kuti u Satanic umasiyana mphamvu,ku family kwanu mesa mumaphanaso nokha nokha,Ukalowa ndare choyamba ukuyenela kuziwa kuti walowa zinthu zopanda thandauzo, Politics ilibe thandauzo logwirika meaning kuti anything can happen in politics,just ukuyenela kuzithemba wekha, that's why ma Raster amati ( politrix) politics
@Pungwe123
@Pungwe123 4 дня назад
Unfortunately this is what he likes so mind your business
@MathiasEgama
@MathiasEgama 4 дня назад
@@Pungwe123 but him he don't mind own his business
@Pungwe123
@Pungwe123 4 дня назад
@@MathiasEgama 😂😂😂😂eish then i rest my case👐👐👐👐👐
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 4 дня назад
Zaziii zaukape
@AyamiMustafa
@AyamiMustafa 4 дня назад
Iwe pwanga ukuthi chani😢
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 4 дня назад
2025 timva zithu
@gkay-striker
@gkay-striker 4 дня назад
😂😂😂😂🙌
@FreedahKabaghe
@FreedahKabaghe 4 дня назад
😂😂😂😂😂
Далее
NKHONDO YAPAKAMWA - MORTON BAGHAYA KUBWENZERA JB
1:35:14
Просмотров 3,5 тыс.
ÚLTIMA HORA! FRELIMO OBRIGADO...
13:48
Просмотров 7 тыс.
LIMPOPO FM - TIKUKUONANI
36:34
Просмотров 6 тыс.