Тёмный

BON KALINDO LERO PA 1 OCTOBER WAULURA NDIPO MUKAMVA KUTI WAMANGIDWA NKHANI YAKE NDI IYI WAING’ALURA 

Makosana
Подписаться 100 тыс.
Просмотров 18 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

30 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 183   
@RuthBanda-p9k
@RuthBanda-p9k 7 часов назад
Speaking with all his heart very powerful
@idenmkumba-q8j
@idenmkumba-q8j 5 часов назад
Kumeneko akamuyitana mary chilima tipitako a Malawi tonse
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 8 часов назад
Izi kulakhula kwatopetsa , bwanji tigwilizane chimodzi, madhemo ayambike omuchotsa paphando
@SteviePatrick-g2p
@SteviePatrick-g2p 6 часов назад
That's great
@JrAlfeoLungu
@JrAlfeoLungu 2 часа назад
Et ndipo zatopesadi ndipo mademo ake akhoza kukhala obeba
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n Час назад
I like this comment. Amalawi tatopa ndiizi
@IchiNyirenda
@IchiNyirenda 6 часов назад
Anyani, agalu amenewa, chimene chinalakwika ndi chani kuti akaone pamene anafela mamuna wake, mulungu onesani ukulu wanu pa a satana amenewa
@PetrosSamuel-rs9wk
@PetrosSamuel-rs9wk 6 часов назад
Malo anafela chilima or kukamangapo nyumba mzabwino kwambili imeneija inapweteka kwambili and mukumbukile ndege kusowa (10:00 am) president kulengeza muma 3 kosaka kuyamba chama 6 pm within 30 minutes kuyimisa kusaka kubwelela ati kukagona kaye kuzayambilaso tsiku losatila ,, akulu akulu or athu aja kanakhala kuti ali ndi moyo muthu wavulala pangozi ya ndenge akale 27hr asanalandile thandiizo sangakhale ndi moyo zosathe ngakhale ili ngozi yagalimoto muthu akagone popo anagwelapo mpana tsiku linalo aaaaaaa mpana pano palibeso wachosedwa tchito zongowoneselatu kuti zogwilizana chifukwa chilima anali osatila kwa msogoleli kusonyeza kuti kumwalila chakwela president bwezi ali chilima so chitetezo chake chimayenela kukhala ndendende cha nsogoleli waziko😭😭😭😭😭😭😭 na yachilima yokha kampeni wakwana
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 6 часов назад
ANDALE ATHUWA SAKHALA MBOMA NDICHOLINGA CHOFUNA KUTUKULA DZIKO LA MALAWI AYI. IWOWA NDIKU NTCHITO KWAO KOPEZELA NDALAMA ZOKHUTITSILA MICHOMBO YAWO. NDIPO IFEYO NDI ZITSILU ZAWO. MWANA WA ZAKA 42 IBRAHIM TRAORE PRESIDENT WA KU BURKINAFASO AKUCHITA ZINTHU ZABWINO MDZIKO LAKE. WATSOGOZA ULIMI WAGULA MA TRACTOR OLIMILA MMAMINDA . KOMA ATHUWA AYI NDITHU AMANGOZIWA KULONJEZA BASI . KUTITENGA IFEYO NGATI ZITSILU ZAWO. KUWAUZA KUTI MWALEPHELA AKUTI WATUKWANA. KOMA DZIKO LA MALAWI KOYA TIZAMPEZA PULEZIDENTI WA MTIMA OFUNA KUTUKULA MALAWI KAYA. KAPENA TIMUPEMPHE IBRAHIM TRAORE ATILAMULILE KAPENA? CHIFUKWA OLO ENA AKULILA KUNJAWA ,AKALOWANSO AZIZACHITA ZOMWEZI . ALI NDI NJALA KOOPSYA AMENEWA NDITHU.
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 4 часа назад
Bon Kalindo is indeed an activist of Malawi. He is spending his resources for Malwians,he is using his money to help the poor and fight for their rights and freedom. Thank you DR BON KALINDO for the job welldone for the voice of the poor who can't voice out for themselves. Bon Kalindo is speaking for all bitter Malawians no wonder anytime he asks people to come out for demonstrations they do it accordingly
@EyobeAyala
@EyobeAyala 8 часов назад
Mademo ..mademo..mademo..mademo..🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉..tituluke tonse a malawi.. tituluke..anyani amenewa awone mbwaza please 🙏 atitola amenewa kwambiri..💪💪💪💪💪✊✊✊✊✊✊ let's fight for our freedom guys
@robinsharawa6994
@robinsharawa6994 6 часов назад
pandiwaza ndi poti "pajatu ndimayenda momunotu inetu sindiri ku South Africa tu, inetu sindiri ku America tu.."
@PatumaCassimu
@PatumaCassimu Час назад
😂😂😂😂
@mervischima3607
@mervischima3607 3 часа назад
Apa ngati simnapite kuma demo nzapita ayelekeze kumuyutanitsa Mary yo.
@BatumeyoChikopa
@BatumeyoChikopa 5 часов назад
Uku ndie kuwaputano amalawi, 😢😢😢I zino ndi mkhaza, dzikotu ndi la malawi not atsogoleli, anthu tkuvutikatu kunja kuno
@FlorenceNkhata-f5l
@FlorenceNkhata-f5l 3 часа назад
Ndimantha amenewo akudziwa chimene an achita koma akunama kuli Mulungu kumwamba
@chiefjusticie
@chiefjusticie 4 часа назад
Mwachindana chindana uko bas muziba ndrama za amalawi 😂😂😂😂😂 born kalindo the DC
@HassanKhebo
@HassanKhebo 4 часа назад
Kutitenga ngati ife anyani.tikubwela kumeneko ku za vota.
@naomiphiri2228
@naomiphiri2228 3 часа назад
.....ukunena zoona DC, ayerekeze kupanga zachimpwilikiti zawozo ndi Mary .. they will surely regret it 😡
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 4 часа назад
Koma amcp mukufuna chani kweni kweni mutichimwisa mwsnva
@HassanKhebo
@HassanKhebo 3 часа назад
The DC bon kalindo we are seriously
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 7 часов назад
Onyoza kalindo ndi asatana onkha onkha asatana agalu
@MagretMakunie
@MagretMakunie 4 часа назад
😅😅😅😅😅 nyonyonyo koma ndaseka kkkkk
@FidesChandama
@FidesChandama 6 часов назад
Kuyankhula zikuoneka sizikutheka apa tingoyambapo kuthamangapo muzeu
@JosophineNkhonjera
@JosophineNkhonjera 4 часа назад
More fire president wathu wathu The D C more fire 🔥
@PhyllisMambo
@PhyllisMambo 4 часа назад
😂😂😂😂😂😂😂kwavuta lero 😂😂😂koma kunena zoona DC umanena chilugamo
@MwinkhulanaLulu
@MwinkhulanaLulu 5 часов назад
Idzi dzikapitilira zomanga mosakhazi ziyambisa nkhondo
@MosesDicostar
@MosesDicostar 8 часов назад
Apolice akumalawi ndovesa chisoni kwambiri
@ShillahLawrence
@ShillahLawrence 4 часа назад
Kungomanga Mary Chilima ndiye Eeeee!kaya!
@AARONCHISUKAMZION-we3vp
@AARONCHISUKAMZION-we3vp 24 минуты назад
Kkkkkkkk tinyamuleni a Kalindo tikagona konko ku Chikangawa,campaigning yose tikachitire konko 2025 Misonzi ya auntie Mary Chilima pa Chikangawa palibe masanje.Ndale zinthu zosiyilana mpakana kuphana. Mtendere apa palibe. 🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗
@Loveness-e5w
@Loveness-e5w 5 часов назад
Tili pambuyo panu a Bon kalindo 😂😂😂😂😂
@LoyceMhango
@LoyceMhango 4 часа назад
Mary musiyeni ukuku ndikupita mikwiyo
@WysonSadiki
@WysonSadiki 51 минуту назад
Koma mr DC palibeso..... ife kumpandaku tikati tadya bwino nyama yake ndi Soya pisesi eishh.... 😢😭
@MosesFanuel-k3u
@MosesFanuel-k3u 5 часов назад
Kulibwino atimalize tonse anyani awa
@EyobeAyala
@EyobeAyala 8 часов назад
Guys..ndikuti tipange mademo a nyoooo guys please 🙏🙏🙏.... Malawi ayake moto kut buuuuuu
@chifundobuledi
@chifundobuledi 8 часов назад
Ndikugwirizana nanu kwambiri
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 8 часов назад
Basitu pakufunika ma dhemo siizi zomangolakhulazi
@mathewsnachuma8086
@mathewsnachuma8086 4 часа назад
MA DEMO AKUFUNIKA VUTO NDI SUPPORT PALIBE OPPOSITION IMAFUNIKA IZIPEREKA NDALAMA KOMA KULI ZIIII KUSATA NDONDOMEKO PENA KUMAONGA ZITHU ​@@WisikiBlack-gj4gu
@P.Bilali
@P.Bilali 3 часа назад
Despite all. Wolira samuseka pakwamwa that speech ya H.E the state president inali yabwino kwambiri and kuimila pamene paja zinali bwino. Komano izizi zomathana ndikalikonse kakambidwa mukuluza direction yet Boma ndilomweli, why fear ?? Iiiiih Bwana anyamata anufe tiuzeni tiyigwire mitima...
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 2 часа назад
Chakwera ndi Boma lake samayenera kufikaso next year, Malawi akanakhala kuti ndi dziko lopanda mantha. Coz akukula ndi mantha ndi Mifuti koma kunjaku anthu zikasolobana Mfuti sayionaso mwakanthu or atafa bola iwowo atamenyera ufulu bas. Koma zikufunika umodzi osati masewera, mwina Chilima akanakhala kuti ali moyo tikanati tiona zinthu, but anyway the brave person are still alive let's unite to protect our country. This is too much
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 3 часа назад
Makosana tisalole kuti anyaniwa adzititola dziko lokhala lathu.Tiyeni timuteteze Madam Mary Chilima ndipo tisavomeleze uchitsiru omwe zinkhanila za mbusa Chakwera zikuchita mdziko muno.Asatana amenewa pamodzi ndi pulezidenti wawo ndinso azibusa adyera awononga dziko kwambiri.
@BensonChilundu
@BensonChilundu 5 часов назад
Koma MCP siizatheka ndithu.Kodi anthu a chipani cha MCP muzasiya liti nkhanza zomwe mukuwachitila a Malawi??Simukuganizabe za 30 years zaku opposition?Komatu dziwani kuti zomwe mukuchitazi inu a Chimwendo,inu a Kamajekete,iwe ochepa thupiwe koma dazi lili phuliphuli yemwe unapha Witica ndi mkulu wanuyo dziwani kuti matsiku anu ndi ochepa kwambiri.Muziwona
@yonademba3342
@yonademba3342 5 часов назад
I hate people who use deep English just to make us intoxicated by execuberance of verbosity betarprutal contraption 😂🙌
@WysonSadiki
@WysonSadiki 45 минут назад
DC.... ngati zingatheke tapangani zotheka tikuvotereni 2025, tikuvutikatu ifeee
@augustMag
@augustMag 5 часов назад
Apolice chikuwankhuza ndi chani? Ndipo Mary Chilima walakwisa chani? Kodi mesa akufuna kudziwa Chilungamo pa ifa ya Dr Saulos Chilima Ndi Anthu 8 anafa pa ngozi ya ndege kuchikangawa akuluakulu a MCP zimene mukufuna ndi chani mdziko muno munthu akanike kulira ifa ya mamuna wake?
@thomsonnkhoma748
@thomsonnkhoma748 6 часов назад
Kung'alura kwabwanji uku Bon!! Tamva, ndipo tamvesesa!!! You shall live long!!! Bon
@abrahamchikuse2213
@abrahamchikuse2213 7 часов назад
Eee, koma or itakhala propagandayo, how can a sober minded person believe kuti bulb ya k1000 ikugulitsidwa pa k45000? Drama at its best..
@BensonChilundu
@BensonChilundu 5 часов назад
Ndi zomvesa chisoni kuti press conference ya dzulo yomwe anapanga hule uyu waku Salima uja ndi uyu okhota mutuyu inali yonyansa kwambiri zoona mkumanena kuti a DPP amamenyana okhaokha yet anawatuma kuti avale makaka a DPP koma anawatuma ndi anyani amenewa.Koma iwe Chimwendo Banda ndi galu wako wachikaziyo ngati nthawi yakwana ya chisembwere muzikapangila ku Salima kwa uyo wa mutu ngati galimoto yochotsa manyiyo.Mwandinyansa nayo press yanu ndipo mudziwe kuti anthu anu omwe anakawononga zinthu za anthu a DPP azagwidwa ndipo choona chenicheni adzawulula anthu amene aja.
@GoodsonDiwadiwa
@GoodsonDiwadiwa 26 минут назад
Ndipo a Malawi tiyeni tigwilane manja tiwakwapule a satanawa Tiyeni timusapote Mary Chilima
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 8 часов назад
The spirit of Kamuzu Banda is with them these MCP murderers, but this time, they will face resistance from the people which our fathers and grand fathers failed to do and resulted in their self imposed exile
@BwanaGD
@BwanaGD 5 часов назад
Koma tiyagalu tonunkha phechepecheti titipatsa ntchito Kodi akutitola kupusa amalawife kugwilitsa zizimna zakumidimazo akuziva phavu kwabili eti ankhumudwa kumwamba kukagolankhula kuti kwantha ndipomwe adabwire kuti amalawi anja ndiawa?
@HAJIUBAYIDABLACK-q7n
@HAJIUBAYIDABLACK-q7n 7 часов назад
Bon Kalindo mumalankhula zambiri zoti anthu atati akunvese bwino bwenzi zinthu zitasintha koma antaa, ndiyeno chilungamo chakambidwa koma sizikusintha mpaka lero Pakadali pano wafawafa time timenye nkhondo yamanja osati yapakamwa chifukwa sakunva kupweteka kanthu kenakalikose, Tiyeni timenyane nawoni tsopano enough is enough
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 7 часов назад
Lero mutha kumayankhul motha mau bwanji dziwan Mulungu amakantha guys Mulungu akuona znsez ndthu koma Mary Chilimayo apitilize kupemphera molimba ndthu Mulungu apukuta misoz komas amuyankha mapemphero ake onse nthawi ifika
@angelmwethewa8010
@angelmwethewa8010 Час назад
Kkkkkkk umwa chani Bornnnnnnnnnnnnn???????????????kkkkkkkkkkkkk lero sikunakuchere bwino kaya dzuwa lomweli???kkkkkkk
@vittazomba
@vittazomba 7 часов назад
Eeeeee lero DC sizili bwino wakwiya kwambiri,aazitsogoleri chonde ganizaniso zinthu zisanavute zachiziwikile izi zikwiitsa anthu ambiri
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 5 часов назад
😂😂😂😂😂 koma bon lero zakunyasa kwambir... Mpaka pamenepo... Kwasalaku upita pa msewu ndi ndodo
@BanetLuka
@BanetLuka 6 часов назад
Zachisoni kwambili Kodi aja adakhapa a DPP ku Lilongwe aja mpaka pano bola silikuwamanga koma uyu chikwanje wa ku machinga masiku ochepa womangidwa koma mcp? Chipani choiipa kwambili
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w 2 часа назад
Ambuye liyendereni dziko lathu la Malawi anthu sitifunirana zabwino ayi
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 7 часов назад
Znse Mulungu akudziwa zmwe zinachitika pa ngozi ya ndege ija Mulungu anaona znse ndthu samagona Mulungu ndye aliyense adzalandira malipiro ale azimene zija silero kapena mawa ndthu
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 6 часов назад
Ndipo boma iri ndilopepera moti athandize anthu ovutika alibe chakudya akulimbana ndizinthu zopanda pake ulamulilo wanu uli pati othandiza amalawi Angofa ndinjala
@AtupereSadiki
@AtupereSadiki 6 часов назад
Ndipo memories are still fresh kma wina asavuka ndithu ayese kupanga za Mary muziwanso
@EliaSiska-n6r
@EliaSiska-n6r 6 часов назад
If it is true shame on those questioning Mrs Chilima. She is still mourning her husband
@billymhoni9527
@billymhoni9527 7 часов назад
Motooooo the DC ndipo ayese kumumanga Mary chilima Dziko liyaka ilili....
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 7 часов назад
Ndipo asayelekeze kumuyitama marry chilima azaona Malawi zomwe itazapange.
@FisherAction
@FisherAction 8 часов назад
Otukwana kalindo mutuwako ukugwira galuweeti mr president Bon be fire keep it up boss
@DauglasBowa
@DauglasBowa 7 часов назад
Kukhala mademo anyoooo Kodi malawi akupita kuti bon kalindo bakili muluzi tv ntanyiwa Amaima pa chilungamo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 7 часов назад
Amalawi mumatha kuyankhul koma zinaz ngt zili ziwanda ai Mulungu atikhululukire ndthu umakwana Bon Kalimdo
@PatumaCassimu
@PatumaCassimu Час назад
😂😂😂😂soya pieces akupulumutsa anthu iiii😅😅😅😅😅😅😅😅
@imraanJafal
@imraanJafal 2 часа назад
Inu nde mamuna weni weni timanyadila nanu booooon kalindo the DC ❤❤❤❤❤❤
@UnarineNyirongo
@UnarineNyirongo 6 часов назад
Mademo ake akhale impish president chifukwa tatopanawo a MCP
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 5 часов назад
Mcp yatha kma Eni wake saziwai Any day kudzakhala mademo a emergency
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 7 часов назад
Iwe uKuti chisiru Kalindo chisiru amako ndi nonse kwana ndi chikangawa galu lwe
@YusufuKaifa-r2y
@YusufuKaifa-r2y 7 часов назад
mandemo mandemo mandemo 🎉🎉🎉🎉🎉 timakunyadirani mr DC president wa a phwawi
@neejoe4251
@neejoe4251 3 часа назад
Kkkk koma ichichi adha....ati inu ndinu zitsilu kwambiri
@chilingachilinga6059
@chilingachilinga6059 6 часов назад
Kmno this government yapala 1000%
@aggogokina8992
@aggogokina8992 6 часов назад
Akatundu athu lero akalipa mokwana akamuna atopa Booon Kalindooo😂💪💪
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon 5 часов назад
Born kalindo ❤❤ our freedom fighter 💪 ♥ 🙌
@CalistaPeter-e9o
@CalistaPeter-e9o 5 часов назад
kmatu munthuyu sakunama ndipo ixi nxoonad ndipo boma ili eash
@rabsonDimba
@rabsonDimba 7 часов назад
Kodi okhapa anthu ndi ongolankhula oyeyenela kumangidwa ndindani?
@francissonani
@francissonani 6 часов назад
anthu akugula ufa wa K200 kuchita kuona ine ndi maso anga,,,,
@Hendersonspoon
@Hendersonspoon 4 часа назад
Mkaka ulikuti ?????? Kunena Kwa nyoooo amakwanira DC
@kingssalema3364
@kingssalema3364 7 часов назад
Hahaahaaaaaaa, Maso tuzuuuuu kumaopsyeza anthuuu hahahaaaa. Mkaka utakukwanaaa.
@HawardMedson-h3t
@HawardMedson-h3t 7 часов назад
President wa mphawi mulungu azikutetezeran ndinu one
@BrightZionga
@BrightZionga 44 минуты назад
Kkkkkk pitani konko DC cccc love you ❤❤
@PrinceBonface
@PrinceBonface 2 часа назад
The dddddddddddddccccccccccccccmoto kut buuu😂😂😂😂😂😂😂
@CathrineBizza
@CathrineBizza 2 часа назад
Aaaa akhuta amenewo ayelekeze ha ha ha mbuli za anthu
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 6 часов назад
Tiyekubwela konko ndinjalawa bola tikafele kundendeko
@prettytambala5687
@prettytambala5687 6 часов назад
Koma Mary yo asamupute dala, tipita nawo ku 30 ko
@samsonjgareta6144
@samsonjgareta6144 5 часов назад
ndizoona ngt akufuna kutamidwa anene tiyende panseu
@HajilaMussa
@HajilaMussa 3 часа назад
Bamboo anyo amakwana akuti nyonyonyonyoooooo😂 bravo.!
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 6 часов назад
More 🔥🔥🔥 Comrad Kalindo ndipo tigwilane manja pachilichonse kuti achenganyawa asatitole guyz
@GRAYJUMAHPHIRIE-n3h
@GRAYJUMAHPHIRIE-n3h 2 часа назад
Timakukondani Mr Bon Kalindooo ❤❤❤❤❤
@VictorMateyu
@VictorMateyu 6 часов назад
TIZINGOWAKHAPA BASI AJAILA BRAVO DCCCCCCCC
@VicentMalopa
@VicentMalopa 7 часов назад
BRAVO NEW GENERATION ALPHA LEADER ❤❤
@OBETEDOS
@OBETEDOS 7 часов назад
Chonde chonde mawa nanuso msazadye banziiiii
@yassinjanna9564
@yassinjanna9564 2 часа назад
TheD.C mumakwana inuyo
@Dineojere
@Dineojere 7 часов назад
Apolic ndi akaporo achakwere zachamba
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 5 часов назад
Dc❤ katundu big ulemuwanu boss ❤
@HardyMw
@HardyMw 2 часа назад
Auzeni achimwene akunthochi
@tracybennie7783
@tracybennie7783 7 часов назад
Tili nkoko. Muyitateni. Muyone. Munyan muona
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 7 часов назад
The DC akatundu omanga ndi mawaya❤❤❤❤❤
@CathrineBizza
@CathrineBizza 2 часа назад
Yomweyo galu iweeee nyo nyo nyo kkkkk
@ernestchinyama1992
@ernestchinyama1992 Час назад
Kkkkkkk 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 tatopa ife
@MagieJames
@MagieJames 6 часов назад
Tili mudziko la ufulu kulira saletsana
@PrinceBonface
@PrinceBonface 2 часа назад
Amenewa ndi zisiri kwambili
@LinlyNgala
@LinlyNgala 3 часа назад
Mufna Mui nkanzi wamasiyeyo
@geofreykandabongomani4715
@geofreykandabongomani4715 7 часов назад
Ulemu wanu big aunzeni chilungamo
Далее