Chakwela ine ndilibe mau pempho langa ambuye mwini mphavu zonse pasi ndi kumwamba atenge ameneyu mwina tipeza ka mphepo kozizilapo chonde ambuye imvani pempho langa ndi kulila kwa amalawi mwaphavu yanu ndithu
Even if atalembetsa ambiri millions and millions pa central region this cannot be a guarantee kuti MCP iwina, musazinamize. Even pa central region tikumva kuwawa chimodzimodzi ndi ma region enawa...... In short 'Central Region will surprise Malawian come 2025 tripartite elections'
The other thing unemployed primary school teachers akuvutika ndi this government ena pano akhala zaka five opanda ntchito very pathetic of which sizinayambe zachitikapo in Malawi ...
Ulikumalawi koma kupusa basi athu azutika ndi ng'amba kukokoloka kwa zakudya kudula kwa fertilizer kt akhale pa mpando anthu ndi amene anamuvotela koma akupanga zopusa nde azimuombela manja iwe ungapeze mkaziwako akugonana ndi chibwezi ungasekelele sukuganiza bwino anthu akulira mmamizimu soya prices weniweniyu 700 Azam 700 mazila 450 1l c.oil 6000
Amamvera propaganda ndi maboza a munthu wa nsanje ndi nkhwizi ngati iye, otchedwa Shadreck Namalomba. Pajatu amatchera khutu kenaka nkumazitenga woziwa nkhani za boma koma ali kape wothaitha.
Ma plan akuchitikawatu anakaphunzira ku Ruwanda koma Mr chikangawa dziwani kuti inu si Mulungu zitizunzani choncho koma muzindikire kuti zomwe muli nazo ndi zotsala za dziko la pansi simudzadzitenga wamulungu, ndipo m'mene zikuchitikiramu mu inu a Mcp mukufuna ku gulitsa dziko komanso komanso mukuyitana nkhondo, Koma choti mudziwe kunja kuno kuli mulungu mwina ma plan wonse