Тёмный

BRIAN BANDA WAMUPANGA INTERVIEW DAN LU WANG’ALURA CHIFUKWA CHOMWE WATULUKIRA DPP KULOWA MCP LERO 

Makosana
Подписаться 93 тыс.
Просмотров 25 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

18 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 301   
@HsienSawez-hr5xq
@HsienSawez-hr5xq 11 часов назад
Si Brian Banda uyu ndipo winayu si Dan lu palowa bodza🫣🫣😁😁
@jeremiahmwawembe
@jeremiahmwawembe 4 часа назад
Aaaa ai Brian uyu akufuna kut akhale ndma views ambiri chabe
@Gautengstanzo
@Gautengstanzo 11 часов назад
Amene amalemba zoti Brian Banda machende Ake Pati. And Ngati alidi danlu akuyankhula apayu mumuuze Kuti mboli yakeso Pati.
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 12 часов назад
Anthu sakuoitila kuti chakwela awinetu ai Koma ndalama zaphwekako Mudyeleni opepela akungogawa ndalama Anthu akudya chitedze Asataniki omse akulowa mcp
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 12 часов назад
Ndikupusa kwa amalawi Mesa akutionongera ndalama zathu
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 10 часов назад
ndipo ndizoona wose aaataniki akulowa mcp
@afanaagobokalawe
@afanaagobokalawe 12 часов назад
Makosana U can du better...U r a brand...uyu si Dan komaso si Brian
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl 11 часов назад
Ndi Dan komano winayo si Brian
@EmmanuelkpPraise
@EmmanuelkpPraise 11 часов назад
Zimenezo ndiye zoona
@TravelodgeMalawi
@TravelodgeMalawi 10 часов назад
😅si Brain Banda
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v 10 часов назад
Eya si brian uyu
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 16 минут назад
Or si Brian koma bola mwamva kuti Dan luuu akutulukani😅
@JordanMasauli-m5w
@JordanMasauli-m5w 4 часа назад
Ngt uli Dan lu Ambuye akukhululukile,,,,wathapo bas ndipo palibe azikupanga follow
@BistonMacheso
@BistonMacheso 9 часов назад
Ndipo sangapange kanthu mulungu atimenyere nkhondo Exsodo 14:14
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 7 часов назад
Amen, ndipo anati tiziyenda atimenyela mkhondo
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 14 минут назад
Musiye kutukwana first mulungu amayankha okhala chete ngati mukudziwa mawu amulungu mudziweso kuti tisaweluzane kuwopa ifeso kuweluzidwa osati tidzidziwa mulungu pamamvuto
@RencoMandah-vd2yp
@RencoMandah-vd2yp 10 часов назад
Nanga bwanji akunveka ngati Moses Kunkuyu........ Dan lufan wayamba kulankhula ngati Moses Kunkuyu 😅😅😅😅
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 6 часов назад
Eti inu aaa zulukhala bwa
@UmaliMmussa
@UmaliMmussa 11 часов назад
😂mukungofuna kutchukisa chikangawa mulibe mawu a Brian banda ndiposo uyu si Dan Lu zaboza iziii
@henrymwale8994
@henrymwale8994 8 часов назад
Uyu ndi Dan lu koma akufusa yo si Brian banda. Dan lu olo misonkhano ya kongelesi akumulengezadi. Koma akungofuna kukapakula awa basi
@MumbasnwaMumba-ih1xi
@MumbasnwaMumba-ih1xi 10 часов назад
Amene akut uyu ndi Dan Lu kmso Brian Banda ndizaboza
@henrymwale8994
@henrymwale8994 9 часов назад
Dan lu walowadi koma uyu akufusa mafusoyo nde si Brian banda
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 9 часов назад
ngatidi mzona Brian timawaziwa mau ake Brain bwelani poyela tiziwe zenizeni
@rexphiri7242
@rexphiri7242 10 часов назад
Dan Lu Nd nothing ku ntundu wa Malawi tilibe nae film
@AnockyDavidd
@AnockyDavidd 30 минут назад
True who is Dan Lu pa ndale?
@user-gp10.10
@user-gp10.10 11 часов назад
Akufusayo ndi kaka dj Chabwera Ausi koma winiyo akumveka ngati Kumkuyu
@CarlosMapwe
@CarlosMapwe 10 часов назад
Iwe Moses kumkuyu mmaso mwako kuleka kumakagawa chakudwa uko athu akudya chitedze ndi zisekese uko😢😢😢
@BatsonMitangaMbewe
@BatsonMitangaMbewe 12 часов назад
aaaaaa bodza bas si brian uyu akulephera kufunsa mafunso
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 3 часа назад
Winayo si Brian Banda komaso winayo akukhala Ngati Kunkuyu bwanji
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 9 часов назад
Good idea ❤❤❤❤ keep it up dan lu
@amonechirwa
@amonechirwa 9 часов назад
Boza chikangawa uyo si Brian Banda aaaa Malawi 2025 came
@rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
@rachidepitamuhamedmuhame-jg9id 12 часов назад
Oyakhayo ndi mozesi kunkuyu
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 11 часов назад
😂😂😂 ineso ndikunva choncho
@phillipchiotcha3197
@phillipchiotcha3197 5 часов назад
Ndie Brian Banda akufuna chani pa headline
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 2 часа назад
Ameneyo si Brian banda ayi zinazi
@MphatsoMwale-it4xd
@MphatsoMwale-it4xd 5 часов назад
Kd dan lufan amayakhula choncho nanga brian banda amayakhulachoncho wanena idzi pathakopamake
@MonijaKataika
@MonijaKataika 2 часа назад
Gwafa wapa chimbuzi amadyedwa ndi alendo...adyende chenene..the response shows he's heart is in DPP yavuta ndi dollar alandirayo..zakayesara zipite kwakayesara. Free stop.
@NEBRA-lm7ji
@NEBRA-lm7ji 10 часов назад
Makosan mwayamb zibwan...tisiya kukupangan follow
@AllanMwakalenga-wn5ib
@AllanMwakalenga-wn5ib 9 часов назад
Awa akufalisa bodza..brian banda wake uti
@KelvinEdwin-bn2qv
@KelvinEdwin-bn2qv 12 часов назад
Kukonda ndalama awa zija anawapasa adad zija zinawathela akufuna akokeleso aaaaaa
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 4 часа назад
Maboza mawu a Brian si amenewo
@giftjamali8204
@giftjamali8204 6 часов назад
Hahahhhahaha koma anthu Ali nkupeka Mau a bayan band ndani samawanziwa
@SamsonKhobiri
@SamsonKhobiri 59 минут назад
Awa nzeru zawathera, mu music awona kt nyimbo zawo amalawi sakuzikonda
@MUSATAFAIIi-c4j
@MUSATAFAIIi-c4j 11 часов назад
si Brian uyo tiziinva voice ya munthu
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 12 часов назад
Amalawi siyani maboza uyu si Brian komanso uyu sidani luu mumuziwe mulungu
@AmonthandieGenamu
@AmonthandieGenamu 12 часов назад
Brian Banda wa ku ntumbo kwanu Makosana? 😂😂😂
@JohnBandawe
@JohnBandawe 11 часов назад
Anthu akudya chitedze inu aaaaah zopepera izi akuguran et 😢
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 12 часов назад
boma ndilomweli bas 2030 ❤❤❤❤❤❤
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 12 часов назад
Zelu mulibe akulu
@AusmanYusuf-b9d
@AusmanYusuf-b9d 9 часов назад
Nyan wa munthu
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 12 часов назад
Zabodza izi si Brian banda zapa social media izi
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 12 часов назад
Dyelaaaaaaaaaaaaaaaa akufuna makobili
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 11 часов назад
😂😂😂😂😂😂 anthu mulipa ganyu angakhale dan luu uyu komaso brian banda uyu iiiiiiiiii ganyu wavutadi
@henrymwale8994
@henrymwale8994 9 часов назад
Dan lu walowadi koma uyu akufusa mafusoyo nde si Brian banda
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 8 часов назад
@@henrymwale8994 asiyeni azipita grace chinga adalankhula kare ife tidamva ndithu
@AdamMakala
@AdamMakala Час назад
Ndamutuluka
@JamesDaud-jz7uq
@JamesDaud-jz7uq 12 часов назад
Si dan luu komanso si brayan banda
@ThokozaniKaluluma-rj6rp
@ThokozaniKaluluma-rj6rp 8 часов назад
Nde munamiza mwanatu si Dan Lu ameneyo
@indiAisha-q2o
@indiAisha-q2o 19 минут назад
Akunama si Dan Lu amosesi uyu mboloyako
@DavieNayuma-h8i
@DavieNayuma-h8i 12 часов назад
Malawi musatinamize uyu si Brian b bodza
@LydialHarry
@LydialHarry 4 часа назад
Sizikubhebha ataaah brian wakeyo wa tchaina siwaoriginal😂😂😂
@HamiltonRaphael-q2d
@HamiltonRaphael-q2d 12 часов назад
uyu si Dan lu Komanso si Brain Banda
@SemteeTambala-rh2br
@SemteeTambala-rh2br 12 часов назад
Zoona
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 12 часов назад
iiiii ndipo serious uyu SI Dan ndipo uyu SI Brain Banda anthu tamapangani za umunthu ndipo Dan lu sangalowe Mcp or patatani mmmmmm apo nde mwanama abambo inu
@AchinaKellz
@AchinaKellz 9 часов назад
Ndachitsiru amenewo ziwanda zawakunga kuyimbaso 0 10
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 12 часов назад
Uyu ndi Ausi ndungu wa Radio Nkhotakota
@user-le3lr6jn7g
@user-le3lr6jn7g 11 часов назад
Mulibe mo Dan lu Brian bandanso mulibemo mu interview
@user-ws9sy7pp3w
@user-ws9sy7pp3w 12 часов назад
Si Brian Banda uyu inu
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 12 часов назад
Regret coming soon...wait for it
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 8 часов назад
🤞🤞🤞🤞🤞
@patrickMakhumba-yc7rb
@patrickMakhumba-yc7rb 10 часов назад
Chitsiru iwe si Brian band mau onyasa ngati ameneo
@PatrickJohnRock
@PatrickJohnRock 12 часов назад
Zinthuz zikungophelezera kalata yomwe anasiya mama grace chinga bas
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 7 часов назад
Zabodza si Brian Banda uyu
@ntombiunice8637
@ntombiunice8637 4 часа назад
Wathawa chipani cha gogo
@BandaBanda-ww9ok
@BandaBanda-ww9ok 10 часов назад
Zaboza izi palibe Brian Banda komanso palibe Dan lu apa
@ishmaelbrighton9885
@ishmaelbrighton9885 3 часа назад
Nanuso mboli yanu kod mumathamanga kupanga post zithu zaboza bwanji Brian band amaveka choncho panyapako
@JasonMailos
@JasonMailos 10 часов назад
Inu machende Anu, Brian Banda sameneyi nyini zamanu mwava dan Lu sa samayankhula chocho bwanjikodi?
@FatimaJuma-k3k
@FatimaJuma-k3k 5 часов назад
Dan Lu nde wapalatu ukajoina nawo tikuferanji kwabambo asikono zoona?
@KalongaWhy
@KalongaWhy 9 часов назад
Dan fan achisilu
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 10 часов назад
Hahaha Dan lu musiyeni grace chinga adalankhula za chipani chamaganzi lero ndi izi koma sizingatheke mulungu ndiwamphamvu
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 10 часов назад
Rip grace chinga
@ChimwemweSauka
@ChimwemweSauka 10 часов назад
Brian wake uti boza limenero
@FrancisBanda-o3g
@FrancisBanda-o3g 10 часов назад
Wina ndi ausi chabwera DJ wa pankhotakota radio station
@rozertmbale9545
@rozertmbale9545 4 часа назад
A Malawi ambiri saona ubwino wa MCP. Ku DPP kwathawa anthu ambiri akulu akulu. Chiliko akuthawa anthu kumeneko.
@jomochirwa
@jomochirwa 7 часов назад
Vuto a dpp munkungotaya nthawi kutukwana pa social midia,tapangani zomaka pa graund,mcp ikukubelanitu anthutu ,mukuwonatu ,samalani.
@NolityKondowe
@NolityKondowe 3 часа назад
Nchifukwa chani anthu dpp akuyituluka.Kuzafika chaka cha mawa January tizamva a china Namalomba ndi Chaponda nawonso alowa MCP.
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 5 часов назад
Pokhapo pongolemba za bodza kuti Brian Banda akufunsa mafuso asali iyeyo ndakana zoti akuyankhayo ndi Dan Lu
@thabitiesulaiman6194
@thabitiesulaiman6194 11 часов назад
Palibe chomwe chimandinyasa kumeneku ndi sound mumayika pasipasiyo uthengo suumafunika zimenezo bwanjikodi
@hanneefmbwana8120
@hanneefmbwana8120 4 часа назад
Koma musamanamizile kuti Brian banda
@Kamwachale
@Kamwachale 54 минуты назад
Akumveka Ngati Kunkuyu
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 3 часа назад
Mawu a Dan Lu ngati Moses kunkuyu zikukhala bwanji
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 9 часов назад
Mapazi anu agalu inu mukutipusisa mukuonangati sitimawaziwa mawu a dan lu komaso Brian banda?
@AlexanderMphalasa635
@AlexanderMphalasa635 6 часов назад
Dan Lu ndi yemweyu but Brian si ameneyo
@PeterNambazo
@PeterNambazo 10 часов назад
Chisilu ichi anthu amutuluka angofuna ndalama bas
@VituIshmael
@VituIshmael 3 часа назад
Wabalalika celebrate wathuyu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 11 часов назад
Aaaa mene wawonongela chakwela ndi MCP yakoyo ndalama dzekakwa anthu a MCP okha nde anthu akupasidwa ma MILION angakane KOMA AMALAWI KU VOTE NDIWE MUNTHU TITSAPUTSE NDI ANTHU AKULANDILA NDALAMA ZA MAGADZI DZIKANAKHALA NYIMBO.IMAWINITSA MUNTHU DAN LU ANAYIMBA ZOKHUDZA DPP KOMA SINAWINE nsono chifunala amalawi 2025 kutsamala umboni woti kuwina kwa MCP tatsankha kubwelela kuchipani chimodzi ndiumenewo bolani pano kuti akuwagula koma 2025 anthu adzilowela kuwopa kumangidwa akawinatso a MCP anthu akuwagula lelowa adzkhala amphawi chifukwa dzipani dzotsutsa dzizakhala dzatha otse MP adzalowa MCP APATU AMALAWI POFUNIKA MAPEMPHELO TIKOMANA NDIMAMVUTO BOLANI PANO KUYAMBA CHABE NGATI MCP IPILILA KULAMULA DZIKO 2025 LA MALAWI UKU NDE KUYIPA KWA MCP IKAMALAMULA AMFUNA IKHALE YOKHA BASI iiii TINAPANGA MISTAKE AMALAWI
@JohminMatick-q5k
@JohminMatick-q5k 8 часов назад
Since this is none of my business, let me count from 1 to 1000. 01,02,03,04,05,06,07,08,09,10,11,12,13,14,15,16,17,18,19,20,21,22,23,24,25,26,27,28,29,30,31,32,33,34,35,36,37,38,39,40,41,42,43,44,45,46,47,48,49,50,51,52,53,54,55,56,57,58,59,60,61,62,63,64,65,66,67,68,69,70,71,72,73,74,75,76,77,78,79,80,81,82,83,84,85,86,87,88,89,90,91,92,93,94,95,96,97,98,99,100,101,102,103,104,105,106,107,108,109,110,111,112,113,114,115,116,117,118,119,120,121,122,123,124,125,126,127,128,129,130,131,132,133,134,135,136,137,138,139,140,141,142,143,144,145,146,147,148,149,150,151,152,153,154,155,156,157,158,159,160,161,162,163,164,165,166,167,168,169,170,171,172,173,174,175,176,177,178,179,180,181,182,183,184,185,186,187,188,189,190,191,192,193,194,195,196,197,198,199,200,201,202,203,204,205,206,207,208,209,210,211,212,213,214,215,216,217,218,219,220,221,222,223,224,225,226,227,228,229,230,231,232,233,234,235,236,237,238,239,240,241,242,243,244,245,246,247,248,249,250,251,252,253,254,255,256,257,258,259,260,261,262,263,264,265,266,267,268,269,270,271,272,273,274,275,276,277,278,279,280,281,282,283,284,285,286,287,288,289,290,291,292,293,294,295,296,297,298,299,300,301,302,303,304,305,306,307,308,309,310,311,312,313,134,315,316,317,318,319,320,321,322,323,324,325,326,327,328,329,330,331,332,333,334,335,336,337,338,339,340,341,342,343,344,345,346,347,348,349,350,351,352,353,354,355,356,357,358,359,360,361,362,363,364,365,366,367,368,369,370,371,372,373,374,375,376,377,378,379,380,381,382,383,384,385,386,387,388,389,390,391,392,393,394,395,396,397,398,399,400,401,402,403,404,405,406,407,408,409,410,411,412,413,415,416,417,418,419,420,421,422,423,424,425,426,427,428,429,430,431,432,433,434,435,436,437,438,439,440,441,442,443,444,445,446,447,448,439,450,451,452,453,454,455,456,457,458,459,460,461,462,463,464,465,466,467,468,469,470,471,472,473,474,575,476,477,478,479,480,481,482,483,484,485,486,487,488,489,490,491,492,493,494,495,496,497,498,499,500,501,502,503,504,505,506,507,508,509,510,511,512,513,514,515,516,517,518,519,520,521,522,523,524,525,526,527,528,529,530,531,532,533,534,535,536,537,538,539,540,541,542,543,544,545,546,547,548,549,550,551,552,553,554,555,556,557,558,559,560,561,562,563,564,565,566,567,568,569,570,571,572,573,574,575,576,577,578,579,580,581,582,583,584,585,586,587,588,589,590,591,592,593,594,595,596,597,598,599,600,601,602,603,604,605,607,608,609,610,611,612,613,614,615,616,617,618,619,620,621,622,623,624,625,626,627,628,629,630,631,632,633,634,635,636,637,638,639,640,641,642,643,644,645,646,647,648,649,650,651,652,653,654,655,656,657,658,659,660,661,662,663,664,665,666,667,668,669,670,671,672,673,674,675,676,677,678,679,680,681,682,683,684,685,686,687,688,689,690,691,692,693,694,695,696,697,698,699,700,701,702,703,704,705,706,707,708,709,710,711,712,713,714,715,716,717,718,719,720,721,722,723,724,725,726,727,728,729,730,731,732,733,734,735,736,738,739,740,741,742,743,744,745,746,747,748,749,750,751,752,753,754,755,756,757,758,759,760,761,762,763,764,765,766,767,768,769,780,781,782,783,784,785,788,789,790,791,792,793,794,795,796,797,798,799,800,801,802,803,804,805,806,807,808,809,810,811,812,813,814,815,816,817,818,819,820,821,822,823,824,825,826,827,828,829,830,831,832,833,834,835,836,837,838,839,840,841,842,843,844,845,846,847,848,849,850,851,852,853,854,854,855,856,857,858,859,860,861,862,863,864,865,866,867,868,869,870,871,872,873,874,875,876,877,878,879,880,881,882,883,884,885,886,887,888,889,890,891,892,893,894,895,896,897,898,899,900,901,902,903,904,905,906,907,908,909,910,911,912,913,914,915,916,917,918,919,920,921,922,923,924,925,926,927,928,929,930,931,932,933,934,935,936,937,938,939,940,941,942,943,944,945,946,947,948,949,950,951,952,953,954,955,956,957,958,959,960,961,962,963,964,965,966,967,968,969,970,971,972,973,974,975,976,977,978,979,980,981,982,983,984,985,986,987,988,989,990,991,992,993,994,995,996,997,998,999,1000 have a blessed Thursday
@TressLuka
@TressLuka 11 часов назад
Pajatu mbalame za mtundu umodzi zimaulukura limodzi ndiye izi mzosadabwitsaa. Psiti...😢
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 11 часов назад
AAA koma guys muli pa ganyu uyu si Dani luu ayi😂😂 even burayan banda amayakhula chocho??
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 11 часов назад
😂😂😂😂 ausi ndungu uyu. Komaso aaaa Dan lu ndakaika ndithu
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 12 часов назад
Komaso uyu si bryan ai
@ChilekaMoyenda
@ChilekaMoyenda 3 часа назад
Wayamba maboza
@SakaLack
@SakaLack 11 часов назад
Sizachilendo idzi tinamuonaposo ife Joseph mkasa mbuyomu poti boma ili likugwirisa tchito ndalama pokopa anthu kuchipani chawo kazidyeni zimenezo Mr.
@MosesLackson-l4f
@MosesLackson-l4f 5 часов назад
Zaziii mxiew😮
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola 6 часов назад
Nankha bwanji Interview yake sikuonesedwa kuti tionedi zaboza izi
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc 10 часов назад
Ndinu agalu mau akusiyanilatu mbuz za anthu
@ChippieBandah
@ChippieBandah 10 часов назад
Kuyankhula mwanzelu Dan lu
@YohaneBanda-w4q
@YohaneBanda-w4q 10 часов назад
Kkkkkkkkkkk ati Brain Banda ameneyoooo koma ine wachiwiliyooo ndikuone ngati moses mkukuyuuu
@lifnetmakoka2175
@lifnetmakoka2175 6 часов назад
mmmmm Boza ili Brain sayakhula chocho mmmm
@jennyx6914
@jennyx6914 2 часа назад
ithink ku MCP uku mkumemene kuki chimake cha ssrsniki kspena illuminate seeiuos oyimbawa bwanji?but let me tell the truth SKEFFA CHIMOTO was my fsbvourite and stull ilove him but eish am disappointed kwabasi
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 10 часов назад
Dan lu kolowa mcp sizachilendo pajatu chipani ichi mchamagazi ndipo kalata ya grace ikuphelezela bs kmso akufusa mafusoyo si Brian banda mabodza bwanji
@MathaNamanja
@MathaNamanja 12 часов назад
Brian waife siameneyu
@SamuelMussa-f4f
@SamuelMussa-f4f 16 минут назад
Muuzen panyero pake olo ali wasatanic sangandichite kanthu mapwala ake dyera osangot akugura bwanj
@SteveniBanda
@SteveniBanda 10 часов назад
Asauka ameneyo akufuna ndalama amugula
@SimonGulani
@SimonGulani 11 часов назад
Kaya Dan achokaku Dpp Kaya Sana choke sizizatipangisa ife Kukavota mopoila ai
@tingamasi106
@tingamasi106 9 часов назад
Nde cholembera kuti brian banda nchani? Ndinu opusa
@BrotherPaul-ln2ld
@BrotherPaul-ln2ld 4 часа назад
Si Dan Lu uyu.
@ASHAMUMATIYA
@ASHAMUMATIYA 48 минут назад
Uyu panyapake
@IsaacKomando-g5s
@IsaacKomando-g5s 3 часа назад
Koma Brian mumamuziwa? Kapena mwakhuta nyemba
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson 6 часов назад
Zabodza izi si Brian ameneyi
@babranzima8120
@babranzima8120 11 часов назад
Analandira ndalama zazawinaso Ata athanasius amenewo
@GreyMwanyimbo
@GreyMwanyimbo 12 часов назад
Umakwana dan luuu
Далее
APM WAFIKA NDIPO WALANDIRIDWA MWANYOOO MU MZUZU
4:09
Просмотров 1,7 тыс.
У НАС ДОМА ЗАВЕЛАСЬ КРЫСА 🐀
01:00