Тёмный

BON KALINDO LERO PA 2 AUGUST 2024 | UTHENGA OPITA KWA OMWE ANALI KU SOUTH AFRICA| 

DZIWE TV
Подписаться 33 тыс.
Просмотров 57 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 226   
@violetpotani
@violetpotani 2 месяца назад
Kupanda inu enafe sibwenzi tikudziwa zomwe zikuchitika mdzikoli... We love you sir 😮
@GladesMhango
@GladesMhango Месяц назад
Amene amadana ndi kalindo sali bwino akufunika mapemphero, Amen
@ZioneMkwanda-y6i
@ZioneMkwanda-y6i 2 месяца назад
Inenso ndikugwilizana Nanu, kuti wodana ndi Kalindo ndi wasatac ,koma bola chilumgamo ukuchidziwa , Mr Kalindo osafooka osatopa kutumikira ife . Zoyankhula zanu ife zimatitsegula mitima ndi maso ndipo muziimabe pachilungamo ndiwe dolo 1 umayankhulira ku Malawi komkuno osati zokabisala ku Tanzania mkumang'alura! 😅😅 More 🔥 Mr president waife osauka, odana naye Dolo uyu ndi wa satanic yotheratu Izoooooo😅😅😅 mumumva Kalindo sanati 🔥🔥🔥🔥🔥 ACHALUME eni -eni ogona kukhomo kosatseka Boneeee Kalindo mwana oopsa kwambiri 😅😅😅😅 love you.
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 2 месяца назад
@@ZioneMkwanda-y6i kutumikila alomwenutu,
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 месяца назад
Amene amadana ndi bon kalindo ndekut kwao sanamulere bwno, boooon kalindoooooo president wathu wathu wa anthu osauka timamunyadira ❤❤❤
@user-cg5ml7ym4v
@user-cg5ml7ym4v 2 месяца назад
Enough is enough tiyamike Mr Born kalindo potikumbutsa ife a Malawi zoyenela kuchita.❤❤❤
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m 2 месяца назад
Chilungamo chimawawa nthawi zonse, keep it up the DC, may God protect you mr kalindo🥰
@HassanDuwah
@HassanDuwah 2 месяца назад
Guys this is true they must pay money bon kalindo he must be president or vice guys he's true man
@WisdomPhiri-sh9we
@WisdomPhiri-sh9we 2 месяца назад
Mmmm but Born Kalindo you are really a true activist and you stand us though am a Zambian but l follow you. Please keep on updating us and never stop doing for the betterment of malawians.
@HassanDuwah
@HassanDuwah 2 месяца назад
@@WisdomPhiri-sh9we ohh uchokela mu 🇿🇲 zd
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens 2 месяца назад
Uyuyu asayimile chilichonse akhale mau a anthu osauka, the real leader of opposition
@WorriedNdhlovu
@WorriedNdhlovu 2 месяца назад
Adanena kale kut iyeza ndale ayi​@@beatsbymcstevens
@RestarUmi
@RestarUmi 2 месяца назад
Ndili momo Mr DC wina anyela
@BryanJSimeon
@BryanJSimeon 2 месяца назад
In the world 🌎 of Ng'alulayizatinon....❤
@ClementBanda-ob8sj
@ClementBanda-ob8sj 2 месяца назад
DC himself 💪
@SahilluYusuf-sk7es
@SahilluYusuf-sk7es 2 месяца назад
This is the true activist in malawi ,we are on his foot
@ObertNyirenda
@ObertNyirenda 2 месяца назад
Pitilizan kuyankhula chilungamo❤
@HildaMachinjiri
@HildaMachinjiri 2 месяца назад
Mumakwana mr kalindo
@ObertNyirenda
@ObertNyirenda 2 месяца назад
That's the fact Mr president osauka
@InocentPetrol
@InocentPetrol 2 месяца назад
Ndizoonadi bwana kalindo
@JosephNgulinga
@JosephNgulinga 2 месяца назад
Ndizowona Malawi tagona pitilizan bon kalindo kutilakhulila
@bestergeorgekabanga
@bestergeorgekabanga 2 месяца назад
❤❤❤❤koma ulamuliro uwuu ndye ulibe tsogolo ndithu, mpakana mwini nyumba adzidula nsokho ndye zopanda nzelutu iziiiii
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 месяца назад
Bakili muluzi tv , Limpopo tv ndi Bon Kalindo Tv tikuyamikeni chifukwa mukuyimila ife osawuka mwa jeniwini poti zipani zotsutsa zikugona kwambiri. More 🔥
@JasonMailos
@JasonMailos 2 месяца назад
❤ ndizoona
@enerstmakochera3956
@enerstmakochera3956 2 месяца назад
Thanks dziwe TV I'm with you on this one
@lloydjeremiah2250
@lloydjeremiah2250 2 месяца назад
The DC ulemu wanu
@FaheemChipojola
@FaheemChipojola 2 месяца назад
Amene amadana ndi kalindo ndi mfiti
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 2 месяца назад
Tilinanu lumozi bon karindo ❤
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 2 месяца назад
More fire iweyo ndi one ❤❤❤❤
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 2 месяца назад
Akumakapepetsa chakwerayo kuti chani😊mupepetsa chakwera ndi chilima chidali chibale kodi
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 месяца назад
Kkkk ndipo Kalindo ndi 1 kkk nyumbadzo ndi za amanu The DC mwana oipitsitsa zedi❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo 2 месяца назад
The DC, k. k osaopa
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 2 месяца назад
Tangomuphani chakwerayo inu nanga azivutisa chonchi kulibe nyanga mwina kwanuko aaaaa
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 2 месяца назад
@@HappyBirchForest-zy8nq watsoka iwe
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 2 месяца назад
@@yowasschitsosa5348 choka iwe back to sender 😈
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 2 месяца назад
We are behind you no matter what Dr chikangawa galu 😂😂😂
@GeorgeTembo-v6i
@GeorgeTembo-v6i 2 месяца назад
God bless you all the time
@dontreybanda278
@dontreybanda278 2 месяца назад
Good massage boss
@CharlesPhiri-v2p
@CharlesPhiri-v2p 2 месяца назад
Mumakwana bwana kalindo ndipo musatope aunzeni zoona
@FisherAction
@FisherAction 2 месяца назад
Indeed mr person of poor president people don't stop acting nice way what you are doing keep it up big ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ for ever
@FisherAction
@FisherAction 2 месяца назад
President of poor people ❤❤❤❤❤❤❤🎉
@ruthkundwe7448
@ruthkundwe7448 2 месяца назад
Komatu uli ndikukamwa myamata iwe,ma point oka oka, continue brada
@GrinTemboh
@GrinTemboh 2 месяца назад
Tiye nawo Kalindo the d c achewa akuzolowela pempho Langa Kwa iwe the d c d p p akalowa m'boma uzakhale ministry of security
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 2 месяца назад
Amfana nambala 1 Bon Kalindo 15:52 olimba mtima kwambiri mmalawi muno, Number 2 bakili muluzi tv, Number 3 NTANYIWA, Number 4 mutholo chikuni chautsi, Number 5 innocent banda, Anthu opusa kwambiri kumalawi ndi awa: Number 1 redson muklo, Number 2 ben longwe, Number 3 billy malata, Number 4 agape khombe, Number 5 layton mangoch, Number 6 ken msonda, Number 7 kondwani nankhumwa, Number 8 sungamoyo , Number 9.... too many to mention eish! , wina apitilize guys
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 2 месяца назад
Yes kalindo he must be president
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 2 месяца назад
Anthu nyumba azivutikiladi kumanga zinthu zake zodula iye azikalandila ndalama ngati ndani?
@RamadanShafisha
@RamadanShafisha 2 месяца назад
Tinatopa nazo izo ife tikufuna uthenga wazitukuko zangozizo ndindale chabe sindimadya ndale
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 2 месяца назад
Nyengo yakuswakuswa
@PanjiNkhwazi-wj1ek
@PanjiNkhwazi-wj1ek 2 месяца назад
Keep telling the truth to the Nation. You always speak for the poor
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 месяца назад
Ursogoleri ndi mphatso osati sukulu kapena mpikisana. Ndimachita chidwi ndi mafumu akumudzi, samakhala anthu asukulu koma amaweruza milandu mwamzeru kuposa ma judge ama PhD koma too corrupt. Mr Kalindo you can be the president, tikusowa mtsogoleri wolimba mtima ndi wachilungamo
@MariamAlabi-t3n
@MariamAlabi-t3n 2 месяца назад
Koma ndiye zafikadi phoyipha mpakana msongo kwachina. Landlord ,iiiiiii kuzisakha ndi nkwangwa. God have mercy.
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 2 месяца назад
Hiyaaa mpaka tax lol yomwe ayiyambayoo saikwanitsaatuuu nyumba tinamanga ndi ndalama dzathuu!ulemu wanu MR Bon kalindooo the DC!
@EgpafMalawi
@EgpafMalawi 2 месяца назад
Aaaah koma yotolela misonkho kwa malandlord zo ndiye sizoona city rates amatolela ija yachepa?
@AnyumbaJulias
@AnyumbaJulias 2 месяца назад
Zoonad anthuwa kuyakhula akuyakhula koma zonvesa chison pa ground muzavotela mcp yomweyo
@livinessSomola
@livinessSomola 2 месяца назад
Komanso nfundo za nsogoleli uyuyu ndi zofota,zonyala kuposa adzisogoleli onse omwe takhala nawo mu dziko lathu
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 2 месяца назад
The DC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 2 месяца назад
@@chimwemwenkute3839 awopsa kma ndi chitini chopanda phaka, kunar UDF itapangidwa chipongwe siinayankhle kalikose, kma a DPP mur busy zamanyazi ka mtundu ka lomwe
@ClementMisozo
@ClementMisozo 2 месяца назад
Kalindo ndi more fire
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 месяца назад
Usadandaule 2025 akapuma mr chikangawayo
@ArnoldThomson-d6v
@ArnoldThomson-d6v 2 месяца назад
Chikangawa wadanda Pelekani report
@Dickson-d5i
@Dickson-d5i 2 месяца назад
Umakwana ada!!
@saulbipa6882
@saulbipa6882 2 месяца назад
They want to modify the report first. Koma they dont know kuti malawians are no longer sleeping
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
Koma Chakwera alibwino bwino?ma landlord anakongolako chain kwake or kwathandidzako pomanga or kugula nyumba🤔 😇something went wrong serious tsalibwino
@HastingsSteven-e8x
@HastingsSteven-e8x 2 месяца назад
❤❤
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 2 месяца назад
Mbudzi zawanthu okubawo
@BonexMussah
@BonexMussah 2 месяца назад
Kalindo ndifana wa bhooo mwana wapa mj ndimamufila ulemu wake mwanawamwa njeza okulira mwamangani ndi usi koma usi mmmmmm mbola
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 2 месяца назад
Ndinavutikandekha kupangisa passport kupita kujon kukagwira magobo nkugula malo anga nkumanga nyumba lero ndaikamo walendi ndie wina azikati ndizilipilapo nsonkho zopusabasi
@JosephLunga-e7q
@JosephLunga-e7q 2 месяца назад
Your good president mr kalindo
@ireenesthermbisa7200
@ireenesthermbisa7200 2 месяца назад
Komatu kalikonse tikaona😢, mpaka Landlord kukhomera misonkho😓😓
@HaroonDaud-w8g
@HaroonDaud-w8g 2 месяца назад
We are solidly behind you 🫡🫡
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 2 месяца назад
Who is Chakwera kuti akampepese iyeyo? Malo mokapepesa kwa Mary Chilima
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 месяца назад
Zoona mr kalindo a pension a mmalawi muno ena zaka ziwiri anthu Sanalandire ndalama zawo boma la chakwera ndi MCP ndilozunza kwambiri
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 2 месяца назад
Iiiiii zafikanso kumanyumba , asaaa ationjeza panseu basi
@RelexRest
@RelexRest 2 месяца назад
Kma ndye mwakwyatu iiii, thank you a dziwe pomatpatsila nkhan zosyana syana
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS 2 месяца назад
Mwamveka inuyo akalindo God bless
@IssahAluba
@IssahAluba 2 месяца назад
Km gati Pali president amenewo wathilidwa manyi nde ndichakwera gati Ali Ndi nzeru avetsetse zomwe akufuna AMalawi
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 2 месяца назад
kumalawi kuno ndiku Gahena nsaname......
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 2 месяца назад
Mnthu wotiyankhulira ndi ameneyu the DC monga ine kapopangolo sindingayankhule koma zimandiwawa mmtima kuopa kumangidwa koma the DC alipo ndithu wotiyimirira kkkkk
@JeremiahChilenje
@JeremiahChilenje 2 месяца назад
Mwana wachabe😅😅
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 2 месяца назад
The Dc born kalindo ndiwani guys mwana olimba mtima
@CathrineBizza
@CathrineBizza 2 месяца назад
Umakwanila report tikufina litulike akubisa chani shupit
@FisherAction
@FisherAction 2 месяца назад
Odana ndi kalindo ndi mfiti oja matewera
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 2 месяца назад
Tikondani akalindo ndosowani MA odiyo anu masiku amenewa Koma timakukondani ameneyotu atukwanidwa sadati
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 2 месяца назад
Eti eti nyumbazo ndizaamawo😂😂😂😂😂😂😂 koma anthu atopa🙌🙌🙌
@ChimmzyMbunju
@ChimmzyMbunju 2 месяца назад
Nyumba kod dzamanuko
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 2 месяца назад
Bon kalindo yoyeeee!!!!❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@WallyMsiska
@WallyMsiska 2 месяца назад
Mr ng'alurization mkulankhula zoona
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 месяца назад
Massive mr DC odana ndinu ndi mfiti.
@HopeLuwangakaunda
@HopeLuwangakaunda 2 месяца назад
Our president BON KALINDO mwana oopsa kwambiri
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam 2 месяца назад
Ife sitizasiya kuyankhula mr chiphe chikangawa ndipo mafumuwonso ndi opusa kopepesa sakukuona? Chikangawa report lifike poyera ndipo ngati lonama tifufuza tokha chilungamo chioneke
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад
Bon Kalindo 🔥🔥🔥🔥❤️🔥❤️🔥 activist Osaopa konse
@ChriffordChihana
@ChriffordChihana 2 месяца назад
Bg mumatiimirira.keep it up
@CharlesKachipanda-jz9jv
@CharlesKachipanda-jz9jv 2 месяца назад
THE DDDDDDCCCCCCC!!!!!!!!!!!!!!!!!
@daviechannel8603
@daviechannel8603 2 месяца назад
Ndipo mavuto ndithu galu ameneyo bwanji ndalama yonseyo yooba mpaka akatolele yamalandodi mmmm koma mavuto afika pena
@festonkapesi3771
@festonkapesi3771 2 месяца назад
My president the dc
@JonesMatthews-p6p
@JonesMatthews-p6p 2 месяца назад
Let's do something guys especially to as we are out of malawi country. Which means Malawian they don't have land. Now the land it's for goverment. What nonsense is this Mr president 😢😢
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 2 месяца назад
Uyu amalandila ndalama kwa chakwera nde chilichotse chomwe akuyakhula ikukhala movies ya tikufelanji
@ChimmzyMbunju
@ChimmzyMbunju 2 месяца назад
😂😂😂😂chilungamo chimenecho
@HaliJana
@HaliJana 2 месяца назад
NGATI ZAMUVUTA ATULE UDINDO GOLOGOLO CHIKANGAWA
@GuliwaGixious
@GuliwaGixious 2 месяца назад
Powerful DC
@jamesnisifol
@jamesnisifol 2 месяца назад
Katundu madzi mr DC 💥💥💥💥
@AgathaJerard
@AgathaJerard 2 месяца назад
Lipoti libwere tikudikilatu pano chikangawa 👍👍
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 2 месяца назад
Big up the DC ❤❤❤❤❤
@DarlsonMithi
@DarlsonMithi 2 месяца назад
Ng'alulisation😂😂
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE 2 месяца назад
Eyadi atitengeradi a muhone abale pa muzimba boma😢
@DumisaniMhango-e4i
@DumisaniMhango-e4i 2 месяца назад
We love the dc than chakwera
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 2 месяца назад
Ndiye nkhani yake kasakaniza😂😂😂😂😂
@RitaKainga
@RitaKainga 2 месяца назад
Auzeni a DC,agalu akuba amenewa,nyumbazo ndzamawoo❤❤❤❤❤
@KondwaniMamveka
@KondwaniMamveka 2 месяца назад
Zona zake👉
@JoeKayira
@JoeKayira 2 месяца назад
Umbuli ndi bvuto lalikulu.
Далее
DIY Pump Solutions
00:18
Просмотров 1,3 млн
Кольцо Всевластия от Samsung
01:00
Просмотров 428 тыс.
Angry bird PIZZA?
00:20
Просмотров 7 млн
Former President Thabo Mbeki speaks about Tito Mboweni
20:48
BON KALINDO LERO PA 22 OCTOBER 2024 |
17:40
Просмотров 6 тыс.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 122 тыс.
DIY Pump Solutions
00:18
Просмотров 1,3 млн