Тёмный

BON KALINDO NDI MALAWI FIRST APANGITSA NSONKHANO NDIPO AOPSYEZA BOMA KUTI APANGA MA DEMO PA 8 AUGUST 

Makosana
Подписаться 88 тыс.
Просмотров 30 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

8 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 131   
@adamhassan7451
@adamhassan7451 Месяц назад
You guys you are the best. Malawi needs people like you for the change ,Mr DC more 🔥🔥🔥
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Timakiyimilirani Ife amalawi ulemu wanu a Malawi first ❤
@daudlwanda9591
@daudlwanda9591 Месяц назад
P
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov Месяц назад
Koma bon kalindo ulemu wanu watching from Pretoria
@ndauzamtonga6719
@ndauzamtonga6719 Месяц назад
Watching from Zambia
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga Месяц назад
Kodi munati pa 31 ndimawatu pano mwayambaso kutchula zapa 8 August mm ndidaziwa ndithu kuti sizingatheke kupanga mademo ayi. Komaso mungosiya kutchula za mademo osati muzidalilitsa anthu then ndikumalepheresa😡
@user-ti9yk4eg2l
@user-ti9yk4eg2l Месяц назад
APA ndy angosiyadi basi
@MzadziWanga
@MzadziWanga Месяц назад
Ndimaona ngt a mawa akusogolera ndi Mr game changer not Malawi first, kapena onse nda amodzi
@isaacbandah3617
@isaacbandah3617 Месяц назад
Mmawa MA demo alipo sizinasinthe ayi
@user-kr1tf2tu7s
@user-kr1tf2tu7s Месяц назад
Zika zake ziti zakumudzi kwanu zazii
@user-ui6vh1ld4f
@user-ui6vh1ld4f Месяц назад
Agulitsidwa mademo
@SoundmasterElectronics
@SoundmasterElectronics Месяц назад
Ma demo akumalawi saphula kanthu timakayenda mu nsewu pomwe yemwe tikumunayo Ali ku state house what's that samamva kuwawa kulikonse that's why sitipindula kanthu komanso anthuwo sapangapo kanthu ngat mukufuna zinthu zosinthe go straight kwa amene akupangitsa not munsewu nkumasokonezanso bizness zovuta kalezi
@emmanuelchirwa3420
@emmanuelchirwa3420 Месяц назад
Thank you brother more 🔥🔥🔥 well done ✅ malawi first to save poor Malawian We all love you , more 🔥🔥❤❤❤❤
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o Месяц назад
I love bon kalindo and malawi First live from ntcheu
@lyiemax
@lyiemax Месяц назад
Beautiful press conference but the problem is the weaknesses of opposition parties of this country , it seems our opposition parties are not ready to rescue it's citizens.
@MrThomas-j9d
@MrThomas-j9d Месяц назад
Thank you B k & your support your freedom fight god protect you each & everytime ( from port Erazabeth kostern South Africa
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h Месяц назад
Mbambande mr DC
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j Месяц назад
Malawi first ❤
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Месяц назад
Watching live from Mangochi mmbaluku
@getbusy7173
@getbusy7173 Месяц назад
bma lake liiiiitiiii zakumachende eti mcp izitixuxa aaaaaaaaaaaaaaa
@vivianmkwate8536
@vivianmkwate8536 Месяц назад
we love you Malawi first Chonde malawi tiyeni tituluke zinthu zisinthe tatopa Amalawi
@GiftMwaungulu
@GiftMwaungulu Месяц назад
mwasinthaso date aaah😅
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Месяц назад
Go! Malawi First, we are supporting you!
@user-fg1me1un8p
@user-fg1me1un8p Месяц назад
Alunta continua Bon your indeed pangolin
@NeverBeforeMnesa
@NeverBeforeMnesa Месяц назад
Mwayiwala road traffic ndi immigration ( driving license & passports )bravo malawi first
@gannkazembe1746
@gannkazembe1746 Месяц назад
Bon Kalindo simunthu waba.
@user-ff9xq5ss8d
@user-ff9xq5ss8d Месяц назад
Watching from msundwe
@JonathanMsiska
@JonathanMsiska Месяц назад
Mademo mwachulusa boza masiku muñgosintha.
@user-ui6vh1ld4f
@user-ui6vh1ld4f Месяц назад
Mwina mademowo akuwagulitsanso chifukwa akungosinthasintha matsiku
@HalimaDamiano
@HalimaDamiano Месяц назад
Bravo the Dc
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Месяц назад
Mumapangila kuti mademowo ku thyolo kapena ku mulnje
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Ine sinatuluke ID should I say ndine wa ku southern region sizikutengela mbali Koma that delays is everywhere so osamatigawanitsa please
@PhillspicJere
@PhillspicJere Месяц назад
Koma munthu mukuti kalindoyu kwao ndi kumalawi komwe kuno? Eeeeeh chifukwa kuda kokhako akuoneka ngati ndiwaku Malli
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd Месяц назад
wabodza iwe ndakuona kale pamtundapo
@YangMaku-x8w
@YangMaku-x8w Месяц назад
Sekwanele, aluta continue Mr kalindo
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Месяц назад
The DC'S mwana woooopsa kwambiri
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад
Malawi first, people first with Boooooon kalindo and the Malawi first tiyeni pansewu on 8th of August
@YasinAdam-pn4bh
@YasinAdam-pn4bh Месяц назад
God bless you Bon Kalindo
@DavidAugustine-y5v
@DavidAugustine-y5v Месяц назад
Zikomo kwambili abon😮 kalindo ambuye azikudalisani
@PhillspicJere
@PhillspicJere Месяц назад
Ambuye musamamupase ntchito nanu inu Mulungu sakondwera ndianthu opusa,
@ThoccoPearson
@ThoccoPearson Месяц назад
@@PhillspicJereoputsa ndiweyo
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh Месяц назад
Chopusa ndiweyo galu
@Brianchisi
@Brianchisi Месяц назад
pangani zazeru kalindo musana mize anthu khondo siyimanga muzi ndikatindiku yangameni mupando momwe mwakhala izachisoni ine siwachipani koma kulila kwa amalawi tinayambaliti kusintha kufike ndi inu takhalandi asogoleri angati anasitha ziko kalindo ngatikuli kusauka tangowa pephani achakwera akuthandizani zione selo munayamba ndinu ngati kopazioneselo zosetapanga tapindulachani nangakatangale anayambaliti mungophesa ana aeni
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq Месяц назад
Mumatsata zimene zikuchitika maiko ena monga Kenya? Kapena mungoyankhula nchimbulimbuli?
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Ameneyu simmalawi ntayeni 😂😂 ndiudindo ngati ndimmalawi kulankhula chomwe chikulakwikacho
@PhillspicJere
@PhillspicJere Месяц назад
​@@SamKaposa-i5cInu Kalindo ndichitsiru sakuimira amalawi mumuuze, akakonze Kaye banja lake hule ameneyu munthu okhalira kuthamangisidwa mma rent koma anali MP
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Месяц назад
More fire Booooon kalindoooo
@MonijaKataika
@MonijaKataika Месяц назад
Am loosing trust on the demos aaaa.. zithera kumabanzi iziii panayambira paja...aaaa😢
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on Месяц назад
Tigulenso ma plasma motchipa🤸🤸🤸
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 Месяц назад
More fire 🔥🔥🔥
@MonijaKataika
@MonijaKataika Месяц назад
Poyamba u said the reason is to let the president to step down..now zina aaaaaa
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Kalindo akugwilitsidwa tchito ndi chipani cha DPP osamuvela akulemeletsa family yake
@Vascomw
@Vascomw Месяц назад
Km mene anthu akuvutikira iweyo kumayakhura chochi ulimbe umuthu
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Месяц назад
INUNSO MUSANAMIZE WANTHU APA KALINDO IZI SANAYAMBE LERO NGAKHALE NTHAWI YA DPP ANALI AKUPANGA ZOMWEZI, INU NDAMENE MUSAKUFUNIRA DZIKO ZABWINO
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Месяц назад
KOMATU INU ANZATHU A MALAWI FIRST LIJA NDI KALE MUNAYAMBA KUKAMBA KUTI KWAKWANA KOMA PALIBE CHIKUCHITIKA ENOUGH IS ENOUGH MUNAYAMBA KUYANKHULA NDI KALE KUKONZA MADEMO KUMAPANGA CANCEL MUMATI PA 31 LERO MUKUTI PA 8 CHIKUCHITIKA NCHIYANI
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Месяц назад
Moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯
@JafaliChiwimbi
@JafaliChiwimbi Месяц назад
Boooon kalindo
@DavieChinkwaso
@DavieChinkwaso Месяц назад
Viva Malawi first, the people first. Pliz keep on voicing for us, we indeed suffering and struggling in our own country.
@AtupakisyeMwakasengo
@AtupakisyeMwakasengo Месяц назад
Mademo nde angosintha sintha bwanji,mutitchosa appertite
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz Месяц назад
Viva malawi fist❤
@ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
@ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan Месяц назад
Power💪🤝🙏👍✅
@KasCarter-k8q
@KasCarter-k8q Месяц назад
Umakwana boooon!
@Okalekale
@Okalekale Месяц назад
Kabungwe ak8a alipo akukapatsa ndalama kugawa ntundu wa a Malawi,Bon Kalindo and his gang are sell outs.Who'ever is sponsoring them has an agenda to divide Malawi.Uyu Kalindoyi ndi owononga.
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 Месяц назад
Thanks to Malawi first❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y Месяц назад
Ngati sakuyankha mafutso anu mesa ndiye Mademo koma inu musindatso ma tsiku zinduzi osamatizilowesa mantha anthuwa ine akunyasa ndikufuna a choke bs
@ZebronTembo-u6p
@ZebronTembo-u6p Месяц назад
Congratulations kalindo these senseless people must learn something from stric
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Месяц назад
Nkhani yatikulu yayikulu yoti opanda ma ID salembetsa vote ipa ndipane pagona nkhani idzi ya mitsonkho ngati amalawi titavota mwaufulu MCP ichoke nde kuti kumankhidwa kukwela mitsonkho kuwononga ndalama za boma kuchoka chakwela ndi MCP boma ndimayankho ADZOTSE AMALAWI AKULILA SIKU NDI SIKU KOMA NDI TILOLE KUTI OPANDA MA ID ASAMVOTE MCP YAWINA BASI NOETSE OSUTSA BOMA PALIBE CHANU INU MUDADWE ID NDICHITSANKHO ZIYENDA LIMODZI BWANI AKUDZIWA ANTHU AKUMWELA AMBILI SAKAVOTA CHIFUKWA ALIBE MA ID OSUTSA CHONDE CHONDE LOWELELANI MA ID ASAKUNAMIDZENI KUTI ALEMBA KACHIWILI AYI BIDZA CHIDULE NDIKUCHOTSA NJILA YA MA ID BASI NDE MWAYI OWINA OTSUTSA UKHALAPA KUPANDA APA BASI OSUTSA IWALANI ZOWINA VOTE 2025 ANYETSA MANYI OMWEWA A MCP
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 Месяц назад
Tsono mademo achitika iweyo atabwerako komwe akupita kapena mupanga iye kulibe? Chifukwatu ngt mupanga iye kulibe palibe chomwe mungapindule
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Месяц назад
King d c malawi
@WilliamGuyJonathan
@WilliamGuyJonathan Месяц назад
Pangolin ❤❤
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Akalindo akumwa tea wakaka kwawo a malawi ake oti akuyimilira kalindo ayime uphungu kwawo azizayimilira athu akwawo
@EliasApofu
@EliasApofu Месяц назад
Pasana pako garu iwe
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Kodi iwe chikangawa team eti mmene wayambila kudandaula muja😂😂😂
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh Месяц назад
komatu anthu ananu pabwino mudabasa galu zoona munthu akukumenyelan ufulu kut mukhale pabwino bas mukumunyoza komatu kalindo yu sakupanga zakunyumba kwake koma kwa Malawi ovutika enanu ndinu abale ake achakwera komanso mkudaya nawo aboma koma Pali ena kunjaku akuvutika kwambiri nde enanu uzimu wamulungu unakuchokelan chifukwa chaziphuphu mukudyazo kuma muziwe kut palitsiku limozi muzawona polekera kulimulungu kumwanbaku
@MCLoudZeka
@MCLoudZeka Месяц назад
Booooon Kalindo
@FelixGambiza-fp7tn
@FelixGambiza-fp7tn Месяц назад
Pa 8 ndi zagwesa mvura mpaka pa 15
@juliochiwalo
@juliochiwalo Месяц назад
Dpp sikukhuzidwa nkhani ndi mavuto ochuluka omwe bona chakwera ndi MCP alibe nazo ntchito
@PhillspicJere
@PhillspicJere Месяц назад
Tiyeni tingoswana yamanja akulu
@ernestnyirongo3962
@ernestnyirongo3962 Месяц назад
Zaziiii
@victorbanda9039
@victorbanda9039 Месяц назад
Atonkhàni mukusowa zochitatu mpaka kukapezeka ukuku aaa
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 Месяц назад
Tilikomweko osaopa osafoka
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Komaso issue ya ma ID even central region ambiri alibe ma ID even ine yanga sinatuluke since last year
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Месяц назад
Ndipo tisindike pamenepo pa chiphaso chaunzika ena sakulembesa
@user-nn7ys7fu5u
@user-nn7ys7fu5u Месяц назад
Tiyenazo kachamba😂
@JohnEliyas-j9j
@JohnEliyas-j9j Месяц назад
Our country has gone
@user-kr1tf2tu7s
@user-kr1tf2tu7s Месяц назад
Zika zake ziti zakumudzi kwanu mwauponda, kwanukomweko
@user-ce9yj9ln4z
@user-ce9yj9ln4z Месяц назад
Pangan zomwedzo bas andikwana kwabas anthu amenewa
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Lilongwe ndiwakulu moti simumadziwa zimenezo mukulimbana ndi Lilongwe bwanji
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Lilongwe wake up kalindo akudana ndi Lilongwe and central region
@user-ri5qm8qo7g
@user-ri5qm8qo7g Месяц назад
Atingulitsa
@Standwell78
@Standwell78 Месяц назад
Apule 😂😂
@OweniMolokooweni
@OweniMolokooweni Месяц назад
😂😂😂😂😂❤❤❤ 31 mandemo
@DavidAugustine-y5v
@DavidAugustine-y5v Месяц назад
Abon kalindo timawanyadila kwambili
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Kodi ku ma demoko nkazi wa kalindo ndi ana ake akakhalako mesa nawoso nda Malawi asamatitenge zitsilu ife anyani amenewa atengeko akunyumba kwake akayende
@HarlodMbalati
@HarlodMbalati Месяц назад
The DC bon kalindo mwana oooo🔥
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Месяц назад
Ulibe nzeru mboli yako wakongeresi
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Iwe watumidwa ndikama jekete😂😂
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Месяц назад
ACHOKA PA 31 JULY PAJA AFIKA PA 8 AUGUST
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Usamale ndiwe ife chimanga tilandila
@TimothyDamiano
@TimothyDamiano Месяц назад
Tiyeni konko,osaiwala kunyamula ma bucket a madzi paja kumakhala tear gas
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 Месяц назад
Kkkkk mposooo poti a police Ake manyakatu amapanga NGT zawo zili pa bwino
@JosephKachaje-mn6xj
@JosephKachaje-mn6xj Месяц назад
It is a time for the Kalindo'S activity to fall down
@alnordtembo8930
@alnordtembo8930 Месяц назад
The DC
@dysontasowana7429
@dysontasowana7429 Месяц назад
Wachepa iwe
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Месяц назад
Kuchema
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Месяц назад
Mwasiyaso paja mmati mupanga mawa mademo?
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r Месяц назад
The DC ndi Mfumu
@user-ri5qm8qo7g
@user-ri5qm8qo7g Месяц назад
Bola asakupatseni kenakake
@AngolanChinga
@AngolanChinga Месяц назад
Yes mr bon kalindo we are in democracy now but we stay like we are not in democracy what is that chakwela machende ake with zikhali ng'oma and all of there
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Месяц назад
Ndipo kwambiri tu
@HusseinRashid-m4l
@HusseinRashid-m4l Месяц назад
2
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Kalindo akufuna kugawanitsa a Malawi
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Amthu anagawikana after ngozi yakuchikangawa ija man
@Okalekale
@Okalekale Месяц назад
​@@SamKaposa-i5cNgozi inawagawa bwanji?,mwina atati Chakwera anapha anthu aja,pali umboni yah pangakhale ponveka pang'ono komanso zingatanthauze kuti pa Malawi umbuli ukadalipo. Peter ndi amene amapanga ndale zogawa aMalawi and kabungwe aka ndikuonamo dzanja lake.Anakapanga ndicholinga chofuna kulepheretsa Tonse Alliance chifukwa zinamuwawa kuti umbava wake unaululika.Ndi mdala osadziwa ndale or kuyendetsa dziko,kwake ndi kuononga,maphunziro sanamuchotse umbuli.
@Vascomw
@Vascomw Месяц назад
Kwvta
@jomochirwa
@jomochirwa Месяц назад
Mademo adatha mphavu palibeso boma limene lidzawopaso mademo.mademo adapita ndi mtambo kazikalimani chaje.
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq Месяц назад
Mukunama kwambiri ANKOLO
@dysontasowana7429
@dysontasowana7429 Месяц назад
Can government respond to you munthu osuta chamba ndi mkwidzi? Inutu mukadakhala ngati munali nduna sibwezi mukulankhula chamba chanucho
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Месяц назад
Akulu vomerezani zinthu zinasokonekera,Kalindo sakulakwitsa vuto lili ndi iweyo
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh Месяц назад
Awawa ndi abale achakwera komanso ndiwomwewo azibale awo akuba ndalama za Boma chifukwa chake akupanga makan koma mziwona musatitenge opusa amalawife iya
@Okalekale
@Okalekale Месяц назад
Anasokoneza zinthu ndi ndani ku Malawi?,tonse Alliance kapena MCP zalowa liti m'boma?,Chakwera walowa liti m'boma?. Mbava zimene zinaononga dziko inu simukuzidziwa?,okay kuyambira 1994 ndi ndani amene wakhala akulamulira?,ndi zipani ziti zimene zakhala zikulamulira?. Bakili UDF,Peter DPP,Joyce PP,izi ndiye mbava ndi zipani zimene zaononga chuma cha Malawi,Kamuzu anasiya chuma chikuyenda bwino. Ngati mukungonena zinthu chifukwa choti ndi inu akumwera ndinu nzika yosafunila dziko lanu zabwino,ndalenza umbuli.Chilungamo mukuchithawa dala pamene mukudziwa anthu ndi zipani zimene zaononga dziko.Kuyambira 94 ndi Bingu yekha amene anapangakonzooneka ena onse ndi useless okha-okha maka maka Joyce ndi uyu akumuti adad a Lomweyi.Peter ndiye muntu oyipa kwambiri chifukwa ndi osadziwa ndale,iye amangodalira kugawa anthu.nfundo alibe anangokhala professor.
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Kalindo akufuna unduna DPP ikazalowa boma chonde chonde anali azanga musavele kalindo
@PhillspicJere
@PhillspicJere Месяц назад
Chosani Malawi yo muyikepo muhlakho first, dzina la malawi osamngopasapo ndizisiru zomwe,
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Mademo pangani koma boma iziyendabe chomwecho ngati a opposition sakulakhula iweyo ndiye boma lingakuvere pitani pàsewupo tikumana komweko
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 Месяц назад
Kawawa kalindo osaopa osatopa
@MarkinaJohn
@MarkinaJohn Месяц назад
Tili ready PA 8ogasiti
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Awa kalindo akudya ndalama za DPP mutuluka nonkha kumwelako
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Nanu inu sizachigaozo malawi first kaya iwe mngwakuti mavuto mngatonse
@YasinAdam-pn4bh
@YasinAdam-pn4bh Месяц назад
God bless you Bon Kalindo
Далее
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Просмотров 87 тыс.
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Просмотров 9 тыс.
EXCLUSIVE WITH KONDWANI NANKHUMWA
36:41
Просмотров 24 тыс.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 116 тыс.