Тёмный
No video :(

BREAKING NEWS CHINYENGO CHA MEC CHAULURIDWA NDIPO A DPP NDI UDF ANAVUTA KU MANGOCHI 

Malawi Trends TV
Подписаться 41 тыс.
Просмотров 20 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

6 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 111   
@AcklenIshmaelkamwana
@AcklenIshmaelkamwana Месяц назад
Problem is a opposition are sleeping too much when you gonna wake up you people of opposition
@JohnAsendi
@JohnAsendi Месяц назад
Mangochi osalola tili kumbuyo kwanu
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f Месяц назад
Kugwira munthu NDI mavoti osapeleka kwa a police tibulani munthu yo kuti a MEC atengelepo phunzuro
@mathewsnachuma8086
@mathewsnachuma8086 Месяц назад
Mwana WA John Tembo sangagwile ntchito imenei achoke
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Ndipo kwambili athu oipa mulungu awaone athu awa ayi sizona ayi kupanika dziko lathu lomwe mmm
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад
Achosedwe basi
@VictoriaWilly
@VictoriaWilly Месяц назад
Azipani zosusa agona tulo zedi..... Sakutipasa chilimbikitso ayi aaaah
@thomasmalenga8194
@thomasmalenga8194 Месяц назад
Nanenzo ndimadabwa kuti Kumangochi kuwina anyani amenewa
@user-mk9ro8fd4u
@user-mk9ro8fd4u Месяц назад
You are very right bro
@user-dh1oi8mb4v
@user-dh1oi8mb4v Месяц назад
Ayambileso ku vota zachamba ife ayi
@ElizabethAlick-e6b
@ElizabethAlick-e6b Месяц назад
Mcp or mwana sangayivotere ndiyokumpha
@EdwinMsengo
@EdwinMsengo Месяц назад
Inu mwayiwala a UDF anapha Matafale, ndipo DPP anapha Issa Njaunju mwaila zimenezi? Agalu inu
@stevietungama9775
@stevietungama9775 Месяц назад
Ine kudabwa mpaka mcp ku mangochi
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Месяц назад
Palowa chinyengo kwambir mesa amayenda ndi usiku kumagawa ndalama tazimva kale zulo usiku nthawi imene ndimachokela ku BT ndinapita kwa m'baluku anyamata amayakhula okha 😂😂😂😂
@user-ws9sy7pp3w
@user-ws9sy7pp3w Месяц назад
Sizingatheke kwathu MCP kuwina trust me guys
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
@@user-ws9sy7pp3w Zatheka ukuwona kkkkk. Madala muli mu denial ndipo mufa ndi BP. MCP is bigger than you think, osati ngati zipani zanu za ma family.
@user-ws9sy7pp3w
@user-ws9sy7pp3w Месяц назад
@@tasmania527 tikumana Ku u president
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
@@user-ws9sy7pp3w Muzatizimulidwaso mwa easy mark my words. Mumadalira ma district ochepa, ife ndi Malawi yonse. Chisankho ndi game ya ma biggie. Inu vuto lanu mumajaira pa social media koma pa ground nada!
@whatsonbanda4277
@whatsonbanda4277 Месяц назад
Mulila adpp msanati utukwana kumeneko mngawine muona 2025 chakwera landslide.
@whatsonbanda4277
@whatsonbanda4277 Месяц назад
Malume zimatheka.mnthawi ya bingu dpp inawina ndi mavoti ambiri mcigawo Cha pakati izi zimachitika ngati chipani muchita zibwana anthu amakuthawani apa mangochi anthu ambiri aithawa.
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
Basi avoteso kachiwiri
@Yaqub-nk4pu
@Yaqub-nk4pu Месяц назад
Opposition dovu kwambiri kaya ndikufatsa kaya ndi umbuli
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu Месяц назад
Kumpeza munthu ndi ma vote aziphedwa osapita naye ku police.
@AngelaGraysham
@AngelaGraysham Месяц назад
Ndipo straight abela
@annembepula
@annembepula Месяц назад
Kubwele MDF kumeneko avotenso
@user-wb9ji3oe5o
@user-wb9ji3oe5o Месяц назад
Kodi aNamslomba mulikutiko, nanga inu a Tupele mulikuti? Mukuyembekezera 2025 kuti anthu azakuvotereni koma muli phe osachititsako msonkhano ngakhale wa ma AREA kuti anthu adziwr kuti mulipo.
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Месяц назад
Ndipo zosatheka kwanthu MCP kuwina ayambilerenso
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Месяц назад
MCP kummwera siingapateyi kalikonse
@annembepula
@annembepula Месяц назад
MEC imeneyi 2025 ayi isayendetse
@user-un4pm4yt5i
@user-un4pm4yt5i Месяц назад
Ayambapotu chidyengotu
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj Месяц назад
Kufasa sikumasiyana ndi kupusa...
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Ndipo 2025 opposition mudzaliranso chimodzimodzi tulo 2 much khangati anthu akukukakamuzani agalu inu zoti chiyembekezo cha amalawi chili pa inu mulibe nazo ntchito mxxxxxx
@ShukuSh-vi1hk
@ShukuSh-vi1hk Месяц назад
Sizingatheke zimenezo pamtumbo pawo okuba tivotaso
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke Месяц назад
Ine kudabwa mangochi mcp
@FrancisMazamba
@FrancisMazamba Месяц назад
Avoteso mcp ayi pano
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Месяц назад
Ine kudabwa kuti kumangochi zatheka bwanji kuvotera mcp chipani cokupha
@OnexPellan
@OnexPellan Месяц назад
Koma abale zimene zikuchitika dziko lathu zovuta kuzivetsa koma tiyeni abale azanga tilimbike kupephera kuti boma limeneli mcp isaloweso boma
@MarcosDjussa
@MarcosDjussa Месяц назад
Aopposition changamukan mulila ndi nthu
@annembepula
@annembepula Месяц назад
Mzimu wakwiya palibe chimsisi
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma Месяц назад
Munya 2025 agalu dpp
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 Месяц назад
Awotchepo MCP singa wine Ndipo Wanthu asalore AMEC ndizitsiru agulidwa,Amenewo nga kupha apha shaniru Ndi Chilima, pamodzi ndi Wanthu wena.Chakwera chirombo chotuluka munyanja Mavudzi amache,muwa menye AMEC wo votani kawiri Zitsiru zimenezo musazi siye Zi achewa zokupha Zo kula mulira Ku meneko
@EdwinMsengo
@EdwinMsengo Месяц назад
Kodi chisankho amaberaso?
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
It's only ma cousin a zipani(UDF and DPP) amene akuliralira. Chipani cha Nankhumwa chanena kuti chisankho chinayenda bwino. This reminds me of Enock Chihana who was also in denial chipani cha Aford chitaluza ku karonga.
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Месяц назад
Pempho langa ndiloti a George chaponda please wake up muchite chotheka MEC yonse ichoke ngati sichoka chaka chamawa anthu azafa ndi khawa
@user-lk3ki9hi3k
@user-lk3ki9hi3k Месяц назад
Our opposition is foolish..... Anthu kuyesela kukupasani support inu muli ziiiii..... Kufuna kutukwana mtundu wanga wachiyao
@douglaskamanga7679
@douglaskamanga7679 Месяц назад
Munanena kuti kunavita ku Mangochi. Zatha basi?
@THOCCOChimbali
@THOCCOChimbali Месяц назад
Palibe angavotele mcp
@franklameck5700
@franklameck5700 Месяц назад
Ife ndi a ku lilongwe koma mcp ikutinyasa ndihu pa chilungamo chake
@user-fq4kv8dj4t
@user-fq4kv8dj4t Месяц назад
Ndipo ine kudabwatu chikangawa aziwina kwathu komwe za manyi basi chikangawa kwathu ku mmwela malo ako kulibe
@Doreen-vw9ws
@Doreen-vw9ws Месяц назад
Vuto anthu zipani zosusa kwathu kuno amafuna aziyenda moyela samafuna kumatengapo gawo ngatitu sizikuwapweteka akapitiliza aziwe kuti akupeleka mpata kwa zigawenga za chipani Cha mcp tasukusulani chisanzo ku Kenya gwilani mbendela yachilungamo
@user-wg8tp8in1v
@user-wg8tp8in1v Месяц назад
Amene akuvutawo ndi aja samavota aja amasapotalela pa kamwa ndi muma social media basi
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Месяц назад
MEC yaulendo uno ibweletsa nkhondo malawi muno ndithu!!!!
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Месяц назад
Born Kalindo akamayankhura a oppositions muzinva!! Apa ndiye mwaonatu muzibeledwa choncho izi muziyembekezerenso 2025 chibwana chakula ku malawi kuno wa pa mpando wa MEC uyuyu atule pansi udindo.
@WisdomMaseko-fi5sv
@WisdomMaseko-fi5sv Месяц назад
Mmmmm mwambo oyamba kuponya vote mumaudziwa koma? Umayamba ndi mbali zonse, Mabungwe ndi zipani zonse.
@abdullahikhazum4046
@abdullahikhazum4046 Месяц назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣👍👍👍👍
@OwenMajoni-qv3eg
@OwenMajoni-qv3eg Месяц назад
Pali umboni obelawo?
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Chakwera anasankha dala mwana wa John tembo ndicholinga kuti adzabere zisankho koma nde bola kungomchotsatu ameneyu satithandiza aaaa
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo Месяц назад
Abera amenewo 😂😂😂😂😂😂
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Mec muyaluka simukukwanitsa ntchito yanu ziphuphu ndi zomwe zakula koma nde Mcp muli pa chintchitotu mpakana kukasaka anthu ku midzi ina
@JuuuKomba
@JuuuKomba Месяц назад
😂😂😂ayawo ndi Amanyi ndinkaatenga mashasha apa ndaziwa usilu wawo
@omarajibu860
@omarajibu860 Месяц назад
Ndipo kwathu kuno zimenezi sizingawine
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Mwachita bwino mwabwera amcp mwina agalu otsutsawa achangamuke atutumuke 2025 isanafike
@AbubakarTengani
@AbubakarTengani Месяц назад
Mangochi ndi ziko pa lonkha zoona zanke mcp palipe komwe angawine
@EllinaBitto
@EllinaBitto Месяц назад
Opposition ingokhalira eee ine akuti akundisaka,eee ndimangeni,eeee tikukuonani zomwe mukuchita eeeee koma kuti adzuke pomwe akhalapo amta😭😭😭😭😭😭 1:57
@EllinaBitto
@EllinaBitto Месяц назад
Komatu Bon akumanena abale😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@DevisonHala
@DevisonHala Месяц назад
❤❤❤❤
@frazereline
@frazereline Месяц назад
Sitisainila mpaka aunike Kaye Madando 😳
@Raph-kayRaph-kay-g5v
@Raph-kayRaph-kay-g5v Месяц назад
Chakwera azawinanso opposition 2much sleeping kufatsa sikwabwino tiluza chilima chifukwa chakufatsa
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Ndipo zoona
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Wapampando wa mec akuyenera kuchotsedwa satithandiza chikuwa akuuwoneka kuti ndi wa mcp
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Месяц назад
Ndiwa mcp kumene achoke basie ngati wayamba iziz panopa nanga 2025 kuzakhala zowona
@HenryChapananga
@HenryChapananga Месяц назад
Kanyimboko mwandikumbutsa malemu atoti manje rip manje
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r Месяц назад
Mec achoke ayapisa vipolewe
@SueWahna
@SueWahna Месяц назад
Zimayi anapasidwa udindo uja sakuthandizan atah ngat kwavuta makhansala kulibwanji ma akulu akuluwa
@AlliSaiti
@AlliSaiti Месяц назад
Zaboza izi
@MonicaSembo
@MonicaSembo Месяц назад
Kodi school unasila mkalasi lanji ? Before I argue
@AlliSaiti
@AlliSaiti Месяц назад
@@MonicaSembo 🤣🤣🤣🤣 sono zikugwirizana bwanji?
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
Chakuvutani ndi tsankho anthu a DPP ndi UDF. Kwa inuyo mumangoganiza kuti anthu akwanu sangavotere chipani cha MCP. Zi ntchito za pa ground ndi zomwe anthu akufuna osati kuwuwawuwa kwanu ngati agalu. You think you're invincible in the south? Wait for 2025 ndipo muzalira mokuwa kwambiri.
@BrianSanuwedi
@BrianSanuwedi Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Chakwera akudziwa kuti palibepo chake
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Inenso ndimadabwatu kuti Mcp singawine ku mangochi
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Месяц назад
Athu kumalawi mwadekha kwambili,ndichifukwa chak
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Месяц назад
DPP ndi Madala a kugona kwambiri
@BaulenChipala
@BaulenChipala Месяц назад
Kodi bas anthu enanu mmaganiza bwanji ? Mufuna zabwino zokhaxokha zikhare zanu? Akulu anthu amavotera munthu osat chipani kapena amen wawinayo niwaku Lilongwe pakut zikuonetsa kit ndinu wasankho ndie mwakhaulatu
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Месяц назад
Mcp woyeee kuwina ndi phavu kwambiri 2025 Mcp itengaso boma
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo Месяц назад
Km zaka zino eeeee kumalawi kwavuta
@captainmdima1102
@captainmdima1102 Месяц назад
Mcp boma!!
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Месяц назад
Olila samulesa pakamwa
@MustapherLino
@MustapherLino Месяц назад
😂😂😂😂😂 MCP woyeeeee sanabere awina basi Mesa ayawo ndi opusa
@thomasmalenga8194
@thomasmalenga8194 Месяц назад
Iwe matchende akho
@mavutomwale6638
@mavutomwale6638 Месяц назад
Koma kumeneko 😂😂😂😂
@KhalideNerve-mu1eq
@KhalideNerve-mu1eq Месяц назад
Ndipo live abela inu akumaaposition mwaonatu mukusiza kwambili
@MosesNdebele-kc2cp
@MosesNdebele-kc2cp Месяц назад
Chakwela ngati angawinenso bansi kumalawi kukhala moto
@MahometAli-e8w
@MahometAli-e8w Месяц назад
Kungowinanso mco yo ine ndidzasamuka ku malawiko ka dzikoko kakangono kma zochitika ngati sasafrica
@GracePendame
@GracePendame Месяц назад
Achoke atikwana
@KhalideNerve-mu1eq
@KhalideNerve-mu1eq Месяц назад
😮😮😮😮😮😮
@charlesbanda7594
@charlesbanda7594 Месяц назад
Abela
@Kasawalah
@Kasawalah Месяц назад
Ndimadabwa ine kubela Basi abeladi
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
Umadabwa chani mwaluza basi. Kuzolowera tsankho inu.
@user-wg8tp8in1v
@user-wg8tp8in1v Месяц назад
Aulusatu pano
@John-to8gl
@John-to8gl Месяц назад
Tikavoteso basi
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
Kuvotaso chani ma bad losers inu? Kumwera nkwa aliyense.
@KondwaniMamveka
@KondwaniMamveka Месяц назад
Zovuta gyz
@marryphili5419
@marryphili5419 Месяц назад
Ndiye kuti MCP abera anthu avoteso
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
Matama anthu a DPP, ati kumazitenga madolo, za zii!
@AbubakarTengani
@AbubakarTengani Месяц назад
Panyopako
@tasmania527
@tasmania527 Месяц назад
@@AbubakarTengani Ukhalira yomweyo yotukwana, savage iwe. Ndipo uzalira kwambiri chuwii! chuwii! chaka cha mawa kkkkkkkk.
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Месяц назад
Atibera volume Cha imeneyi tiyitche kut volume 11 chifukwa ankayamba kale
@jomochirwa
@jomochirwa Месяц назад
Ndiye mukulila chau khansala ndiye chaka cha mawa mulilatu zenizeni mudzalila dikilani.
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Ndipo zakhala bwino
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Mwina adzuke
Далее
BUS REZVIPOKO (EPISODE 2)
16:20
Просмотров 58 тыс.
Bike Challenge
00:20
Просмотров 12 млн
KUYANKHULA KWA JOYCE BANDA
21:25
Просмотров 15 тыс.
NDALOTA MALOTO OOPSA KWAMBIRI
7:25
Просмотров 674
BON KALINDO WABWERANSO NDIIZI TAMVERANI 05/09/2024
16:42
ZOVUTA ZEDI  || PART 28
11:40
Просмотров 468