Тёмный
No video :(

BREAKING NEWS NAMIYANGO - MUNTHU WAPEZEKA ATAFA MNYUMBA KU NAMIYANGO. 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 66 тыс.
50% 1

BREAKING NEWS NAMIYANGO - MUNTHU WAPEZEKA ATAFA MNYUMBA KU NAMIYANGO.

Опубликовано:

 

23 апр 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 76   
@patriciakanjanga1284
@patriciakanjanga1284 3 месяца назад
anthu akachite lenti pakhomo panu ndinu makolo aanthuwo chonde mukaona kuti khomo silikutsegulidwa kwa masiku angapo chonde muzipita nkukaona chachitika ndi chani mpaka masiku angapo landlorad osadziwapo kanthu mzimu wao uuse mutendere
@ThembiweKapukayenda
@ThembiweKapukayenda Месяц назад
Eish too bad😢😢
@collinstrevor
@collinstrevor 3 месяца назад
Zimu wake sukhala chete wapanga zimenezi adziwika
@user-tg3ju1mw9t
@user-tg3ju1mw9t 3 месяца назад
Zomvetsa chisoni 😭😭😭😭😭😭 komanso titengelepo phunziro chifukwa tima wanzako ndi sidya lina, Rest in peace mama
@WestonMuyimwa
@WestonMuyimwa 2 месяца назад
Rip
@user-kw1wo2cr3p
@user-kw1wo2cr3p 3 месяца назад
Malandlod muzikhala serious 4d
@hethermvula4156
@hethermvula4156 3 месяца назад
Landrold walakwa chani?
@stephenschipolo5296
@stephenschipolo5296 2 месяца назад
Umatha Harry. Keep it up! Well covered and narrated
@nkhalangomultimedia
@nkhalangomultimedia 2 месяца назад
Thank you, I will
@AngungaThatcherNgoma
@AngungaThatcherNgoma 3 месяца назад
Good Narrater
@user-us9et2fq3k
@user-us9et2fq3k 2 месяца назад
Following
@mphatsolupiabanda6910
@mphatsolupiabanda6910 3 месяца назад
We love you Director wa mkhalango multimedia
@user-oe8ts5ez6g
@user-oe8ts5ez6g 3 месяца назад
Mmmm Sad😭
@sibokawana2358
@sibokawana2358 3 месяца назад
So sad😢😢
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 3 месяца назад
Eish 😭😭😭 Kulakwa
@endphiri3933
@endphiri3933 Месяц назад
Inna lilah wa inalahijuna
@khadjahmustafa8273
@khadjahmustafa8273 3 месяца назад
My home land Namiyango
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 месяца назад
Very sad 😢
@ChifundoMwale-yp1iz
@ChifundoMwale-yp1iz 3 месяца назад
😢😢😢 shem
@user-lq9qi5ru4h
@user-lq9qi5ru4h 3 месяца назад
Eishii 😭😭😭😭
@StanleyMatewere
@StanleyMatewere Месяц назад
Eish....too sad
@EmilyPade
@EmilyPade 3 месяца назад
Sad news
@CharlesMadulira-px8yq
@CharlesMadulira-px8yq 3 месяца назад
Mmmm very sad anthu tikulimba mtima moopsa
@bmbboymstyles5894
@bmbboymstyles5894 2 месяца назад
Eishhhh koma zinthu zake😢😥😥
@zaithwachiwaya8885
@zaithwachiwaya8885 3 месяца назад
😭
@AnitaChakwana
@AnitaChakwana Месяц назад
Ine mmoyo uno ndaphuzila zambili muthu ndimamuwopa ndipo sindidzakhulupilira muthu ndachita matha iiii😭😭😭😭
@Zamwano
@Zamwano 3 месяца назад
Moyo ophana achinyama chepesani sibwino kuchosa moyo wamuzako ngati mwalakwilana kambilanani mwaufuna basi Chatha Chatha mukapeza wina,,,, landlord alibe vuto pamenepo sankaziwa chilichonse oipa ndiwakuphayo Ambuye Mulungu amukanthe komwe aliko Galu kwabasi
@PempheroPaliani-ke3ez
@PempheroPaliani-ke3ez Месяц назад
So sad
@user-nu3kk8xr4s
@user-nu3kk8xr4s 3 месяца назад
May her soul rest in peace
@phylessmphanda3251
@phylessmphanda3251 24 дня назад
RIP 🙏
@Takondwac
@Takondwac Месяц назад
😢😢😢😢😢😢
@gideonnyirongo2202
@gideonnyirongo2202 Месяц назад
Manase
@user-wo9hi8te5f
@user-wo9hi8te5f 3 месяца назад
Ina Lillah waina ilaih rajuhunah 😢😢😢
@user-ul5wx6kb4f
@user-ul5wx6kb4f 3 месяца назад
😭😭zovesa chisoni
@user-yl3bq4pn7u
@user-yl3bq4pn7u 3 месяца назад
This is too bad
@mercymagola
@mercymagola 2 месяца назад
😭😭😭😭😭😭
@egreymkumba-tj5ji
@egreymkumba-tj5ji 2 месяца назад
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@RichardMwamadi
@RichardMwamadi Месяц назад
Zomvesa chison koma wapanga zimenezoyo mulungu amuwone
@NdazionaKumcheza
@NdazionaKumcheza Месяц назад
Landlord ogona osachita monitor wa lent wako
@MosesChileka
@MosesChileka Месяц назад
Dzimuwamunthu, ndioopya apezeka
@issadinala125
@issadinala125 3 месяца назад
Eeeee zosaendatu iz 😢
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 3 месяца назад
Tiuzeni malonda omwe amachita nsungwanayo osabisa tangonenani kuti anali hule bwanji???
@janemanyamba7201
@janemanyamba7201 3 месяца назад
Iwe chisilu eti
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
My Malawi 😭😭😭😭😭
@janemanyamba7201
@janemanyamba7201 3 месяца назад
Kuyeza kwakanika?
@AyandaTshontini
@AyandaTshontini 3 месяца назад
Akapezeka munthuyo straight wakumaula munthu woipa kwambiri khalidwe laukape
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
Nayenso aphedwe
@Yusufu-ul5ec
@Yusufu-ul5ec 2 месяца назад
Eish zosayenda mmmmm zosakhala bwino Mzimu wake uuse mu mtendere
@amoschilangiza
@amoschilangiza 2 месяца назад
Zachitika liti?
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
Koma azimunafe eeeeeeeeeee zovuta zedi mmmm😢😢😢😢😢😢
@user-fu7kx8is6q
@user-fu7kx8is6q 2 месяца назад
Zomvetsa chisoni 😭😭😭😭
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 3 месяца назад
Zomvetsa chisoni kwambiri😢
@nimrodkapingatheu5475
@nimrodkapingatheu5475 2 месяца назад
Eni ake nyumbawa nganzeru... Ndi munthu wachikuliledi
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t 3 месяца назад
Khalidwe lophanali silingasinthe khalidweli anthu akuchicha kuwonela chifukwa pano mulandu wakupha ulibe ntchito khalidweli labwela ndianthu andale able athu achialubino anatha milanduyake kukulibeko mpaka pano lelo ena ndiaja anapha witika nanga mayi wakulizevu banki uja Malawi tiyeni tsiku Lina tizikhalangati osamva tiyambe tokha kulañga anthu opanga chipongwe azawo tikawagwila chifukwa kupolisi kulibe chimene chiliko kukhoti nakonso kwangosala mapoto obowoka okha okha
@janemanyamba7201
@janemanyamba7201 3 месяца назад
Alandlod mumakaniza kii kwa m,bale wake????
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
Azimunawo anagona nawowo anali angati??
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 3 месяца назад
Mkulakwa kuchotsa Moyo wanzako
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 3 месяца назад
It's too bad eish kma zophanazi Eeeeee
@DuncanMataka
@DuncanMataka 2 месяца назад
Ambuye amulankhule wapangazoterezi mwazisisi amuziwe yesu.
@user-lh3kk3qu2o
@user-lh3kk3qu2o 3 месяца назад
Khalango maltimadia ndi dilu
@AminSoko
@AminSoko Месяц назад
Zovutatu malawi mmmm
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
Malawi mmmmmmmmmmmmm
@chifundoalfred14
@chifundoalfred14 2 месяца назад
Zovuta kwambili
@TeresaSaudeNampalala
@TeresaSaudeNampalala 2 месяца назад
Eee zomvetsa chison
@Lufeo-kx8kf
@Lufeo-kx8kf 2 месяца назад
Sizinthu zabwin koma 11:19
@ChrispinChikagwa
@ChrispinChikagwa 3 месяца назад
Zosakhala bwino
@EmmanuelManiya-dz5ry
@EmmanuelManiya-dz5ry Месяц назад
Zoopsa kwabasi
@BudaEarth
@BudaEarth 26 дней назад
Zoopsa
@Cynthia-gv9gh
@Cynthia-gv9gh 2 месяца назад
Imfa yomvesa chison pamaso ngat akukonda mtima muli nkhondo,rest well mama😭😭💔
@EnockMtengula
@EnockMtengula 3 месяца назад
Eeeeee km
@CharlesMulikhiwa
@CharlesMulikhiwa 2 месяца назад
Akapezeks waphayo aotchedwe chifukwa akapita ku polisi kungopereka 3000 basi amutulutsa then aziphabe
@patricktembo1160
@patricktembo1160 2 месяца назад
Zomvesa chison kwambili 😢😢😢
@user-kp1wr4ql5d
@user-kp1wr4ql5d 3 месяца назад
Zosakhala bwino
@patricktembo1160
@patricktembo1160 2 месяца назад
Zomvesa chison kwambili 😢😢😢
Далее
NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA
17:06
Просмотров 5 тыс.
Symmetrical face⁉️🤔 #beauty
00:15
Просмотров 4,3 млн
Sky News Breakfast with Wilfred Frost | 31 July 2024
2:56:00
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 102
29:34
Просмотров 20 тыс.