Тёмный
No video :(

NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 5 тыс.
50% 1

Chonde mvetserani mwachidwi nkhaniyi ndi kuwathandiza kuti chilungamo chichitike - NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA

Опубликовано:

 

26 май 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 39   
@user-qk1mp9qc5r
@user-qk1mp9qc5r 2 месяца назад
Mmmm shame 😢😢😢😢😢zovesa chisoni abale Mzimu wawo uwuse mu mtendele sure munthu anamfa imfa yowawa
@ShadreckMwija
@ShadreckMwija Месяц назад
Ipakaso okupha kumachalenja ondandaula Malawi wakaka ndiuchi unja akupita kuti wasanduka wamangazi ndi misuzi? Zikomo Mulungu ndiamene akuziwa akuthandizani akumbanja sizinaenereke kutero ause mutndere chimwene waifeyo pooezaso amapita kukapanga zachalichi muyembekezere kuona zachilendo kwaoseo amen
@OlivaKambelembele
@OlivaKambelembele 2 месяца назад
Eish chilungamo chikuyenera chiyende ngati madzi apa amqbungwe pls athandizeni nkhani yokhuza iyi😢😢
@JAMESSAIZI
@JAMESSAIZI Месяц назад
Ndipo ndizooba 😢😢
@PangananiChikaoneka
@PangananiChikaoneka 2 месяца назад
Limbani mtima chemwali. Mlandu sumaora. Mudzasuma boma likadzasintha. Yembekezerani pa Yeheva basi. Pepani 😢😢😢
@LucyKasengwa
@LucyKasengwa 2 месяца назад
Very sad 😭😭
@GladysChiwanga-vd9zp
@GladysChiwanga-vd9zp 2 месяца назад
Mulungu oziwa chilulungamo akukhuzeni ndi dzanja lake pemphero langa ndi kuthekera kwachofuna chanu (justice)
@chrispahuwa
@chrispahuwa 2 месяца назад
Mmm yandikhuza komanso kundililitsa Mulungu akukimbitseni mitima yanu nonse akubanja
@user-jk4ew3pm6l
@user-jk4ew3pm6l 2 месяца назад
Achakwela mungotipha amalawi tonse mutchuke ndinu,,, pepani akubanja.
@joelkatembe9198
@joelkatembe9198 2 месяца назад
ine ndingakaibwenze live imeneyo ndipo eish angamve kunyuunguunya
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 2 месяца назад
Koma dziko iliri limakonderad anthu alemera komanso andale omwe akulamula pa nthaw imeneyoyo,,kumupha munthu opanda chifukwa aaah
@thokochilimba-bs2mm
@thokochilimba-bs2mm 13 дней назад
Koma dziko ili ndagoma nalo😢😢
@AlinafeZimba-d6h
@AlinafeZimba-d6h 7 дней назад
Zomvetsa chisoni
@ThokoKamvuma
@ThokoKamvuma Месяц назад
Zomvesa, chisoni pepani ndithu.
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 14 дней назад
Pepanpepan akubanja
@EstherKanjanga
@EstherKanjanga Месяц назад
Pepani ambuye alowelele
@starlonJames-qr4xl
@starlonJames-qr4xl 2 месяца назад
Aeee zosankhala bwino hey km dziko kd likupitakuti😭😭😭 pepani pepani akubanja
@user-dc3bo2ey8t
@user-dc3bo2ey8t 2 месяца назад
Zovetsa chisoni ndithu
@EsnartMateuchi-bz7bo
@EsnartMateuchi-bz7bo Месяц назад
Rest in peace
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 2 месяца назад
This is very bad, I hope people in authority can help this family. Mr Mgombe why?
@hanneckkadyampaken2197
@hanneckkadyampaken2197 2 месяца назад
Too bad
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 2 месяца назад
Ineyo vuto ndi mm'ang'anja ingotumani munthu akatape phazi basi tilange
@robenmatchilinga604
@robenmatchilinga604 2 месяца назад
Ambuye akhururukre pepan akubanja
@user-kv1ik8tj6k
@user-kv1ik8tj6k 2 месяца назад
Sizoona ulamulilo uwuwu siulibwinoayi guys chakwela atimaliza guys tiyenitimpephelelechakwela amwalile guys atiphatuuyu
@user-lj3dx7wz9t
@user-lj3dx7wz9t 2 месяца назад
Anthufe koma chikondi chimatisowa kwambiri ambuye yekha ndiamene akuziwa koma
@nadiahPhiri
@nadiahPhiri 2 месяца назад
Anthu kuyipa kuposa Satan 😭
@LM-gz5pk
@LM-gz5pk 2 месяца назад
Ku police kunalowa chinyengo pano... Kumwamba kuli Mulungu onse apanga izi komaso akubisa chilungamo Mulungu akukatheni
@angellahmuwowo9413
@angellahmuwowo9413 2 месяца назад
Pepani akubanja very sad
@JamesPaul-rg6tj
@JamesPaul-rg6tj 2 месяца назад
Farawo kkkkk mbambanfe
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 2 месяца назад
Kodi mulibe anyamata oti atha kungobwezera okha zachambazi inuyo musadandauleyi ingobwezerani basi
@BentryThupa
@BentryThupa Месяц назад
Pepani
@KavisikaMaria
@KavisikaMaria 2 месяца назад
Sorry
@OmarSalim-jo4ne
@OmarSalim-jo4ne Месяц назад
Chipani cha mcp
@OliverNkhoma
@OliverNkhoma 2 месяца назад
Uyuyu kungomuphanso pogwiritsa ntchito gulu
@ChrispinChikagwa
@ChrispinChikagwa 2 месяца назад
Mulungu amabweretsa zinthu poyera ndipo choonadi chidziwika komanso munthu umakolora chomwe wabzala. Mu mtima mwanga mukuwawa ndipo mulungu chitani mukuweruza kwanu
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani Месяц назад
Pepani Mulungu atithangatire bas
@JAMESSAIZI
@JAMESSAIZI Месяц назад
Zikomo
@elias.m.chunga
@elias.m.chunga 2 месяца назад
Very bad
@ThokoKamvuma
@ThokoKamvuma Месяц назад
Zomvesa, chisoni pepani ndithu.
Далее
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 106
28:26
Просмотров 18 тыс.
UMBONI WA IMFA YA JOSSUA MZEMBE
14:24
Просмотров 52 тыс.
Symmetrical face⁉️🤔 #beauty
00:15
Просмотров 4,2 млн
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 114
28:51
Просмотров 12 тыс.
DRIVING SCHOOL- Episode 166
15:17
Просмотров 96 тыс.
MBIRI YA LUCIUS BANDA
6:19
Просмотров 9 тыс.
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Просмотров 175 тыс.