Тёмный

BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI MWAKADAULO ZOMWE ZITACHITIKE DZIKO MUNO LERO PA 19 OCTOBER 2024 

Makosana
Подписаться 110 тыс.
Просмотров 34 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 90   
@GeorgeChitapapata
@GeorgeChitapapata 2 дня назад
2025 tiyembekezere imfa zambiri coz ife tikuotcha state house mec ikapanga zakutonso
@kejescompany-zi1ft
@kejescompany-zi1ft 2 дня назад
Iweyo nde wanzeru ase,, ndikuthandizila ndipo program yakoyo ndalowa nawo
@ErickIssah
@ErickIssah День назад
Ndipo asayelekeze kubela
@RiteRoderick
@RiteRoderick День назад
Ndipo Koopsa tizaotcha state house komanso parliament
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Gyz ndikugwilizana nanu ngati mec situla pansi udindo mmalawi muno mtendere sukhalamo chikangawa adziwe izi zachibwana ife sitifuna mcp ikutitengela kumtonso
@HawardKalipande
@HawardKalipande День назад
Jessy kabwila atiyankhule za nkhaniyi mwina sitima ija ili kunyumba kwawo
@lameckmajiga5426
@lameckmajiga5426 2 дня назад
Vuto ndife amalawi sitimagwilizana pofuna kupanga zithu!! Chakwela akanakhala kuti ndiwaziko lina atamuchosa pampando kummawa komwe!! Tili ndiphanvu yomuchosa pampando chifukwa ndife amene tinamuyikapo!!!
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 2 дня назад
Eya zoona
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 дня назад
Chakwera kungowina mobera tigawana dzikoli
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift День назад
Sizija amayakhula mwana wa hure okuda uja,amat ngambwi ngambwi xija
@DennisTobias-b4r
@DennisTobias-b4r День назад
Akabwira Ali kuti hippo ya mcp kuchikamwa
@IssahAluba
@IssahAluba День назад
galu wina aziti Boma ndilomweli lambuyake Chan
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 2 дня назад
Mafutawo asowe kwambiri mmesa mkuti peter ndi nkharamba mukhaure kwambiri muzithaime kaye
@MosesChiwaka
@MosesChiwaka День назад
Following Times Tv with much curiosity, Times continue giving us the best.
@Bowa-c7g
@Bowa-c7g 2 дня назад
Chikangawayu mungochosa pamademopa mukadikila ku Vota sangachoke garu ameneyo
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 дня назад
Malawi dziko lathu likupita kuti our father have mercy
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 2 дня назад
Vuto ndiloti boma ili ndalama likuongongera zinthu zopusa, eg kumangotaya mmisonkhano, kugupeleka ndalama kwa anthu oyimba kuba ndi akatangale ochititsa manyazi ndikupanda otsogoleri
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 дня назад
Amec musatitelo kod mwadya zingati kod athu azingalembetsa zopanda chaudzika kod.
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 2 дня назад
Mumufuse uja amati kwabwela mafuta ngambwi ngambwi uja kodi wapita kutiko mayi ameneuja kapena komwe amakhala simukukuziwa
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 2 дня назад
Tobias....president of his wife and children.
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens День назад
😂😂😂
@WilfredGunya1
@WilfredGunya1 День назад
Mayi malawi muno 2025 ndipomwe mudzadziwe kut timaganiza mosiyana gat siziyenda bwino khondo imfa zidzakharapo maiko ar ndikhondowo kod siworemera km khana adindo mudziva zathu anu bass
@FatimaAdam-r5y
@FatimaAdam-r5y 2 дня назад
Tigendana chaka chino mwanyooo
@SymonMawaya-b6o
@SymonMawaya-b6o 9 часов назад
Atola nkhani tithandizeni ife makolo osauka ana athu akubwezedwa mma school a boma chifukwa cha ma uniform imodzi mwa iyo ndi mbvama school Ku Lilongwe Kodi mabvuto ake amenewa makolo osauka akwanitsa kugulira ana ma uniform paja Mayi kaliyati amaletsa zimenezi Ali mmboma Nthawi Ina yake
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Jessy kabwira mutu opanda sisiwo hule iwe uli kuti iwe ndi chikangawa wakoyo Mesa mumati mafuta abwera? Ali kuti zisilu inu
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq 2 дня назад
Anthu alembesa bwqnji alibe lD,,2 years now no ld,,and am nt alone,,
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 2 дня назад
Plz chonde muchoseni galu uyo pampando palibe chimene akuchita kungowononga ndalama basi
@MorgenYarman
@MorgenYarman День назад
Sitima Ija Inabweretsa Mafuta Aja mafutawo Ali Kt?
@PiusMpando
@PiusMpando 2 дня назад
Chakwera ukuiiwala umphawi
@BlessingsLigwese-m6i
@BlessingsLigwese-m6i 2 дня назад
Bola aliyense alembetse zisakhale zomati machine avuta
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 дня назад
From Cape Town mitchells plain town centre. Mafuta alipo zambili ngabwingabwi osadanda. Boma ndilomweli ee chakwela. 😂😂😂😂Chikangawa woyeee
@FidesChandama
@FidesChandama 2 дня назад
Kodi mesa adatiuza kuti mafuta abwela ku Mozambique pa train ndipo tili ndi mafuta ngambwi ngambwi nanga atha bwanjiso
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 дня назад
Tinenereni .
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens День назад
Pa train pamabwera diesel ekha biggie
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens День назад
Yomweyo toby😅
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 День назад
Chakwera sakufunika
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w День назад
Kuphana kuphana bc chkangawa achoke
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev День назад
Kabwira nkholo yake ndithu
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 дня назад
How can mcp member be wankulu wa mec.....anabel john tembo
@APOSTLEBJ-tc5fp
@APOSTLEBJ-tc5fp 2 дня назад
Boma ndilomweli palibe kusintha😅😅😅😅😅😅mafuta ngambwingambwi
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 ngambwingambwi yemweyoo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@aubreykamwendo4315
@aubreykamwendo4315 2 дня назад
Ajao anabwela pa stima aja ali kut woke up malawi 😢
@omarajibu860
@omarajibu860 День назад
Dziko likufunika asogoleri a serious ili
@MlaziJames
@MlaziJames День назад
Atule pansi udindo chikangawa
@EsetaGerate
@EsetaGerate 2 дня назад
😂😂😂 jesey kabwira kuntumbo kwako ndimachende achakwera, chimwendo Banda mukamat boma ndilomweri mumanena boma lake liti
@trickermussa472
@trickermussa472 2 дня назад
Ku Lilongwe nakoso mafuta akusowa kkkkkkkkkkkkkk
@TalumbaNjowela
@TalumbaNjowela 2 дня назад
Boma ndi lomweli tingosittha chipani 😅😅😅
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Danlu ndi azako mukuti boma ndilomweli, inuo muli ndi amanu? Zisilu inu,mafuta sakupezeka palibe chilichonse chikuenda mumuze chikangawa wanuyo kuti ngati sakusamala dzikoli tiligawanapo
@AshimayeGama
@AshimayeGama День назад
Olo tivote aganidzakale dzonela
@HopeeNaomi
@HopeeNaomi День назад
Zoonad mtendere ndiofunika
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga 2 дня назад
ine ndikuti kodi pampando ungamuyike busa ndikuuzeni amalawi president amasayina zinthu zoyipa kuti dziko mubwele ndalama ndiye uyu ndi busa angayendese ziko muganize bwino busa sakhala president chifukwa busa amapanga za ufumu wakumwamba kodi amalawi munachita kulozedwa ine martin muziganiza bwino amalawi uyu si busa koma satana analibe ndalama mukumuyika munthu opanda ndalama boma kuti akhale wankulu kodi angatani kumaganiza amalawi muzikhala ndi dzelu ku school sanapite mokwanila za ikonome samayiziwa
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z 2 дня назад
Kodi zimafuta zonse zinabwela zija zinatha?😂🙌
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 дня назад
Nkhani ya mafuta zakhalaso bwanji poti a Kabwira ndi Chakwera amakalandila sitima za mafuta ku Nsanje. Ndipo amadzitama, apita kuti mafuta.
@DianaMmagisa
@DianaMmagisa 2 дня назад
Boma ndilomweli la chikangawa party
@LoydKamtedza
@LoydKamtedza 2 дня назад
Kodi siamati sitima inabwela ija inabwera ndimafuta atha pompano 😂😂😂😂😂😂😂😂 koma chikangawa ayaluka 😂😂😂😂😂😂😂😂
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 2 дня назад
Chimwendo akukhuyu kamajikete mayi ajawo achakwela kunena kutu abweresa mavuta zoonadi athu inu umapita kusinkhono wachakwera chifukwa chiyani
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 2 дня назад
Kodi wazobwirabwira uja paja mesa Amati apule Akeo abweresa mafuta ndye alikut agalu inu
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 дня назад
Koma machine zitilora ai tingwilitsile manyo basi palibe no smartmatic out
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 2 дня назад
Boma NDI lomweli adatero kabwira anthu akugona panja kufuna mafuta chisoni Kwambiri
@FrancesPeter-xw3vb
@FrancesPeter-xw3vb 2 дня назад
Mesa sitima yafika kulilongwe yamafuta kodi ndiye mafutayo aChakwera awamwa kodi 😂😂😂😂😂😂 koma Malawi dziko laamphawi mmmmmm
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 дня назад
Kodi atobiyasiwa ndiyeso watiwo,? Kodi dzikoli mulitenga ngati dimba eti zitiso izi nanga? Muzikatsekula manda bwanji enanu?
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 дня назад
😂😂😂😂😂
@ChimwemweMathyola
@ChimwemweMathyola 2 дня назад
Zachisoni anthu akuti boma ndilomweli
@ChimwemwePhiso
@ChimwemwePhiso 2 дня назад
Chikangawa watiyenjeza
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 2 дня назад
Chisilu mayi yolamu ujawiso asamange 2025 osewo wosaziya mbafa
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 2 дня назад
Aliyense wobadwira mmalawi akavote basi kopanda chiphaso chifukwa galu uyo sakufuna kt Madera ena akhale nacho chiphaso unya uwona 😂
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 2 дня назад
Ntendele ena akufuna kubela
@jennyx6914
@jennyx6914 2 дня назад
brian banda ndi anzako chonde pangani programme ndi nduna za boma la mcp alongosole afunsidwe mafunso pankhani yamafuta asangothamangila kuyankhazipani za dpp afford ndi utm kkk
@AnthroGondwe
@AnthroGondwe 2 дня назад
Chilenga chimuthu chachambechabe kukune zithu kwaine iyeyo ku nthalire vikumunyela mavi mboloyake
@shafiemalobvu
@shafiemalobvu 2 дня назад
akuti boma ndilomweli kufuna kulakwitsana malankhulidwe
@FatimaAdam-r5y
@FatimaAdam-r5y 2 дня назад
😂😂😂😂😂 kulakwisana bwino
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 дня назад
Osati atilakwisa kale or mulungu atabwela usikuwu atha kupeza kuti dziko lonse lino palibepo olungama mwina athakupeza athu abwino nda kumkuyu achimwendo ndi azikhale
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 2 дня назад
Agalu.awa.achoke.bas
@SaedJafari-z7r
@SaedJafari-z7r 2 дня назад
Apule tobi
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo 2 дня назад
boma ndilomweli paja akumabwera pa stima
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 2 дня назад
Palibe chimene chikuyenda ku malawi
@MbelekaAbdullahWhyte-p1i
@MbelekaAbdullahWhyte-p1i 2 дня назад
Ku Malawi kwanunkha linya.
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 2 дня назад
Iwe nkosi kalembera wamzika ayendebwino mtendere ukhalapo apo biii kalikonse tikaona
@jennyx6914
@jennyx6914 2 дня назад
boma ndilomweli kkkkkkkk mafuta aja ankanena apita kwayani? ndiye tiziti bon kalindo ntanyiwa ndi ena amalankhula za mcp kuti ndi akathyale akulakwa kapena ndi aboza??? booon kalindo the dc
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
Tikuzaocha zambili za boma tikayamba zathu pompano
@MariaNyamwera
@MariaNyamwera 2 дня назад
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😊😭😭😭😭😭😭😭🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🌹🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢💕💕💕💕💕💕💕💕💋💋💋💋
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes 2 дня назад
Nanga mafuta adza amanyadisa Jessie kambwira ni chakwera Ali kuti maexa amati bakili muluzi tv ni mtanyuwa amanama
@jennyx6914
@jennyx6914 2 дня назад
zachisoni kunkuyu chimwendo zikhale kuti ati chani zamafuta poti amankhula kwambiri agaluwa kuonjezapo ben longwe kape ofanana ndi nsonda kuonda mutu pano
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Akakhal msonda wasala lilime lokha ndi mano basi
@TomasDzifoole
@TomasDzifoole 2 дня назад
Anene bwino bwino chikangawa zamafuta,
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 2 дня назад
We
@BrightZionga
@BrightZionga 2 дня назад
Jesse kabwila kachiphazi ulikuti ngambwingambwi watha bwanji munatamikatu ndi kunkuyu wako komanso chimwendo umunthu mulibe shame on you+ chakwera
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 дня назад
Ndipo tsikulija akuchita kuyankhula mwaphuma lilibodza koma anthu ena inuuu
@Peter-n3v7p
@Peter-n3v7p 2 дня назад
Ndiponso Inu mayi uyu amati kabwilayu eee ndiwamkamwa mwa boza
Далее
skibidi toilet multiverse 042
20:57
Просмотров 4,7 млн
Тестирую гаджет для роллов! 🙈
00:42
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Просмотров 118 тыс.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Просмотров 184 тыс.
skibidi toilet multiverse 042
20:57
Просмотров 4,7 млн