Тёмный

CHAKWERA ANAKAZIWA KUTI ATAYANKHURE ZA IMFA YA CHILIMA KU NSONKHANO WA MCP ZIFIKA APA SADAKAYANKHURA 

Makosana
Подписаться 95 тыс.
Просмотров 28 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 262   
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c 2 дня назад
Ambuye mukule ife tichepe wonetserani poyera zomwe ife taphimbidwa apatseni mtima wamphanvu wose aktimira amen🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼
@patesnkajenda4258
@patesnkajenda4258 День назад
Don't give up Mr ndilipopo kusatila osaopa💪🏾💪🏾💪🏾💪🏾
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 дня назад
This guy he need a support please guy's is powerful in this time
@Malawian-q5f
@Malawian-q5f 2 дня назад
Wosangolemba chichewa bwanji 😂😂😂😅
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 дня назад
@@Malawian-q5f whatever bro anyone can make mistakes
@hendricksmlendo6192
@hendricksmlendo6192 2 дня назад
Our support could be in demonstrations, these guys are very pheee!!!
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 2 дня назад
Mr Namiwa chonde chonde Tigwiren Manja please please tikufuna tidziwe choonadi Mmm Malawi wanukha kwambiri
@augustMag
@augustMag 2 дня назад
Ndipo dziko la Malawi lafika powawa popweteka Ambuye atimenyere nkhondoyi limbani mtima dziko likufunika kuomboredwa Dr Saulos Chilima anakankhala moyo anakawina mavote mu 2025 komabe Mulungu satitaya never give up Mr Namiwa go ahead osafooka osatopa kutiyimirira ❤❤❤❤
@GraceMwase
@GraceMwase 2 дня назад
A Namiwa ndionse aku CDEDI Mulungu akudalitseni mochuluka ndipo akulimbitseni mtima nakutetezani kuti mupitilize kufufuza zaimfa imeneyi. Chonde chonde musalandire zindalama zamagazi za MCP Mulungu wathu akuona ndipo nkhondoyi tiwina
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 2 дня назад
Kukufunika anthu ngt awawa more fireeeeeeeeee Namiwawa ❤❤❤❤❤❤❤❤
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 дня назад
Umayitha Namiwa,keep it up
@robertrichman9376
@robertrichman9376 2 дня назад
Keep up Namiwa, we're with you, MCP kwake kwatha no matter what
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 дня назад
Kod ame comanda akugwirabe tchito mpaka rero why?
@MosesTangwe
@MosesTangwe 2 дня назад
Kuteroko mwasokoneza dala kuti zisamveke bwinobwino 😢
@MussaZimba
@MussaZimba 2 дня назад
Namiwa komwe uliko uchive mutimamo kuti ifeyo amalawi tilipambuyo panu ❤❤❤❤
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 2 дня назад
Keep it up Comrade Mr Namiwa asamaone ngat iyeyu Ndi President oyamba kapena omaliza ayi a Malawi!!
@JacobMsukwa-q6v
@JacobMsukwa-q6v День назад
Pa Chilima pokhapo ine ntima wanga unasweka ndi ndisweka pakanapano💔💔💔
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift День назад
Ndikanakhala fit mmm ndikanalorera ukathere kwa chakwera ,koman ndimapephera kt chona chizaziwika
@HildaMbizi
@HildaMbizi 14 часов назад
Zoona pasakhaleso ngati 1983 iyayi apapa tifuna chilungamo chioneke ambuye tithandizeni
@McshonWilliam
@McshonWilliam 2 дня назад
President wontani osakonda anthu ake pamene akulira, mmmmmm this is not good at all and yet tinamusankha kut azilamulira dziko koma relo tasanduka makape 😢😢😢😢
@prescottchambo4665
@prescottchambo4665 День назад
The enquiry must happen and thanks very much comrade Namiwa for the boldness... you aren't alone the Heaven is with you and will back u always coz you are standing on the truth...
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 дня назад
Bravo Sylvester Namiwa and CDED
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 2 дня назад
Bravo 👏 CDEDI...Malawi freedom fighter 🇲🇼🫡✊️
@ALEXJOSEPHYNTHULU
@ALEXJOSEPHYNTHULU 2 дня назад
mr Namiwa Muli ndisongolo labwino kulimba mtima pachilungamo zili mwainu 🔥 🔥 🔥 🔥
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 День назад
I like this. Atitola anthu amenewa tinavota kuwaika pa mpando chifukwa chokonda SKC komanso posatira kuti anachita kupemphedwa kuti azichepese mkuluyu atsogole koma eeee akuoneka anangobisa mawanga ndiovuta mkhalidwe lake.
@kennymwanyongo8165
@kennymwanyongo8165 2 дня назад
The background music is so loud. And the sound quality is very poor. Could the producers be serious with their job please!!!
@brianjames211
@brianjames211 2 дня назад
The world is expecting much better production so please media produce a better coverage or audio conversations, this airing is very bad in signals
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 2 дня назад
Bravo Comrade Namiwa
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 2 дня назад
VERY POWERFUL MR NAMIWA.OSAPHETHIRA...
@andreabanda7838
@andreabanda7838 2 дня назад
This is very good. A pule asamaitenge nkhani iyi mwachibwana. A commission of enquiry is very important.
@InnocentDzanja
@InnocentDzanja 2 дня назад
MCP chipani chobowa bwanji satanic party......
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 дня назад
Amene anaimbira litchad chimwendo banda kuti asakwere ndege akufunika timudziwe tikamupha ngt galu
@DanielMaruwo
@DanielMaruwo 2 дня назад
That's very very good you are a true leader
@HamidMasamba
@HamidMasamba 2 дня назад
More fire Mr Namiwa, mulungu adzikupasani mphanvu ❤❤
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 2 дня назад
Keep it up Mr namiwa... Chilungamo chiyende ngati madzi
@Halima-i4x
@Halima-i4x 2 дня назад
Anthu takwaiya 😢😢😢 dziko lamalawi 💪💪💪ndipo zionesela zichitika kun tili okoseka
@JillianAgulhas-k1s
@JillianAgulhas-k1s 2 дня назад
Kafukufuku wadege achitike ndithu malipot omwe anabweretsawo ife amalawi samatigwila mtima or mpang'ono
@InnocentBanda-ze8de
@InnocentBanda-ze8de День назад
God b with you guys and Malawin 🇲🇼
@FlechaChipeta
@FlechaChipeta 2 дня назад
Big ❤❤❤❤❤
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 2 дня назад
🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Chilungamo chiyende ngati Madziiiii......Big up CDEDI More Fire Namiwa
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi 2 дня назад
BG up Mr namiwa ❤❤
@FaithGondwe-o8c
@FaithGondwe-o8c 2 дня назад
Very powerful MR Namiwa . Ntchito tingwire Limodzi iyi .🔥🔥💪💪👍
@AddSley
@AddSley 2 дня назад
We need these type of people in Malawi
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 День назад
God bless u mr Kabambe 🙏 ❤️ ♥️
@AustinNangwale
@AustinNangwale 2 дня назад
Keep it up boss 💪💪💪
@DadTshepo
@DadTshepo 8 часов назад
Comrade NAMIWA Mulungu adzikutetezani nthawi zonse ndipo akupatseni madalitso mmoyo wanu
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 дня назад
Well done cdedi mosogozedwa ndi mr namiwa
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 дня назад
Keep It up Good Mr Namiwa
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift День назад
A sidedi ziwan ku chakwera ndi muthu mozi olimba tima ,and so samalabada zamwoyo ya athu,koman tilorera apange chilichosi pa moyo wathu💪
@DouglasDimingu
@DouglasDimingu 2 дня назад
Koma anthu awawa achipani cha MCP amamva koma zomwe aMalawi amayankhula?
@BrightNgulube-h4w
@BrightNgulube-h4w 11 часов назад
Uyu Chakwera akufunika kugendedwa nthawi yake ndiyino ya campaign awona mbwaza
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Час назад
Powerful speech
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 2 дня назад
Keep up Namiwa atiwuze ife atolankhani tsapita kukawafutsa anthu kumalo kuja
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 2 дня назад
Osaopa osafoka big up CDEDI kutolodwa kulipodi tikangokhala chete
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 2 дня назад
Umakwana Mr Namiwa,,,,tili pambuyo panu
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 дня назад
Sizikuveka bwino
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 дня назад
More fire guys tiwombore ziko mukamwa mwa agaluwa
@ayamijackson1443
@ayamijackson1443 2 дня назад
On the point mr namiwa my lovely Malawian let's go this is time to take action chilingamo chioneke
@peterlowole7841
@peterlowole7841 День назад
God is our saviour,, koma tikufuna owinayooooo azawapase 24hrs after kulumbira abweze ndarama zathu zimene akubazi ndikumagulira oyimba ndi andale ,zilizathu kumene , what a shame, or aza wonetse nkhope ngati achisoni ,ayiiii atikwana,tifera Malawi wathu.
@ElizabethKamiza
@ElizabethKamiza День назад
Vuto anamiwa mutu wanu sukugwila tchito mukulongolora koma palibepo mukupanga zikutiwawa kwambiri we are tied with this nonsense mcp government
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 2 дня назад
More fire 🔥 Namiwa azatitole chikangawa umakwana big man 👨 🔥 🙌 no matter what chikangawa waga bas will don't need this president again kkkkk chakwera anthu akukudikila ku chipiku pls 😀 👏 👍 😉 😳
@CharlesMmaniwa
@CharlesMmaniwa 2 дня назад
Forge ahead Mr Namiwa we are together with single aim
@rhodachavula7739
@rhodachavula7739 2 дня назад
Ambuye akutsogolereni mpaka a Malawi adziwe choona .
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 2 дня назад
He need to come and tell the nation and what I don't understand is that do we really need to pleade to him does he not know that commission of enquiry will solve or make people calm down and stand what happen.. Maybe he put his hand on this.. If they are scared of upcoming election they are going to lose anyway..
@ProspaDMitummba
@ProspaDMitummba День назад
Zoona choonadi ciziwike more fire
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 День назад
munthu uyuyo needs much support coz waima pachilunamo ..dzikoli crsly sililibwinotu...anthu akuvutika especially mamidzi umu uhm may God forgive&help us and hv mercy us👋🙏
@chesterkumwenda
@chesterkumwenda 2 дня назад
Achoke pampando
@PaulKambuzi
@PaulKambuzi День назад
Pachilima pakhapo mmmmm ine ndisaname mtima umandiwawa osat masewera
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 дня назад
Mbuzi za asirikali
@CharlesZidana
@CharlesZidana 2 дня назад
Gentle men ,it is enough.things are worse,we are not citizens in this country
@comfortndema
@comfortndema 2 дня назад
Osaopa osafooka big up CDEDI
@JosephyKadenga
@JosephyKadenga День назад
Zikomo mr namiwa poyenda nanu pa nkhaza zomwe tikukumana nazo
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 2 дня назад
More fire comrade namiwa Allah azikuyang'anirani thawi zonse
@VanessaAlinafe
@VanessaAlinafe День назад
Acdedi mlibwino kwambiri pangani zinthu zothekela nkulu ameneyo achoke basi komaso anthufe tisalekelele Acdedi wokha ayi nafe titengepo gawo lothandizana mawo azathu pamene akuphila zinfumdo zotyakuka bwino zikomo kwambiri
@RuthMkangala
@RuthMkangala День назад
Very powerful
@JusticeKalemba
@JusticeKalemba 2 дня назад
More fire 🔥 namiwa
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 День назад
Media mukulongosola Sound kumapeto chifukwa all along poor sound why why why ? Munena bwino
@JhadahLeafs
@JhadahLeafs 2 дня назад
Amatelo awa akambilanakale pamenepo kenako munva kulizii malawi zikolonvesa chisoni
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 дня назад
Anthu Akuda kumuvotela munthu kumuika paulemelelo inu ndikumadya chitedze. Ma MP Nyumba zomwe akumanga komanso magalimoto akugula ndi vote yako,
@EDSONNAKULENGA
@EDSONNAKULENGA 2 дня назад
Anamiwa mukuyakulazoonazake ikalepobasi kufikila chilugama chibwelepoyela salomu
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 10 часов назад
Ndimadabwa ndi afitiwa Chikangawa akamabwera kuchokera kunja basi kumudikira KU airport. Kodi a malawi ena mitu yawo yikugwira ntchito bwino. Report la uchitsiru NDI Germany yoo
@HajiraMustapher
@HajiraMustapher День назад
Chilungamo chiyende ngati madzi and akanakhala kuti achakwera ndi MCP siikuwakhudza zangoziyi bwenzi onse amene anali pa durty achotsedwe ntchito olo suspend koma mpakana pano palibe aliyense anachotaedwa ntchito
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 дня назад
commission ikufunika osafooka Malawians atitora kwambiri
@HamzahBenson
@HamzahBenson День назад
Eish kom dziko la pass ngati bodza ndithu chilima kuli ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii anapitad mmm
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v 2 дня назад
Mistake anapanga a Chilima inawaphesa nkusiyanso amalawi pavuto lalikulu
@KentWilliam-r2v
@KentWilliam-r2v 2 дня назад
Oyess zoonadi a chilima vuto ndi phuma
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 дня назад
Anthu oyipa kwambiri a mcp your days are numbered a moyo komanso olamulira dzikoli chifukwa sinu Mulungu
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 дня назад
Avarentino mpili munkanamiza ana amanu kuti ndege ili uku mukuyenera kuphedwa nyumba zanu ziyatsidwe muphedwe ngt agalu
@chikoko-uj2tt
@chikoko-uj2tt День назад
Achilima anachita kuphedwa MCP ikubisa chilungamo nevertheless we need justice 4 his death
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 2 дня назад
Bungwe losafuna kunyengelera boma lopanga zopusa komaso bungwe losadya ziphuphu za boma ,zitsilu zayamba kunena kt bungwe loimila dpp umbuli nd dyela ... idyan ife tikufuna chilungamo.
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 2 дня назад
Koma bungwe ilili eishiii likutimenyeradi ufulu they deed support
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 2 дня назад
Zoona osamusekelela chakwela atiyakhe mafutso amenewo
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 2 дня назад
Chilungamo chiyende ngati madzi zimatiwawatu ife 😢
@AnnieNyirenda-d5t
@AnnieNyirenda-d5t 2 дня назад
More fire brother namiwa ulemu wanu
@HenryMziwanizga-p1d
@HenryMziwanizga-p1d 2 дня назад
Uyu ndi Julius malema waku malawi amalawi tiyeni tigwilane manja
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o 2 дня назад
Tangopitan ku musewu mose muja munayambira kuophyeza
@WallyMsiska
@WallyMsiska 2 дня назад
Chakwela akunamizidwa ndi omuzungulira atitenga ife analawi ngati ndife ogona iwo azelu
@JasonMailos
@JasonMailos 2 дня назад
Tiyeni nawooni tisasekelele mademo wo tiliwokozeka kaleife
@MariaGatoma
@MariaGatoma 2 дня назад
Amen inu mwasakhidwatu nfi mulungu,,chifukwa mfundo zanu zikulowa mtima mwa ina aliyese yemwe ali ndi mafuso ochuluka,,,komaso aziwe kuti ma plan okupha chilima anapanga ngati mbuli,,maso anu akuona patali
@AlickKapapa
@AlickKapapa 2 дня назад
Kodi payifa ya olemekezaka mwatumidwa mwatumidwa or bwanji Ngati mkufuna za kafukufuku waku Germany simkukhula kapangeni wanu basi free koma munthu alindisiku lo badwa ndi la kufa
@DoriceMagawa
@DoriceMagawa 2 дня назад
Ndinu olimba mtima tawona km tisave kt akugulani a mcp. Till
@donexmakande5979
@donexmakande5979 2 дня назад
Well done mr namiwa
@MangaDamiano
@MangaDamiano День назад
More fire
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 2 дня назад
Kodi nanga Ali ku manjako sayankhula timvenso mawu awo
@SteveKanongwa
@SteveKanongwa День назад
Inuso simutha kutenga action koma kumangopeleka masiku bas mose munambira muja zinthu sizikusinthabe
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 2 дня назад
Suzinenezo comite ya chani.achoke basi 14 days yoti achoke asati comite
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj 2 дня назад
Chikangawa ndi munthu omva zake zokha ngakhale ali msogoleri wampingo
Далее
Running With Bigger And Bigger Lunchlys
00:18
Просмотров 35 млн
Rocketing: Israel escalates Lebanon conflict
21:08
Просмотров 9 тыс.