Тёмный

Chifukwa Chomwe Taimon Tipa Wachokera Dziko La South Africa.. 

Sam Malvitha
Подписаться 89 тыс.
Просмотров 13 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

7 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 76   
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 дня назад
Kelly Kay you can't compare with Taimon Tipa, Tipa ndi machine owopsa zedi komanso got uncountable fans❤❤❤❤
@laurencepetani860
@laurencepetani860 2 дня назад
I like this guy for his music, it touches me so hard, I was wondering where about of him but now am happy to hear that he is still doing music big up tipa boy!!!!.
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 2 дня назад
Yes ndizitheka ndi big man ameneyu timakonda kwabasi
@rabeccaphiri1333
@rabeccaphiri1333 2 дня назад
Obviously he will make it no doubt
@WAXBDJANGOSMOK
@WAXBDJANGOSMOK День назад
tonse timankonda❤❤❤
@AllanBanda-x5p
@AllanBanda-x5p 2 дня назад
Dolo kwambiri taimon tipa ❤❤❤😊😊
@ChancyDzinkambani
@ChancyDzinkambani 2 дня назад
Abooleza ameneyu muli mfundo za bho mu nyimbo zake ziti wina aliyese angathe kuzikonda and nabora atsogoze mulungu
@trymoo8479
@trymoo8479 2 дня назад
Don't hate him....uyu amayimba bwino 🎉🎉
@LinnyMkomwa
@LinnyMkomwa 5 часов назад
Uyuyu ndi Dolo❤
@paulphiri-fz9me
@paulphiri-fz9me День назад
Taimon is the best
@KondwaniMarkoBilliat
@KondwaniMarkoBilliat 5 часов назад
Welcome back madhala. Uyu amaika music ndipo agwesatu azibambo enawa
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 дня назад
This guy is talented ndipo ndi makina owopsa zedi❤❤❤❤
@JaydeeAchalume
@JaydeeAchalume День назад
Aliyese amakhala ndichisankho inde iyeyo Ali okhozeka ndithudi chifukwa ndimaloto Ake angathe kukwanilisa inde kmso atafuna kubwelela Ku south kuthekela alinakoso nde let's go sapot fanayu apitilize missions
@fikrumokoro-u2l
@fikrumokoro-u2l День назад
Yah he can also make it,because talent is an unique
@IbullaTaimu
@IbullaTaimu 6 часов назад
Taimon ndidolo akuyimba mwachikoka
@HunswellJailos
@HunswellJailos День назад
Waganiza bwino. Coz nalo dziko la south Africa likadayambaso kumusaka kuti lizipindula mwa iyeyu. Zosatila zake zikadakhala ngati za Bushiri. Kuthawa mkusiya chuma dziko laweni. Tipa fire.
@LeonardoTitosQuiniosse
@LeonardoTitosQuiniosse 2 дня назад
Ine ku moçambique 🇲🇿 taimon tipa amatha apeza malo chifukwa amatha kuimba za tathauzo
@aungankadzinja
@aungankadzinja День назад
Inu Adawo Amaswa havy kulibe kunong`ononeza bodo ai Chifukwa Amaswa kwambiri nyimbo zake ximatiwaza havy
@WithekReuben-u2s
@WithekReuben-u2s 2 дня назад
Eya ndizotheka chifukwa athu akumukonda kale
@HAPPYNKHOMA-z1z
@HAPPYNKHOMA-z1z 2 часа назад
Mwana amatha uyu akwani sye yekha inanso akusaka zomwezo
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 дня назад
I love you tipha
@StevenJalifu
@StevenJalifu 2 часа назад
Mulungu sasankha ponchukila, polemelela etc ngati wachoka dziko la south africa kuti akukapanga za music basi kumalawi sanapange chiganizo chabwino akhale kuti wachokela zina osati zimenezo inde ku south ndikodula kupanga nyimbo kusiyana ndi kumalawi koma bwenzi akumangopanga record ndikutumiza basi ndi mfana wabho kwambili tipa.
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 2 дня назад
Ngati nyimbo zake zizikhala zimenezi ndizotheka komanso ngati angasankhe kusalowerela ndale zichita bwino koposa
@JankaJafali-s9i
@JankaJafali-s9i 2 дня назад
Aboledza ❤🎉 ndikatundu mwanayo
@GeorgeJali-hs8of
@GeorgeJali-hs8of 2 дня назад
He's going to make it
@WilsonMavuto-tf4nj
@WilsonMavuto-tf4nj 2 дня назад
Ada awa amaimba
@JafarFrank-u6q
@JafarFrank-u6q 2 дня назад
Is going to be the best 🎉❤
@ChitalakaKumwenda-e8t
@ChitalakaKumwenda-e8t День назад
Taimon Tipa ndi Dolo angofunika support ya mphavu
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago 2 дня назад
Taimon will make it and mpata anaupeza kale,,,space mu music industry yake ilipo kale
@ToxAlimonjaimeJaime
@ToxAlimonjaimeJaime 2 дня назад
Ndimmene akuimbila zitheka
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 2 дня назад
Sasafulika kkkkkkkk
@BrianMwante-q6d
@BrianMwante-q6d 2 дня назад
kkkk
@HappyJohn-vw3ul
@HappyJohn-vw3ul 8 часов назад
Ku Malawi ufiti basi😢😢
@ChifundoAmos
@ChifundoAmos 2 дня назад
Mesa zikakamuvuta akabwelera ku South Africa
@RAPHAELMASAMBA-nd9qk
@RAPHAELMASAMBA-nd9qk 2 дня назад
eeeee man mwana uyu amatha ifeyo tili kulikonse komwe angapite eeeee waivera suli wekha ija waswatu
@VictorUsen-f7d
@VictorUsen-f7d 2 дня назад
Ndidolo uyuyu zitheka kwambirinso mosakaikila
@SurpriseNgobeni-k6z
@SurpriseNgobeni-k6z 2 дня назад
Zitheka palibe so ataaa
@BrianAmbeswa
@BrianAmbeswa 2 дня назад
Ndizotheka abowoleza basi
@YamikaniMasuli
@YamikaniMasuli 2 дня назад
Mzotheka kupeza Malo pang,onopang,Ono azakewonso sanangofikila kuzpezela Malo, akuyimba bohboh bass.
@MartinNgoma-tp2jk
@MartinNgoma-tp2jk 2 дня назад
Amaimba bwino tipa love more
@KalistoKabila
@KalistoKabila 2 дня назад
Zowona zatheka ndidolo
@PreciousNgalande-b3d
@PreciousNgalande-b3d 2 дня назад
Ali kale mu line ndi katundu taimon
@yohanekhwatcha355
@yohanekhwatcha355 2 дня назад
Uyuyu waboleza kale!!!!
@BishopMaxwell
@BishopMaxwell 2 дня назад
Uyu wabooleza kare amwene
@MosesDicostar
@MosesDicostar 2 дня назад
Walakwisa kwambiri
@IsaackYesayaBanda
@IsaackYesayaBanda День назад
Ea timamukonba kwmbili tamulanbila
@VincentMwenso
@VincentMwenso 19 часов назад
Aaaa inu mwanayu aboolez ndpo osakaik mix mafuso enawo nd otsitsilan pas
@basheerkachelenga9198
@basheerkachelenga9198 2 дня назад
Ayi nachita kugwidwa ndi yifeyo wotsati anangochita chigano ayi aaaa chonwelela kumqlqyiko ayi kunama aaaaa
@MathewsMynus-v9u
@MathewsMynus-v9u 2 дня назад
I like this guy
@MadalitsoDchapendeka
@MadalitsoDchapendeka День назад
Madara akuimba bwino kwambiri
@TinoCharamba-hr9el
@TinoCharamba-hr9el 2 дня назад
Taimon ndimunthu amene amayimba bwino kwambili ndipo kubooleza sikuvuta chifukwa ndiwoyimba yemwe amayimba waukadaulo
@ArronBenson-g6d
@ArronBenson-g6d 2 дня назад
Ndidolo uyu
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 дня назад
Kukaika ndi chimo. Zitheka bora faith
@abdukarimmponda5698
@abdukarimmponda5698 2 дня назад
Iyenso ndi dolo basi
@PaulNkhata-c3b
@PaulNkhata-c3b 2 дня назад
Pafunika kt alimbikile kwambiri
@ThungeMauziboy
@ThungeMauziboy 2 дня назад
Aaaa iwe Mesa waboleza kale ameneyi
@NoluvuyoMatutu
@NoluvuyoMatutu День назад
he is better
@SurpriseNgobeni-k6z
@SurpriseNgobeni-k6z 2 дня назад
Eeeeee Koma mnyamata uyu amaimba bwino nyimbo zatanthauzo
@MilianoMenard
@MilianoMenard День назад
Dolo
@PricillaDamane-h1v
@PricillaDamane-h1v 2 дня назад
Tips nidolo osati zinazo
@Alexchikweza
@Alexchikweza 2 дня назад
Zitheka kwambiliso ubwn wake sanachoke atanyoza amfumu
@VincentMaluwankhata
@VincentMaluwankhata 2 дня назад
mkulu uyu moopa kumwamba sanje siya bwino uyu amaimba sati sewelo ndipo abooleza mosakaika
@AkifaIssahfelson
@AkifaIssahfelson 2 дня назад
Akwanisa
@MadulaGift
@MadulaGift 2 дня назад
Asakaike nyimbo zake zimaveka bwino kwambiri anthu amukonda
@thabangmaepa9322
@thabangmaepa9322 2 дня назад
Uyu waboleza kale
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 2 дня назад
Bola asalowere Ku mipingo ya chionongekoyi ili dziko munoyi
@RaffiqMahmoud
@RaffiqMahmoud 2 дня назад
Aliyense amakhala ndi omusatila ake ,ndipo aliyense ndi dolo pa luso lake
@JamesiDavie
@JamesiDavie 23 часа назад
Aboleza
@ThungeMauziboy
@ThungeMauziboy 2 дня назад
Iwe onesimus siwa international?
@ChancyDzinkambani
@ChancyDzinkambani 2 дня назад
Asam mwanayu mukufanana nayetu
@sammalvitha
@sammalvitha 2 дня назад
Hahahaha
@yamotojay1211
@yamotojay1211 2 дня назад
❤❤❤❤
@VeronicaSekobi-is6dk
@VeronicaSekobi-is6dk 2 дня назад
❤🎉
@Mohammed-sk1fy
@Mohammed-sk1fy 2 дня назад
Zonse nd nthaw abooletsa ndthu
@EduardocadamanjatomasCadamanja
Aupenza
Далее
UMBONI WA EVANGELIST GOLDEN LAPANI
34:01
Просмотров 5 тыс.
Bro's Using 3 Weapons
00:36
Просмотров 4 млн
would you eat this? #shorts
00:13
Просмотров 3,2 млн
Taimon Tipa_SIWE WEKHA (official Visualizer)
3:53
Просмотров 137 тыс.