Тёмный

CHIHANA NDI NANKHUMWA AVUTA UKU | 

DZIWE TV
Подписаться 32 тыс.
Просмотров 42 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

27 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 126   
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 3 месяца назад
Big up Mr Chihana though sinamveere zomwe mwayankhula ndangowona anthu akuyamikira
@JIMMYWATHONJE
@JIMMYWATHONJE 3 месяца назад
Straight to the point Mr Chihana
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 3 месяца назад
Nduona ngati akuopaa kkk ufulu weni weni tilibe kweni kweni
@Edson-sj8vn
@Edson-sj8vn 3 месяца назад
Mawa lisathe kalindo amasulidwe chakwera &usi tionana 2025
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 3 месяца назад
Nkukuyu ungotaya nthawi kulankhula zopusazo asakuziwa kuti Chakwera ndi nsogoleri ndani sangalalani ndi gulu lanulo LA uchigawenga mcp 😭😭😭😭😭🐊🐊🐊🐊
@JohnsonRannel18
@JohnsonRannel18 3 месяца назад
Ufulu wake ndiye wutiwo mungomanga adzanu ndi kuphaso azanu
@AlickMDayi
@AlickMDayi 3 месяца назад
Anthu amenewo ofufuzawo pls Mr Chihana muwonetsetse kuti asachokele ku Butchery kumene amatinamiza kuja kuti akagura Feteleza anthu akuba awa ndi kupha oyipa a MCP
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 3 месяца назад
Memories will remain fresh even after 100 years. Let's remember them in a special way and continuously pray for their Souls to rest in eternal peace.
@PaulMwachande
@PaulMwachande 3 месяца назад
Nankhumwa wayamba kulankhula chifukwa sanamusankhe kukhala vp
@BrightZionga
@BrightZionga 3 месяца назад
Dzaka 60 really 😢😢😢 Malawi udzakula liti 60 years still kuvala pampaz shame on you kunkuyu
@EdwardMukholi
@EdwardMukholi 3 месяца назад
Nanga anthu amene mukuwamangao mukutathauza kuti mukulira bodza bwanji Mr president
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 3 месяца назад
Aaa atenga anthu osadziwika cholinga choti adzattwudze mabodza ANTHU AKADZAMANENA KUTI CHILUNGAMO ACHIBUTSA ADZIMANGIDWA NDE MCP IMENEYO NDEGE YOTI DZIPANGIDZO DZINA ANACHOTSA MO MA PHONE KUTENGA KUMAFUFUDZA POKAPELEKA MA FON AFUTAMU CHILICHOTSE AAAAA amalawi mufunilanji omboni wina apa zawoka dzokha kuti chiwembu chokodza MR CHIHANA THANKS U SO MUCH KOMA A MCP AKATULUTSA BODZA LAWOLO ngati inu mudzayankhule potsusana a MCP mudzayembekedzele kumangidwa CHIFUKWA PANO DZIKO LA MALAWI LAFIKA ULAMULILO WACHIPANI CHIMODZI CHAKAKA NYALENDA NDADZANU ENA MUNATILAKWILA AMALAWI MUDZIWE DZIMENEDZO
@hajjdaud123
@hajjdaud123 3 месяца назад
Anawo akhala osabereka
@FrankMkwala
@FrankMkwala 3 месяца назад
Chihana very good
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 3 месяца назад
Chihana well spoken,
@robertnambazo9936
@robertnambazo9936 3 месяца назад
Akuziwa kuti anthu sazapitako awatuluka anthu awa
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 3 месяца назад
Agalu mumuziwaso Mulungu
@ElizabethKhosa-gx3wt
@ElizabethKhosa-gx3wt 3 месяца назад
Chingawenga choopya cha chakwela panopa chikufuna kuphe bon kalindo
@marryphili5419
@marryphili5419 3 месяца назад
Musatinyasepo apa ufulu womwe mukunena ndiye wuti Malawi wake wuti womwe Muli wufulu za ziiiii
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN 3 месяца назад
Boon kalindo ndikumufuna osat inuo,chokan apaaaa
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 3 месяца назад
Ukuona ngati anthu akukukhululukini mwanya akupha
@storytambala6088
@storytambala6088 3 месяца назад
Hmm iwe Kunkuyu, ndi Chakwera musatiputsitse apa.
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 3 месяца назад
Mwamasukatu mpaka zikhulupiliro zosakhala bwino? Globe vaccine akukupatsani thandizowo ndi ayesu? OK.
@victorauwana7258
@victorauwana7258 3 месяца назад
Ziko la Malawi lakwanisa zaka 60 pokweza pasogolo umphawi wathu
@LamieTiger-ff7cj
@LamieTiger-ff7cj 3 месяца назад
Chakwera mukanangot kukhala Za satanic metsa inu ndi satana
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 3 месяца назад
Agalu kumkuyu mapwala ako
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck 3 месяца назад
Bodza limenero manyazi achakwera
@yusufbakali
@yusufbakali 3 месяца назад
Kukhuyu zikhare chimwendo chakwela osewa adyeretu chaka chamawa chawoo palibe anthu tinavota kare kufa kwa chilima
@Chayibujackison
@Chayibujackison 3 месяца назад
Ife tikufuna bon kalindo mawa atulusidwe
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 3 месяца назад
Ngakhale atapanga zokoma bwanji a mcp kuphiphilitsa za imfa ya chilima even atati apereka nseu wot chilima road sadzawinabe awa.ndinu okupha okupha basi munapha nzanu mbili sizafufutika.
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 3 месяца назад
Ofufuza akhare a independent osati oziwana ndi mcp ai sipamveka black box ili kutiko choyamba?
@richardManemba
@richardManemba 3 месяца назад
Ayii akupangila kt ufulu wa amalawi uchoke km osalola kungolola bas zabwelela zakale
@chimwemwekamwana787
@chimwemwekamwana787 3 месяца назад
Mukuopa kut anthu akutukwanani.. nanga mmene mukuoneramu amalawi tili pa ufulu ifeeee.. ai muli ndi manyazi ndithu
@isaaczuze
@isaaczuze 3 месяца назад
Kunkuyu uzipemphela kwambili kuti boma lisasinthe ...boma kungosintha iwe uzafela kumdende ....unapha allan witika chifukwa cha mkazi .....munthu wopusa iwe kwambili mbuzi
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Mukut mulira maliro nanga chowangira anthu mukulira maliro ndi chan?
@AndrewMukhwapa-qj4vo
@AndrewMukhwapa-qj4vo 3 месяца назад
Very good a Chihana
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 3 месяца назад
Iwe mukuyu matako yako wapulika chakwel nayo pathako pake
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 3 месяца назад
Akuopa kuti akakuwidwa ku 6 July 😂😂😂😂 mwabalalika makape
@inamrigala
@inamrigala 3 месяца назад
Muvesen akunena ufulu obela a malawi galuyu okukuda kukeqma
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 3 месяца назад
Stupid you guys in chakwera team Mwapha chilima anthu inu mukukayankhula zautsiru
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 3 месяца назад
Koma kachere anachulukitsa kulibe dzina lina
@DennisDonework
@DennisDonework 3 месяца назад
Afiti inu palibe ufulu nanga born kalindo akutani ku selo
@ALLIEDAUDI
@ALLIEDAUDI 3 месяца назад
Inu nosenu ndinu agalu kwabasi ifetu tikungo funa kuti bon Kalindo wathuyo tipaseni achainiyakefe
@RichardTuluka
@RichardTuluka 3 месяца назад
Ufulu wake utiwo
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 3 месяца назад
Opemphera ake ndani zigawenga inu?
@MikeTwaibu-i1h
@MikeTwaibu-i1h 3 месяца назад
Ma billion chikondwererowo nde tigawanepotu sizausiru apa
@BlestoneJonas
@BlestoneJonas 3 месяца назад
Kunkuyu udzinena kuti presdent wakoyo wanena kuti osati walamula ai
@RamseyMkwaira
@RamseyMkwaira 3 месяца назад
Inunso mukuziziwa zimenezo
@isaaczuze
@isaaczuze 3 месяца назад
Mulila bwanji poti mwachita kumupha chilima koma ndizokhumudwisa kwambili
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 3 месяца назад
Wanena zoona chihana
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 3 месяца назад
Akuti muli wufulu m'malawi zoona
@TwayibuChimbama
@TwayibuChimbama 3 месяца назад
Kusilamulila kwake kopa anthu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
Dzaka 60 yoh bwanji dziko lili paumphawi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 shame
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 3 месяца назад
Mafumu opusa kuyamikila katemela kusiya chakudta
@FionaKhoma
@FionaKhoma 3 месяца назад
Masiran born kalindo kaye mukubisa chan pomumanga iyeyo
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 3 месяца назад
Following
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 3 месяца назад
Mufika kumeneko nonsenu kumeneko za chamba 6 July muzakhalamulibe moyo inu agalu eti mboloyako
@yusufbakali
@yusufbakali 3 месяца назад
Mbudzi iwe
@ThomasMunyolowa
@ThomasMunyolowa 3 месяца назад
Osati kuopa ku kuwizidwa
@JimmyMhango-d5n
@JimmyMhango-d5n 3 месяца назад
Chakwera ndiwe mbuzi wamva , galu , nyani chittsru cha munthu
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 3 месяца назад
Iwe kumkuyu ndiiwe mbuz et ufulu wake ulikut popeza mungomanga aliyese brushit zako
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад
Zaziiii
@louisgolden
@louisgolden 3 месяца назад
Kodi July yili Liti Koti muyambe kunena Za 6 July
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 3 месяца назад
Anthu tili ndi mafunso kumene
@ClementMinyanga
@ClementMinyanga 3 месяца назад
Ufulu wake ulikut???
@chrisboyce2
@chrisboyce2 3 месяца назад
Simbi ya moto Mr Chihana 🔥🔥🔥
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 3 месяца назад
Kulibe ufulu ku malawi mcp is fokolo
@isaaczuze
@isaaczuze 3 месяца назад
Kunkuyu panyapako galu iwe
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 3 месяца назад
AChakwela ngt watopa nawo udindo yingotula pasi coz ukupanga chibwan
@MoosaSame
@MoosaSame 3 месяца назад
Mbolo zanu
@Sugerman-tw4do
@Sugerman-tw4do 3 месяца назад
Zopusainu
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy 3 месяца назад
A MCP mwadya zomwezo tiyen tionane 2025
@MosesMasambuka
@MosesMasambuka 3 месяца назад
I hate afana oganiza bhoo asiya Malawi Ali mavuto kmanso kupanda ufulu wa dimokalase
@IshmaelDouglas-j5i
@IshmaelDouglas-j5i 3 месяца назад
L0
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 3 месяца назад
Kalindo ndi galu yadpp ndiye pano tapumako koma anthu amene amangidwa wa akanene umboni pa yifa yachilima noti kutiazingobwebweta zaboza ayi
@rechealbracia-vk7np
@rechealbracia-vk7np 3 месяца назад
Pamtumbo pako ufulu ukupita iwe kukamwa mwiii suganiza za sogolo la ana ako galu iwe machende ako 😂😂
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Achisilu awa ,kalindotu amanena zoona
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 3 месяца назад
Olo ukususa cilungamo ukuciziwa kt mcp yapha cilima galu ndiwe
@goephreynuh6857
@goephreynuh6857 3 месяца назад
Iwe panyini pa mako kwambiri
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 3 месяца назад
Mbuzi yamunthu yoyenda mwamatama iku nyela... mwatumidwa ku mcp munya nanuso mutu ngati odzadza madzio ndi ufiti hiyaaa
@IshmaelDouglas-j5i
@IshmaelDouglas-j5i 3 месяца назад
L0😅
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 месяца назад
Iwowa mituyao sigwira kunkuyu ndi chakwera wakoyo ndinu mbuzi mukati ufulu odziramulira what do you mean? Momwe mukuyendetsera boma lero mukuona ngati dziko liri pa ufulu popeza muli busy kupha anthu komaso kumanga anthu omwe akukudzudzulani ndiye nkumati dziko liri pa ufulu inu agalu kwabasi zigawenga
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 3 месяца назад
Ufulu wake utiwo
@DorotyMussah
@DorotyMussah 3 месяца назад
A kunkuyu mzimu wa witika muli nao pamutupo
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 3 месяца назад
Akuna adzakondwerere kuti zomwe.amafuna zatheka pokupha chilima
@IshmaelDouglas-j5i
@IshmaelDouglas-j5i 3 месяца назад
Ol
@JamesOsman-cz9cw
@JamesOsman-cz9cw 3 месяца назад
Mcp people machende anu nonse
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 3 месяца назад
Iweyo Kumkuyu ndi Chakwera wakoyo God must punish you, Mukukamba za kukhudza Maliro a Dr Chilima chonsecho mukungotiphimba kumaso.
@mussakathumba128
@mussakathumba128 3 месяца назад
Komanotu kunena chilunga amalawife tikufatsa kwambiri plus ulemu too much.chakwera wationjeza akungopha anthu ngati khuku tinayenera kumuchotsa before mavoti
@MatiasChimsakasa
@MatiasChimsakasa 3 месяца назад
Komano bwanji anthu anasangalala polumbilitsa olemekezeka a vp koma 6jly ayi Kodi undiuthenga wanji mukupeleka kwa ife achinyamata
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 месяца назад
Muchoseko zaka 4 zomwe mwalamulilaz kulibe ufulu ndiye kt tili ndi zaka 56 xaufulu
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 3 месяца назад
Dzaka 60 za democracy minus 4 ya chakwela tikusangala dzaka 56 coz dzaka 4 za chakwela kulibe ufulu
@MisheckAselo
@MisheckAselo 3 месяца назад
Kodi ufulu ulikuti, ku malawi kulibe ufulu chifukwa achina kamulepo ndi kalindo mudawamanga chifukwa chomenyera ufuluo, komatu Boma ili litipweteka ndithu
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 3 месяца назад
Nanu tazingodurani nkhani zofunikirazo ndikumaponya apa osati ndi nkhani zopoira zomwe
@HeedsonJere
@HeedsonJere 3 месяца назад
Chihana anamumana udindo ku tonse allias
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 3 месяца назад
Mapemphero ake ati komanso abusa achokera mpingo uti Please leave God alone please
@GiftManuel-er7yh
@GiftManuel-er7yh 3 месяца назад
Amaio akunama mwana sangabadwe kutha miyedzi 6 asanamupitenao ku chipatala ku scale
@ShaliyaMusa
@ShaliyaMusa 3 месяца назад
Ndiwomwewo mfiti. Chikwelayo paribe kikna
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 3 месяца назад
Amene adzapite ku mapephero amenewo mutu wake suyenda bwino mwalo mopangitsa mapephero olapa mudzikapephera chani Mulungu akamva zimenezo magazi akuyenda Malawi mo simukuwawona, mwazi wa anthu osalakwa ukufuulawo simukuoona mapephero achani mudziwerenga bible before kuchita zithu za ziiii mudzikapha Ana azanu ngati khuku mtendere simudzaupeza mpaka mutabwera poyera kulula
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 3 месяца назад
Sure
@dysonfysonchifundo2284
@dysonfysonchifundo2284 3 месяца назад
Ndipo ofufudza sakuyenera kuitanidwa kuchoka ku boma cos ndiwomwe analephela kupulumutsa anthu, in other way, boma ndilimwe lapha anthu
@josephchirwa-jt7jx
@josephchirwa-jt7jx 3 месяца назад
Kodi ku malawi kuliso ufulu?
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo 3 месяца назад
KOMA BOMA LA MCP 😢😢😢 AWA SI ANTHU KOMA AFITI ASATANIKI
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on 3 месяца назад
Or mpunga wa nyama tisadyenso?? 😢😢😢
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 месяца назад
Good Mr Chihana
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 3 месяца назад
Chakwera ndi lwe nkukuyu agalu nose mapemphera achani fiti lnu nose ndi manganya tikulira chilima wanthu lnu mumumasure bon kalindo ndi kamulepu boma lakhaza lri mwayiwara kt mupeze ma udindo ndi chilima nose 😢
@charlesvenacio9773
@charlesvenacio9773 3 месяца назад
Malawi muno mulibe umfulu
Далее
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA
10:10
Просмотров 255 тыс.