We know that you, Bakili Muluzi TV, are king of kings of history and whatever you report on Dr Chilima's death is true. May God bless and give you long live. May Chilima's soul rest in peace.
Thanks to to bakili muluzi tv.they are serious indeed to continue with sacrifice like they saidBut Malawi need to wake up.MCP must be canceled from Malawi as a politically
Bakili muluzi tv ubwino wake nkhan zanu sumangopeza ndipo zinthuzo zimaziyabkhulanso zokha zomwe Ainu akewo zimachokera mkamwa mawwo keep it up bakili muluzi tv
Ubwino waBakili muluzi tv ndiumenewu iye Lero sanayankhulepo koma tazionera tokha ndimaso zomwe zimakambidwa ndi a MCP akanganyawa zoona mission yawo adayamba 2022 Lero amugoneka mzawo mmmm only God knows 😭😭😭😭
Malawi is no longer Godfearing nation because our leaders in all sectors Lack philanthropy and patriotism. May God rebuild and guard Malawi against lucre minded spoilsports!
Ndipotu muona Ngati mwabisara Koma ili ndi dziko kwanzanuyu kwathaaa mwamupha Monga mwakufuna kwanu Koma dziwani Kuti God is watching and your day is coming àñthu ankhaza inu akupha mwazi ulipamitu panu