Amayiwa ndi amene anapangisa kuti a Malawi asakhulupilire azimayi pa maudindo osiyanasiyana Makamaka pa udindo wa pulezidenti Kumavera za azungu, Kuba ndalama za ndege a Malawi ali duuuuu..osafusako Kaya a Malawi anapangilidwa mankhwala Kaya?
Aliyense anali wabwino munthawi yake komanso woipa munthawi yake sakhala wabwino mu zonse. Mwachitsanzo bingu amene mukumunena kuti ndi wabwino, alipo ena amkamunyoza Ali mmoyo
He is the very first thief of a president of Malawi 🇲🇼 he went to London to donate money from Indians who were kicked out of Malawi 🇲🇼 by Kamuzu Banda because of corruption. He told them to give him £2,000 each to come back to Malawi 🇲🇼