Тёмный

COMRADE NTANYIWA - NANKHUMWA AKUFUNA ABWERERANSO KU DPP-WINA WAPITA NAYO LIMODZI WARRANT OF ARREST. 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 39 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

10 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 136   
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 дня назад
Nuff respect comrade ntanyix....you got no idear how much pple likes this channel
@osmaniwen2979
@osmaniwen2979 15 часов назад
Comrade Ntanyiwa Ur the One❤
@GiftMlinde
@GiftMlinde 2 дня назад
Greatt abweleleeee kumakhululukilanaaa
@AuphieBannet
@AuphieBannet 2 дня назад
Tili nanu ❤Mr. MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani nthawi zonse
@dalitson3558
@dalitson3558 2 дня назад
We need him back he’s good man, anthu amakhululikilana
@YusufuYunusuSavielMakey
@YusufuYunusuSavielMakey 2 дня назад
𝐮𝐤𝐮 𝐠𝐨𝐨𝐝 𝐦𝐚𝐧 𝐰𝐚𝐤𝐞 𝐨𝐭𝐚𝐧𝐢 𝐨𝐦𝐚𝐠𝐰𝐢𝐫𝐢𝐭𝐬𝐢𝐝𝐰𝐚 𝐧𝐭𝐜𝐡𝐢𝐭𝐨𝐰𝐨
@augustMag
@augustMag 2 дня назад
🔥🔥🔥🔥 Abwerenso ku DPP Tawalandira bwana Nankhumwa ndi wanthu wanthu amenewo🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤
@Fanie-i7z
@Fanie-i7z 2 дня назад
Ngati iwe ukuti anthu asamvere limpopo iwe amakutuma ndani kuti uzimvera ambiri timamukonda amatidziwitsa zobisika keep it up Mr. Mtanyiwa tikumvera pano pa Port Elizabeth RSA.
@SaulosMbuna
@SaulosMbuna 2 дня назад
Comrade osayamba kudzikaikira ayi...u are a real big boy..
@SolomonAmiduh-y6x
@SolomonAmiduh-y6x 2 дня назад
Anankhumwa welcome back ku dpp siyanani ndi chikangawa
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 дня назад
Comrade ntanyiwa fans let's gather here much love you do open our eyes always ❤️❤️❤️❤️
@KandawekoChirambo
@KandawekoChirambo 2 дня назад
Viva Limpopo Vivaaa
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 2 дня назад
Motooo kuti buuuuu Comrade, musatope, osagonja ndipo osafooka Mulungu ali nafe nthawi zonse Aaaah inuuu, kkk Ana achepa awa zayamba kuyang'ana kungolo mizimu ya anthu ochuluka munawapha osalakwa inu mumati
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
More fire comrade ntanyita osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka tituluke mukaporo tilinawo pano ndi boma ra crocodile
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Timakunyadira ntanyiwa,umakwana DPP oyeeee!
@MagretMakhumula
@MagretMakhumula 8 часов назад
Bravo nakhumwa go back that's we want
@BairdThomas-c2k
@BairdThomas-c2k 2 дня назад
mwana wolowerela nankhumwa timulandila
@WilisonWilliam-d9j
@WilisonWilliam-d9j 2 дня назад
❤❤ife waiting
@DCpangolin
@DCpangolin 2 дня назад
Asamulole ameneyu
@MonicaSteve-t5p
@MonicaSteve-t5p 2 дня назад
Bas abwelere wadziwa ubwino wa adad ❤❤
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 дня назад
Kondwani nankhumwa ngati akufuna kuti abwerere ku dpp ndakayika bola asakakhale spy wa mcp
@amosphakira7936
@amosphakira7936 2 дня назад
😎😎 Adawa amaitha 😅😅
@DadyPatrickMtondo
@DadyPatrickMtondo 2 дня назад
Because he knows that he won't be an MP again, writing is on the wall!!!!
@EmmyYafete
@EmmyYafete 2 дня назад
Abwerere palibe nvuto timulandila,kunkhululuka basi ndimasewera adziko lapasiwa.
@BilalAliyah-k1f
@BilalAliyah-k1f 2 дня назад
🤝
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug День назад
Yomweyo chikangawa iwe 🎉🎉🎉🎉🎉
@FredKanyerere
@FredKanyerere 2 дня назад
More fire comrade, zovetsa chisoni.
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 2 дня назад
Nkhondo ndi anasi anampereka yesu ndiwomwe amadya naye rimozi amene atapereke u t m mmanja mwa adani ndiwomwenso akuwoneka ngati abwino
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx 2 дня назад
Uyu ngat abwere ku dpp basi azatenga udindo 2030 serious boss Anakhumwa your welcome Mr Nakhumwa
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 2 дня назад
Asayelekeze kupita ku Pej house,, ndipo asayandikilane ndi Adad athu,, angawapopele poizon.. Amutuma ameneyo, siza straight zimenezo..
@Maickfoness
@Maickfoness 2 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma nanuso mukati mukomese
@CatherineDesire
@CatherineDesire День назад
Koma mtanyiwa mwana iwe mmmmh ndi Junior wa Blenac 🤣🤣🤣🤣🤣🙌yomweyo mtanyiwa
@MalickMkweche
@MalickMkweche 2 дня назад
Comrade ntanyiwa ifetu daily tikupemphera kuti mulungu amenye ekha mkhondo chifukwa zikoli ndilamulungu analenga ekha panalibe omuthandizira
@augustMag
@augustMag 2 дня назад
Tinakusowani bwana mtanyiwa ❤❤
@JamesLongwe-qz9fd
@JamesLongwe-qz9fd 2 дня назад
Mukhululukireni munthuyo abwelere kunyumba kwake
@VincentKalata
@VincentKalata День назад
Kkkkkk apapa ndye Ntanyiwa wabweladiieee
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes 2 дня назад
Vuto la nankhumwa ukazitape usankhulupilirika
@TrevorDyer-z5h
@TrevorDyer-z5h День назад
Nankhumwa ndi nthira kuwili asamulole
@LonelyMkupa-v9v
@LonelyMkupa-v9v День назад
Safunakotu Nankhumwa ku DPP mungo zivuta anamuchosa akataniko
@BandahLemos
@BandahLemos 2 дня назад
Antanyiwa oyeeeee 🤣
@MerryWayson
@MerryWayson 2 дня назад
Asamulole kubwelera Nakhumwayo akudya ndalama za MCP ameneyo mapeto ake azipanga maboza akufuna akhale kazitape azizitenga ku DPP azipita nazo kwa anthu akuphao A MCP asalole AMuthalika please
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 День назад
Ndipo asamulole galu ameneyu
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 2 дня назад
Koma zoona zomwe munenazo a Ntanyiwa activist samsara wachipani,koma inuyo mumaonesa zoti mumasapota DPP ngati si UDF koma mbali yanu muli DPP
@AlinafeBanda-x2p
@AlinafeBanda-x2p 2 дня назад
More 🔥🔥🔥
@BettyByson-t4z
@BettyByson-t4z День назад
Nankhumwa ndiwe galu kwabasi ndi ulowera kuti😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 2 дня назад
Abwerere basi akondwani,,ngakhale mwana wolowerera atabwerera kwa atate analandilidwa mokondwera ,,,ambiritu abwerera
@TerezaJaenda
@TerezaJaenda 2 дня назад
tili pompa ifee ❤❤
@OssmanAbubaker-m5u
@OssmanAbubaker-m5u 2 дня назад
Ifeyotu timakudalirani musatisiyetu tokha brother timenyelereni nkhondo
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Ntanyiwa usatinamize ndiwe wa chipani Cha nkhalamba chija koma wauponda chifukwa nkhalamba yako ija siyizabwerelanso boma kwake kunatha
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 2 дня назад
Mukumveka bwino kuno ku south Africa
@IrvinLeo-y1n
@IrvinLeo-y1n 2 дня назад
Palibes mumakwan kugon osamv limpopo ndimadwal
@Felista-m4q
@Felista-m4q 2 дня назад
Abwerere bas kudiyana ndikut apite chipan chakupha
@LonelyMkupa-v9v
@LonelyMkupa-v9v 2 дня назад
Wanama Mwana waki sindi Nankhumwa ai ai
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Nanga nkhope ya peter muthalika
@Moses51
@Moses51 2 дня назад
Andu adamuyendela Padela
@AngolanChinga
@AngolanChinga 2 дня назад
Auze ntanyiwa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 дня назад
Ndipo ife a DPP sitingalole kuti nakhumwa abwelele akhoza kubwelela zolinga osati m, tendele ifeyo takana akhale ndi chikangawa party wakeyo
@NickSomba
@NickSomba День назад
Mulandileni koma mumpinye ku branch kapena ku constituency basi akayamve 1
@lungsTug
@lungsTug 2 дня назад
Apepetse basi akadekhe mwano ayi
@MikeLodzi
@MikeLodzi 2 дня назад
bwana mumatiimilila koma chonde kanyimboko kamatithela bundle
@AnniePetro
@AnniePetro 2 дня назад
Abwelere timulandira
@wezimwalebanda-ux4sm
@wezimwalebanda-ux4sm 2 дня назад
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 2 дня назад
Comrade ndikunva kukoma zedi Auzidwe basi.
@FunnyKatchenga
@FunnyKatchenga День назад
Nsalunso za DPP anazigulitsa che nankhuo😂😂😂.
@emilynthite6545
@emilynthite6545 2 дня назад
Asamulole nakhumwa kuti abwere ku dpp
@yassinn5634
@yassinn5634 2 дня назад
Activist amasapota DPP osangonena kuti ndi area governor wa DPP bwanji?
@floncejeche8647
@floncejeche8647 2 дня назад
Ntanyiwa kumadaso mbeeee iwe iwe
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 2 дня назад
Ulemu wanu
@johnnyirenda5848
@johnnyirenda5848 День назад
Kondwani Nankhumwa Akuchedwa nthabi ndi yemweyi Abwerere Azikagwira Ntchito limodzi ngati Ngwirizano Ndi Chipani Chake SI vuto ayi Ndi Ntendele
@HarryMsudzula
@HarryMsudzula 2 дня назад
Akaliyati sianthu olimba pandale that's the down fall yake ndipo asatibowe azivaya
@JohnMankhwala
@JohnMankhwala 2 дня назад
koma andale simuzamveseseka mpakana Yesi azabwela .
@Johnybegood260
@Johnybegood260 2 дня назад
This guy will only make you angry I hate MCP koma propaganda ya nkuluyi penapake ndima ndi munthu wama boza bola bon kalindo
@yassinn5634
@yassinn5634 2 дня назад
Inu mwamuona lero . Kungoti alibe ma source abwino amene angamampatse nkhani ndiye zambiri amangopeka. Kwakuti akulu akulu ena achipani chake cha DPP amanyasidwa naye.
@TrevorDyer-z5h
@TrevorDyer-z5h День назад
Ndiwabodza uyu akumuipitsa kaliati munthu oti ndiyemwe waigwila utm kuyambila pachiyambi
@Johnybegood260
@Johnybegood260 День назад
@@TrevorDyer-z5h ife utm timayikonda
@ERNESTOFERNANDO-sk5mb
@ERNESTOFERNANDO-sk5mb 2 дня назад
Ndipo ndineyo amene ndikazapepese Kwa APM ndikwathu uyu munthu salakwila ntengo
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Ntanyiwa machende ako pamozi ndi mayi ako chitsiru iwe ,machende amako
@andreabanda7838
@andreabanda7838 2 дня назад
Timasuleni pamenepo.
@PeterChima-s9u
@PeterChima-s9u День назад
inde inde
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 2 дня назад
Palibe osAlakwisa ngati wZindikila kulaksisa kwake kakhululukidwe, koma pofunika kuwonesesa ngat asali kazitape akulu wa mcp
@TrevorDyer-z5h
@TrevorDyer-z5h День назад
Mukufuna adzamalize chipani akabwera
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal 2 дня назад
Nankhumwa alibe chipongwe aaa abwere basi
@afana当二mtotera
@afana当二mtotera 11 часов назад
Umachulutsa akunama galu iwe ndi wa dpp usatinamize
@kaphika
@kaphika День назад
Comrade wa DPP uyu, aziti alibe chipani.
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 2 дня назад
Galu iwe wa Limpopo machende ako chaka chonse ndi onse okusapota
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 День назад
Ubwino wake enafe tilibe machendewo koma timamusapota koophya
@CollinsMwale-l4p
@CollinsMwale-l4p 2 дня назад
Asabwerere ai ndiwowombanisa
@Noel-r8u
@Noel-r8u 2 дня назад
Nankhumwa mbuzi yamunthu
@KettieNathaya
@KettieNathaya 2 дня назад
A Kondwani twkulandilan kuno ku DPP koma osabwerelw ukazitape muno ayi
@christopherMacheso
@christopherMacheso 2 дня назад
Akabwera azakhala munthu wamva eti?
@DoreenBanda-hg7oe
@DoreenBanda-hg7oe 2 дня назад
Abwerere wadziwa kulakwa alibe
@AngellaAnge-p7x
@AngellaAnge-p7x День назад
Asamulole nankhumwa kubwelera ku DPP Njoka imeneyo
@MynessChirwa
@MynessChirwa 2 дня назад
Abwerere zitha kukhala bwino
@ShillahLawrence
@ShillahLawrence 2 дня назад
Ayenera kulandilidwa chifukwa ndi kwao
@AKMASEKO
@AKMASEKO День назад
Tumfuna mtsogoleri ngati wadziko la Bukinafanso munthu odziwa umphawi wawanthu osati ofuna kudzilemeletsa mmatumba mwawo
@FrazerKhoriyo
@FrazerKhoriyo 2 дня назад
Za ziiii
@CharieChristo
@CharieChristo 2 дня назад
Abwerele ndiolandiridwa
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 4 часа назад
Nakumwa osamulola ku dpp apite ku mcp ngwamavuto ochuluka uthila kuwili ameneyo
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 2 дня назад
We don't need him, he just showed us how an settled he is, ndale za nkodzo tatopa nazo, take us seriously, we are not going to stand and look anymore, malawi up, n do right thing
@EvanceGoliath
@EvanceGoliath 2 дня назад
Koma ntanyiwa titan kut chakwela achoke
@LuciusScott-h7b
@LuciusScott-h7b 2 дня назад
Abwere koma asiye chibwana
@MoreenMponda
@MoreenMponda 2 дня назад
Abwereko bas bola asabwereleko topola
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv 2 дня назад
Mundale mulibe udani
@MerryMphande
@MerryMphande День назад
Akhale konko mesa anapanga chipani chake
@MrMagombo
@MrMagombo День назад
A Nankhumwa asapitenso ku DPP. AKASOKONEZA.
@afana当二mtotera
@afana当二mtotera 11 часов назад
Koma udzinena zoona osati za manyizo
@GeofreyRhonard
@GeofreyRhonard 2 дня назад
Ndale ndi nkhondo
@BennieKanama-yr3sh
@BennieKanama-yr3sh День назад
1by 1 atha onsewa
Далее
Bro think he the MC.. 😂👊🔥
00:20
Просмотров 10 млн
Born Kalindo wa lero pa 11 October 2024
17:17
Просмотров 23 тыс.