Тёмный

DJ MUNYANANE AKUNG’ALURA LERO NDIPO KWAVUTA CHIFUKWA NDE YA MSONKHANO ILIMO UMU 

Malawi Trends TV
Подписаться 43 тыс.
Просмотров 4,2 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 50   
@LuciusScott-h7b
@LuciusScott-h7b 5 часов назад
Zowona mbwiyanga wamkulu ndiwamkulu more fire
@ChristopherChapeta
@ChristopherChapeta 5 часов назад
😊😊😊😊😊😅
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 4 часа назад
God z watching everything,,HE release us
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 2 часа назад
There was one minute silence in memory of the 8 died in chikangawa tragedy at Katoto freedom park.
@BoydchonthaniBanda
@BoydchonthaniBanda 4 часа назад
Nanga Iwo a MCP bwanji sanapite nawo a achewa a chikawa party
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 3 часа назад
Apm my vote kuti KHAA 2025
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 4 часа назад
Agalu okupha ana anjoka okupha awa more fire bra Kuti buuuu
@CatherineMunthali-r1f
@CatherineMunthali-r1f 5 часов назад
Alomwe ndekuti alipo 14 million
@SurprisedCells-ny6gx
@SurprisedCells-ny6gx 4 часа назад
Munyanane ndiwe munthu wankulu Awuzen agalu awa
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 5 часов назад
Mcp yayamba kupenga misala yakwiya ndi mizimu yomwe munaipha ku chikangawa ija munya muwona Mulungu akutsitsani anthu atsankho inu a Mcp Mulungu wakutembenuzirani msana wooooooooooh
@EnockMasiye-e4j
@EnockMasiye-e4j 4 часа назад
Tikunena Pano mwazi waenda pa i anthu aphana pa lord Brock ya pa 4 miles
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 3 часа назад
❤❤❤❤dpp moto
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 4 часа назад
Moto Kuti buuuu more 🔥🔥🔥💯 munyanane more fore we love u bra
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 3 часа назад
Zosangalasa zoona big man
@LloydMulauzih-g5s
@LloydMulauzih-g5s Час назад
Achewa Sanapite bwanji
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw Час назад
Umayitha boss
@EmanuelwakayKamangah-ch9cg
@EmanuelwakayKamangah-ch9cg 4 часа назад
Bingu my vote
@SiphoZungu-tt9iu
@SiphoZungu-tt9iu 6 часов назад
Ekwenden not embangweni
@SifatiMoses
@SifatiMoses 2 часа назад
Ndipo manyazi ake osowa polekeratu wakulu ndi wakulu basi.
@LindaMalikita
@LindaMalikita 4 часа назад
Ndipo zoona mawu aleloso kuchrch amatelo ozikweza azasisi ndipo ozichepesa azakweza ndye musamvutikanenawo achikangawa party mwazi wachilima ndianthu ena ukuwazuza. Iwo sunali sonkhano kunali show komaso show yake yolowa anthu onunkha kamawa onkhaonkha😅😅😅😅
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx 5 часов назад
Chimwendo milomo ngati katundu wa mvuu Peter sananyamuletu munthu anthu anawapedza komweko aziwoonatu chikagawa palibetso kuwina
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 4 часа назад
Yako ija munyanane
@ajasikalonga3210
@ajasikalonga3210 2 часа назад
Ben Longwe ndi kape
@AshimayeGama
@AshimayeGama 3 часа назад
Ndipo amapanga mademo atakhuta pano sakukhuta asangapange ma ndemo
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 5 часов назад
Richard amanunkha mukamwa
@OssmanAbubaker-c6o
@OssmanAbubaker-c6o 3 часа назад
Zoonadi DJ Munyanane timakunyadilani kwambiri mumatiyimilira APM ndi akatundu .MCP nthawi yanu yatha mumangidwa nonse 2025
@CatherineMunthali-r1f
@CatherineMunthali-r1f 5 часов назад
Ife sialomwe koma tikuti a Peter woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeè
@rashidadan2533
@rashidadan2533 5 часов назад
Tinene mobweleza , Avala za blue ndi a DPP akukambilana zachipani . Enawo avala zofiilawo mcp zigawenga zaku malawi za M,21 zikukambilana zokupha anthu
@SusanHara-l1t
@SusanHara-l1t 5 часов назад
Not at Embangweni, but at Ekwendeni (correction)
@SamNkhomo
@SamNkhomo 5 часов назад
Alomwe oyakhula chitumbuka
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t Час назад
MCP kubalalikatu anthu akupha
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu Час назад
☑️☑️☑️☑️☑️
@euninceChimombo-j5y
@euninceChimombo-j5y 4 часа назад
Yakwiya ndi mizimu
@SamNkhomo
@SamNkhomo 5 часов назад
Zachisoni ku MCP
@ChikondiChimwaza-i8l
@ChikondiChimwaza-i8l 3 часа назад
Akulira kkkkkk amalankhula chitumbuka aja anali alomwe,kkkkk aziona okha mesa Iwo ndi omwe ananyamula anthu ku Lilongwe
@SamNkhomo
@SamNkhomo 5 часов назад
Auzeni sakukhulupilila makape amenewa
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 часа назад
Satana alibe mphamvu yoposa ya allah , allah ndiwakhulu palibe achite, chachikulu tiike maduwa mapephelo palibe chosatekha, boma tikutenga tisaope
@GrecianWyson
@GrecianWyson 36 минут назад
❤❤❤
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 Час назад
Wa mcp unali ku ekwendeni not embangweni ayi
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 6 часов назад
Munyanane tawuzeni amenewo abeni longwe mbunzi yamunthu anya manyi
@mollymasangano473
@mollymasangano473 5 часов назад
Pamenepa pakupereka umboni kuti sanalowe Boma siyinali elections yachilungamo chifukwa chiyani akudzikayikira (kudzidabwa wokha kapena kuthuthum.ira .
@MartinDZOWA
@MartinDZOWA 4 часа назад
Mabodza manyazi osati alomwe
@MariamJaffali
@MariamJaffali 2 часа назад
Koma ndiye mcp ndichipani chamagazi ndithu
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 5 часов назад
Zoona
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 5 часов назад
Koma kapen ya chaka chino ikoma kwambil chikangawa ndiye mutu wakhan
@timothymhone2340
@timothymhone2340 2 часа назад
Alomwe alibe khalidwe kutukwana basi
@WinessMatcthuwana
@WinessMatcthuwana 6 часов назад
Zamanyazitu
@SamNkhomo
@SamNkhomo 5 часов назад
Satana ndiolephela
@MynessChirwa
@MynessChirwa Час назад
❤❤❤
Далее
Ромарио стал Ромой
00:46
Просмотров 448 тыс.
O’zim bilib ketvotudima😅
01:00
Просмотров 844 тыс.
Распаковка Monster High Potions #monsterhigh
01:00
TURKEY | A Muslim Superpower?
13:52
Просмотров 60 тыс.
A ENOCH CHIHANA KUYANKHA MAFUNSO
24:54
Просмотров 1,8 тыс.
Ромарио стал Ромой
00:46
Просмотров 448 тыс.