Тёмный

NKHANGA ZAONA MADZULO ANO MA PLAN A CHIMWENDO APHEDUKASO NDE KULI KUYALUKA 

Malawi Trends TV
Подписаться 43 тыс.
Просмотров 10 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 65   
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 23 часа назад
Chikangawa must go APM MY VOTE
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 23 часа назад
Awa kwawo kwata dpp❤❤❤ boma
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 23 часа назад
Big up Comrade Mtanyiwa
@traceflyton
@traceflyton 23 часа назад
big man inu ambuye azikutetezani nthawi zonse dithu
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 22 часа назад
God bless u a ntanyiwa❤❤❤
@SammieDickson-ln2hp
@SammieDickson-ln2hp 23 часа назад
Dpp woyeeeèee
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 22 часа назад
Apa ndiye ndigona bwino ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@AuphieBannet
@AuphieBannet 23 часа назад
Yamba kale kunjenjemela a MCP Yomweyoooo Limpooopo 😂
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 22 часа назад
Ntanyiwa Machine esh dolo kwambiri
@Atheeeefire
@Atheeeefire 21 час назад
Big man ntanyiwa respect
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 13 часов назад
Mizimu yawakwiyira Anya adziwona Mulungu sangatisiye tikubvutika APM woyeeeeeeeeeee❤❤❤
@TameeraInglis
@TameeraInglis 3 часа назад
Comrade Nthanyiwa you are protected by the blood of jesus ,psamls 27:3 Lingakhale gulu la ankhondo limange misasa kuti andithyole, mtima wathu sungachite mantha.
@serakillo8668
@serakillo8668 13 часов назад
Ine dzulo bp kushutar mpaka kulephera kungwira phoni apa eeeeh kumbali yathu tili bwino apa ndimwe tea my vote Apm.❤❤❤❤ khaaaa nkhaaaa manyazi chikangawa
@MandalaChaona
@MandalaChaona 18 часов назад
Chimwendoooooooo!!! Chakweraaaaaaaaa!!!! Chimwendooooooo!!! Chakweraaaaasaa!!!!! Munayiyamba yoti simuyimaliza, nanga ali Ku UNGA wo akaona sadzikodzera😂😂😂 any plans you do Chimwendooo you will never succeed,zayang'ana Ku dash board 😂😂😂 Wezi,Wezi zikutheka ndi The Commander Commarade aka Mtanyiwa " Man on the touch line" Stay blessed as usual 🙏 Stay safe as usual ✊ The true Freedom fighter ✊✊
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 22 часа назад
Chimutu ngati chidina achimwendo
@YankhoGuza
@YankhoGuza 22 часа назад
2025 DPP ikulowa basi chikangawa wanya basi naye nthawi ikubwera yoti azuzike
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 22 часа назад
Ndipo Chilima anamupha mopanda ma plan di zitsiru za anthu zokupha esh
@kettiemkweu4528
@kettiemkweu4528 21 час назад
Ipatseeeeeeeeee motoooooo😂😂😂😂🙏🤗🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@ulemunkhoma2867
@ulemunkhoma2867 22 часа назад
Wawa ndi we number one
@IssahNgalinje
@IssahNgalinje 23 часа назад
Tell me mr ntanyiwa what's going on the I'm here already
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 23 часа назад
Ufiti wa Richard fumbi la zinyau
@stevenwatch126
@stevenwatch126 23 часа назад
❤❤❤❤❤❤
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 14 часов назад
APM DPP my vote
@lyiemax
@lyiemax 12 часов назад
Ana achepa MCP singamake, 2025 DPP Boma!!!!. Forward ever and backward never ❤❤❤
@JasperKaleni-dx6nn
@JasperKaleni-dx6nn 13 часов назад
😂😂😂😂😂😂😂😂apm my vote
@MatthewLameck
@MatthewLameck 21 час назад
Koma mtanyiwa ulindi mtopola😅😅😅😅😅 mpaka yehomva mbusa wanga ndilibe kusowa😅😅😅😅
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 23 часа назад
😂😂😂 mumakwana ntanyiwa more fire
@DigleDafter
@DigleDafter 22 часа назад
Chikangawa ndege inagwa bwanji 😂😂😂😂wina agwa ndi BP 😂😂😂
@MussahJenala
@MussahJenala 20 часов назад
Salute
@DoreenLivata
@DoreenLivata 23 часа назад
Chimwendo ayaluka nthawi yake ndiinoi umva kuwawa
@CadTafa2
@CadTafa2 22 часа назад
DPP boma
@fedson2050
@fedson2050 23 часа назад
God is in control.
@violetpotani
@violetpotani 8 часов назад
Mumuwuze chimwendo yo mutu ngati bokho😅😅😅ati kumenya kugwetsa ife tanyenyanyenya
@KennedyKanyama-ce8lb
@KennedyKanyama-ce8lb 23 часа назад
Achimwendo mukundimvetsa chisoni kwabas. Kkkkkk kkkkkk kkkkkk kkkkkkkkk muthu akamafa amayamba mapilikaniro kukhotha ndue ameneyu mulekeni. Vuto siyeyo koma umphawi.
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 5 часов назад
Ana achepa awa DPP woooyeee more 🔥🔥
@KellyMemba
@KellyMemba 9 часов назад
Kkkkk km kumeneko more fire
@ChimwemweSauka
@ChimwemweSauka 2 часа назад
Wosalandira ndalama za magazizo malume.
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki 22 часа назад
Lichadi mutu wawukulo
@JulietMunthali-g9b
@JulietMunthali-g9b 11 часов назад
Big mistake indeed kupha SKC amawonangati athananaxo ndepanotu mwasegula khomo adadi alowe nyumba mwawo kkkkllll
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 23 часа назад
Chinyau chochedwa Richard Chimwendo kkkkkk
@MatthewLameck
@MatthewLameck 21 час назад
Ulendo wina tikachitila kwawo koko sokhano akazinyela yekha
@EverlantNdeule-w6t
@EverlantNdeule-w6t 10 часов назад
🔥🔥🔥
@AubreyMatress
@AubreyMatress 12 часов назад
Chikangawa party music show😂😂😂, kulira kuti pyoo pyoo_ adad anena kut sanati awona nyekhwe kukubwera zinthutu ku DPP. Ine wakwa nyau komweko koma vote yanga ndi APM
@LovemoreJeremia
@LovemoreJeremia 22 часа назад
Anaimba nyimbo ikumveka mpasiyi adaimba ndani please
@PhiripChinkango-k5p
@PhiripChinkango-k5p 9 часов назад
Umakwana iweyo comrade ntanyiwa
@PreciousChlima
@PreciousChlima 22 часа назад
A mcp kkkkkk inali ku show ya
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 12 часов назад
asiyene awa asanene chilungamo Koma Choti aziwe chakuti achimwendo olo asanene chilungamo Koma thawi izakwana olo mufune musafune mudziwe Kuti muli ndimulandu ndiamalawi ayemcp mudziwe dzimenedzo
@wisdomblack-u8n
@wisdomblack-u8n 13 часов назад
APM BOMA
@FlorenceNkhata-f5l
@FlorenceNkhata-f5l 7 часов назад
Anapanga mistake yoipa kwambiri anaganiza ngati si anthu akulu akulu
@ShayibuJames-xc8il
@ShayibuJames-xc8il 22 часа назад
Koma kunena zoona antanyiwa ineyo ndimakuvetsani paliponse koma dpp apapa yayamba bwino ndipo tsogolo likuoneka chonde chonde pangani program yawo a dpp anene kuti mavuto awo aja akozabwanji malawi trends tv chonde aempheni antanyiwa awauze a dpp atiuze kakonzedwe kawo kokoza malawi anene kuti anene akoza bwanji mavuto awo chifukwa malawi mmmmhh ayi adasiya kukoma izizi zikuzuzitsa ife akumudzi
@PempheroAlli-v8y
@PempheroAlli-v8y 20 часов назад
Next year onse awochedwe oyamba akhale chimwendo ukumulemera ndi mutu wakewo
@idenmkumba-q8j
@idenmkumba-q8j 12 часов назад
Auzeni kuti ndalamazo akapeleke kumachinga komwe anthu akudya chitedze kuja
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 22 часа назад
Emen
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 20 часов назад
Kodi inu muzingokhalira za chiwembu basi?koma ndinu zisiru eti?
@lingsonmitunda293
@lingsonmitunda293 21 час назад
Richard Chimwendo ndi kape weni weni
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 22 часа назад
Komandiye.akuliratu
@MatthewLameck
@MatthewLameck 21 час назад
Wina azinyela ndithu
@EnerstManess
@EnerstManess 23 часа назад
Comred wayiwalatu kuna kugawa ma 2pnso kut anthu apite ku music show
@RoseThindwa
@RoseThindwa 21 час назад
Shame on you chikangawa party kuonjeza kuchuka pazinthu zoipa
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 21 час назад
Kmsotu anthu anali kumenekuja achita kubwela nawo kuchokela kwawo osati akokuja 😂😂😂 APM BOMA bas 2025
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki 22 часа назад
Km mcp aaaaaa mitu yawo sigwila chito
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 3 часа назад
Muli chi tchito guys
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 17 часов назад
Chimwendo banda nachimutu sumakuremera mutu wakowo bwanji pano ndi mbuyako chikangawayo thawi yanu yatha munapanga big mistake to kill 9 people in plane so now your time is going to end for show will be know mcp next year mcp what you know only killing people like fish prepare to go for good chikangawa team
@AlickJinamu
@AlickJinamu 21 час назад
❤❤❤❤
Далее
DPP ndi Comrade Timothy Mtambo agwirizana.
1:31
Просмотров 22 тыс.
A ENOCH CHIHANA KUYANKHA MAFUNSO
24:54
Просмотров 2,7 тыс.