Тёмный

Dr Bingu Wa Mutharika best advice to malawians; Malangizo a Bingu kupita kwa amalawi. 

Bakili Muluzi TV
Подписаться 114 тыс.
Просмотров 61 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

31 май 2022

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 70   
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj Месяц назад
Anthu abwino sakhalisa paxiko I remember you Bingu Mtharika I miss your voice and incouge
@Slyvester-zs6ww
@Slyvester-zs6ww Месяц назад
M'dima sumadziwa kut kuwala kuli pomwepo. This man, anali muongoli wa dziko lino la malawi. Koma dziko silinadziwe.
@selectorbillbox3505
@selectorbillbox3505 2 года назад
ZIMANGOONA KUVUTA BUT THIS MAN USED TO INSPIRE ME A LOT MAY YOUR SOUL CONTINUE RESTING IN PEACE WISE TALKING
@chisomombeta6446
@chisomombeta6446 7 месяцев назад
Ulemelero wa malawi unachoka basi ....Bingu was q blessing and special gift to us malawians koma tinali mu m'dima.May forgive our country and give us someone like him😮
@sakingomane5819
@sakingomane5819 2 года назад
He was best President ever in our loved country Malawi
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
0
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
O
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
0
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
0
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
O
@seanmsutu6848
@seanmsutu6848 Год назад
This was a real man to govern Malawi
@brinokasekani7295
@brinokasekani7295 2 года назад
We lost such a great and visionary leader in him. May you still continue resting well Pro Bingu Wa Muthalika
@brinobota6637
@brinobota6637 26 дней назад
The best president ever in Malawi, continue resting in peace Pro Bingu Wa Munthali. It's my prayer that God should give us a wise n strong president
@bobkenneth2947
@bobkenneth2947 Год назад
I will mourn and celebrate Bingu Wa Mutharika for the rest of my life he was a good and wise president..RIP MY PRESIDENT.
@tingo3155
@tingo3155 Год назад
I'm one of a Malawian who was inspired by Bingu, May his soul continue to rest in peace
@AlexisKantondo
@AlexisKantondo 7 месяцев назад
We're still crying for you late Genius Bingu
@ririvilla1423
@ririvilla1423 Год назад
True leader we miss u
@aaronkachipeso3586
@aaronkachipeso3586 2 года назад
Kuno chomwe amadziwa atolankhani ndikufalitsa zoipa zokhazokha osati zabwino kkkkkkk apapa am glad kuti Bingu anawatsukuluza hvy And ichi ndichidziwitso chimodzi kuti atolankhaniso nawo ali patsogolo pakubwezeretsa chitukuko cha dziko lino pa mmbuyo. mutha kudabwa inu kwaona atolankhani omwewo lero akumutamanda Bingu kuti anali mtsogoleri wabwino
@xanderotc
@xanderotc 2 года назад
We had a true leader. Honest and caring character.
@robertnyasulu1384
@robertnyasulu1384 Год назад
Ndinadziwa how great he was atamwalira. You the best president we ever had
@goodwellchanunkha1971
@goodwellchanunkha1971 2 года назад
A leader with fatherly heart and love. Keep resting easy ngwazi
@bilali869
@bilali869 Год назад
great leader ever n ever
@dominicmphepo-jk8lk
@dominicmphepo-jk8lk 7 месяцев назад
We had genius But God love him most Keep on resting well our hero
@jevamchitakupha
@jevamchitakupha Месяц назад
God choose the best
@williamdaisithom5913
@williamdaisithom5913 2 года назад
Good speech that people with good confidence will follow it forever, he died for body only but spirit for him still alive. Your body rest in peace almighty name of Jesus Christ Amen 🕊📖.............✍
@user-zq1oz9of7s
@user-zq1oz9of7s 12 дней назад
Vito loti mumayamikira munthu Akachoka He was Give the right path for development and mwadala tinampereka uyu
@benjaminkampiyon1130
@benjaminkampiyon1130 2 года назад
This dude was genius indeed
@imranmposa2788
@imranmposa2788 2 года назад
That was the best advice from bingu
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 2 года назад
We miss our best president ever In Malawi 🇲🇼
@michealmussah261
@michealmussah261 Год назад
We really miss him now
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 11 месяцев назад
I miss this president and we've never had a president like Bingu wa Mutharika and we'll never have a president like Dr Bingu wa Mutharika in Malawi
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Год назад
Amalawi Amapangirana Nsanje Mpaka zaka Zino, Ndimaopa Kupanga Associate Ndi Amalawi Anzanga. Amalawi Ndinu anthu oipa kwambili
@osamabinraden9391
@osamabinraden9391 2 года назад
Awa ndiwo mawu amawi amalawi kaduka basi chomwe timadziwa😁😁👍
@louisbonongwe4864
@louisbonongwe4864 2 года назад
We lost such a great Leader
@WiseJordan-ds6km
@WiseJordan-ds6km Месяц назад
Marvelous
@RICHARDA.Y.SAKALI
@RICHARDA.Y.SAKALI Месяц назад
l proud of speeches of this formar president.Rest in peace boss.
@sab311
@sab311 Год назад
On point
@hendrixkaitano4242
@hendrixkaitano4242 2 года назад
Wiseman
@hopeskafumbiphiri6011
@hopeskafumbiphiri6011 Год назад
wow ine kumva kukoma
@kassimjummah3018
@kassimjummah3018 2 года назад
Abingu muwuse muntendele 😭😭😭😭
@glorytchezan5157
@glorytchezan5157 2 года назад
Rest well Mr bingu
@owenmalongo4116
@owenmalongo4116 Год назад
Only the one and the best president in our country anaphuladi dziko pamoto may continue rest in peace 😭😭😭
@user-ux6cw2gq2n
@user-ux6cw2gq2n 4 месяца назад
We will never to forget sir🙏🙏🙏🙏🙏💔
@chrismakhela7133
@chrismakhela7133 Год назад
We loss ...RIP Father Muthalika
@allanmakwiti5145
@allanmakwiti5145 2 года назад
Inu aBakili News Channel mukuamva malangizowo?
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 2 года назад
Zinali Mbubzi za aKAZITAPE.
@FatimaMwanyali
@FatimaMwanyali Месяц назад
Kodi jelouse mupita nayo kit? ❤❤❤❤❤
@user-ne9qn5nm9d
@user-ne9qn5nm9d 10 месяцев назад
Inuyo Munali Tate weniweni, Rest in peace
@levisonmthawanji4232
@levisonmthawanji4232 2 года назад
RIP
@aubreychuma5449
@aubreychuma5449 2 года назад
Madala kuyionera patali game
@longimtimabii1017
@longimtimabii1017 5 месяцев назад
Sunga yelekeze ndi manyi ali lelowa.awa anali wakulu
@ibrahimjim281
@ibrahimjim281 2 года назад
Munthuyu amaona kut akumutaisa nthawi 😂😂
@anifoiuene6301
@anifoiuene6301 2 года назад
Takutoperani a MCP
@elufedavid3788
@elufedavid3788 2 года назад
Tavelani malangidzo
@aaronkachipeso3586
@aaronkachipeso3586 2 года назад
@@elufedavid3788 ndipo ugalu wakesotu nde winawina nanga zugwirizana bwanji ndi MCP apa? Uchimidzi
@user-ig7dv8rp7r
@user-ig7dv8rp7r 5 месяцев назад
Anali tate wa nfuko
@innocentmanyera1861
@innocentmanyera1861 Год назад
Wa dpp iwe hiyaaa
@anoldkapolo4493
@anoldkapolo4493 Год назад
Mzimu wake uziusa mumtendere osatha munthu oyipa uyu mafuta atavuta mkumati kagone pamsewu. Aaah kunapita mfiti
@peteruko
@peteruko 2 года назад
Am dying 😂🤣
@leviticusbonfancio
@leviticusbonfancio 8 месяцев назад
Awa adali am'dala bambo
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 Год назад
I like Donald Trump's stand on CNN, He calls them fake news kkkkk
@enockthomasloyidi4914
@enockthomasloyidi4914 2 года назад
🤣🤣🤣🤣
@gastahlubi
@gastahlubi 2 года назад
ndine wa mcp koma pa bingu hmmm zinali nkhani zina mpaka 2009 mutu wanga unapenga bingu ngati anatumidwa ndi ambuye kudzatilamulira moti pazoipa zake zimene anthu amanena ine ndimaziika m'manja mwa mulungu coz satana anakwanitsa gawo lake kutitseka maso ndikumadana ndi utsogoleri wangilo
@gastahlubi
@gastahlubi 2 года назад
koma osati zinazi kungoonjezela kuipitsa mbili yake koma sindikukhulupira kudzaonaso tsogoleri ngati ameneyu ngakhale kamuzu sangafike pamzelu zake rest in piece baba
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 Год назад
Tulukani Mcp man mutaya nthawi
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 10 месяцев назад
Zooonadi zokhazokha satana ndiwochenjera koma pomaliza💔💔
@imaanasibu7267
@imaanasibu7267 2 года назад
Wiseman
@amoschilimba4377
@amoschilimba4377 Год назад
Nthito za manja ake ndio nkhani lero Anasiya zonse phazi ndi mulomo Mzimu wake ukuusa ndi mtendere
Далее
KU MCP KUSAMBWAZANA ZAMASEWERA AYI 🔥🔥🔥🔥
24:59
СМОТРИМ YOUTUBE В МАЙНКРАФТЕ
00:34
Просмотров 977 тыс.
TILI PANO NDI PA MALIRO
3:47
Просмотров 160 тыс.
Bingu from Perth & Asia Part 8 - Press Questions 1
13:21
Mkangano wa Lucius Banda ndi Bingu
13:20
Просмотров 150 тыс.
BAKILI MULUZI KUCHEZA NDI BRIAN BANDA 11/05/2024.
58:38