Тёмный

Mkangano wa Lucius Banda ndi Bingu 

Sam Malvitha
Подписаться 86 тыс.
Просмотров 172 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

30 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 150   
@sammalvitha
@sammalvitha 7 месяцев назад
Remember to subscribe ❤
@werlemsitima
@werlemsitima 7 месяцев назад
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 7 месяцев назад
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 7 месяцев назад
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 7 месяцев назад
😊
@twenage
@twenage 3 месяца назад
Q😊😊q​@@werlemsitima
@DeboraNembele-ri3bh
@DeboraNembele-ri3bh 7 месяцев назад
Freedom fighter anali Evison Matafare oyamba komanso osiriza anthu opanga za person siabwino nthawi zonse
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 4 месяца назад
Inu ndi anthu aja okonda munthu ukufaaaa
@giddymarley112
@giddymarley112 7 месяцев назад
Bingu nd great man. Amaona patali. Malawi pano akuvutika coz Bingu sanamalize tym yake
@JamesjamesJames-w3l
@JamesjamesJames-w3l 2 месяца назад
Lucius banda sanali munthu wa freedom fighter Malawi koma freedom fighter wozipezela chuma yekha
@HandyChipets
@HandyChipets 2 месяца назад
Not 1997 but after the UDF convention in 1994 at NRC Bingu made his UP.
@chiefjusticie
@chiefjusticie 7 месяцев назад
Lucia's Banda anayesesa mokwanila kutimenyela khondo ndipo oyimba ambiliwa akutchuka chifukwa cha iye he is bg boss
@davidwakhokamoto1124
@davidwakhokamoto1124 7 месяцев назад
I hate Lucius Banda ndipo ndiwadyera kwambiri amkagofuna kumamudyera bingu nde ataona kut bingu simuthu oti akhoza kumupusisa ayi
@franciskameko2586
@franciskameko2586 7 месяцев назад
Si wabwino Lucius Banda
@nysonzeperiana9869
@nysonzeperiana9869 7 месяцев назад
Munthu oipa uyu ndiokonda ndalama nthaw amadana bdi bingu chifukwa samaonapo cholowa...ngati ali munthu osaopa why now ogokhala or nyimbo kuimba ..sakuona anthu kuti akuzuzika
@simphiwenyirenda2392
@simphiwenyirenda2392 Месяц назад
Za dziko lapansi ndizovuta...lero ndi mbiri..rest well legends.
@patricgama4788
@patricgama4788 7 месяцев назад
ali biz kuba ndalama dza boma ndi mcp iweso masu mutu wako sugwila ncthito iwe ungamayamikile galuyu
@MoosaSame
@MoosaSame 7 месяцев назад
Ndie ngat siwantha bwanji relo asalakhula namapwalayu alikut
@che-dandamaleta361
@che-dandamaleta361 2 месяца назад
Aaaaaaa!
@Ghama-k4i
@Ghama-k4i 2 месяца назад
Koma ngat uziopa kutchula zomwe ukuziwa bola usamapange
@DAVIESMDIMBA-ob9vq
@DAVIESMDIMBA-ob9vq Месяц назад
He mentioned Bingu wa Munthalika in his song called Ndisiyileni kanga
@BushiriliveTV
@BushiriliveTV 7 месяцев назад
Lucias Banda ndi wadyera komanso munthu waziphuphu kwambiri amayendera MSCE yabodza cholinga chofuna kulemera, pano siuyu aChakwala ampasa mpando wakhala pheee
@forbesslemusani3601
@forbesslemusani3601 Месяц назад
Mumaitha bwana ndipo mwafotokoza moveka bwino.
@franciskameko2586
@franciskameko2586 7 месяцев назад
Lucius Banda munthu woipa kwambri but he's a pretender ngat ndwa bhobho
@FredodHawadi
@FredodHawadi 7 месяцев назад
Zowona zake waononga anthu ambiri galu ameneyi🤔😢
@FredodHawadi
@FredodHawadi 7 месяцев назад
Ndy Pano akuti chani agalu okonda ku dyesa mimba zawo😢
@NzeruDesign-ut1go
@NzeruDesign-ut1go 7 месяцев назад
Mot uzingofotokoza apa ndye ukuopa zchan?
@ChrispinKaundama
@ChrispinKaundama Месяц назад
Bingu amadya mkaz wa soja
@mathewstembo1778
@mathewstembo1778 2 месяца назад
So far so good
@jamessaiti
@jamessaiti 7 месяцев назад
Pano anampasa bazi ameneyo
@patricgama4788
@patricgama4788 7 месяцев назад
amadana ndi chilungamo wautsilu ananga pano akuti chani ku mcp chifukwa ampasa mpando kumalawi balibe amene angaipitse bungu
@MoosaSame
@MoosaSame 7 месяцев назад
N hate Lucius munthu woipa kwambiri
@SamSinoya
@SamSinoya 27 дней назад
Zanziko lapansi izi
@MartinLuther-o2z
@MartinLuther-o2z 7 месяцев назад
Pano zikumuvuta pati kuzuzura Boma la mcp
@AmadumtungasudiSudimtungaamadu
@AmadumtungasudiSudimtungaamadu Месяц назад
Ky zaw izo aona kt atan😂😂
@mosesharoldngolombe
@mosesharoldngolombe 7 месяцев назад
Pano zinthu nde zikuyenda bwino? Ali kuti nanga bwanawa 😂😂😂
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 7 месяцев назад
Achitsiru aja
@MackKalilombe
@MackKalilombe 8 дней назад
Malawi
@ClementKampaka
@ClementKampaka 7 месяцев назад
Kudali Billy kaunda yemwe adalimbana ndi bakili kapena mudali muli ana
@MoosaSame
@MoosaSame 7 месяцев назад
Munthu wadyera uyu galu
@madalitsochabwera5903
@madalitsochabwera5903 7 месяцев назад
Ndisiyireni ena amati amanena Mulli kaya kkkk
@mosesharoldngolombe
@mosesharoldngolombe 7 месяцев назад
Ineso namva chomcho
@maggiekamphinda5699
@maggiekamphinda5699 7 месяцев назад
Muli ankayenda ndi ndani Mlaka ndi bernadetter?
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 7 месяцев назад
Mmmmmm lusius wakupha uyu anapha oyimba azake ambiri ATI asachuke kuposela iye
@chiefjusticie
@chiefjusticie 7 месяцев назад
No mukulakwisa mukatelo kod mayiko enawa anthu samafa nakha anthu ena osayimba ndipo sanatchuke komwe anthu akumuzi samafa ndi infa za m'zizizi munganene kuti ndi bwana Lucia's Banda. No come on guys let's us learn to respect our favorite artist from our country because if we could no palibe Munthu yemwe angawalemekeze
@zionekanjoka7575
@zionekanjoka7575 7 месяцев назад
Mmmmmm
@Ndendendlovu
@Ndendendlovu 7 месяцев назад
Uyu ndigalu wadyela
@kingwaltermdezo
@kingwaltermdezo 2 месяца назад
My opinion Lucius sanakhalepo freedom fighter, unali chabe mukwiyo after bingu kuchoka ku UDF plus ma personal issues awo. Uyu kumapetoku atapasidwa udindo anangoti ziii kumanyambita misonkho ya amalawi
@CharityChinoko
@CharityChinoko 2 месяца назад
Lucius tikukulira ife amalawi
@SurprisedDrumKit-ql7rj
@SurprisedDrumKit-ql7rj 7 месяцев назад
Boss apa ndie meatinamiza zoti Lucius dagulidwazo mmm
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Месяц назад
Banda anali kape dissed nsanje port calling it dziwe la mng'ona....bingu was genius
@NicholasKwajama
@NicholasKwajama 7 месяцев назад
Mukutiwuza zinthu zoti tikudzidziwa kuposa inunso
@ZahirZaheer-h3d
@ZahirZaheer-h3d 7 месяцев назад
Don’t talk lies now
@edinabornface
@edinabornface 2 месяца назад
Iwe ukukana kung'alula chifukwa choti ulibe lawyer nde ife tipange suggest lawyer timutenga kutu?
@ArexBright
@ArexBright 3 месяца назад
Sorry wapita mwachangu coz timadikila kt ayibe nyimbo mubo lilipoli koma ay zidko limatha bas kulimbanila nkazi kaya zichani tilibe nazo ntchito koma ife tingoti abuye wayakha bas RIP BINGU MUTHALIKA
@MrChimtengo
@MrChimtengo 2 месяца назад
Lucius anali wadyera amadana ndi bingu chifukwa sanamupasa mpando,
@KikaImran
@KikaImran 2 месяца назад
Sukutchula maina ndie chomatizuzir kumvera nchiyani?
@MarthaKhumbanyiwa
@MarthaKhumbanyiwa Месяц назад
Likw
@AlexKaunda-x3p
@AlexKaunda-x3p 7 месяцев назад
Pano bwanji wangoumba mlomo akuziwa kuti chakwera amudula machende
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 7 месяцев назад
Sam mavitha umakhwana
@giftjimu6685
@giftjimu6685 2 месяца назад
Lucius anali osokonedza komanso wadyera, amalimbana ndi boma lomwe sakupindula kanthu
@PqapTheOnly-r2p
@PqapTheOnly-r2p 2 месяца назад
6
@chisalebeston
@chisalebeston 7 месяцев назад
I like you Sam a historian
@raymondchautsi6282
@raymondchautsi6282 7 месяцев назад
Nde Pano sakuyankhula ndizopusa zomwe akupanga achakwelazi??🙄
@mariamhassan4089
@mariamhassan4089 7 месяцев назад
Tadziwa nao
@SérgioFernandoKangombe
@SérgioFernandoKangombe 2 месяца назад
Uyu anali munthu oipa kwambili ndipo kufa kwa bingu amadziwako kanthu
@isaacdemba2401
@isaacdemba2401 7 месяцев назад
Umangoyamba nkhani ukudziwa kuti suyimaliza nanga chomabisira mayina ndichani?
@JanetJamesMachila
@JanetJamesMachila 7 месяцев назад
Lucius banda dyera amafuna bazi koma anaona kuti bingu anali dolo sanamupatse 😂😂palibenso president angazafanane ndi bingu 😢😢alucius nanga lero muli kuti dziko lili pa moto ili
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 месяца назад
The woman probably was Calista as all these were parliamentarians. Not so ?
@robertmakupe2863
@robertmakupe2863 7 месяцев назад
Ase iwe ukumutama galu uyu alikuti luciac freedom fighter wakunyumba kwako tu
@AndrewChasweka
@AndrewChasweka 7 месяцев назад
Komanso ngat kumalawi kuli andale osadziwa chomwe akupanga one of them ndi Lucius
@MacloudKasawala
@MacloudKasawala 7 месяцев назад
Amanena bingu emweyo
@JasperKaleni-dx6nn
@JasperKaleni-dx6nn 7 месяцев назад
😂sam iwe umandiwaza 😊
@BornMandala-rz1dk
@BornMandala-rz1dk 7 месяцев назад
Ndisiyileni kanga nyimbo ija imanena Bingu😊
@ChifundoSikelo
@ChifundoSikelo 7 месяцев назад
Amanena bingu kuti watani?
@patricgama4788
@patricgama4788 7 месяцев назад
bingu anapotsa kamuzu muzochitika pa 7eyes yake ndiye mungama fanidze ndi galu yo lus
@JessicaChabwera
@JessicaChabwera 6 месяцев назад
Ndipo ameneyu anamunyoza bingu kwabasi pano akukanika kuyankhula mmene anthu akuvutikila
@websterkausiwa8919
@websterkausiwa8919 7 месяцев назад
Nawesotu nyimbo zachamwiniyoo usamangochaputaa ndiza Tygrin zoo
@HenryChunga
@HenryChunga 6 месяцев назад
Soja wa mphawi , speaking on behalf of the poor masses
@ErnestKanthiti
@ErnestKanthiti 7 месяцев назад
Ine zambiri ai guys ngati mukuidziwa kanyimbo kameveka kumapeto koo ndiuzeni kuti anayimba ndindani chonde
@sammalvitha
@sammalvitha 7 месяцев назад
Search nyimbo ya Sam Malvitha youtube chanel... muipedza ...pa youtube pomwepa boss Anaomba ndi Yb Africa ndi Kikey Malawi
@WisdomKmsiska
@WisdomKmsiska 3 месяца назад
Anapangitsa kuti mnyenyembe afe si uyu mkumutama apayi?
@MphatsoSoko-p3l
@MphatsoSoko-p3l 2 месяца назад
Mavicha kape waboza iwe wasowa zokamba
@MoosahMtambo
@MoosahMtambo 2 месяца назад
Tilibe any suggetion tell us please
@LouisJamali-z7v
@LouisJamali-z7v 2 месяца назад
Bola Bikili muluzi t.v.
@chauncychauncy1683
@chauncychauncy1683 7 месяцев назад
Uztchula Maina iwe ase aah ukuopa chan
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc 7 месяцев назад
Alucias inu ndinu achitsilu inu mulibe nzeru
@KalipentalaFred
@KalipentalaFred 3 месяца назад
Dorangoni wilison
@PatrickIman-n2u
@PatrickIman-n2u Месяц назад
Fantastic . Big up!!
@HestingsChapola
@HestingsChapola 6 месяцев назад
Mumatiuza zomwe sitimaziwa bwana mupitilize
@MORESSRAJABOCINGANO-rz1lt
@MORESSRAJABOCINGANO-rz1lt 3 месяца назад
I'm sorry forget you
@mayesohenry
@mayesohenry 3 месяца назад
Which freedom has he fought ?
@livisonchinsamba5655
@livisonchinsamba5655 2 месяца назад
Anali SOJA wa amphawi
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 7 месяцев назад
That's why Lucious Banda panopa sakuyimba nyimbo zolongosoka,, mmbuyomu album yonse imakhala nyimbo zonena Bingu yekhayekha
@loidchikoti9338
@loidchikoti9338 6 месяцев назад
Abodza inu munene kuti inuyo mzanu ndi bingu osati bandayo
@AshrafuKalimula
@AshrafuKalimula 6 месяцев назад
Tay green aise
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 7 месяцев назад
Ndepano lucius banda wanuyo sanagudwe ndi ndalama?
@WilliesMasanjala
@WilliesMasanjala Месяц назад
Umakwana brother
@yamikanifischer
@yamikanifischer 7 месяцев назад
If he is strong why now
@ChiwalePhade
@ChiwalePhade 3 месяца назад
Tsoja wampaw
@DamianoEdward
@DamianoEdward 7 месяцев назад
Soja ndi soja basi
@beardmakwale-r8n
@beardmakwale-r8n 3 месяца назад
Sam mavita kapenso
@MemoryTambula
@MemoryTambula 2 месяца назад
Rest well soldier
@FrancisMusonda-h7p
@FrancisMusonda-h7p 3 месяца назад
Sir Paul banda is alive
@alexnyirenda123
@alexnyirenda123 3 месяца назад
Imfa ya Munyenyembe imandiwawa
@HarrisskudzaiLimula
@HarrisskudzaiLimula Месяц назад
Nice
@Daneck-rm1gg
@Daneck-rm1gg 3 месяца назад
Rest in peace
@JonathanHenry-e9e
@JonathanHenry-e9e 2 месяца назад
Mumakwana inuyo
@MussaHassani-zg1hm
@MussaHassani-zg1hm 2 месяца назад
Thanks Good 👍
@DoricaMzeweza
@DoricaMzeweza 7 месяцев назад
I like some navter go ahead
@brendaMkandawire-n2m
@brendaMkandawire-n2m 2 месяца назад
I like
@al-sudigang3299
@al-sudigang3299 3 месяца назад
Rip
@HenlyTiyesi
@HenlyTiyesi 4 месяца назад
Muli
@FRIDAYBANDA-m8i
@FRIDAYBANDA-m8i 2 месяца назад
Good
@Mphamdala
@Mphamdala 7 месяцев назад
Kachunyau kunena nyau king?
@sammalvitha
@sammalvitha 7 месяцев назад
Kkkkkkkk
@EdinahPhiri-z5o
@EdinahPhiri-z5o 7 месяцев назад
Amati yimilira wulemu wawo
@MusaKim-l3s
@MusaKim-l3s 2 месяца назад
G up
@FrancisMusonda-h7p
@FrancisMusonda-h7p 3 месяца назад
Paul banda alipo
Далее
Катаю тележки  🛒
08:48
Просмотров 615 тыс.
Grace chinga analosera kale Za Tonse alliance
10:49
Просмотров 8 тыс.
born kalindo was lero pa 1 October 2024
18:10
Просмотров 2,1 тыс.
Oimba omwe ananyozapo Bushiri
13:06
Просмотров 498 тыс.
The life of Livingston Kasozi living with Aids
16:04
Просмотров 37 тыс.
Peter Nsauka-Tribute to Lucius Banda-# tidzakusowa
4:12
CRUISE 5 WITH THOMAS CHENKHUMBA CHIBADE
47:02
Просмотров 235 тыс.