Тёмный

EXCLUSIVE INTERVIEW: Kucheza ndi Mr Norman Chisale 

Malawi News Update
Подписаться 37 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 28   
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 4 месяца назад
Am so touched, yooooh kmanso sakuopyedza km mtima kuwawa
@samuelsergio5343
@samuelsergio5343 4 месяца назад
Inuyo sister.tsiku lina athu adzakumenyani.simunaphuzire bwino za kafusidwe kazithu.
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 4 месяца назад
Kodi bwanji mukubweleza kutumiza bwanji panyapako
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 4 месяца назад
Chisale is right, Ineo I know Malawians better, timachulutsa bodza kwambiri, this is why situtukuka ndipo sitizatutuka mpakana kalekale ndipo tidzafa osauka.
@MakawaBenjamin
@MakawaBenjamin 4 месяца назад
Zomvesa chisoni kwambiri
@BrightMphamba-w8u
@BrightMphamba-w8u 4 месяца назад
Machine
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 4 месяца назад
Munthu wakulu kwambili 💪💪💪
@MakawaBenjamin
@MakawaBenjamin 4 месяца назад
Mr chisale mumakwana kwambiri
@AlihIbrahim-w6n
@AlihIbrahim-w6n 4 месяца назад
Jimmy izitu ndiye zopusa wanva,,,,Interview yakalekale iyi ukuyibweletsa leloso bwanji galu iwe eti
@YamikaniAmos
@YamikaniAmos 4 месяца назад
President adali chisale osati Peter
@phillipstamaley7901
@phillipstamaley7901 4 месяца назад
Koma mbuli iyiiii eshiiiii
@ishmaelbrighton9885
@ishmaelbrighton9885 4 месяца назад
Kod ma information wa akumakupezani mochedwa eti zithu zakale mukuyika lelo
@MakawaBenjamin
@MakawaBenjamin 4 месяца назад
Atonse alliance muzayankha pangapite nthawi
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 4 месяца назад
Zoona Chisale mtima utha kuwawa or ndi takhara ine
@StiveKantiki
@StiveKantiki 4 месяца назад
Muziti miseu akumbakumba ndi iti fusolo muzitelo aleyer
@tasmania527
@tasmania527 4 месяца назад
Wakuba uyu
@IssahFrank-j8z
@IssahFrank-j8z 4 месяца назад
Chisale
@KondieOne
@KondieOne 4 месяца назад
Bwanji osaika zatsopano bwanji
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 4 месяца назад
Zamphanvu
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 4 месяца назад
Munthu amagwira ntchito wagula zinthu zake nkumamufunsa kuti ndalama wazitenga kut??? aaaa aaaa ku Malawi amadana ndimunthu akalemera
@LukaThawe
@LukaThawe 4 месяца назад
Munthu ukulandira 50 pin ndiye ugule ndege sakufufuzakumeneko Kuti ndalama wachokanazo Kuti
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 4 месяца назад
mwasowa zochita pa zodiak kd zakale idzi
@MimuOmar
@MimuOmar 4 месяца назад
Only God Knows
@MimuOmar
@MimuOmar 4 месяца назад
Aaaaaa nde kokagula zinthuko mpaka secret code ya president? aaa kunalidi zibwana
@LukaThawe
@LukaThawe 4 месяца назад
Wakuba uyu galu wachabechabe
@Billi5
@Billi5 4 месяца назад
Ndiwe kape
@JerryChain-cz8ru
@JerryChain-cz8ru 4 месяца назад
Bwanji ukuyika zinthu zakale ukuziwakuti ndi data kuwonongayi🙄
Далее
Interview ndi Norman Chisale
1:05:22
Просмотров 250 тыс.