I am a Catholic, when God sets rules,He does so out of Love, not out of hatred. Catholic rule on LGBTQ was not segregative, it was so to uphold and protect God's law on marriage. Now Catholic move to bless LGBTQ is daring God, that what you don't consider worthy,we can consider worthy. This is pride of the church. Kodi munthu angakhale wachifundo zedi kuposa Mulungu, to the extent of blessing the devil? Catholic church and its leadership thinks it's not doing enough on mercy, and thinks can do it enough by blessing the devil.
God's message to all sinners is repent, change your ways and be a new person by building new character. Isn't this a blessing to all of us? This blessing is not enough for LGBTQ people and so they need special blessing from God Himself in this Catholic church????
LGBTQ community ili yokondwa ndi kalata ya Papa. Check their social platforms. You can't change someone by blessing them. You can only change nkhosa zotayika powaunikira za mau amulungu. Yesu amalora Aliyense even ochimwa koma amawaunikira mau amulungu then mkuwakhululukira machimo pamapeto pake mkuwauza kuti musakachimwenso.. Sindinamvepo yesu akudalitsa tchimo. Yesu samanyengelera tchimo amawauza anthu ochimwa kuti Ana anjoka inu. Fr. Nthalika please don't mislead people. I have been following you for many years. You have been my mentor spiritually. Chonde pempho langa musasocheletse anthu.
oh ok I understand that some people are being blocked from kingdom just simply we judge them... Jesus himself want all of us to be saved!! tiyeni tiwathandize anthu amathanyula kuti akalowe kumwamba osati powaweluza koma powaonesa chikondi chaMulungu
Ndinu anadi muuzimuuu. Kkk papa z playing games simukudziwaaa. Bible ili tatiyeni tidziliwerenga zenizeni. Papa knows what he is doing simwana. Mudzazindikira bwino patsogolo. Ubwino wake wayambapo akuonetsa mawangaa
Athu atopa kale ndizachakwera ndy inutso mukuima pa guwa kubweresa so nkhani ya bodza apa.... timakunkhulupirira ukamalalikira apa kumakusata ndy apatso wayamba kulalikira zabodza zoonatu eti 😢😢
The church must condemn all evil acts, ndiye bwanji lero church ikusonyeza kuti ena ndi machimo ndithu ena simachimo kwenikweni. This is where church has fallen short. If all were sins, and the church was blessing all sin actors, now why specifically blessing LGBTQ. Does this move mean previous messages of God's LOVE to them was unreachable? not effective? not enough?
Tipemphe inu atumiki athu...kumachita resist ziphunzitso zina zachilendo. St Paul anasutsana ndi St Peter ...ataona kuti zochita zake zikusemphana ndi zimene amalalika. Tizindikire kuti Pope Francis akuchita ma blunder ambiri. Panopa akuchita cancel ma conservative Bishops ndi a Nsembe. Ndikunama? Ma prophecies a Our Lady of Fatima ndi Akita...tawaiwala? Apa tinene zoona kuti the seat of St Peter, has been occupied by someone with questionable character.
The document specifies only homosexuals (same sex couples) what about single mothers? What about polygamous? What about those who sin in different ways? Why only same sex couples??? There is no blessing in the Catholic church without ritual - how will you be doing that?
Prior to this declaration, the Pope was presented with dubia from five Conservative Cardinals -regarding the direction of the Church. Nothing tangible came from the Pope. Unfortunately, he's been accommodating the views of pro-gay Priests, Bishops and Cardinals. Recently, he(the Pope) has been canceling Conservative Priests, Bishops and Cardinals. Is it not outright hypocrisy? I am not impressed.
Abambo mukunama nkhanizi ndiziwiri zosiyana. Mwavomerainuzo ndi za kusodomu ndi Gomorrah. Zisanzo zanu mzosamveka , musamaleni ndi matemberero mukuwaputao. Ndipo wagwadi katorika. Amwene wamkulu wa mpingo ndi Yesu osati papa. Musawasokerese anthu sianu ndi aMulungu musamale . You are missing the context of the passages that you are using from the Bible.
Munthu wamatanyula tsangabwerere ku munthu umene mulungu adamulenga nawo koma anthufe timatsiya uchilengedwe wabwinonu kupita ku matanyula. Plz tell ur papa he is wrong in this one do nt defend zinthu zolakwika ineyo ido follow u as munthu oyankhula chilungamo
Ndiye ngati mpingo umachita kale izi, umadalitsa kale anthu mosayang'ana zambiri, chifukwa chiyani kuchita kukwera pa chulu kulankhula zodalitsa same sex couples. Why too loud now?
A nsembe a f nthalika amenewo simulidziwa Bible inu tetezana udindo wanu koma nkhani ndi yoti you can't bless what God said it's sin shame on you and your leaders
Fr nthalika you are speaking as if you never got Bible training. Zomwe walankhula papa ndi ndale osati za usembe kapena chipulumutso. LGBTQ members alipo mu Catholic church, enaso ndi ansembe ena ndi ma nuns, ena lay people. Inuyo mukungolankhula mwamantha chabe ndi authority of Rome, kuti angakuchotseni or kukuimitsani unsembe, you are only following obedience oath, there is no Bible truth in your homily. Would you condemn Jesus Christ for what He told Samaritan woman? You are brain-washed kunyambita zili zonse zonena a zungu aku Rome, you are a Rome puppet.
Fr Nthalika stop preaching this nonsense of blessing amathanyula or risk loss of trust from many souls you lead to True God. Padziko lino pa ochimwa abwino. That's rubbish, be a man of brains and faith in God.